BRIAN BANDA WAKUMANA NAZO PAMENE AMACHEZA NDI DR JOHN PAUL AKU MCP LERO PA TIMES EXCLUSIVE 28 SEPT

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 сен 2024
  • BRIAN BANDA WAKUMANA NAZO PAMENE AMACHEZA NDI DR JOHN PAUL AKU MCP LERO PA TIMES EXCLUSIVE 28 SEPT
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Комментарии • 180

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 5 часов назад +10

    Zoti ndi DR akudziwa yekha ,mbuli yeniyeni

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 5 часов назад +5

    kd 2014 amalawi amandya shitese ifuse galluyo asamaneney sa DPP

  • @dinchisale
    @dinchisale 5 часов назад +5

    Abambo awa ndi achitsiru

  • @Chikulamayembe57
    @Chikulamayembe57 5 часов назад +4

    This kind of arrogant talk is absolutely abhorrent!

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 5 часов назад +5

    The guy doesn't debate as an intellectual, he is just politicking there ,nothing else

  • @ChimwemweKamanja
    @ChimwemweKamanja 5 часов назад +4

    Ndimaona ngt John Paul ndidolo koma ndi mbuzi yeni yeni 😂😂😂😂😂😂

  • @ChrissyBhima
    @ChrissyBhima 5 часов назад +3

    Koma ngati kunja kuno kuli makhruku ndiye ndi masapota a MCP, blayani oloko iwe dzikoli sukuwona Mene zinthu zilili?anthu mene akudandaulira mavuto too much ndiye wina Kumati DPP singawine?kkkkkkkk Kodi muzavota pa family?samalani mayankhulidwe anu

  • @AkiduMakwinja-x1h
    @AkiduMakwinja-x1h 4 часа назад +2

    Don't blame Brian Banda of course he is independent.....called journalist so mukati muwona ndi Dpp yanu what you mean 😂😂😂.Boma la Chakwera lalephela complety

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 5 часов назад +2

    😂😂😂😂😂😂😂 Brian banda iweyo ndi katumdu watengesa kapolo uja kuno 😂😂😂

  • @HenzieChingombe
    @HenzieChingombe 5 часов назад +2

    Mcp 2025 ku opposition basi. Chakwela ndi mbudzi

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 5 часов назад +2

    Koma Mwaonjeza kuba ndalama zathu zamisonkho yathu 😂😂😂😂

  • @GodfreChayamba
    @GodfreChayamba 5 часов назад +2

    Chisilu ameneyo walephera nthawi yonse kuwina bwanji amuyamike yemwe anampha uja chilima

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 5 часов назад +2

    Mapwala ako iwe ulibe zelu iwe kapolo Brian mpase mafunso kapolo ameneyo

  • @NthawiKatanga
    @NthawiKatanga 5 часов назад +2

    MCP sizawina uyu ndi chisilu chamunthu anthu akudya chitedze

  • @AnockyDavidd
    @AnockyDavidd 5 часов назад +2

    Mbava izi pakilani get out you think Malawian ndi zitsilu.

  • @KelvinPhiri-z9d
    @KelvinPhiri-z9d 5 часов назад +2

    Sakanawina kupanda uja anamupha uja achokanso mu 2025

  • @KennKasonde
    @KennKasonde Час назад +1

    Kwacha !!! Kwacha !!!for what??? vibanthu vosayamika inu. Muyiwale za 2025.

  • @shenwaahabdulhakim
    @shenwaahabdulhakim 4 часа назад +1

    Mwana uyu anangoziyamba Sakufunikila banda apite ku Zodiak sakudziwa zomwe akulakhula 😂😂😂

