ZOKUTI NDI ABUSA AKUDZIWA NDI AKU LILONGWE~ LERO CHAKWERA WABWELA MOTO KUYANKHA KUKHAZULA DPP YONSE
HTML-код
- Опубликовано: 7 фев 2025
- Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika
HlS exllence professor Peter muthalika
The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2025 to 2030 wooooooo
Nonse okugwa zifufu chaka chake ndichino mukomzekele kugwa zenizeni .
Koma Mutu wakuvutani presdant ndiwina kind his excellency Wina mlibe or manyazi
Awuze presdent ndi APM osati chikangawa akumbuse mwina ayiwala makape
@@rashidadan2533 in your dreams
@RodrickLucious kkkk ndiye inu azifufukale muzangopitilila komko
even the president knows tym up
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Koma anthuwa ndi mbulidi. 2019 DPP Naye zimakhalanso chonchi. Nthawi yawo yatha awa. Mudziphunzirapo pa zomwe zinachitika Kwa mnzanu. 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Kunyikatu uku.
Mukumunyoza pitter Inu ndi ana kwambri pitter muthalika my vote ❤
MCP yatizunza kwakwana
Ife go Kwa DPP basi iya
Ndipo watidzunza tatopa nadzo idzi. 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 even njoka yikamafa silephera kuphuphako 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@@RexMbewe-y5j mmmmmm ingosiyani zomwe mukulakhulazo ndizopanda mutu
1. No fuel
2. No drugs
3. No forex
4. No servant leadership
5. Very high cost of living
6. High inflation
7. No funding in district councils
8. To much false promises
Boma ndi lomweli💔
Apm my vote DPP 2025 boma
Kuphupha kumeneko muzipita kukasiyae
Eya kaya kuphupha
Anthu oyipa inu kumpha zanu chifukwa cha udindo zaziiiii
Kulibeko chazelu kumalawi uko dpp my vote
Chimwendo muzeni chilungamo chakwela
Apm pa 16 September pano bomba
Mwachepa nazo kwambli Peter my vote
Kumaliza kuonera msonkhano wa Chakwera ndiukape ndipo sindikwanitsa MCP pack and go!!! Chilima ndionse munawapha aja akuzunzani munya RIP Saulos Chilima
Koma DPP Ndiye simukumagona nayo tulotu esh
Akupumira mkwapa😢
Koma ndiye akuchita kulimbana nayo ngati kuti chipani chotsutsa ndi dpp yokhayo 😂😂😂😂😂
Ndimene ikuwamvetsa kupweteka panopa ndichifukwa nthawi zonse amangoti APM, APM ndi mahule awo achina jessy.
Mwana akulira ndinkodzo wake omweee
Achedwa awa!!! Nthawi yawathera kale
Iwe usamunamize nzakoyo muuuze chilungamo km kt even tomato m'modzi wafka pa 1000.
Ndalama zachitukuko ndiza amalawi siza Chakwera. Munalola bwanji chikangawa. Apolisi azi kwange. Ife toto.
APM my vote chikangawa time is over
Time up MCP
Chakwela unaphelanji chilima
APM mpulumusi wanthu kkkk n my vote 🎉
Pa group zero , fertilizer 135 pin , sugar 3500, nima 750 chimanga 1600 per kg
Koma abale kumalawi kuno kwavuta athu ambili Ali mululu wanjala kobasi eee koma chakwela akulimbana ndi fundo yasukulu anthu sanadye awa
Uchisilu weni×2 malembo congress party makape okhaokha
Ulindi ntchito Chimwendo sunati 😂😂😂😂😂
Bwana musaiwale soya p. Wakwela ntengo😢
RIP skc Chikangawa yatikwana
Chimwendo akulira lero ma vote tisanaponye, mwati pa 20 September tikamakalumbilitsa Kabambe kukhala state president awa sadzamwalira ndi BP?😂
Apule anumber 6 zero kwa zero inu ndeeee kaya
Achitsilu awa, mwazidziwa litiro chakwela mwaba ndalama za mbili za amalawi 😊😊😊
Dpp my vote
Can't you see the nervousness 😂😂😂😂😂😂😂
Apure,,, nthawi ija mumalolera angakhale mvula ikugwa mmati amalawi ndili nanu pamozi ndipo simumathawa koma pano mukuti malingana ndi nyengo iyi mvula ikhoza kubwera mupange changu changu,,,ayi chabwino madala koma chilungamo chache nchoti inuyo simmayenera kuyimaso simutha zisiyeni bas zomwe mwapezapo ndizomwezo,,,,mapwara anu
Abakha okhaokha awa palibe chadzeru apa tamavomelezani kut munabwela boma kuzaba kuzaononga Malawi wabwino uja
Ayi mukwiye musakwiye chakwela sakufunika chakachino tikufuna dpp mukukwiya ndizanu komamukuchoka chakachino mukunamizana
Chakwela wawonjeza mukuchoka inuathu kumupoto kumwela pakati isanje tu chitipa akufuna dpp chakwela ayi
Kodi opposition party ndi DPP bas??? Anyamata a MCP bodza sikuthandizani.
