We supporting you leader of Oppostion but to say trueth oppostion leadership in pariament is sleeping too mutch iz ndzomwe zikupelekaso mavuto dziko muno chifukwa achina chimwendo akupanga zomwe akufuna chifukwa omwe ali nd phavu zot angatsutse ndkulimbana nd mchitidwewu ndiomwe amapatsidwa kathaw kochepa mot idz zomwe mwapangapa zokaikitsa kut zikaphula kathu ku meneko
🔥🔥🔥 Bwana Chaponda chooonde musakaiwale za smart matic achoke machine amenewa
Wabaya
Aaa awawa sakutithandiza ayi akupanga ndende ndizomwe ankapanga Nankhumwa
This is good mikanena zomwe mwaziona good chaponda
Chaponda zipita ukalime fodya ku estate nanunso munkangoba ndalama nthawi yanu mafuta amasowa
We supporting you leader of Oppostion but to say trueth oppostion leadership in pariament is sleeping too mutch iz ndzomwe zikupelekaso mavuto dziko muno chifukwa achina chimwendo akupanga zomwe akufuna chifukwa omwe ali nd phavu zot angatsutse ndkulimbana nd mchitidwewu ndiomwe amapatsidwa kathaw kochepa mot idz zomwe mwapangapa zokaikitsa kut zikaphula kathu ku meneko
Ineso ndukaika kuti zitipinduliradi from south Africa CPT
a servant leader is supposed to be like what Chaponda has done osatengera feeling yanu kwa Chaponda as human being
That a good leader should be
Adakati president amayendela chochi bwezi tilipatali ndithu
Tamayakhulani zoveka ,mumenyera ufulu wa ndani,angopitani ku parliament ko mukapange ndalama zanu osati ife amphawi,komaso Inu mukhala kuti kuti muzifusa mafuso ambwelerawo.
Mbudz iwe ukudziwa chan
a chaponda kusowa zochita bas palibe chazeru pamenepo olo mutayenda man DPP
ayi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Aaaaa
Paja naeso aliboma ntchito zake zinali zomwezo za kuba siuja anaba ndalama za chimanga nkuotcha ma office kubisa ma umboni
0:25 Mayi navicha anali ndi molaroo izi zakalamba
Zoona bwana awawa atitola kwambiri akuchulusa zibwana ndalama zogulira mafuta kusowa koma zoendera kumakapanga zopoira kunja ndiye ikumapezeka bwana mukatifusile mafusowo
Ah inu munthu adaba chimanga lero mkulupilira ah Amalawi osamachedwa kuyiwala inu
Mutu ngati mbidzi
Mwayitha bwana
M'mukhulupirira bwanji uyu Mesa anabera amalawi chimanga
Koma sangapose okupha chilima uja
Ngati mumaba ndalama yachimanga ndiye lero mungapereke solution kwamalawi
Unatha mulandu umeneuja anauwina ndpo boma linampasapo zake
Mafuta atakha kuti afika mbuzi iwe
From leader of opposition to jornalist
Akulu inu mumachulutsa zoyankhula.mwapanga post kut tionele km ee
Anaponda chimanga awo aaaah
Koma anthu amadyabe olo aziba nkut chimangacho chimapezeka nkona amaba
Zaziiii, nthawi ya Bingu mafuta sanasowe?
Sizinafike apa kuvomereza ndikwabwino mwina iweyo ulibe galimoto sukudziwa momwe zikuwalira
Muchedwa kukamba zakalekale onani zomwe zili pa ground pano man
Kape ameneo akudziwa chan za mavuto a dziko munthu ndzatenge
Ngongol ndye akukunizan mugul ndi chani pano heheheh president opanda network uyoo mukhaul ndlm mulib mwatha kuba
Koma zinaz ,nde muganize kut chapondayo Mr kachimangayo mene wakalambilamu angakubwereseni mafuta
Nde nyau yakoyo yukanika kubweletsa bwaaaa???
Nde nhau yakoyo yukanika kubweletsa bwaaa?
Ai awapatsa mimba amako
Awawa amaba ndipo chimanga chambiri koma chimakwana timadya mokwana
❤❤
Zazi mimba lendelende kukalendela filling station ndikumanena kuti zithu zawavuta andani ngati muli ndikuthekela kuthetsa vutolo bwanji osapangapo Kathu osatenga bwanji mafuta anuwo ndikupala anthuwo zoyankhulazo sizitithandiza bwana tikuzi kuti mukumenyela nkhondo yanu osati nkhuthandiza vutolo ayi ndiye panganipo kanthu osati kukayendela anthu ndiye mwayendela ma filling station mafuta mwabwelesamo yankho ndiayi ndiyezulu zaluzilipati...
Chitsiru iwe mesa mbudz yako chakwerayo ndamene akulephera kubweretsa mafuta angokhalira kuba ndalama mbudz iwe gulugunyinda bwamtasa wachabechabe
Chigawenga chakwera amati akonza znthu asiye mafuta mesa president ndiiyeyo heheh wakhaul ndpo sanati ngongol ndye akuchikaniza pano hehehe boma ilo losowa mafuta simunati mumaon ngt chani heyiiii
Inu maganizo wanu wothandiza ndi wotani?
Chaponda ndi one ❤❤
Kumudzi kuno mwachidule njinga yamoto ndi ambulasi tikadwala malo amene galimoto singafikeko njingayamoto ndi thandizo lopezekelatu chonde anjinga zamoto musamawachite nkhaza
Useless Leader Of Opposition. Anatopa awa afunika panyumba pheee pachimpando cha ndalemba uku akumwa thobwa ndi zizukulu
Mmakwana bwana akafotokozedi bwino Achakwera Monday
Akuluwa adakalamba Palibe ndava po chanzelu
Akalamba ndagogo ako omanga mvula aja
Olo muyende DPP ayi
Nkhalamba izi what new could they bring to Malawians.
Abelekera mwana amako
Alindiutsogoler oganizira anthu osati zinazi zadyera, kupha ndizigololo
@@MacfelsonMunthali kkkkk koma ndipo. Basi azitiuza zinthu za 1940 zooona? Anyamata osewa? Kkkkk
Akalamba ndi amako ndi bambo ako
Mwachita bwino bwana
😂
Koma atithandiza achapondawa nphayi izi
Eeesh
Opposition leader must be vocal 🎉osati za ujentele
Iyaa awaa sakufaitila we are tired
Why is he asking obvious and stupid questions
Dyooooooo
Carthy maulidi penapake naweso mutu wako sukugwila bas kungokutola tiye uzikalemba za ma filling station kusowa zochita mwina
😂😂😂