Oimba omwe anatha ataimba ndi Lucius Banda

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 окт 2024

Комментарии • 110

  • @SazieMhoney-bi4pe
    @SazieMhoney-bi4pe Год назад +12

    Lucia's Banda ndi wo yimba amene Ali ndichikondi komaso olimbikisa luso la oyimba Kwa anzizake poti munthu ndi ovuta safuna kuyamikila mutima kapena zochita zazache ndipache enawo amafuna kudesa mbili ya Lucia's banda.poti munthu wina alience Ali ndivuto koma Lucia's sakhomelela anthu koma anthuwo mwina zoimba simbali yawo angodusamo chisanzo muphuzinsi atakhala osula ana mukalasi koma sionse amakhoza sabuject yamuphuzinsiyo olakwa amankhalamo tiyeni tikondane amalawi luso lamunyozo supindula 😭 ambuye akukhudzeni

  • @JuniorAbasi-eb5ce
    @JuniorAbasi-eb5ce 11 месяцев назад +2

    Vuto layife A Malawi timakhala busy ndi munthu kodi ndi ndani sanayimbe mu zembani bandi kupanda ulemu basi vuto ali busy ndi mowa azimayi khuma namitsila Lucius banda🕺💃

  • @Wyson-bo3sp
    @Wyson-bo3sp Год назад +9

    Oyimbawo ngati amangokhalila mowa,kulimbana ndi akadzi namatenga matenda si udindo wa lucius banda ayi.polibepo umboni ulionse osenyeza kut Lucius banda amakhomelela oyimbawa .akadakhala odzikonda Lucius banda sibwebzi ataimba ndi oyimba ena omwe ankaineka otsatsamba koma iye adazichepetsa so don't blame our legend Lucius banda.

  • @ChisomoMakanda
    @ChisomoMakanda Год назад +3

    Lucius sakhomelera oyimba akumalawiwa vuto most of artists here in Malawi have got no professional managers and most of the times anthuwa simaprofessional artists komanso vuto maartist akuno have got no financial advisors as a result they don't go far

  • @SandraIssa-lo8il
    @SandraIssa-lo8il 3 месяца назад

    Lucius Banda was a gentle man. He was a good person.He was a true son of the soil. May His Soul continue to rest in eternal peace

  • @OmarYusuf-TV
    @OmarYusuf-TV Год назад +2

    Amangokhala atha basi
    Ndiwoyimba ambiri omwe atha sanayimbe ndi Lucius Banda eg mbenjere

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 Год назад +3

    Akumulakwira soja, sanathe chifukwa cha soja ayi

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Год назад +3

    Tinangodandaula za achalume uja basi the rest God knows basi 😢

  • @EmmanuelHiggaPhiri
    @EmmanuelHiggaPhiri Год назад +1

    kumunamizira basi,, osewo amene anathawo kut uwaone amangokhalira mowa ndie angapite nazo pati

  • @brianochiumia9087
    @brianochiumia9087 Год назад

    Kwa omwe amatsatira music yakumalawi from 1998 chilungamo ndchoti Lucius ndiwonkhomerera Mufusen Dan Lu samabisa mot onse omwe anayimba ndi Lucius koma akupitilizabe ndchifukwa Choti anthuwo ndi amtima komaso mwano omva zawo zokha mpake akupitilizabe

  • @yamiemsusa3200
    @yamiemsusa3200 Год назад +3

    Point of collection,😂😂 akayimba ndi oyimba oti zao sizinatheke koma ali pa pic amatheratu.but don't compare ndi namadingo kapena piksy poti awa ndi oyimba kuposa lucius yo

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Год назад +1

    Once they gotta money there are not think where they coming from, yet they state enjoying with friends girl friends taken them selves like big man .Some of them the never go to school so they don't know what there doing with money

  • @JamesChapola-m8u
    @JamesChapola-m8u Год назад

    Athu enawo amatambila limozi tayelekezani nyimbo zomwe amayimba akupitililawo ndi amene akumathawo muona kuti zanzelu ndi ziti?

  • @BeatricePhiri-kx5rh
    @BeatricePhiri-kx5rh Год назад +2

    Ine ndimaona ngati ali mka spirit kenakake uncle banda 😎cz sizoonayi

    • @Deajay-jn8cf
      @Deajay-jn8cf Год назад

      Ndizokut maguyz omwe akukhala osatchukasowo ndekut sanawa sayine 😅😅😅

  • @rhabsonchilembwe320
    @rhabsonchilembwe320 Год назад +1

    6:46 anthu amene amakana kujoina zomwe Lucius Banda amafuna ndi chifuk chake samatha koma amene amavomereza ndamene akumveka mpaka Lero look at their status you will understand

  • @JackEdu-ys8ok
    @JackEdu-ys8ok Год назад

    Ine ndikuyankha komaliza ndipo momasula dziko Kuti si Lucius amene amachitsa koma Kuti ali yense ali ndi mbali yake.bwanji manga Billy k. Mpaka pano ndiwotchuka ?,Mlaka?. inunso musalimbikitse udani.katelele anayimbapo ndi Lucius?

