*(TINA Lyrics)* Artists: Phyzix, Ace Jizzy & Beejay Beatmaker: BFB Engineer: BFB *(Intro)* Yeah Very Good/ Very Good Yeah Exklusive/ It’s Only Entertainment *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina *(Verse 1: Ace Jizzy)* Anabadwa nthawi ya Bakili IVON // nthawi ya UDF... ndi Yellow BORN // koma apa ndili ntiakazi TINA M'TINA // tufanana maina....TINA, M'TINA // uyuyutu aise uyu aise ndi NKAZI WABWINO // izi or kale lija ndiNKAZIWA BWINO // komano utilore nkazi ifeyo tili BHO!! // ma ex aMATILIRA ngati uLIMBO // suli ngati tiakazi ta ITI // tovala TIGHT // hehehe NAH ITI // toyenda NIGHT // akazi enawa paiweyo SAMAFIKA // sangaimbeso dancehall koma attention ama SEEKER (Masicka) *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina *(Verse 2: Phyzix)* Verse pa beat/ maliro Sneaker kuphazi mpaliro/ ndikatenga bebi yako ndekuti ndi mpaliro/ am top of the table doyilo/ Tha! Tha! Tha! boyilo/ mfana wofewa bondo elbow/ mwadzadza ma oil/ China nchina mkazi yemwe ndimafira m'Tina/ umadziwa akazi okongola amaswa mitima/ ntchito za mum'dima usathamange taima/ ikamandimenya stress ndimapita kokathima/ ineyo ndi wina/ sine loser ndine winner/ ndimamenya zi ma hit komanso ndili ndi dzina Zomwe ndimapanga ndili khethe khethe ndi udolo/ ineyo ndi ma hit ma hit/ tili ngati khutu ndi ndolo *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina *(Verse 3: Beejay)* Koma ase tinayo akangodzuka Cha Usiku/ Udziwe kuti Wez Day imeneyo silake tsiku/ Ndupanga za Tina .. Ndamukweza Coach afike ku Dinner/ koma Sikuti iye ama cheater ndi Kinnah/ Ndine mfana Wamamuna phwanga sinditha kuima/ Ndimathamanga Bee AKA Khrishna/ Amavina ngati Mphepo Hiroshima..sungamudye phwanga Ukuziwa kuti Sinsima/ China ndi china Man / ichi ndikumanani Tina akafika Amakumanani/ Phuma nanu .. Kuuma nanu Ase uli ndi Mkazi wako ..Koma ineyo.. *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina
TINA VIDEO OUT NOW 🔥🔥🔥 Official Video: ruclips.net/video/pAYn1eFkGKU/видео.html Lyrics Video: ruclips.net/video/pyL-oZ8q0V4/видео.html Spotify: open.spotify.com/track/3mCC9kfQvQ6EwJFxWKuFL4?si=znUl05VqSYeOH6JryZLcdw Apple Music: music.apple.com/mw/album/tina-feat-bee-jay-ace-jizzy/1663605026?i=1663605027 Malawi Music Dot Com: www.malawi-music.com/P/25-phyzix/13629-tina/20082-tina-ft-beejay-and-ace-jizzy Mikozi: mikozinet.com/id/tina-explicit-ft-beejay-ace-jizzy-prod-bfb/
This is prime time media version. The clean edit. You can stream or download the dirty version on the other platforms such as Spotify, Apple Music, Deezer, Malawi Music, Mikozi etc…
*(TINA Lyrics)*
Artists: Phyzix, Ace Jizzy & Beejay
Beatmaker: BFB
Engineer: BFB
*(Intro)*
Yeah
Very Good/ Very Good
Yeah
Exklusive/ It’s Only Entertainment
*(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)*
NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA
Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina
Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina
Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo)
Tina Tina Tina Tina
(Molalo)
Tina Tina Tina
(koma tiaKazi)
Tina Tina tina
(Molalo)
Tina Tina Tina Tina
*(Verse 1: Ace Jizzy)*