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 5 часов назад +1

    This is an interview osati zaku zodiak, aaaaah uko😂😂😂

  • @CollngsNapulu
    @CollngsNapulu 4 часа назад +1

    Abulayan akuayisani thawi ameneyo mutayeni

  • @AnockyDavidd
    @AnockyDavidd 5 часов назад +1

    This is not 1960 mbuzi zanthu

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala 5 часов назад +1

    Hhmmmm.. awaso ndi amatukututu

  • @KalipentalaJamu
    @KalipentalaJamu 5 часов назад +1

    Akunama emeneyu akawalala

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 5 часов назад +1

    Boma losasiwa ikonome

  • @PhilimonThegha
    @PhilimonThegha 5 часов назад +1

    Ukunama iwe ine ndili ku south Africa mafuta kumalawi ndiwodura

    • @AbelBlack-f9q
      @AbelBlack-f9q 5 часов назад

      South Africa yake itio nawe 23r panga masamu ndizingat makwacha.mafuta ku Malawi ndi 2700pr litre.musamangonena nzamutu mwanu

  • @SandraBanda-hd1li
    @SandraBanda-hd1li 4 часа назад

    Brian. chonde. musamaitane,.. Zitsilu.pa.air. nkulu... uyuyu... Machende.. ake.. ndithu..... adzingodya.... ndalamazo....... Sawina

  • @HumblenessTafari-sc8xs
    @HumblenessTafari-sc8xs 4 часа назад

    Nkhani ikhale ya chakudya osati magetsi akulu akulu feteleza mpaka k105 ,000????????

  • @wisdomblack-u8n
    @wisdomblack-u8n 4 часа назад

    Brian akuluwo akulakhula zopusa ......zikuoneka kut amaganiza ngat mwana .......azakhumudwa APM akulamula

  • @NthawiKatanga
    @NthawiKatanga 5 часов назад

    Uyu ndichisilu kwambili munthu wakumudzi sangakwanise kugula feteleza mukuluza 2025,,,,mufune musafune chikangawa yambilatu kulongeza

  • @crispinekapenda
    @crispinekapenda 3 часа назад

    Ndipo mcp mudzagwa mochititsa manyazi,mudxathawa kuno,chilichonse chomwe tinakuikirani pa mpando simunapange,mulira ndithu,tikungokuonani

  • @mustafailanga2585
    @mustafailanga2585 3 часа назад

    Kunena kwandithendithe nanthabwe anazitengela achimwene tiona 2025 sichilima kulibe

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg 3 часа назад

    Brian musiye kapoloyi palibe chomwe angatiwuze ife zamuvuta kale apa

  • @charlesjimu6054
    @charlesjimu6054 4 часа назад

    Not what we expected from munthu olephera kuyankha mafunso chindunji.😮

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 2 часа назад

    😂😂😂😂koma ichiii yaaah chimbenene chenicheni,komaso ndanva ndi MWANADI

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm Час назад

    Akuluwa nzeru alibe sakudziwaso chimene akunena

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano 3 часа назад

    Mutadya ndikukhuta mumati DPP simayendesa bwino ziko lelo muwadyesa athu chiteze mukuti zilibwino mutuwako iwe

  • @JoyceJJames-kj7tg
    @JoyceJJames-kj7tg 5 часов назад

    Abambo inu ndichisilu kwabasi anthu mene akuvutikira. Kumadya .chiteze ambuye akuyendereni

  • @khoviwaedward
    @khoviwaedward 4 часа назад

    Koma MCP ndiye kuyalukatu, akusowa chonena chomwe mcp yapangira amalawi. Zamanyadzi kwambiri

  • @AbuduRajjabu
    @AbuduRajjabu 3 часа назад

    Kodi iwe John fusolo suwukuliva njanjiyo mwamanga koma mukuzemba kuyakha bwanji buludzi

  • @Ertyvhk
    @Ertyvhk 4 часа назад

    Malonjezo Anu alikuti ? Amzanu a DPP anapanga chitukuko muno fetereza 17 thousand PANO 130 000 tikakatenga kuti ndalama zogulira fetereza

  • @DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
    @DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 4 часа назад

    Ndizoona ine ndinachoka ku Malawi ndilikuno ku zambia magetsi amayaka five hours kenako kuzima 10 hours

  • @FamousJohnathan
    @FamousJohnathan 4 часа назад

    Economic analysis akukambayi sakuitsatanso.. Akukakamira nkhani ya njanji... Fertilizer ndi 96 thousand.. Wa kumudzi ndalama ngati iyi aipeza bwanji.. Akati global crisis, what does that mean?? Taona ndalama ya ma neighboring countries ali constant and stable. Nchifukwa chani every month kwacha yathu ikumagwa?

