Peter Munthalika wachitisa Manyazi chipani Cha Lazarus Chakwera

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 21 янв 2025

Комментарии • 34

  • @Tophillpvtsecondary-x7l
    @Tophillpvtsecondary-x7l 4 дня назад +1

    RIP mr chilima munakaziwa munakafatsa Ku dpp , munafera udindo okhala wanu ABISALOM

  • @feniasande6695
    @feniasande6695 3 дня назад

    VP RIP, munatikankhira Ku motoooo 😫🙌

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 4 дня назад

    APM 100%💙💙💙💙

  • @RIGHTEOUSMISESA-h5b
    @RIGHTEOUSMISESA-h5b 4 дня назад +3

    Chilima mwana wamwano... Mwana onyoza makolo afe ndithu

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 5 дней назад +1

    Adad woyeeee

  • @LoyceChipwaila
    @LoyceChipwaila 7 дней назад +5

    Chilima unatitengera kumazuzo udakapilira bwezi ulindimoyo ifeso tilipena osati izii mmmm.

  • @isaaczuze
    @isaaczuze День назад

    Akulu awa ndichifukwa anaphedwa chifukwa cha phuma komanso matama
    ..lelo ali mmanda....munthu ameneyi anali wosokoneza kwambili

  • @HappySally-x3b
    @HappySally-x3b 6 дней назад +2

    Chosaziwa😢

  • @CatherineNantchengwa-d4w
    @CatherineNantchengwa-d4w 6 дней назад +1

    Awaso anatigwetsera kuphompho aaaaaaa

  • @EnerstManess
    @EnerstManess 4 дня назад +1

    Kan adakuchita sacrifice ya chipan chawo ngoma yolilisa

  • @MadalitsoAbambo
    @MadalitsoAbambo 5 дней назад +2

    Chilima ndipakedi kufa kulakhulisa amkulu aja

  • @ChikumbutsoChomali
    @ChikumbutsoChomali 4 дня назад +1

    Pano akutimvesa kuwawa mkulu uyu eeeee ai zikomo

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 4 дня назад +1

    Anachitira campaign chigawenga komanso mbava

  • @SahilluYusuf-sk7es
    @SahilluYusuf-sk7es 6 дней назад

    They are critically true to what we have faced bola DPP bac eeetu

  • @JudithMbuba
    @JudithMbuba 4 дня назад

    Nanunso zinthu zidakwera maiko onse iwowo azatsitsa mukumama adpp ndi mumene adzunzira

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 7 дней назад +5

    Zoonadi anthu timamukonda Peter

  • @josephymunthali
    @josephymunthali 4 дня назад

    Vuto ndiloti simuyenda, mudziyenda... Ndi phindu locholuka bwanji limene Anthu akummwera apeza, mu nthawi imeneyi.

  • @ChikumbutsoChomali
    @ChikumbutsoChomali 4 дня назад

    Akulu awa amalakhula eeeee ndpo mudali kunyoza mwa akulu awa mmmm zimandinkhuza kwambir akamalakhula zonyoza Peter thaw zambir misokhano yake sindimamvera amalakhulisa kwambir

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 4 дня назад

    Adye siwakwane ngati mmene anawadyera a Biyeni ndi ena 8 aja kuti boma liwakwane. 16 tiwachotsa.

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 4 дня назад

    Nkhaai ikhale yolimbana ndi MCP eee abale pepani Zina. Akula nkhswe okhala pachipaznde

  • @NdaonaMsowoya
    @NdaonaMsowoya 6 дней назад

    Umunthu ndi wenkha olo banja lomwe linatha ngati unasiya ana ntati sakupasa ulemu ndiye kt ununthu unalibe ndiye mcp umunthu alibe

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 4 дня назад

    A MCP nthawi yawo yatha, sangathe kukonza mavuto ambiriwa munthawi yochepayi. Iwowa kwawo kwatha, olo atatani.

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi 5 дней назад

    Ndipo ndi zoona zomwe mukulakhulazi a MCP sakunganiza zimenezo

  • @GeorgeMartin-z7u
    @GeorgeMartin-z7u 4 дня назад

    Chilima anali munthu oyipa unatipweteketsa

  • @JemesMalawa
    @JemesMalawa 3 дня назад

    Dpp ndi chipani chafuko olo mcp kut idye nsima nkhani ndi chimanga bas

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 6 дней назад

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 6 дней назад +1

    Anapanga zofoila..but i just feel sorry for loosing his life.. may he cont resting well

    • @daviechannel8603
      @daviechannel8603 2 дня назад

      @@MonijaKataika ndipo zoonadi chilima watigwesela kugahena koma pena sichilima koma

    • @MonijaKataika
      @MonijaKataika 2 дня назад

      @daviechannel8603 kkkk koma ndani he had too much followers n then took all to tonse alliance 😆

  • @MacbillyNgwira
    @MacbillyNgwira 4 дня назад

    Senseless.

  • @alfredmongola900
    @alfredmongola900 7 дней назад

    mcp inakukonza iwe phuma too much

  • @alfredmongola900
    @alfredmongola900 7 дней назад +2

    Uyu mapwala ake ndiyemwe anapangisa kuti amalawi azivutika

  • @josephymunthali
    @josephymunthali 4 дня назад

    İnuso ndinu mbuli, ndinu ma TV representative, Koma muli Ndi mbali.