Anabadwa nthawi ya Bakili IVON // nthawi ya UDF... ndi Yellow BORN // koma apa ndili ntiakazi TINA M'TINA // tufanana maina....TINA, M'TINA // uyuyutu aise uyu aise ndi NKAZI WABWINO // izi or kale lija ndiNKAZIWA BWINO // komano utilore nkazi ifeyo tili BHO!! // ma ex aMATILIRA ngati uLIMBO // suli ngati tiakazi ta ITI // tovala TIGHT // hehehe NAH ITI // toyenda NIGHT // akazi enawa paiweyo SAMAFIKA // sangaimbeso dancehall koma attention ama SEEKER (Masicka)
*(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)*
NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA
Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina
Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina
Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo)
Tina Tina Tina Tina
(Molalo)
Tina Tina Tina
(koma tiaKazi)
Tina Tina tina
(Molalo)
Tina Tina Tina Tina
*(Verse 2: Phyzix)*
Verse pa beat/ maliro
Sneaker kuphazi mpaliro/ ndikatenga bebi yako ndekuti ndi mpaliro/ am top of the table doyilo/ Tha! Tha! Tha! boyilo/ mfana wofewa bondo elbow/ mwadzadza ma oil/ China nchina mkazi yemwe ndimafira m'Tina/ umadziwa akazi okongola amaswa mitima/ ntchito za mum'dima usathamange taima/ ikamandimenya stress ndimapita kokathima/ ineyo ndi wina/ sine loser ndine winner/ ndimamenya zi ma hit komanso ndili ndi dzina
Zomwe ndimapanga ndili khethe khethe ndi udolo/ ineyo ndi ma hit ma hit/ tili ngati khutu ndi ndolo
*(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)*
NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA
Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina
Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina
Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo)
Tina Tina Tina Tina
(Molalo)
Tina Tina Tina
(koma tiaKazi)
Tina Tina tina
(Molalo)
Tina Tina Tina Tina
*(Verse 3: Beejay)*
Koma ase tinayo akangodzuka Cha Usiku/
Udziwe kuti Wez Day imeneyo silake tsiku/
Ndupanga za Tina .. Ndamukweza Coach afike ku Dinner/
koma Sikuti iye ama cheater ndi Kinnah/
Ndine mfana Wamamuna phwanga sinditha kuima/ Ndimathamanga Bee AKA Khrishna/
Amavina ngati Mphepo Hiroshima..sungamudye phwanga Ukuziwa kuti Sinsima/
China ndi china Man / ichi ndikumanani
Tina akafika Amakumanani/
Phuma nanu .. Kuuma nanu
Ase uli ndi Mkazi wako ..Koma ineyo..
*(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)*
NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA
Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina
Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina
Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo)
Tina Tina Tina Tina
(Molalo)
Tina Tina Tina
(koma tiaKazi)
Tina Tina tina
(Molalo)
Tina Tina Tina Tina
Mutu wa Physics nawo uyimba liti 😜😜😜
Fire 🔥🔥🔥
Eeee komatu ma guy's munayi pweteka... Keep fine burning 🔥🔥🔥🇿🇦🇻🇨
That Bee jay's energy 💪
Tina , mulalotina❤❤❤❤
Yaaaaaahhhh 🔥🔥🔥dope video for the bangerrrr!!! Team work really makes the dream work.
Energy ⚡️
That fire of Bee Jay ayaya
Ace Jizzy’s word play is top notch 🔥🔥🔥
Friends from area 25 💥💥💥💥✔ Tina on repeat
I like the video and very simplistic.
This is very good work ✅
Thank you 😊
🎉🎉🎉🎉
TINA VIDEO OUT NOW 🔥🔥🔥
Official Video: ruclips.net/video/pAYn1eFkGKU/видео.html
Lyrics Video: ruclips.net/video/pyL-oZ8q0V4/видео.html
Spotify: open.spotify.com/track/3mCC9kfQvQ6EwJFxWKuFL4?si=znUl05VqSYeOH6JryZLcdw
Apple Music: music.apple.com/mw/album/tina-feat-bee-jay-ace-jizzy/1663605026?i=1663605027
Malawi Music Dot Com: www.malawi-music.com/P/25-phyzix/13629-tina/20082-tina-ft-beejay-and-ace-jizzy
Mikozi: mikozinet.com/id/tina-explicit-ft-beejay-ace-jizzy-prod-bfb/
Great video concept...
