Mr khad kuzangobwera ndi yao ija

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 20 окт 2024

Комментарии • 42

  • @PetrosMunthali
    @PetrosMunthali 2 месяца назад +2

    Perfectly said. Why is he clinging to UTM? Leave UTM alone. Thanks Khad.

  • @CatherineSachemo
    @CatherineSachemo 2 месяца назад +2

    Perfect said USI akuoneka KUT Ali ku MCP

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 месяца назад

    Manganya ndiwe wa MCP. Kukhala wa MCP ndichisankho chako koma kunamizira kuti ndiwe wa UTM ndi khalidwe la ukanyimbi==Chiphwisi.

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 2 месяца назад

    Eish koma zinthu zake mmm kumachita kudzitama kuti amadziwa kupempha 😂😂😂 dziko laipa mmmm pa ground sipalibwino

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 месяца назад

    Manganya ndi nfiti anapeleka Chilima muja anati pheeee anangonva za iimfa ya chilima muja angangoti ndapelekadi ine???????yudasi weni weni

  • @SamsonNyadan
    @SamsonNyadan 2 месяца назад

    Paja umkatiso Kabambe ndimbava, ndeno tikumve ziti ase? Utibalalisatu

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli 2 месяца назад

    Uyu ndichakwera yemwe

  • @Alicia-ns5ho
    @Alicia-ns5ho 2 месяца назад

    Olo ndimwana yemwe akuziwa kut akuluwa nga Mcp

  • @kaungabondera892
    @kaungabondera892 2 месяца назад

    What is the picture in front screen doing?????

  • @ELLARTONKAMBALE
    @ELLARTONKAMBALE 2 месяца назад

    Yakula ndi jealous Chilima ndiamene anamuona Usi kuti ndiyekhayo wa nzeru angathandizane naye,so izi sizabwino Kabambe ndi wa DPP uku akufuna juga koma simukudziwa l lov UTM koma mgwirizano ukuvuta tiyeni tigwirizane

  • @lastonesaizi8732
    @lastonesaizi8732 2 месяца назад

    manganya akuwona ngati chakwela angadzamusakhe u VP kachiwiri

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801 2 месяца назад

    Manganya ndikazitape akufuna kunsokoneza utm ndicho linga chofuna kusangalatsa chakwera, angochokelatu Ku utm asakumangeni kumaso a utm

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence 2 месяца назад

    Manga ya ndiopanda nzeru ,iye akufera kanthawi katsalaka,angozipaka milandutu uyu nthawi yotha itha

  • @HamanjaManyela
    @HamanjaManyela 2 месяца назад +2

    Fact

  • @RodgersBaluti
    @RodgersBaluti 2 месяца назад

    Mbuli iwe maganya sapanga zako umutsatilanji

  • @SamManyawa
    @SamManyawa 2 месяца назад

    Mukulimbana ndi manganin osamuuza chakwera wanuyo bwanji kupusatu kumeneko

  • @FysonMkuzura
    @FysonMkuzura 2 месяца назад

    Manganya tinamugwira kale ufitii!!

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 2 месяца назад

    UTM singawine olo utakuwa mwabwanji

    • @Thembokatuli
      @Thembokatuli 2 месяца назад

      Simwamupha chilima nde iwina bwanji

  • @GeorgeMuserima
    @GeorgeMuserima 2 месяца назад

    Give him time so that we can judge perfectly

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 2 месяца назад

    Manganya ndi peturo anakana chilima ali moyo ndikupita kwa chakwera kupha chilima chifukwa cha udindo alibe nawo fundo zenizeni

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence 2 месяца назад

    Koditu angakhale MCP siingawine,ndipo siidzawinanso

  • @NumbDee
    @NumbDee 2 месяца назад

    UTM
    Singawine
    Not now

  • @ndatsalapatimsanjama9844
    @ndatsalapatimsanjama9844 2 месяца назад +1

    Kodi ndinu pa chibale??? Mukufananatu

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 месяца назад

      😂😂😂😂Mutimangitsatu
      Palibe ubale tangofanana boss😂

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 2 месяца назад

    Facts

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 2 месяца назад

    We need change time is gone please

  • @MadaalaYare
    @MadaalaYare 2 месяца назад +1

    Muwuzeni iye azipanga za MCP ayiwale za

  • @SamManyawa
    @SamManyawa 2 месяца назад

    Akugulani inu osapanga mfundo zanu bwanji,,,mukamanva jealous ndirimenelo titan pasanja nanu mukanene zanu don't point someone

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 2 месяца назад

    Manganya satana

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 2 месяца назад

    Manganya ndi wa Mcp osati utm

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 месяца назад

    Manganya ndi kachisilu

  • @GoldenNamanguya-q9u
    @GoldenNamanguya-q9u 2 месяца назад

    Utm singane

  • @MadaalaYare
    @MadaalaYare 2 месяца назад

    Iwe wamaliwi camera tikufunaso tiziziwa za khondoso ku FB su kupezeka

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 месяца назад

      Ndakupatsani link tu koma
      Tandipezen ku WhatsApp 0899688320

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 2 месяца назад

    Mbambande

  • @DanielnachanzaBanda
    @DanielnachanzaBanda 2 месяца назад +1

    Mbu

  • @GoldenNamanguya-q9u
    @GoldenNamanguya-q9u 2 месяца назад +1

    UTM singawine

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад

    Manganya he's useless person munthu Zoona unganene kuti ndine katswili pa zopemphesa zoona zamanyazi

  • @RodgersBaluti
    @RodgersBaluti 2 месяца назад

    Mbuli iwe maganya sapanga zako umutsatilanji