Welcome Dr George Thupuwela Chaponda as leader of opposition. Your opposition leadership reminds me of the old good days of Mbuya Gwanda Chakuamba as leader of opposition in Malawi. Kudos and bravo to your team Dr George Thupuwela Chaponda otherwise we have wasted good 4 yrs of opposition duties under Kondwani Nakhumwa (from 2020-2024). The past 4 yrs was just useless and waste of time. God bless malawi and God bless the leadership of opposition in malawi.
Mwachepa , MCP is a very big party. Munachipeza chipani cha MCP ndipo muzachisiya chili even stronger. Inu muzingokhalira kulongolola ngati ntchentche zikusangalalira manyi.
We can confirm Kuti Kondwani uja watitayisa thawi Kwambiri. Kususa kwake kukanakhala ngati Kumeneku zinthu i hope zinthu zikuyenda bwino kwambiri and Malawi sakanaonongeka ngati m'mene waonongekelamu. Komano MCP they make mistake kumuhonga Kondwani kuti asamawasuse koma azingopanga zinthu m'mene angathele and the end zawagwesa m'mavuto and the result no more kulamulila they are finish!!!!!!
Andale nonse zanu ndizimodzi. Panopa kwakucherani mdziputsitsa amalawi. Nonsenu simukonda dziko lino. You are just power hungrily. Mkavoteredwa basi anthufe mwatisiya. Nonsenu ndinu akapsyala. Panopa ndipo mwaona ubwino wa Chilima ndi UTM?
Exactly this is their own problem ukukudi kuyake Moto, they are taking us for granted, ku trip kopita president koma akumachita kutenga gulu for what and which Money are you using kukusa anthu onsewo wokakwela ndege, for what, and what will some of the people going to do there,,this is unacceptable they can't embazzle our Money Infront of our nose, Enough is Enough
Alone gadama...dicki matenje...twaibu sangala ...achiwanga... Sadiki Miya... Albert muwalo.. Alani witika .. saulos chilima.. and 8 others...my question is..how many people did MCP killed all together?? chakwela what is your problem??😭😭😭😭😭
Anthu angapo takhala tikudandaula nkhani ya ka sound kamamveka pansipo koma simumatimvera bwanji??munanena kut mwamva koma mpamene mwaonjezera volume,,,why?!
Yes English ndiyofunika komabe nkhani ngati izi tamayankhulaniko chichewa kuti a Malawi osamva kuti mcp ikuononga zinthu azimvako. (2) inu a DPP chinakuvutani ndichani kumuika handsome, wise guy, wachinyamata ngati Suleman kukhala president and opposition leader? Achapondawo kulankhula kukuvuta plus satha mahawu mu parliament muja,, bolanso anavitcha aja 😂 apapa a Peter Muntharika muganizepo bobo to change your opposition mupereke kwa mkaladiyu. Namalombwa umakonda kuyankhula mokuba kuti udzikondedwa munchipani komanso mupangane support anthunu kuti mugwetse mcp kuti mzima wa Chilima udzause mumtendere. Suleman for president ❤❤❤
I would like anthu monga hon :suleman,jean ansah,Mr kaluwa kuti akhale ndi ma udindo akalu akulu ku DPP party I hope anthu ngati awa they can change life of malawians including Mr president author Peter wamutharika and hon :namomba ndi anthu olimba mtima kuteteza life and situations of poor malawians anthu monga ine omwe tili kumudzi
Chakwera kuyendayenda ndi m'mene ziriri kumlw sikoyenera But I don't blame him coz he do knw what he's doing and he is the state president without knowing the meaning 😢😢😢
Guys truly iyiii nde opposition yamangana guys kuli mphangala zoziwa zinthu ku opposition ukuu guys awaa aaa MCP achoke basi let's go pansewu atikwana .ku mcp kulibe amene aziwa zinthu basi apule basi tikukoza zinthu
Welcome Dr George Thupuwela Chaponda as leader of opposition. Your opposition leadership reminds me of the old good days of Mbuya Gwanda Chakuamba as leader of opposition in Malawi. Kudos and bravo to your team Dr George Thupuwela Chaponda otherwise we have wasted good 4 yrs of opposition duties under Kondwani Nakhumwa (from 2020-2024). The past 4 yrs was just useless and waste of time. God bless malawi and God bless the leadership of opposition in malawi.
