Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
No secret under the sun,,Mhsrip SKC and 8 others 😭😭😭
We are with you Mary chilima😢
Ine Ndimakhala kukasiya kwawo kwa chakwela, kuno kuli njala yoopsa anthu tikudya dothi komanso dothilonso likupita kwakutha chifukwa zikhawo zonse zinatha. Mutiyankhulileko kubomako akalindo achakwela anasiya kubwela kumudzi kwawo kuno chiloweleni m boma.Kwa akufuna kwabwino tiyendeleni kuno ku kasiya.
We are still mourning our president
The first president in Malawi he gonna go to jail its chakwela chikangawa 1 day it's 1 day judgement Day
Mary tili nanu limodz chilungamo chiwoneke
God is God and will never Change one day is one day
Mbambande the DC 🔥🔥🔥
God is still saying something
Mwang'alulatu aPresdent anthu ndipo mumaitha..kkkkkk....the DC
Hahaha Mulungu ndi ndi kukhwima zisanayambe za yenderanapo bwana kalindo,ingopangani za ndale osaikamo Mulungu muzanuzo bro
MCP akuyesera kufuna kubisa zokhuza ngozi imeneyi, koma chomwe sakudziwa aliyese anatenga gawo pa ngozi imene ija azayankha.
"My God was in Chikangawa"
MCP YASAVUKA NDI UFITI
Diso kulipa diso tidzaonana bomali likadzatha and police yonse ikutumidwa ndi mcp tidzakuchotsani ntchito komanso tidzakumangani
Achitsilu a DPP inu tamangopangani campaign basi timakudziwani inu
😭😭😭😭😭😭dzukani dzukani
Zoonad chilungamo chiwoneke poyela
Mulungu wake uti akalindo
Iwe leave bhon kalindo a lone open ur eyes
Eti mulungu ndi zopepelazi sizigwilana...😂
🙏🙏🙏🙏🙏 amen
Our DC cc
Pls ndimafuna number ya khalindo
No secret under the sun,,Mhsrip SKC and 8 others 😭😭😭
We are with you Mary chilima😢
Ine Ndimakhala kukasiya kwawo kwa chakwela, kuno kuli njala yoopsa anthu tikudya dothi komanso dothilonso likupita kwakutha chifukwa zikhawo zonse zinatha. Mutiyankhulileko kubomako akalindo achakwela anasiya kubwela kumudzi kwawo kuno chiloweleni m boma.
Kwa akufuna kwabwino tiyendeleni kuno ku kasiya.