  • @briantembo2258
    @briantembo2258 Год назад +1

    I agree lucius banda ndinfiti yoopsyaaa

  • @ahmadjamahiryajuma6456
    @ahmadjamahiryajuma6456 Год назад

    Ndi zoonadi.
    Lucius waimba ndi K milan waku zambia,
    Koma Ali kuti K milan?
    Chibade,
    Maka wa,
    San B,
    Matumbi,
    Cos chiwalo,
    Charles nsaku,
    Charles snenetre,
    And many more

  • @eliasmoyo2739
    @eliasmoyo2739 Год назад

    Iweyo Nd opusa palibe cha mzelu chavekapo apa kungofuna kumuipitsa Muthu galu iwe

  • @AnkeybonkeyChanzah
    @AnkeybonkeyChanzah Год назад

    Ndi okha anthuwo kupanda experience pa lunso lawo nanga enaw akumvekabe bwanji zinjoyi vuto lake Malawi

  • @TachikoMwanamanga
    @TachikoMwanamanga 10 месяцев назад

    😂😂mwasowa zochita ..belekani mwana adzikupatsani busy oyimbayo anali okutha kale musanamizile Lucius Banda ....vuto kumalawi school sinatipindulile that's y we busy stoking other people's life instead of kupanga ndlama

  • @SandraIssa-lo8il
    @SandraIssa-lo8il 3 месяца назад

    Ayi ndithu si Lucius Banda amene amapangitsa anthu enawo kuti azitha, koma okha ndithu

  • @MwenyeCheNsoma-gb2yz
    @MwenyeCheNsoma-gb2yz Год назад

    Kumayamika abale. Musayiwale amene anagwetsa chibade Raph Chi'ngamba.

  • @andrewkalima
    @andrewkalima Год назад

    Ofoila ndi oyimbawo amangodya ndalama ma plan samakhala nawo,nanga Chibade yo kachasu tho kumaziiwala yekha ndie muziti Soldier aziyenda nawo kuwalesa kachasu

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 Год назад +1

    Wayesesata apapa kkkkkkkkk
    😂😂😂

  • @georgejim51
    @georgejim51 11 месяцев назад +1

    Zoona akuluwa sali bwino or ndipo mulingu awakathe motheratu

  • @MacloudMwale
    @MacloudMwale Год назад +1

    Very nice continue may friend

  • @josephchipangula4562
    @josephchipangula4562 Год назад

    Sindine waku Balaka Ayi koma ndati ndineneko chithu chimodzi Lucius ndiye modzi mwa munthu yemwe wawakeza oimba ambili kuti tiyambe kutchula zititengera thawi koma ndingopereka chitsanzo ndi Chibade momwe amamwera mowa do you nthink angapite patsogolo zina tiyeni tizinyamuka komanso zingavute Maka aliyense amakhara ndizofooka zake ndiye osamangoona zofooka tiyeni zabwino muzinenanso mwachidure ma band ambili tikuaonawa ena anachika mu band ya Lucius

  • @LimzeySande
    @LimzeySande 11 месяцев назад

    Oyimba omwe anatha ataimba ndi lucius ndi oyimba omwe anayamba kuyimba muthawi yama tape ma memory card ndima USB ndamene anmaliza athuwa chifukwa anali anthu okudya ndalama mopanda bajet kunena zoona ma tape amat akatulusa nyimbo amaidyerela chaka chonse ma CD memory card ndi USB ndizomwe zinamaliza oimbawa osat Lucius Banda ayiii

  • @tenexchikumba
    @tenexchikumba Год назад

    Soldier ndi legend ,wakutha amatha yekha

  • @ancientnkhata1137
    @ancientnkhata1137 Год назад +1

    Lucius Banda ndimunthu wachikondi kwambiri. He wants other musicians to prosper .

