I am amazed and could not do otherwise but to share the link of this interview to others. Iyiyi anthu akuyenera kuwonera ndithu. Zamanyazi kwambiri zikuchitika m'bomamu. God bless you Suleman for the courage to come on air. Kukhala koma kumeneku.
Ana adaddy are very excited to hear this shame from the Christian pastor president. What a shame Reverend but why why why? That is why Chizuma was arrested bcoz she was about to arrest the biggest sharks thieving from Malawians.
If all these rumours are true then am very disappointed and I think mum Lioness is going to be even more disappointed to hear that President Chakwera is failing Malawians.
It's amazing to see some people are still patriotic about this country.
😅 19:56 😅😊
19:56
19:56 19:56 😅
I am amazed and could not do otherwise but to share the link of this interview to others. Iyiyi anthu akuyenera kuwonera ndithu. Zamanyazi kwambiri zikuchitika m'bomamu. God bless you Suleman for the courage to come on air. Kukhala koma kumeneku.
Ndipo share everywhere amalawi amve zoona nkudziwa zomwe akutichita anthuwa 😢
Kuphwasu kuphwasula anthu ngati bwana Sulema ndi ochepa pa Malawi pano bravo to him
Eeeeeeh tili pa mavuto ngati dziko...... respect to Mr suleman
Suleman akuziwa chilungamo and akufunisitsa a malawi tiziwe chilungamo
Chakwera can never be convicted because of Malawi constitution protects him, the only way to deal with him Impeachment or massive demonstration
Zinazo a brian musamangova ayi mayesaso dpp ndi imene inkapanga zodziwa wokha sankava za azawo!tsono lero ndiye adziwe kuyipa.chakwelaso nawo chimodzimodzi.tilibe kothawila.
Heart breaking!
Ah Suleman awa ndi fire osati mphwawo wa IT uja anatinamiza ayi
This is massive 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
I cry for my beloved country.
Onelove to the highest degree
😭😭 Chakwera's leadership mudzanya.Mr S. Suleman ❤❤
Dzikoli tigawanepo bwanji?.?.?
Ziko iri tigawane, mpoto tiyima patokhaaaa
U deserve a crown 👑 suleman inuyo mukadakhalapo anthu angapo dzkoli likadayenda bwno
Chakwera is heartless and useless leader we ever had in the country
It's tough!
Malawi Ali Pa Moto atilandise ndindani Chaka cha mawa Kuli njala yowophwa
Ana adaddy are very excited to hear this shame from the Christian pastor president. What a shame Reverend but why why why? That is why Chizuma was arrested bcoz she was about to arrest the biggest sharks thieving from Malawians.
Interesting
Alright.....ife nde tili chete kuvetsera
Thieves are really stealing in Malawi. This is a serious curse to the children of Malawians, and it's not fair for poor people and taxpayers.
Amango imitsidwa ntchito ochepa chabe koma kubako amaba ndi akulu akulu mkona amaimilana shame!! on Malawi president
If all these rumours are true then am very disappointed and I think mum Lioness is going to be even more disappointed to hear that President Chakwera is failing Malawians.
😭😭😭
Mbava za mcp zikutionjeza