  • @charlesmbewe4001
    @charlesmbewe4001 4 часа назад

    Uyu ndi mbudzi ya munthu mcp chichokereni 1994 amawina otsangoyamika bwanji kuti kupanda uja amupha uja (Chilima) ndi zipani 7 bwenzi ali kuti?

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 5 минут назад

    Abambo awa ndi achitsiru mmutu mwao muli mamina

  • @Frank-q5i6v
    @Frank-q5i6v 4 часа назад

    Mbuli iyi ingochukusa phokoso ingamati amalawi tilibwino regime yakwera phwala lako wamva

  • @AndrewChibisa
    @AndrewChibisa 4 часа назад

    Machende ako bryani, Dpp idamanga ma killomiter angati? Umaba iwe vomereza galu iwe

  • @crispinekapenda
    @crispinekapenda 3 часа назад

    Join paul bwera ku mchinji kuno,akumaika matumba a dothi mu njanji ana mkumang'amba komanso kuno sitima sinafike,samalani polankhula ife tili mumbali mweni meenu,Do the basic needs pliz,Fertilizer wa universal 10 pin,Malipiro akwere,ndalama mukungogwetsa

  • @Hamilton-f2q
    @Hamilton-f2q 3 часа назад

    Kape ameneyo panyapake akudxiwa mmene tikubvutikila kumamidxi kuno adzamvota yekha dxakeyo

  • @GrevazioBanda
    @GrevazioBanda 4 часа назад

    Ablayan tilekereni tidzavota tekha mcp motooo chakwera 2030 woooo udzasamuka kuno kumalawi iweyo ndi pitala wakoyo

  • @LonexWataya
    @LonexWataya 3 часа назад

    Ndi chifukwa chani sanapange school Ku Malawi .olephera awaachotsiru awa

  • @LonexWataya
    @LonexWataya 3 часа назад

    Ndi chifukwa chani sanapange school Ku Malawi .olephera awaachotsiru awa

  • @FelixMpale
    @FelixMpale 4 часа назад

    Boma ili palibe chimene akupanga ndalama yagwa kwambiri komaso njara zinthu kudula ntchito kusowatu achoke

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 3 часа назад

    Abambo awa ndiachitsiru sakudziwa zomwe anthu akukamba kunjaju

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 4 часа назад

    Koma munthu ma degree mbwelera zake izizi aaaaah....Dr John muzitolere

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 4 часа назад

    Zikuonesa kuti cholinga cha pa RUclips macadet simuchidziwa uchisiru wakuchulukirani mumaona ngati Aliyese azikamba ndi zokomera inu umbuli,munthu Amene ukumupanga hate or atakamba zanzeru sumafuna kumvera

  • @prestonkasito1815
    @prestonkasito1815 5 часов назад

    Koma zoona lero mukukana kuti simunapambane mothandizidwa ndi UTM

  • @StellaPukutani
    @StellaPukutani 3 часа назад

    Ndiye mmene mukuonekeramu munaphunzira koma munthu osapita ku school akhoza kukuposa nzeru

  • @GrinTemboh
    @GrinTemboh 3 часа назад

    Amenewo ndi achisilu a Brian nsiyeni agwidwa manyazi alulephela kuyankha

  • @mustafailanga2585
    @mustafailanga2585 3 часа назад

    Anthu osayamika kupanda chilima bwezi mulindani

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 5 часов назад

    Uyu ndiwabodza zedi mwee koma akuti Dr choonsecho manyazi alibe mmmmm usawi chani???