  • @petercheeseboymokoena8659
    @petercheeseboymokoena8659 Год назад +2

    Soldier Lucius siwolakwa

  • @TumamMsume-dd9nw
    @TumamMsume-dd9nw Год назад

    Mayaz watukula ma artists ambili

  • @amonprincegenamu7203
    @amonprincegenamu7203 Год назад

    Moses Makawa sanathe alipo ndipo akudya ndalama remember sizoti ndi oyimba onse omwe azakhale oyimba mpaka kale ayi even inuyo mukamagwira ntchito muziyembekezera kuti muzapanga retire don’t blame Lucius Banda 🤨🤨

  • @sprianobanda195
    @sprianobanda195 Год назад

    Oimba mukunenawo sanapite Ku school amangopanga Za chimbulimbuli

  • @DavieFabian
    @DavieFabian Год назад

    Aaaaa akudziwana ndkomwe amapitako enawo anathawo amayimba muchoonadi

  • @Deajay-jn8cf
    @Deajay-jn8cf Год назад

    Hahahahahahaha music industrie guyz simapanga nawo muganizazo

  • @josephchipangula4562
    @josephchipangula4562 Год назад +2

    😂Nthawi Ina ndinamverako interview ya Billy Kaunda anacheza naye koma anayamukira Lucius kuti ndi modzi yemwe anamuthandiza kumu bweretsa pa stage mpaka Anthu kumudziwa

  • @EmmanuelKamsale-ph1nr
    @EmmanuelKamsale-ph1nr Год назад

    Sizoona, oyimbawo akayamba kutchuka amatailira mkachitidwe kazinthu, monga kumwa,akazi,fodya komaso samapanga invest ndalama zomwe akupeza panthawiyo

  • @DaliAnthony
    @DaliAnthony Год назад +2

    Lb is legend

  • @kawanasamson3069
    @kawanasamson3069 Год назад

    Ma artist akale amawapweteka kachasu aaaaaaa lucias ndi tate no mistake

  • @mkakenishaba6291
    @mkakenishaba6291 Год назад

    lucius anayimbapo ndi Billy kaunda sanathe ilo ndi Boza musamunamizile lucius

    • @LimzeySande
      @LimzeySande 11 месяцев назад

      Akut omwe anaimba ndi Lucius osathawo ndi asatanc azake koma kunena zoona oimba omwe anayamba kuimba muthawi yama tape anali okudya ndalama mononga ndiye kutabwera ma CD memory card ndi USB ndizomwe zamaliza asat Lucius ayiii

  • @TamandaniSada
    @TamandaniSada Год назад

    amene akutchukawo inuso mukuziwa ndima😅😅😅😅

  • @InocencioJorge-vu2gx
    @InocencioJorge-vu2gx Год назад

    Very Nice brother

  • @WisdomMwitha
    @WisdomMwitha Год назад +1

    Buyomo zoonandi lucias banda analimbe chikondi ndithu ndioimba azeke ndipo amapondeleza Okay sizoona kuti lucias banda amaononga loso lawathu Koma vuto ndalakuti lucias banda amokonda oimba azeke azekewo akachuka samafuna kuwatukula Ali ang,ono ang,ono chifukwa buyomo amakhomelela oimba ambili ndiye zimatengela kulimbikila ndimakani aimboyo kundutsa mavuto osiyanasiyana chosecho Lucias banda anathandizidwa alleuya band ya katolika koma amasowa chikondi ndioimba azeke boyomo moti pachipand kuchuluka kwa mastudiyo sibwezi oimba tilinawo mwai ndi technology inabweletsa kuti oimba achuleke komaso oimba awonetse luso koma pachipanda izi athu ngiti Lucias banda mwezi akukhomelebe oimba koma panopa anaona kuti olo akhomelele palibe chomwe apindule chifukwa mastudiyo ndiyambili chifukwa mumaona kuti lucias banda amokonda kuimba ndioimba azeke koma mbuyomo kunena zoonandi lucias analimbe chikondi

