AMENEYU NDI DJ MUNYANANE NDIPO PALIBE KUPUMA KU MPANDAKO AKANGOTULUKILA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 4 окт 2024

Комментарии • 45

  • @JosephLemani-qq1is
    @JosephLemani-qq1is Месяц назад +4

    Mbambande munyanane osavotela mcp nyasi kwambili 🎉🎉🎉🎉 timakunyadilani kwambili 💪🤝

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq Месяц назад

    LOMWE ULI BHOO KWAMBIRI LISTEN FROM NYODOLA SOUTHERN EAST AFRICA

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 Месяц назад +2

    mr president and vice president may God continue to protect and bless you

    • @paulmolowa2688
      @paulmolowa2688 Месяц назад

      Panja ndi alamwanu? Ayi zikomo

    • @LoydKamtedza
      @LoydKamtedza Месяц назад

      Patumbo pako mwana wa hule iwe ndi Mr president akoo achikangawao

    • @TiyanjaneMkwate-we8gu
      @TiyanjaneMkwate-we8gu Месяц назад +1

      Yes God should continue bless them so that they can be able to see sufferings of poor malawian voters

    • @wittinessnkhokwe
      @wittinessnkhokwe Месяц назад

      Chitsiru china Ichi chokumwa mmadzi ometela ndevu.jb akuti mapwala ako

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Месяц назад +3

    Olo atapanga zotani palibe amudzutse chilima ndi athu 9 aja , waitaya garu iwe chakwela, garu bolaso garu , koma a malawi tiyeni pasewu uyu achoke abale ,chikutisangalatsa chani kodi anyamata, zoona tiziluza dziko ndikuwawitsidwa ndichakwela ngati iye ndi mulungu zoona

    • @DjshukulanGift
      @DjshukulanGift Месяц назад

      Pa sms yanu ndachedwapo mot sindimaivesa koman ndaivesa ,ndikanayakha zolakwika pomwe inu simunalakwe,yaa izodi ndizoona Malawi anali wa kaka ndi uchi koma pan mmm

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Месяц назад +2

    Ndipo ndemweyo Mc Cathy anadzamzembetsa nzake Ku South Africa wasatanic nzakei aluthera anthu limodzi😈😈😈😈chikangawa

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa Месяц назад +2

    Kuyipa kwachakwela chikangawa

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga Месяц назад

    Yemweyo wabweraso mnyanane tawajonjejonje kapena tawakazingekazinge andalewa😂😂🎉🎉🎉🎉

  • @Lunnah-b1t
    @Lunnah-b1t Месяц назад

    Uwasambwadze ,mapeto following u i❤❤❤❤❤

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson Месяц назад

    DJ this is good man

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Месяц назад

    Following you DJ tinya nawe❤❤❤❤❤❤

  • @llewellynkhungwa4712
    @llewellynkhungwa4712 Месяц назад

    Inudi Anya nanu.....🙌

  • @VioletChandire
    @VioletChandire Месяц назад

    Afa ndi chikumbumtima mr chikangawa

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Месяц назад +1

    Mumakwana Mr

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p Месяц назад +1

    Ngongole yamagazi tiona zinthu kkkkkk

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад

    😂😂😂😂😂 uyu asaka ndithu kkkkkkkkk❤❤❤

  • @JohnLabion
    @JohnLabion Месяц назад +1

    Mumakwana man

  • @ChirwaFebe
    @ChirwaFebe Месяц назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MerryWayson
    @MerryWayson Месяц назад

    🎉🎉 🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤ Rordiny

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Месяц назад +1

    Ngati eeish ndingatukwane

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 Месяц назад +1

    Kkkkkkk wandibaya MCP ulipo yankhatu akuti mulungu wachitira Dara kugwesa Ndege kuti tione ngati Ndege imavura zovala anthu ... Palibe chisisi ....
    Eti tipempherere gozi mukupanga nokha kkkk
    Koma lero ndaseka !! Dziko la sataniki ili

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa Месяц назад +1

    Ndipo president uyu chakwela ndi ochimwisa kwambili

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Месяц назад

    Munasowa dj

  • @levisonchimseu2779
    @levisonchimseu2779 Месяц назад

    Iweyo ngati wokhudzidwa wathandizako ndani in your life? Tamusiyeni Ussi, mukungotaya nthawi Achimwene

  • @JorgeSacuate
    @JorgeSacuate Месяц назад

    Amenewa a MCP azayakha afune asafune pangatalike Chilango chilipo ndinthu

  • @MercyKatongo-p9b
    @MercyKatongo-p9b Месяц назад

    Too bad for that

  • @IdressaMussa
    @IdressaMussa Месяц назад

    ❤❤❤❤💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes Месяц назад

    Niwolose mkakutafune party rest in peace SKS

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Месяц назад

    Mr chikangawa akwawonesa anthu kwiyo kwambiri

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe Месяц назад +1

    Tukwana ase palibe vuto covid 19 ndiyonama imeneyija achibare nonse ndimbari imozi ya satanic imeneyija
    Mcp ndiyokupha yasakho next year palibeso kulamura mcp chikangawa imeneija

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er Месяц назад

    Afiti aanthu amenewo.anthu osaganiza za amzawo

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Месяц назад

    😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa Месяц назад

    Komaso shabulika anapindika kale pano zachipembezo akumalowesa ndale nde asakhe chimozi ndale kapena zachipembezo

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 Месяц назад

    Dikila Madzi adutse you gonna see

  • @MercyKatongo-p9b
    @MercyKatongo-p9b Месяц назад

    Pepani

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga Месяц назад

    mutu wankhani ndi otani

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 Месяц назад

    Anakamutenga mzake wa satanic ki South Africa

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 Месяц назад

    MANGANYA ZIKUBWERA UDZALAKA LAKA KULOWA LANYERERE TINTEDI WAKOYO SUDZAKUMBUKILA KUVALA DIKILA

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa Месяц назад +1

    Kuyipa kwachakwela chikangawa