  • @DavieAlumenda
    @DavieAlumenda 5 часов назад

    Palibe chomwe mukupanga a MCP koma kuonjezera umphawi dziko muno mungokakamira za njanji za fertilizer ukukanika kuyamkha bwanji chomwe mungadziwe amalawi simbuli zoti mungadzinamize ayi

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm 51 минуту назад

    Kkkkkk akuithawa ya fertilizer galuyo

  • @lisawillers7066
    @lisawillers7066 4 часа назад

    A mcp mudakakhara nonkha simukadawina muzinthokoza Dr Saul's Claus chilima ndi campaign yomwe adapanga pokopa anthu kut avotere tonse alliance yanu ndipo muyenera kumamuyamika mphanje yomwe adakumenyerani

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba 5 часов назад

    Brian umayenda mmbali, wakumana nayo DR John Paul. NZERU IZO

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 5 часов назад

    Dpp kumva nayo pain koma eesh. bwanji osanena zipani zinazi bwanji Dr onama awa vomerezani mwalephera inu.. Chikangawa..

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 4 часа назад

    Kamunthu koprpera kajeket kagala kumalankhula zopupyazo abale ako akufa ndinjala ube zambili ndalama zanthuzo uszadye moyo wako ose chifukwa zako chakwerayo nde tikumsesa posachedwapa

  • @AronLuka-ue5hl
    @AronLuka-ue5hl 5 часов назад

    PANO NDE ZILIBWINO TIUZENI, PANO A MALAWI NDIOKWIYA KWAMBIRI NDIMENE MCP IKUPANGILA ZINTHU ZAKE PANOPA A MALAWI SI MUNGATHE KUWAPUSISA MCP PALIBE AKUYIFUNA ANTHU ADANAYO KUKHOSI MUZIONA 2025 MWANYANYA KUBA BODZA KUWADYESA ANTHU CHITEDZE, ZIKHAWO MIYOYO IKUSITHA NDINU NOKHA MUKUBA NDALAMA BASI FETEREZER WA 18 PIN, RELO NDI 120 PIN PAMENEPO ZIKUYENDA

  • @MrcoolChachason-o6q
    @MrcoolChachason-o6q 3 часа назад

    Iwe machende ako ukuganiza Kuti MCP ingazawine?

  • @FelixMpale
    @FelixMpale 4 часа назад

    Chakwela it's nothing better DPP time was right

  • @LiffaChinkhota
    @LiffaChinkhota 5 часов назад

    Eya akunena zowona Boma ndilomweri ndithu koma tisintha chipani ndi president boma sitimasintha adziwe zimenezo galu ameneyu

  • @Jacksonmuhackeya
    @Jacksonmuhackeya 4 часа назад

    Chisiru ameneyi waba zambili ATI akufuna zioneselo aziona

  • @LonexWataya
    @LonexWataya 3 часа назад

    Ndi chifukwa chani sanapange school Ku Malawi .olephera awa

  • @AbuduRajjabu
    @AbuduRajjabu 4 часа назад

    Kodi inu njanji yake iti nanu simukulozatu zazelu pamenepo awawa akuziwa koma sanganene chilungamo

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 5 часов назад

    John Paul ndiwe Garu kwabasi lnu simudzalowaso m'boma

  • @lisawillers7066
    @lisawillers7066 4 часа назад

    Brian Banda you're number one to ask questions this politician are full of liars

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 5 часов назад

    Panonso ndife wokwiya kwambirinso kuposa paja pa dpp. Aonanso galu ameneyu. Zili bwino kwa iyeyo

  • @diversonkondwani2388
    @diversonkondwani2388 5 часов назад

    Chimutu chikulirenji koma nzeru palibe

  • @floncejeche8647
    @floncejeche8647 5 часов назад

    Sangati uze za Njanje yaku Mozambique chimozi mozi kuyimbila manya Mimba yoyipeza kumati ndimabeleka ine anthu akufuna sima not azakwayenizo

