And all of you guys are so special, real talent iyi guys! Iyiyo iyi ndi talent mbambande, you are touching many young souls. Bravo, lots of love to you all.
ati uyu ndani, SELINA she is Tadala ameneyo analinso chibwenzi cha BIMA kkkkkkkkkkkk henewe komano its behind the seen Sukuzwa iweyo Selina , mulibho guyz
Nkhan ya min bus yo ikumandipasa chidwi kwambir😂😂😂 My wife is a Doctor ndkuvuta kwa zinthu pa malawi ineyo chete ndimayendesa min bus yathu . This is real life pa ground the youth are living in denial.😂😂
Khaniyi kut ipitilile kukoma, Selina ndi hannareen akuyenera agwilizane chochita kut amukhawulise bhima alinukhe dziko avutike then azabwereranenso ndi Selina ngat banja ndipo mapephero aja azalowe pakat pawo kut bhima azakhale okhulupilika pa Selina. Then mulongo wa Selina azakwatilane ndi hannareen kut chilamu cha selina ndi hanna chizakhale chikupitilila. Inu mukuwona bwanji gys
Tadala is that you🤣🤣🤣 chete ngati sumabweza moto
@Selina, that was good to voice the mantle out, "kukuona iweyo ndi misozi Kwa ine"
Berthia, Sellina and Hanareen woooow, you guys are great actresses 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Mumakwana mukumveka uchita ukhala serious ngat zeni zeni 🎉🎉🎉🎉🎉 zilibwino koposa ❤
Berthia kuzichepesaa plus acting big up😢😢😢Selina received your flowers 🎉🎉🎉🎉🎉
I like Berthia. she really knows her role
Let's just accept that Berthia is real actor
And all of you guys are so special, real talent iyi guys! Iyiyo iyi ndi talent mbambande, you are touching many young souls. Bravo, lots of love to you all.
Nayenso Jerry😂 koma big up guyz
Koma apongozi ndiaphuma awo eeeh😂😂🙌🙌
Guy's mumakwana eish berthia ndipo umakhala serious pa zomwe ukupanga big up
Tadala tiuze chomwe umapiira kumeneko😂😂😂😂😂😂😂
Celina and Berthia are good actresses..
Very good very good our people
More fire gyz apapa mwandimaliza
I enjoy watching this😊👍
Berthia is really great actress, I'm really impressed.!
Baby baby kkkkk😅😅😅😅I love that 🎉
mbambande much respect to Berthia Maranatha not forgetting Selina
ati uyu ndani, SELINA she is Tadala ameneyo analinso chibwenzi cha BIMA kkkkkkkkkkkk henewe komano its behind the seen Sukuzwa iweyo Selina , mulibho guyz
Serious onsewa ma role awo amaatha mmm.big up guys
Serina is My best actress ❤
@bethia, efforts to apologize, so good, even if it may not be well received.
Uncle wa bima for the first time seem to be imparting some degree of sense into bima, za ku pemphera. That's good start morally.
Eeeeeeeeh gyz mukukwanisa iiiish 🔥🔥🔥🔥
Berthia and Serina wow Big up Girls ❤❤❤
Satana unachita kumpanga wekha 😂😂😂😂
Kodi mwasintha tsiku? Fukwa ine lachinayi gulani bundle yanga dikilani yeee kuli ziiii
Bethia ndika beautiful girl ❤ guys
I love your show guys keep it up😘
Koma Tadala kudekhatu ngati subweza moto😂😂
Hannah has to dress like Ali ku office not the casual
Bhima ndi chiwanda sangatheke.
Koma Selina big up u do everything so perfect dear mmmm respect
A bethia mwaonesa u serious nice one 😅sopano iwe tadala ukachite kufasa chomcho 😂😂😂😂 iwe ndiye upepesa liti
Ati satana wake wako unampanga wekha😂
Komaso zama love its most underrated drama in malawi
koma ndiyokoma heveee
Fact
Kkkkkk km Selina ndi Bethea kuli zithu
kkkkk Bhima uziyenda Limbe chigumula kkkkkkkk
Bethia umatha ase.