I agree with mmwenyeyo wa BT ku 2025 kwatalika kwambiri anthuwa achoke basi atikwana chisankhoso chisakhaleko ayi chifkwa aluza kale
Yomweyo a DPP apa mukubwera boo
2025 kwatalika adzipita dzikoli litha ngati ma curtains
I agree with Sameer Suleman this Manyaka Government ( Mcp) must go we are tired of this nonsense 4sec Chikangawa
Mwachepa , MCP is a very big party. Munachipeza chipani cha MCP ndipo muzachisiya chili even stronger. Inu muzingokhalira kulongolola ngati ntchentche zikusangalalira manyi.
@@tasmania527chikangawa oyeeeee😂
Ambuye alemekezeke kuti sopano tili ndi opposition ku parliament, hopefully zinthu zisintha sopano,,wow!!!am very happy for that
Llg meet😮 hi bed x BBC l
😅
Jinx😅v😊
V😮😢 job
L
🎉
😅
Lv😮bh.ln.😅
Am happy for u all guys this is what we call patriotic leadership 💪💪💪
Amene amapangisa kuti opposition ikhale yofooka anali nankhumwa uja chifukwa anali mnthira kuwiri
Good message guys Chakwela you mast go watikwana
❤❤ God is good bolako tili ndi anthu akutiyimilira a DPP musatope and musasiyile pa njila god bless you all
Nkhani yabwino ma MPS athu, tonse tikhala pansewu mademo basi.
Fire fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 mademo achitidwe ndipo chikangawa aona polekela
Much appreciate to the leader of opposition
Sammeeir sagawa masiwiti
Uyu ndamuziwa mochedwa 😂😂😂 alibwino kwabasi nasaaa
Ndipo mr samy ndi one ndipo amaimilira amalawi
Ndipo Man osatekeseka
Anthu akufunika ku Malawi kuno nd amenewa
Very powerful man
DPP congratulations apa ndiye mukuonetsa kuimila a malawi
Ndipo apitilize a DPP adziwe kuti dzikoli ndi la a Malawi si la achewa okha ayi
Palibe Za kuyimila amalawi DPP chipani choipa kwambiri
Zako zmenezo 🥱🥱@@LukaThawe
Zikatele mademo ali pafupi ❤❤❤
Chikangawa he must go
We can confirm Kuti Kondwani uja watitayisa thawi Kwambiri. Kususa kwake kukanakhala ngati Kumeneku zinthu i hope zinthu zikuyenda bwino kwambiri and Malawi sakanaonongeka ngati m'mene waonongekelamu. Komano MCP they make mistake kumuhonga Kondwani kuti asamawasuse koma azingopanga zinthu m'mene angathele and the end zawagwesa m'mavuto and the result no more kulamulila they are finish!!!!!!
100%❤❤
Thanks our readers these are the checks and balances we craved for... keep up the pressure
Nanu pangani mademo mesa nawo analowela mademo omweo aaaaaa
2025 is far guys duleni ma battery mr chikangawa yooo 😂😂😂😂
Tiyeni kumademo. Chakwera asatuluke kupita ku China.
Mr chaponda job well done, siza Nankhumwa zija ayii
Refreshing to see the opposition at play follow through on issues to logical conclusions. Checks and balances is your duty. #Malawi 🇲🇼
Well my mam grace l loves u my sweetheart my vote is you all my family
Sulemani ndi zungu musaiwale zungu amanena chilungamo koma bodza amadananalo. Ndibwino kuvomeleza kulakwa kenako anthu amakukhululukila. Well done Mr Sulemani, DPP my Vote ❤
Nice one thanks so much keep it up please
Dpp my vote ❤
Keep it up ma honorable ❤❤❤❤ this is what we called opposition
Andale nonse zanu ndizimodzi. Panopa kwakucherani mdziputsitsa amalawi. Nonsenu simukonda dziko lino. You are just power hungrily. Mkavoteredwa basi anthufe mwatisiya. Nonsenu ndinu akapsyala. Panopa ndipo mwaona ubwino wa Chilima ndi UTM?
