Koma chipani Cha mcp tidapanga bwanji amalawi kugani zochiyika pa mpando, kod amalawi azanga ngakhele mukut Inu mcp simukudabwa kut ustogoleri WA mcp ukuchulika nkhani maka zokhudxa ziwembu gyz ku malawi MSI ku American tichenjele
Kodi inu Big kukakamilaku kt mulamulire dziko ili mukukonda amalawi kapena mukufuna kutimaliza? Uhuh eheh God will provide if you or not kondani mtumdu wa Malawi mkatimotu muli abale anu iiii koma
Chakwera aziona zimenevakuchita hakainde hichilema amalemekeza anthu awe chakwera salibwino 🇿🇲
Ana achepa ubwino wake ana tikubadwafe tikuwona mcp zimene ikuchita. No vote mcp
Dziko lanthu no peace Malawi's tafasa kwambiri mavutowa sazatha khaza kumangana , kuphana ndi boma ili action ikufunika sooner the better
Ulemu wanu big man
MCP Zomwe imaganuza ndi za Upanda basi.
Kupha, Kupha, Kupha hmmmmm.
Nkhani ya mademo a malawi tinakozeka kale kale vuto ndilomweli loti amatumidza adzikwanje basi koma anthu ali okozeka mudzawonanso nokha comrade. Akuona ngati akamanga cisale apeza mpata omupha APM mcp ikungodzivuta asiyeni awona cinameta nkhanga mpala, comrade mangochi timufunila dzabwino dzonse mmene muyendele mutiuza.
Darkness cannot drive away darkness and hate cannot drive away hate, only love can do that, chakwera doesn't have love, ngakhale mkadzi wake amadziwa
Wlcm back SIR COMRADE MTANYIWA achita bwino kumukaniza ameneyu
Inuso ndionysdilidwa 🔥🔥🔥
Mulungu wathu sanakhare chete atimenyera nkhondo
MCP taiziwa ana ife we don't want chakwera
Amuchita bwino kumukana kwa Americans ndpo nyumbayo yachitaso bwn kupsa mizimu ya ononga mulungu alupo
Comrade Malawi wavunda ambuye atiyamganire.
Mbambande iweyo comred mcp yachepa Chaka chino ikuvaya
Trump ndimuthu woopsa asapange chibwana chakecho
Uyu guys amene mukumutcha Chakwera he's very stupid man why can't he gives up the match
Koma akafika kumeneko pofunika akamumange anfunse kuti kunzatani sitinakuyitane
Kkkk chakwera mizimu ya anthu 9 kuchikangawa yamukwiiyila
Mumakwana boss ndimadabwat kusowaku
Inuso timakunyadilan mbali yakuno 🔥🔥🔥
Koma chipani Cha mcp tidapanga bwanji amalawi kugani zochiyika pa mpando, kod amalawi azanga ngakhele mukut Inu mcp simukudabwa kut ustogoleri WA mcp ukuchulika nkhani maka zokhudxa ziwembu gyz ku malawi MSI ku American tichenjele
Iiii koma dzikoli abale
😂😂😂😂
Zikomo tamva mawu anu
Koma mulungu aliko kunja kuno
Kodi inu Big kukakamilaku kt mulamulire dziko ili mukukonda amalawi kapena mukufuna kutimaliza? Uhuh eheh God will provide if you or not kondani mtumdu wa Malawi mkatimotu muli abale anu iiii koma
Chakwera tamakhala kaye pankhomo kuti chuma chiseveke please tadzimvani chisoni kwa anthu a ku Malawi
Kodi chikangawa ndi chani makamak kukonda kuyenda ngat galu wa chiwewe
Ukakhala kuti mwaiwe mulibe utsogoleri...zotsatila zake mzimenezo😂😂😂
Ndipo nde Chakwera watikwanadi