KOMA ANTHU NDE AKUYANKHULATU ZOKHUDZA REPORT LIJA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 дек 2024

Комментарии • 7

  • @PeterMwakihana
    @PeterMwakihana 2 часа назад +3

    No matter how the truth can not be disclosed. Ambuye azatulusa lake nthawi ikakwana.

  • @RabeccaMkandawire-i9j
    @RabeccaMkandawire-i9j 2 часа назад +2

    Ife a Malawi sitikhulupilira

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q Час назад +2

    ngani yose ilindi mbavu seniseni nkwa shimwendo banda ankusiwa ngani yonse ankuwopha nkuyalussa boma lonkuba nkomaso lonkupha amallawi shosani shinkangawaw 👊🇿🇦🇲🇼

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l Час назад +1

    Anthu awa asatipwetekese mutu nkhani yose apeleka pa commission for inquiry anakhala pasi ndi kulipeka bodza chifukwa chake amachedwa kuti apange commission for inquiry anthuwo anali busy kupeka kaye bodza lomwe atulusa dzulo lija

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 9 минут назад

    Ndege yimeneyi inayenda yekha komalizira atawapopa magazi ziapolisi zaku State House ndi Israel and mulonda wapa tawer anamupha uja mcp chipani chamagazi

  • @benjaminnkhata5121
    @benjaminnkhata5121 33 минуты назад

    Sunakapeleke umboni wako UK bwa?

  • @AwidsMaseko
    @AwidsMaseko 3 часа назад +1

    Kodi a Namiwa aja ndi pachibalenso eti??