    • @WisdomMwitha
      @WisdomMwitha Год назад

      Ndizoona ndithu kuti bwa big man lucias banda boyomo muthawi yawo sanachitebwino pakuthandiza oimba pomwe amati mulungu amadalitsa ukathandiza azako ndiye bwizi panopa timanena kuti oimba ambili anampuzitsidwa sir lucias banda koma muthawi yawo sanachitebwino pakuthandiza oimba ambili amakhomelela oimba ambili zikmatengela kulimbikila ndimakani aimboyo kundutsa mavuto chitsazo namandingo amene mukunenayo ikanakhala kale sikanaimbane komaso lucias akanasikasaka njila zoti namandingo asachuke oaswa ngiti Lulu ndikulimbikila kwawo koma muthawiyo sikuti lucias banda zimakodweletsa ayi chifukwa amafuna azichuka yekha bisi chitsazichi kunali oimba ambili omwe muthawiyo amaoneka osauka. Pakusowa chitandizo chalusolawo koma lucias banda samawathaniza mwaona koma chifukwa chakuti technology inabweletsa kuti oimba ambili adziwike chifukwa chake munaona ena oimba osauka anayamba kulimbikila kuonetsa luso osewa anaimba ndi Lucias banda chifukwa chakuti Lucia anawona kuti mulimpindu panopa chifukwa mastudiyo anachuluka sindingakhomeleso nditani nditani bola kupeza pindu lochepa kuimbila limodzi koma mukanena freedom fighters wanyimbo kwathu kono ndiye modzi mwaiwo ndi Lucias banda ndipo timapelaka ulemu kwambil chifukwa chakuti anaingwila tchito kumenyela ufulu kuti oimba ambili tizidziwa kuti kukamila kuimba kwabwino zokhazo anaika dziko lamalawi pamapu ndipa timapelaka ulemu ndithu koma kutukula oimba ambili ayi boyomo muthawi yawo ndamene amangwetsa oimba azake anali wachebe koma panopa nasiya zimenezi chifukwa anavomeleza kuti oimba achuleke maufulu ndiyambili

    • @WisdomMwitha
      @WisdomMwitha Год назад

      Ndizoona ndithu kuti bwa big man lucias banda boyomo muthawi yawo sanachitebwino pakuthandiza oimba pomwe amati mulungu amadalitsa ukathandiza azako ndiye bwizi panopa timanena kuti oimba ambili anampuzitsidwa sir lucias banda koma muthawi yawo sanachitebwino pakuthandiza oimba ambili amakhomelela oimba ambili ndiye zimatengela kulimbikila ndimakani aimboyo kundutsa mavuto koma sizali zopmpweka

    • @WisdomMwitha
      @WisdomMwitha Год назад

      Ndizoona ndithu kuti bwa big man lucias banda boyomo muthawi yawo sanachitebwino pakuthandiza oimba pomwe amati mulungu amadalitsa ukathandiza azako ndiye bwizi panapa tikumati tosefe tinampuzitsadwa ndi sir lucias banda koma muthawi yawo amapondeleza ndiochepa omwe akapeza mwai ndikupita patsongo ndikutulidwa ndi Lucias banda pokha pokha

  • @George-ux7vq
    @George-ux7vq 11 месяцев назад

    Jealous basi, Lucius Banda ndi amfumu mu nyimbo

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk Год назад +1

    Nice one 🎉😍

  • @TrustMataura-ii5wt
    @TrustMataura-ii5wt Год назад

    Zabodza Lulu sanaimbe naye? Nanga Kelly Kay bwanj

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 11 месяцев назад

    thawizina tizivomeleza kalikose Kali ndithawi palithawi wakubadwa ndi yakumwalila

  • @lysonkaselema7321
    @lysonkaselema7321 Год назад

    Zonama
    Sam Smarks bwanj?

  • @BrianMalindima-n8r
    @BrianMalindima-n8r Год назад +1

    Oimbawo amangokhala kuti atha basi

  • @AlexKaunda-x3p
    @AlexKaunda-x3p Год назад +2

    Ndi wa muthi

  • @JonathanMkwamba-bz6du
    @JonathanMkwamba-bz6du Год назад +1

    Lucius ndi okhomelera oyimba izo ndiye ndi zoona.

  • @YASSANWADO-jk4xp
    @YASSANWADO-jk4xp Год назад

    Ndizovutilako km akuziwandi god ndilibe umbon

  • @FrankHassan-u1u
    @FrankHassan-u1u Год назад

    It is true

  • @josephbanda4973
    @josephbanda4973 Год назад

    Koma ndiye

  • @mouricesaidi5348
    @mouricesaidi5348 Год назад

    LULU
    MLAKA MALIRO
    PATIENCE NAMADINHO
    DAN LU

  • @grolywchirombo510
    @grolywchirombo510 Год назад

    Akadakhala amaononga tikadaonera mlaka anthu mmumangodana naye

  • @amineasalimu1986
    @amineasalimu1986 Год назад

    Lucius alibe vuto oyimba enawo ndi manyaka basi

  • @preciousdyton910
    @preciousdyton910 Год назад

    Sizoona kuipitsa mbiri ya munthu mwina akanakhala kut onse omwe anaimba ndi iye anatha ndy tikanadabwadi

  • @ThabodariusMasingi
    @ThabodariusMasingi 11 месяцев назад

    Vunto linalipo ndkusalimba mtima ena akuvekawa analowa usantanic

  • @CanadaTambala
    @CanadaTambala Год назад

    Oyimba enawo amalimbana ndi adzimai komatso mowa

  • @gereya
    @gereya Год назад

    Iwe ndiwabodza makawa sanathe

  • @RabeccaMkwezalamba-e5i
    @RabeccaMkwezalamba-e5i Год назад

    nthaw ikakwana.yakwana.bs😂😂

  • @jameswajumpha6790
    @jameswajumpha6790 Год назад

    Wow sammalvita

  • @carlolinemndala3634
    @carlolinemndala3634 Год назад

    JANTA SANATHE BWANJI?