Kkkkkkkkkk you guys deserve an award honestly
Ngati zeni zenidi bethia eeh ngat ndilire😂
Ati bethia akufuna number ya uncle a bhima🤣🤣🤣🤣
Kom Bima uja ndi makina guys, akazi mpaka 4 at once 😂😂😂
Can't wait for next episode
Limbikilani guys mukutipatsa chimwemwe tikuonela kuchokela Botswana Capital city Gaborone
Ka bethia kakat kanvetse chison😂😂😂
Celina umatha please muzabwelelane ndi bima
Can't wait to watch the next episode,!
Uncle amunthu samayeneraso kumakakumanas ndi mkazi aaaa khalidwe labwanji
Wow! Bimah sadzatheka😊
Berthia iweyo kulimba ntima kukhala pampando ndi Selina ukufuna mbama chan
Following from pretoria guy you give a hint of Home kwathu nkokoma musazafe achina selina ,bhefia, Hannah nonse
Ka bethia kakat kanvetse chison😂😂😂L
Bethia satana wake anampangadi yekha😂😂😂
Mukafuna muthu oojezera ndilipo ine
Berthia ndiwa serious,,,,big up kkkkkk
Sellina mpaka mumpase munthu mbama zomwezi 🤣🤣
Zili nyatwa guys Koma just add ka nthawiko at least 40minutes love U guys all
Km Selina sakunama befia mwanyanya
Next maguys keep it up zamalove ❤❤
Maranatha eeeee
Nice 1 guys😍😍
Selina koma yiwyo umatha ndi saname umatimvetsa kukoma kwambiri komanso guys sewero munalijambula bwino munali serious ntchito yabwino
Keep up guys❤
Makwana guys😂❤
Nkhan ya min bus yo ikumandipasa chidwi kwambir😂😂😂
My wife is a Doctor ndkuvuta kwa zinthu pa malawi ineyo chete ndimayendesa min bus yathu .
This is real life pa ground the youth are living in denial.😂😂
Nice text fast plz
Mukukomesa Selina ndi anzako
Kkkkkkk phima kulibe kkkk Koma gayez kkkkkk katadala NDE kadekhatu 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Selina Mo fayaaaaa
Khaniyi kut ipitilile kukoma, Selina ndi hannareen akuyenera agwilizane chochita kut amukhawulise bhima alinukhe dziko avutike then azabwereranenso ndi Selina ngat banja ndipo mapephero aja azalowe pakat pawo kut bhima azakhale okhulupilika pa Selina. Then mulongo wa Selina azakwatilane ndi hannareen kut chilamu cha selina ndi hanna chizakhale chikupitilila. Inu mukuwona bwanji gys
Sellina nde umakwana aise
Ma guy acting mumatha that's nice
Izo💥
Ma girls awa eeee amakhwana
Zili bhooo
🤣🤣🤣🤣Tadala a Rasta 😂😂😂 Selina eeee 😂😂😂😂 team yose mumakwana
Berthia ur good actress 😅
Nice guys
Selina nkazi ofuna banja
A tadala adekhatu😂😂😂😂
Bhima osafulumile kugulitsa taxi please dekha Kaye 😂
mabusy ako Selina amandisekesa 😅😅 my favorite 🎉
Zogwiliragwila kuchuluka😂
24 ikuchedwa Abale😔😔😔
Tadala wafatsatu kkkkk
Tadala kudekha😅😅😅😅😅
Nice take bethia
Bethia ngati zenzenid tu😭
Nice
Kkkkkkk Selina you are going through a lot
Celina sakuyenera kukhululuka mophweka aaaa
Mukafuna muthu ndilipo ine 😅😅
Satana omupanga yekha😅😅😅
Maranatha eeee ai ndithu
Best actress
Dancan ati break thought yimeneyo kkkk conductor wa bima kkkk
🎉🎉
Koma berthia amatha kwambiri
Sellina mukhululukireni nzanu please 😅😅
Berthia akuvetsa chisoni abale😢😢😂😂😂
Ngati ulire munthu😂😢
😂😂😂koma Bhima wapezeka😂
Mukafuna muthu ndilipo ine 😅😅 18:51
Kuchimuna kulibwino
Berthia 🎉🎉
A Rasta😂😂😂😂😂😂😂😂