  • @YusufGunde-qy9tu
    @YusufGunde-qy9tu 3 часа назад

    Agalu amenewa akufuna achinyamatafe tiyambe kuvala ma bomba et

  • @FinasonSmart-j9d
    @FinasonSmart-j9d 5 часов назад

    John Paul siwakumalawi njanji amanga ndi a kumo sambiqi ifeyo mbali yathu

  • @LydiaMushala
    @LydiaMushala 5 часов назад

    Kuzaterera athu ndi maso .vote ndi mutima.aliyense ek ha ekha

  • @IddieMwanyali
    @IddieMwanyali 4 часа назад

    😂😂😂😂😂 kma uyu ndi nyani weniweni sakudziwa akulankhula

  • @MartinsilverChirwa-fv9wn
    @MartinsilverChirwa-fv9wn 4 часа назад

    Mtendere ubwerepo Malawi... God help us

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 5 часов назад

    😂😂😂😂koma galu ameneyu akudyadila akuti chimanga 45,,,m'buyomu 70000😂😂😂😂nanga feteleza akugula ndalama zingati kkkkkk akuti kuno kujoni mafuta ndiwokwela than malawi akunamiza omwetu alibe galimoto kuno ife tikugula 26 per liter,,,yomwe ikupanga 1500 mwk,,,ndiye kumalawi alipa bwanji per liter😂😂😂galu iwe kobasi

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 24 минуты назад

    Zitukuko akunena John ndizosapindulira munthu wakumudzi.
    Wanena za magetsi,njanji,miseu ya mu Lilongwe siingapindulire osauka mmudzi.
    Katundu wakwera kwambiri pansika komanso mismanagement ya public funds has worsen under the leadership of Chakwera

  • @DanielKatengeza
    @DanielKatengeza 4 часа назад

    Km iwe ndy pamtumbo ndithu John Kapito wamanyi ndithu

  • @AckduFackson
    @AckduFackson 4 часа назад

    Ameneyi galu kwabasi akukana zinthu akuziwa kt amalawi akuvutika kumakanika kuyankha mafuso osavuta ngat awa bulayan akuthera mawu Garu ameneyi ngat Dan lu uzapangeso interviews

  • @BlessingsManyamba-e6o
    @BlessingsManyamba-e6o 4 часа назад

    Keep on voting words people are watching

  • @diversonkondwani2388
    @diversonkondwani2388 5 часов назад

    John Paul ndiwe bulutu ,chidempete cheni cheni umunthu ulibe

  • @AlexChagunda
    @AlexChagunda 4 часа назад

    Kape wachabechabe njanji yake iti timuona Chaka chamawa kape amenei kwakwana

  • @AlexChagunda
    @AlexChagunda 4 часа назад

    Bambo akakwatira mkazi oti anakwatirapo ndiye ndikumakamba za mamuna amene wasintha nawe it means you don't have plans for today and tomorrow tawatulika kale awa

  • @ChitanMangon-c4j
    @ChitanMangon-c4j 3 часа назад

    Mbava imeneyi chaka chammawa Ku maula ndi mbuzi zimzake

  • @shenwaahabdulhakim
    @shenwaahabdulhakim 4 часа назад

    Iyi ndi mbala iyi koma tiona 2025 ngati sapezeka ku jele

  • @wisdomblack-u8n
    @wisdomblack-u8n 4 часа назад

    Ameneyo u Dr wake ndiwa ufitidi mwalasa

  • @JoseMasulan
    @JoseMasulan 3 часа назад

    Iwe ndiwe kapee tandzingopitan mukapephe uko

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 5 часов назад

    Sakanawina awa agaluwa awonanso sawina 2025 apm atipulumusa

  • @GreshamManda
    @GreshamManda 3 часа назад

    Iwe opusa kwambiri k
    Iwe Galu kwa basi

  • @StanleyMakombe-hy3fu
    @StanleyMakombe-hy3fu 4 часа назад

    Kodi kape uyu mwamutenga kuti 😅😅😅

  • @MichaelKachiboo
    @MichaelKachiboo 5 часов назад

    Koma zakuti anthu akudya citedze mukudziwa

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala 4 часа назад

    Munthu uyu ndisatana machende ako basi