Ine palibe chapindu ndi wandale wa kumalawi palibe chikuwoneka zopusa bas mwina tidikile ufumu wa yehova bas azaweluza ndithu maufumu okubawa mwina anthu samadya mbewu
zachisoni chakwela misikhono yomaliza zachisoni achakwela dzikoli lavuta kulamula zavuta a zachisoni kulakhula komaliza basi sitidzaonaso abale koma tinawakonda kwambili koma Zachisoni zawavuta abale koma kukamala kosekunja koma dziko lavuta koma basi dzikozekani kunyumba ya chifumu basi ena akubwela
Ndmomwe mulili amalawi nde mukachoka pamenepo milomo mbuuuu nga mwapaka phulusa ili njala😢😢
Zovesa chisoni
Mwazindikila mochedwa nthawi yanu yatha bwana chakwera
5 years tchito kuwongola mafupa ndi kusunga black box kunyumba kwako chikangawa
😂😂😂😂😂😂 indeed chikangawa
DPP WOYEEEEDE❤❤❤❤❤❤❤ APM WOYEEEE❤❤❤
Chakwera ukupenga koma sukuziwa amene akukuombera Manjawo ndi agalu bolaso mbuzi
Mwachedwa bwana nduna zanu zaba for 4 years mukuwachotsa lero ? Mwaononga Malawi kwambiri.
Who will going to school on an empty stomach, people want food on the table
Anthu aku wateng pa truck 🚛🚛
Zimene munalonjeza si zimenezo bigman...tapangani zomwe munalonjeza mmaderamu!
Komaliza
Ndipo big simukunama...munthuyu ndi galu kwabasi!
Mmmm...koma anthu nkhope zikuoneka zoofuwa ndi njala komanso kusamba opanda sopo😂😂😂😂😂
Ndizisilu za anthu,Anthu ombwambwana
tikufuna brack box osati zopusazo akuvotera amako iwe
Kunali azimayi ndi ana okhaokhatu 😂😂😂
Apa simupalupha, you may lie & lie but the end has come bye 👋
Chakwera Stika, your time is up
Kuombera mmanja m'bwelerazi'??
Time
Stop abusing the people by making them attend useless rallies, big mouth
Ndiye akutchera zaka 5 osaona. Nduna uchotsa miyezi 6 yi. Zaka 4 kumangolengeza kuti ndichotsa kwatsala miyezi 6 muchotsa ndani. Za ziiiii
🔥 ndilomweli 🔥
La mako
Phwala la bambo ako Nd lomweli
Ya CCAP inatha...koma izi ndi nkhamba kamwa chabe
Uyuuu ND onama ndpo osafuna kunvomereza kulephera
Ine palibe chapindu ndi wandale wa kumalawi palibe chikuwoneka zopusa bas mwina tidikile ufumu wa yehova bas azaweluza ndithu maufumu okubawa mwina anthu samadya mbewu
Palibe zomwe wanyoza Peter Munthalika chomwe mungadziwe a President sayakhula zosakhala bwino
Kkkk Kodi misonganoyo izichitikila ku page house 😅😅😅
Koma pepani bwana nthawi ndiye yantha or muwachotse sangadandaule akudzitso kuti mwaluza kale zisankho ndiye musatinyase
Azimai afoyila zowonaa mulibe chakudwa nyumba mwanu kufuna 2000 😁 koma azimai akumalawi
Zauchisilu basi😂😂😂
Awuze makape
Anthu sakudy ali ndi njala
Aaaaa chakwera iwe nthawi yathatu tiye kuchikangawa kuja
Mr koongola mafupa. zithupya zinadya noofu kusala mafupa.ziliko Mr zithupya
Camera mn naye aaaaa kudula timafuna timuone mmene amanong'onezerana asa
zachisoni chakwela misikhono yomaliza zachisoni achakwela dzikoli lavuta kulamula zavuta a zachisoni kulakhula komaliza basi sitidzaonaso abale koma tinawakonda kwambili koma Zachisoni zawavuta abale koma kukamala kosekunja koma dziko lavuta koma basi dzikozekani kunyumba ya chifumu basi ena akubwela
Amalawi ena ngophusa kobasi achakwera anapha chilima ndi ena 8
Mr chikangawa mfiti
President wakulilongwe osat Malawi
Nthawi yonseyi munali kit tiyambila kuchosa inu bwana pa may pa mwalephela bas
Kwanu konko, seselekerani kwinako tione
Awawa kumango waone bans ndiowinawina
Anthu Dinu opepera
Onsewa ndi ombwambwana, makape
A chakwera ndiribe nanu vuto , amalawi amapanga munthu kukhala wanzeru or opanda mulibe vuto koma anthu kukugulitsani tikuwona , Malawi ukubalanji?