Chimweñdo ukukumpusisanitu A Chakweratu apule mukupeperatu
Kuwiwna mcp nkhondo tikwapulana coz muzabera sitldzalora
Kuzuzika ndi mtima ,jxt pack & go
Ndalama yonseyo musaiwale ndi misonkho yathu ,ndizomwe tinamulembela chakwela ntchito , bweletsani mfundo osamalimbana ndi muthalika , Nanga zikwanje zija ?
Vuto apule mukunvera chimwendo ,munyera 6 months yomweyi mpaka kuchosa nduna shame
Koma chimwendo ndi opsesya mtima srs 😢😢😢
Chakwera ngati nsete kuchemelera galuyo
Simungachotse mcp inu zilichimodzimodzi kumalota uli ndalama nthumba koma podzuka umawona ulibe ndalama zinzachitika ndinu adpp pa17 mudzadzimuka kutulo boma atatenga chakwela mudzadzipha enanu ndithu kapena mudzathawa dzikomuno ndithu
Kkkkk😂😂😂😂😂 garu ndi garu basi 😂😂😂😂😂😂tym Up 🎉
Kumeneko ndi kulira kwa mcp pachintumbo pa kamuzu
koma amarawi umburi ukukuvutani kwambili basi yoooo zazii zinthu zadura basi nyoooo kupusa chifukwa cha 2000 kwacha koma amarawi umburi
Tamuonereni Akumvetsela zopusazo.Anthu amadya ambulance mankhwala kuchipatala chake chakwanu. Komadi DPP simukugona nayo
2025 APM Bomaaaaaaaa
Only the almighty God knows
Achimwendo ndiwe ukupangisa pule wanthu azikhala oipa chigukwa chamalankhulidwe anu ndi booza limenelo umanamiza pulezident msiyeni mchitidwe otenga anthu uku ndi uko kumanena taona mmene anthu awa kuchuluka chonde
Chisiru cha president
Muthalika akubwera September makape a musipi mudzipit mmakwanu
Koma iwe chimwendo zomwe.ukubweketukazo ndizoona kapenainu ndi anthu aja mukumamunamiza chakwera kuti zilibwino koma mukuliona dzikoli lomwe likupita. Muyenera kitamandira chifukwa Inu muli kudziko Lina Malawi Ambuye akuthandizeni
Bodza mcp sinzawinanso muno mw chimwendo usamunamize chakwera
Achmwendo tini lachmanga 26000 ku karonga
Nyau zose kudambwe muzikadzolaso matope zitsilu ndi azimai anu aja akwaswundwe osavala mapanti matako fumbi phaaaa kuti ai atigwililila aaaaaaaaaaa
DPP idapitadi ndizovutadi kubwereranso BOMA
Bwana chakwela chakachino mukuchokamuboma tatopananu
Zimene akukamba achilundi ndiza opposite
Panyeropako chimwendo mfiti iwe 50kg ya chimanga ilibwanji?