Powerful Powerful Powerful mgwilizano❤❤❤❤
We need report out,,,,
I love you mama grace kwelepeta am your child from jokala tc Zomba
Now we know that there is an opposition....thanks to all opposition parties present here❤❤
More 🔥🔥 DPP kumeneko ndiye kuzuka your only hope for Malawian 💃💃💃
Game changer,ndipamene pati paonekele khoswe pa sindwi.Opposition timayembekezela koma imeneyi.
Pamademopo pali bwino 😊😊izi zikuchitikazi zopusa srs
Ku dpp kuli ma shashanso kani,,keep it up zawavuta a MCP
😂😂😂😂❤
AmasingorA joker kkkkkk🔥
Let the government know that as citizens we will not sit while they are abusing our patience. we will go in the streets till the recind
💪💪💪
Kukanika kutulusa LIPOTI LA NDEGE 😂😂😂... Afiti 😅
Kodi zikuvuta pati kunena chilungamo,kaya ndizaboza anthu adziwe choona
Simunamve kuti report atulutsa ndi aku germany?
Athu akuziwa kale chilungamo kodi muthu akakhala mfiti amavomera?kuma voti basi next year
@@dilmayankam4052 Kwatalika amwene tiyeni tivote next month
Sure Sulyman
In politics nothing happen by accident... when is happening... just know that it is well planned by the way..
Exactly this is their own problem ukukudi kuyake Moto, they are taking us for granted, ku trip kopita president koma akumachita kutenga gulu for what and which Money are you using kukusa anthu onsewo wokakwela ndege, for what, and what will some of the people going to do there,,this is unacceptable they can't embazzle our Money Infront of our nose, Enough is Enough
Apm my vote
Akuziwa kuti chilungamo chinaziweka kare kuti anachita kupha anthuwo nanga akurephera kubwere poyera bwanji anthu amatopa ndiye ndatopa
Am in support of Suleiman the guy is saying the truth enough is enough
Waiting allowance for UTM And Dpp 🥳🥳🥳🥳
Fire up my mpe
Achakwera ndi munthu ouma mtima alibe chifundo ndi umphawi womwe amalawi akukumana nawo
Nchifukwa chake Tembo adamusankha.adamuona kuti ndi oipa mtima.alibe chifundo ndi munthu.akungoyenda opanda chomwe akubwera nacho.
@@Dauson-j5i U President wu anawutengera mphuzo. Sanatengere kuti a thandize Amayi ayi. Mbuzi ya ku Kasiya
Carry on guys
Ndiye tamuoneni chilima pa mbalipo😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 handsome guy
Anaphela njilu
Ndipo kuvetsa chisoni
Alone gadama...dicki matenje...twaibu sangala ...achiwanga... Sadiki Miya... Albert muwalo.. Alani witika .. saulos chilima.. and 8 others...my question is..how many people did MCP killed all together?? chakwela what is your problem??😭😭😭😭😭
Keep the fire burning Suleyman, 2025 kwatalikadi, tiyeni tiwachotse m'boma asatanawa before 2025,
Meaningful conference
We really needed this kind of opposition earlier on
kondwani Nakhumwa watichedwesa 😢
Kodwani Nankhumwa uja Mulungu amukhululukire chifukwa amanga chija sichilungamo 😢😢😢
Anthu angapo takhala tikudandaula nkhani ya ka sound kamamveka pansipo koma simumatimvera bwanji??munanena kut mwamva koma mpamene mwaonjezera volume,,,why?!
😅😅ndpo inuuu
Akuna mxiwe kt payima ophunzira😂
Kakutopetsa hvy
Good move let's fight together
Chakwela... silent killer... manipulator... A man with flowery speech without action is called... chakwela...Mr chikangawa
Yes English ndiyofunika komabe nkhani ngati izi tamayankhulaniko chichewa kuti a Malawi osamva kuti mcp ikuononga zinthu azimvako. (2) inu a DPP chinakuvutani ndichani kumuika handsome, wise guy, wachinyamata ngati Suleman kukhala president and opposition leader? Achapondawo kulankhula kukuvuta plus satha mahawu mu parliament muja,, bolanso anavitcha aja 😂 apapa a Peter Muntharika muganizepo bobo to change your opposition mupereke kwa mkaladiyu. Namalombwa umakonda kuyankhula mokuba kuti udzikondedwa munchipani komanso mupangane support anthunu kuti mugwetse mcp kuti mzima wa Chilima udzause mumtendere. Suleman for president ❤❤❤
Nice
Chichewa chikifunika, ife sitikumva
Zoona
Im agree with Sameer 2025 its too far so what is next step we need that ma demo
Congratulations DPP, UTM and AFORD now we can confirm that us Malawians we have strong Opposition in Parliament.