Nice song, great video
Fire
Vele good Vele good
The true definition of thinking outside the box🙌
The video is legit 🔥🔥
Big baaaaad video guys Eeeeh 😀😀😀 keep it lit🔥🔥
Beejay🔥🙌
Ace jizzy 🙌🔥
This,guy has,came,whit,fire
Bee jay is something else i love that guy, 😘 akuti kuuma nanu 😂😂😂😂
Hit 🔥🔥🔥🔥
Concept mwala 🎉🎉🎉
Wimbo mzuri or good song by apelius kamugisha from Bukoba Tanzania
Tina💙💙💙
Bee jay🔥
Video 🚀✈️✈️
Shout out to the videographer LANGSON KALUA...AKA Lang k...🔥🙌
Ukali wanu bigy🔥🔥🔥
Tina❤
Ine nde Tina mukumunenayo..... Much respect azimuna
Love from kawale 💯💯💯💥💥💥💥
Video is legit
Video of the year 💫
Keep it up man bee jay
Phyzix umabwera ndima concept abho and umatha kusankha ma artist oika munyimbo💥💥💥
Uncle ❤️🇲🇼
Magic guy🔥
men this mad cool yooo tiphulise ma speakers
The video is firee🔥🔥🔥
Tina! Tina!
Zambia is listening and vibing to this jam too💪💥
Moraro. Tina tina tina 💥💥💥
🔥🔥 Hip hop game
Massive video….Malawi hippop to the world
Bee Jay nd machine 💣💥
Ilibho heavy
Hit Fire
Nice one ma big
Fire🔥video.
Gamba sazatheka....area 36 (mwenyekondo)Tina...Tina
Best music video and song also 🔥🔥🔥🔥🔥🔥Chaka chabwno ich
The true definition of hip hop.... 🔥🔥🔥🔥
Tina adah
Hit mesa ma gee
phyzix muli kuganiza mwachabe
This is such a fun song and great video 🔥🔥🔥
Thank you 😊
Phyzo anabwera
Hit tezma from Zambia
Very good very good my brother from another mother @Black Don music world
Feeling Good/ Feeling Good
Mumakwana Ayobe🔥🔥🔥🙌🙌
Too far ghetto 🔥🇲🇼
💪💪💪💪
Wow🔥🔥🔥🔥
What happened to gwedeza chimbina? 😂 love the video 🔥🔥🔥
This is prime time media version. The clean edit. You can stream or download the dirty version on the other platforms such as Spotify, Apple Music, Deezer, Malawi Music, Mikozi etc…
G.O.A.T🔥
Yako ija🔥🔥
FIRE PHYZIX
Bee jay hook mwaika bhoo
Energy everything on point 🔥🔥🔥
Vídeo of the year
Zambia 🇿🇲 has confirmed
🇲🇼🤝🏽🇿🇲
Nyimbo yasintha iyi, Bee Jay ufotokozatu iwe
Wow... This is fun🔥🔥🔥 nice visuals
International madala🔥🙌
🔥🔥🔥🔥
Moto
Fire mabomba🔥🔥🔥🔥🔥
The chorus!!!🥲🔥🔥🔥🙌🏽
Energy ⚡️
TINA MTINA🎉
Yo yo yoo. 🔥🔥. Munyengera
Muli fire
International moves
This is super dope n on point🔥🔥🔥🔥... Beejay guy ndi Katswiri
BeeJay voice is dope
No cap, no keezy. Vids is lit💯👌
Tina Tina Tina 🔥🇲🇼🥳
Massive🔥🔥🔥🔥🔥💕💕
Munachedwapo🔥✌
love thissss
Anakudya anawo 🙌🏽🙌🏽🙌🏽
Lol okay 😁
Nyimbo🔥🔥🔥🔥
Such a fun video 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
The beat so appealing and nice video not forgetting " Ndine mfana wamamuna nde sinditha kuima"...
Very Good 🔥💪
Great work mudala
Thanks Mudala 🔥
Very good very good
Yakwana 🔥🔥🔥
Nice
Mmakwana a phyzo
Salute
Energy yakeyo🔥🔥🔥
Tinatinatuna🔥🔥🔥🔥🔥🔥