mcp, ituluka or mutavota banja lako lose chimwendo
The last kick of a dying horse
Boma ndilomweli mwauponda amalawi mudzawadziwa pa september
BG up
Sizingatheke kut tonse tikomele mbali imoz koma na ine APM vote yanga basi
Amcp zigawenga za dziko la Malawi be careful mdzamangidwa agulugunyinda inu ntchito yanu nkumanga anthu basi
Kkkkk km muthu ukamafa mumayambad ndi mkutu mcp yatha bs 2025
Inutu olo munyoze peter dzwani wakut akulowaso mboma km zoti mudzabelaso mavote iwalani mwazunza mtundu wamalawi kwakwana kuvomeleza ndkwabwno ,,palbe chanzeru chomwe munganeneso apa moti mudzilimbana kuthesa njala ,,kut katundu atsike km busy kunyozana agalu inuu president anali bigu bas zaziiii
zikolino achakwela mwana kwakwana kapimene muline madaliso mwangobwelesa minyama zikomuno kungobwelesa ufiti basi kupha ndikuba zopanda zelu anyapapi
Kukasiya kwawo ,koma konvesa chisoni ,bamk kulibe, shame apule 😂😂😂
Athuamene mulinaeo pamusikhano wanuwo 100peleset ndi adpp angofuna kudyananu
mesa akuti amawongola mafupa iwe ukuti zikuyenda bwino katundu wakwera mtengo ziwawa mumachita ndinu nomwe
Apm 2025 bomaaas
Chilima anali ndani fokofo munya
Koma ndale Ayi zikomo Malawi ali pa moto kwambiri kamba ka atsogoleri ofoyira wa
Aaa takagwerani ukoooooooo
Atopa akulu akulu awa tsopano amtaba koma muzelekezeka
Ndizawonana pa 16 September apa mukanankhara muzichosera masiku
Ndinyoza kwinako 😞
Pulezident kulakhula bwino kwambiri anthuwa ndiamene amachedwesa zinthu
Ifeyo timaonanga ndikusokhano Kani ndikumalilo tamvatokha kuti mpasiwa nanga pasiwapo sindekuti mkumalilo mmmmm ayi mwafadi 2025
chimwendo umayankhula ngati ukuyankhula ndi ana mafumu ukunenawo zili mumtima
Ofoyila ndiweyo
Ukamakamba za dpp umandikanda pachilonda chosapola,chonde chonde usadzakambeso ngati umakumbukira
Chakwera and chimwendo mbolozanu anthu akuvutika ndi njala mudzimu inu kumayakhura mwatuz
Boma illoooo kkkkkk laza my vote
Ndipo ndikuona kuchedwa kuti tikavote zindinyasa iye amenei aaaaaaaaaaaa akanaziwa zili manganizo awanthu aaaaaa chimanga pano thumba 100000 zooona fetelezar 140000 anena zooona amenei ndimunthu koma
km nthawi yanu yathaa bas ife nde tatopa nanu inu aaaah
Achimwendo ndinu anthu oipa kwambili wakuthandizani uyu kazombo lero mukufuna kumutenga ngati munthu oipa lero
Zukuvutani mcp basi
Achimwendo zipatara makhwara Ake Ali kut. Inu boza len Len kma ife ndiye tathana nanu
Msonkhano wa MCP mukuyankhula za Dpp why mantha MCP Chikangawa
Munthu wamoyo kuvotera APM?
Chakwera wamuona mwana wake kuti uyu ndiye akuonjezera kuwanamiza amalawi.komanso anayamba nkhani ya mseu wa m1 koma kumene yathera ngati ndayimva bwino bwino ngati
Kkkkk wayithawa
Mene ikubwela kwachami ? Mboli Yako chimwendo
Otsogoleri opha anthu. Ife takugomerani ndi ngozi ya chikangawa yotochita hire anthu
Kupanga manyaxi chinkhumba iwe
Ndie iweyo ungamenye ndani
Abale abale abale antaba ma lubino aja mwadya mukadyelaso kumeneko yanu ija kkkkkk dpp2025 to 2030 mcp paulendo paulendo paulendo paulendo ungoti gula fodya mokuba chaka chino udzapeza ma voti okwana5 koma ukagula bwino mavote uzapeza mwina okwana 55 dpp izapeza 1000000v
Ya Allah pls take out this filthy leadership on the throne....and give us the knowledged leader