Kodi akuyendetsa dziko ngati farm yake bwanji hahahahaha you beta resign Mr Pule
This is a good opposition not that time mumangomenyana nokha nokha muja.... Apa nde mwayamba zantchito keep it up
Powerfull mesage
Ndipo ku china akukapangako chani chitsiru ameneyu mutu wopanda zeruwo
Congratulations 🎉
The plan that you used to kill chilima was not mature.. that's why we all know what you did
Amwene please tiyen tipange mademo.koma apapa ndiye chaponda ayi takunyadiran zedi osusa, pitilizan kuimira amalawi osauka.
Chakwela wapha chilima ujha chifukwa Cha udindo 😢
Ankayesa zida waonekera poyera Mr Chikangawa ayalulepo watitopetsa atitha mfiti m'busa wakupha chisatana chanyanga
Yes please zigawenga izi za mcp zisowe basi
Powerful 💪💪
l can't wait chakwera you can go
I would like anthu monga hon :suleman,jean ansah,Mr kaluwa kuti akhale ndi ma udindo akalu akulu ku DPP party I hope anthu ngati awa they can change life of malawians including Mr president author Peter wamutharika and hon :namomba ndi anthu olimba mtima kuteteza life and situations of poor malawians anthu monga ine omwe tili kumudzi
Mr Chikangawa Bola akanapanda kubadwa
Ya asilikaliyo to DRC......ndi fuel from DRC yabaya koopsa
Ooh allah protect and guide all leaders how stand with Malawian peoples 🇲🇼🤲
Madem akhalepo akuzolowela asatanic amenewa
Salaimana is the best fighter
we had a dead opposition..for 4yrs....thumbs up akamuna inu
Chi Nankhumwa uja ndamene amawononga dziko,lero mcp yakumana ndi opposition leader yeni yeni
I'm here for suleman
Sitikusewela kumene 💪💪💪
From the contradiction made by the president and Kunkuyu even if they don't release it ,i have just used my 99 about what is really there
Kho anatichedwetsa awa nde anthu viva opposition leader
Chakwera kuyendayenda ndi m'mene ziriri kumlw sikoyenera
But I don't blame him coz he do knw what he's doing and he is the state president without knowing the meaning 😢😢😢
Akwedza bwanji mafuta maulendo ali mkati mpaka ku China and America mmmm
Kodi maulendo chakwera opita kunja amalawi tikupindulapo chani?
Ndipo asatuluse zosephana ndizomwe a malawi akudziwa, coz a natiphera anthu.
Guys truly iyiii nde opposition yamangana guys kuli mphangala zoziwa zinthu ku opposition ukuu guys awaa aaa MCP achoke basi let's go pansewu atikwana .ku mcp kulibe amene aziwa zinthu basi apule basi tikukoza zinthu
Koma ndiye achoke pa 2530.00 kwacha ........ndiye tilire bwanji abale
Please mukalowa boma groom Denis Mahata aswell he is king game changer
Tazimitsani motowo tikupysa Kono Inu wolemekezeka athu. Tikukutsatirani mwachidwi❤❤❤❤❤❤🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Tikumva kuwawa
DPP ndi chiyembekezo cha ife a Malawi
Fire DPP
DPP my vote
Amalaw
Kulira
Sikudzatha
Maremu
Bingu
Munamunyoza
Mpaka
Munapita
Paseu
Kt
Achoke
Inu
andare
Musamatipusitse
Ndpo
Inuyo
Nkhani
Yakupha
Siyachrendo
Matafare
Means
Wasikulu
Ija
Kungotchuko
Ochepa. Relo
Mukufuna
Kukhala
Abwino
next time muzajambulile camera osati ka itel ko
Nkhani yabwno kwambiri many things must come to a true guidance
This one is really an opposition leader
Suleman ndi more