  • @NamahappyMostrator
    @NamahappyMostrator 9 месяцев назад

    Zaboza iya

  • @amidujumo5612
    @amidujumo5612 Год назад

    Za bodza lucius wayimba ndi anthu Ambali koma mpaka pano akuyimbabe

  • @ImrranGideon
    @ImrranGideon Год назад

    Soldier ndidolo guys

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Год назад +1

    Lucius Nd makina

  • @ibratime
    @ibratime Год назад

    Iwe ndi wabodza kwabasi osewo omwe ukwachulawo sanathe paka pano

  • @TomHardy-b4x
    @TomHardy-b4x Год назад

    Ndiwokha oyimbawo nkhani ndi mowa ndi fwodya

  • @HamdanMasuku-b3n
    @HamdanMasuku-b3n Год назад +1

    Uli nd vt ndwe ase

  • @shaffidanikeni2502
    @shaffidanikeni2502 Год назад

    Bola usajuke kusiyana kupa abareako

  • @josephchitsulo5882
    @josephchitsulo5882 Год назад

    M'dima ndi kuwala siziyendela limodzi

  • @JumaJonas-d2x
    @JumaJonas-d2x Год назад

    Ayi oimbawo ena ama mixer too much

  • @kasupeowenpaul
    @kasupeowenpaul Год назад

    Nanga janta yomweyo galu iwe ndi hit apa wanama aise

  • @DalitsoTsogolani
    @DalitsoTsogolani Год назад

    IWE ULI NDI NSANJE NDI LUCIUS BANDA, THE GUY HAS LIFT UP A LOT OF ARTISTS, MPAKA PANO AKUIMBABE, DAN LUFANI WAIMBAPO NDI LUCIUS NGATI SUKUDZIWA UFUNSE NYIMBO YA SHUPI ANALI NDI LUCIUS, NANGA MLAKA MALIRO? NANGA BILLY KAUNDA? NDI ENA OTERE? KUKAKHALA KUTHA ZIMAMHALA ZIFUKWA ZAKE MUNTHUYO NGATI IWEYO😅😅😅

    • @sammalvitha
      @sammalvitha  Год назад

      Oneran video yonse... Before kundichita criticize

  • @MarleyMussa-pd2nd
    @MarleyMussa-pd2nd Год назад

    Ndiwabwino

  • @chissanobanda5004
    @chissanobanda5004 Год назад

    Iwe Lucias Banda alibe vuto

  • @bushchunga1930
    @bushchunga1930 Год назад

    Ea ndioona

  • @kho7676
    @kho7676 Год назад

    Zabodza amaziononga okha lucius ndiwa bhobho

  • @francismilanzi1599
    @francismilanzi1599 Год назад

    Nsanje

  • @FrednadLimited-me2td
    @FrednadLimited-me2td Год назад

    Yea is two that is carfet

  • @jamessaiti
    @jamessaiti 11 месяцев назад

    Soja amatha kuyimba

  • @sammalvitha
    @sammalvitha  Год назад +1

    Remember to subscribe

  • @wenfridamuhura-tb1wd
    @wenfridamuhura-tb1wd Год назад

    Vuto ndi oimbawo not Lucius hiyaaa

  • @timothylipenga8413
    @timothylipenga8413 Год назад

    Ndi zoona

  • @lacksonmanyewu3615
    @lacksonmanyewu3615 Год назад

    Enawo anakana ku satanic pamene enawo anavomera ndi nkano akuimbabe

  • @jastenmposa3686
    @jastenmposa3686 Год назад

    Lucius alibe vuto

  • @MoosaSame
    @MoosaSame Год назад

    Mphamvu zakumidima zimezo

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Год назад

    Zoona

  • @IssahFrank-j8z
    @IssahFrank-j8z Год назад

    Zakumidimazo

  • @JonathanMkwamba-bz6du
    @JonathanMkwamba-bz6du Год назад

    I like this topic

  • @felixmoyo5944
    @felixmoyo5944 Год назад

    Bodz

  • @FrankHassan-u1u
    @FrankHassan-u1u Год назад

    No

  • @SANi-x2z
    @SANi-x2z 8 месяцев назад

    NO