The DC the president of poor pple ine ife amalawi timakunyadilani kwambiri ambuye azikutetezani nthawi zose ndanyadira mwakaponda pamzuzu inudi ndinu president waife amphawi ndipotu the DC munayenera kukhala president wamalawi yose
Bon Kalindo the flip-flopper...wayambanso kumuyamikira Vitumbiko Mumba utamunyozanyoza, I'm sure after listening to Kulinji program on TTV. Udzidekha ukamva nkhani before quickly condemning people
Dc ndi iwe dolo, koma apa wanena za anthela kuwili kodi mmesa mangochi amayenda nd mcp thawi ina yake amakunyozaso that time koma apa wamuonesa ntima wabwino big up mr president of poor people
Zoonadi andunawa mwawawunikira bwino kwambiri akalindo congras
Nice to hear from our own beloved president the Dddddd Cccccc!!!! Mwana owopsaa kwambiri, proud of you our beloved president
Big man the DC zoona zake auze mwina angave
The DC the president of poor pple ine ife amalawi timakunyadilani kwambiri ambuye azikutetezani nthawi zose ndanyadira mwakaponda pamzuzu inudi ndinu president waife amphawi ndipotu the DC munayenera kukhala president wamalawi yose
The president of the poor malawians may God be with you.The DCCCCCCCC CCCCCCCCCCCC from mulanje Malawi southern Africaaaaaaaa
Big up the DC
APM my vote🎉
Osaopa osatopa osafooka comrade the dc
Ine ndkuthokoza iweyo Mr DC wasonyeza kut umatha
Love you dear
Muthu wakulu kwambiri ❤
Umakwana big
Chakwela ndi boma lake anamuphela dala chilima, ndale zophana zambuli, kumalimbikila school. Infa Yachilima ija simuzakhala ndintendele achakwela ndikupusa munapanga kuja
Bon Kalindo the flip-flopper...wayambanso kumuyamikira Vitumbiko Mumba utamunyozanyoza, I'm sure after listening to Kulinji program on TTV. Udzidekha ukamva nkhani before quickly condemning people
Umakwana ase
Kumupha chilima ndi anthu ena aja ndipomwe anapha MCP, ndale zopusa zipakilani like it or not zipitani
Number one❤❤❤
Kkkk kalindo ulimbo
Justice for Malawians. Enafe sitinalembetse. Timadwala. Tinaona chamwayi kuti tikalembetsa. Fight for us Comrade Kalindo
Dc ndi iwe dolo, koma apa wanena za anthela kuwili kodi mmesa mangochi amayenda nd mcp thawi ina yake amakunyozaso that time koma apa wamuonesa ntima wabwino big up mr president of poor people
Kumeneko ndikumuonetsa uchitsiru mangochi kuti munthu amene umamunyoza ndi amene amakuthandiza
TIMAKUVERANI KUPOSA RADIO 📻
Mumakwanila a president athu
Chakwera ukunama kwambiri unyamanyi pompano
The DC
Mumakwanila a president
Mulungu akudalisen kwambiri
Ndipo ife takamidwa kukalembesa ndimbuzi ximenezi
Mbambande inuyo
You're really a freedom fighter the president of the poor in malawi
The DCCCCCCCC mumakwana
Madala kuribeso umakwana
Osaopa
🎉🎉
🔥🔥🔥🔥
Bravo
❤❤❤😂😂😂
🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🎶
Uyu palibe Cha nzeru angakambe
State house ya achakwera😂😂😂
Kkkkkkkk kd achakwera simupsya mtima? bweretan bomba liphulitse malawi paja mudana ndi chilungamo kunena zoona boma lanuli latsala ndi anthu adyela okhaokha km okonda Malawi sangaime kumbali ya mcp mind you amene umati boma ndi lomweli mumva mtidzi chaka chino beran koma simukuwinabe