Anrhuwo ndiye akumvesa chisoni adya koma
Man wa ndiofoiladi
Kkkkk koma ndaseka
Uyu wabodza chakwera nthawi yonsei analikuti kodi xool m'mwenzi itatu yatsalai?
Zochosa nduna mukanayamba 2020
Anthu oipa mitima inu Muzakaphya kumwamba mukuzunza mizimu ya a Malawi pano
Zochotsa ndunazo ndiye mwachedwa nthawi yatha paja mukupitatu musaiwale achimwendo asamakunamizeni
Tsopano iwe nthawi yoseyi mwakhala muli pampando koma popanda chochitika mbalame iwe chitsilu cha munthu nthawi yako yatha.
Compassion imayamba before ntchito kuyambika mukufuna kuwabera anthu.
Pitani bwino
Ayende bwino makape, mbuzi za anthu
Palibe zovotera nkhalamba, boma ndilomweri sitikusintha
Amalawi kupusa 😢😢koma umbuli yaaaa
Chakwera mboleyake waononga dziko
Choka iwe pa.....
Komaliza Agide😂
Koma timafuna kurakhura chiringamo ngat chakwera Boma ndiromwer
Zala five
Chikalipo Binalisoni abwana mvomelezani kut mwayinu mulibe utsongoleli
Azimayii ndiomwe akuononga zikoli
Chakwera Wokupha
Chakwera wa TSANKHO
Chakwera wa mkhanza.
Kodi ukuzikakamiza utalephera bwanji, unatsegula wekha Ku kamwako Kuti utalephera kukwanirisa malonjezo udzatula pansi Udindo. Tsopano chikuvuta mchiyani.
MPHYODZA Magazi ndi Mikodzo.
Ngati sunaphe Tulisa Black Box
Omuvotera anthu akumuziwa
Nthawi yanu bwana yatha sakani Zina zochita mpaka rand 1 to mwk 220
Apule akunenepatu ndi ndalama zathu
Diwe wazelu koma wachedwa chakwela ubwele ku dpp chito ilipo
Bwana chakwela nduna yanu kunkuyu anaudza dziko kuti black box asunga pabwino tifunsileni kuti ili kuti , chifukwa boma likubwelalo liifuna
Koma chakwera sakuchoka Boma ndiromwer
Kumalawi kono palibe andinyatsa ngati chakwela
Zomvetsa chosoni Achakwela ziko lawakanika nthawi yakuthelani bas
Machende ako chakwera limodzi ndi nduna zako zosavinidwa MCP siingawinetso bola rastar chikomeni
Simuzawinanso
machende ake ameneyo
Ndipo iwe aise akuzichedwesa satana iwe Chakwela
You should have be ashamed your self when you spoke to Malawians who are sick and tired of this poor leadership.
Bwana mwazindikila mochedwa chifukwa nthawi yanu yantha
Wawona ntawi yatha ngati ozindikila zopusa basi
Ukamange ku kasiya kwanuko, mbolo yako chakwela, siya Kaye dzimenezo, kawone Kaye dzikuchitika ku lower shire. Mbolo yako ndi vice wakoyo..
Siwonse afika pansonkhanopotu kuti azamuvotela iye sizingatheke
Mmadikira zionongeke kae mmhhh anthu andale oipa bas nfundo zabwino zikuonesera mochedwa
Koma chakwera akufuna kukoza dziko ramaraw
Nose mukuti boma illoo mapwalanu pati
Chibwana chimenecho chata pamodzi ndiiwe
Apa mayakhula bwana congrats
Za ziii
Achitsiru awa
Kukwima kwambili achimwendo
Pali akufuna iwe
Ndinu munthu omvetsa chisoni pamodzi ndi azimai olukutawo, shame upon you
Boma ndilomweli
Koma bodza awa azasiya
Zopusa zen zen
Vote ndi mutima.tika voteraso MCP agogo gonani
Kkkkkk anthu sakuziwa enafe tinalembesa kale tifuna pa16 September satana azaziwe Chakwera sali yekha
Wabodza
Boma ndilomwero 😊
😭😭😭😭
Galu
nonsense thawi yakuthelani nthawi yake mukayipezela kut zamanyi bas
Boma ndi lomweri basi kulibe kusintha wansanje akabitsare
Ine sindinyengelela kape iweo panyoo pako Boma ndilomweli la mako? Mmene dziko lilimu ungamanene zompusa zakozi apapa gwape iwe? Za boma ndilomwezo mudzikawawuza achamanu dzisilu inu.
Kujiya ndinjala kusowa zochita