UTHENGA OPITA KWA MCP 20 September 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 ноя 2024

Комментарии • 105

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i Месяц назад +5

    No matter what chikangawa you can be president again in Malawi go away mr president chikangawa anthu akukudikila ku chipiku pls 🙏 😢 😀 😆 😄

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 Месяц назад +4

    CHAKWERA NDICHITSILU KWAMBILI AKUPITILIZA IZI CHITA CHIFUKWA AMALAWIAN SITIKUPANGAPO KANTHU AI TINGOWONERERA ZOPUSAZI NDALAMA MALO MOTHANDIZA ANTHU AKUVUTIKA NDI NJALA IYE AKUTENGA NDALAMA KUMAGULA ANTHU ZAWUTSILU OSE OYIMBA AMENE WAGULA CHAKWERA AMALAWIAN TIGENDE OSAWOPA TAFA KARE

  • @Antonyrobart-e3h
    @Antonyrobart-e3h Месяц назад

    Mr kalindo osaopa kumanga manga Manja ndimimyendo Samanga pakamwa 😊

  • @ChristopherJohn-u5i
    @ChristopherJohn-u5i Месяц назад +5

    Azatipase mtendele ndi yesu yekha amene samasitha ngati munthu komanso sakhumudwisa Amen

  • @StellaMichael-s4d
    @StellaMichael-s4d Месяц назад +5

    MCP singasithe ndiyamagazi bas akufuna asataniki awo

    • @ShammyBlessingsChisinga
      @ShammyBlessingsChisinga Месяц назад

      DPP munayiwala ma alubino munkapha aja zinali nkhuku zimene zija nanga Njaunje ndanga Robert chasowa

    • @jimmywhitecollins
      @jimmywhitecollins Месяц назад

      Kulibe chipani chopanda magazi issah njaunju Macdonald masambuka buleya lule alikuti. Muwatulusa kumpotoko

    • @fosternyirenda-wo4eb
      @fosternyirenda-wo4eb Месяц назад

      Ma albino mkaphaso ndinu.mesa muli mu Boma amangeni kaa ngat anaphadi ndi wooo

    • @JIMMY12CHIRWA-e6y
      @JIMMY12CHIRWA-e6y Месяц назад

      Chopusa iwe waiwara zomwe inapanga dpp ku Mzuzu

    • @JIMMY12CHIRWA-e6y
      @JIMMY12CHIRWA-e6y Месяц назад

      ​@@ShammyBlessingsChisingaosati ma alibio okha anapha azibale a2 ku Mzuzu 22 dpp

  • @jimmywhitecollins
    @jimmywhitecollins Месяц назад +1

    Osamangoti ndikudziwa kumene munakumana nenani dzina lamunthu malo ndidera osamangopusisa anthu. Iwenso ukudya ma burns a dpp

  • @jimmywhitecollins
    @jimmywhitecollins Месяц назад +1

    Mcp chiyambileni multiparty sinabeleko masankho usatipusise

  • @KennedyKanyama-ce8lb
    @KennedyKanyama-ce8lb Месяц назад +1

    Idzidzi ndizoonadi ineo ndimkangomva but now ndadzionera ndekha. Koma ndiyankhule zoona mcp is bard party this is true. Ma program anu kumangokhara oipa bas. Mmmmmmmmm this party mmmmm beyond athu oipa kwabas.

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift Месяц назад +2

    Tiyenazon bg agaluwa atitopesa

  • @VeroMpanda
    @VeroMpanda Месяц назад +1

    Olo agule dan lufan ndiye aphula chani

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano Месяц назад

    Komatu zikoli Sila MCP zikoli ndilathu

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 Месяц назад +1

    500 million kwacha kungoipeza all over sudden! Afufuzidwe and wapeleka ndalamayo ndani , waitenga kuti? Za Mai Chilima itayeni imeneyo. She is not the solution of Malawi issues.

  • @AnthonyZuzePhiri
    @AnthonyZuzePhiri Месяц назад +1

    bon 😊 i lov this man

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 Месяц назад

    Ife kuno kumpoto wathu ndi APM yemweyo

  • @VeroMpanda
    @VeroMpanda Месяц назад

    Olo agule anthu ochepa anthu amudzi alipo ambiri ndipo dpp moto

  • @SkeffaKaifa123
    @SkeffaKaifa123 Месяц назад

    DC❤

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f Месяц назад

    Ma cadet awa, kodi nthawi zose nkhani ikhale ya mcp basi. Dpp idaononga zinthu zingati agalu inu

  • @GanizaniCBanda
    @GanizaniCBanda Месяц назад

    Iweyo umangofuna kutchuka ndiwe kape

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym Месяц назад

    Ndpo iwe kalindo wamulimbikilatu Mery chilima yo azavotere ndani ndipo azapanga chani kutundu wa aMalawi zaziii 😮😮😮😮

  • @EmmanuelMphande-f4l
    @EmmanuelMphande-f4l Месяц назад

    Bon kalindo number one mcp matako yawo wose

  • @GabrielGasiyo
    @GabrielGasiyo Месяц назад

    Kalindo ulibe anthu okutsatira iwe olo Ku mademostrarion ako sikumaoneka munthu

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma Месяц назад

    Takusowani akalido mulibodza aaaaaaaaa iwe takudziwa n

  • @TomasDzifoole
    @TomasDzifoole Месяц назад +1

    Amene mukunena kalindo ndiwe opusa kalindo amanena zowona .

    • @jacquelineboya9529
      @jacquelineboya9529 Месяц назад

      Inde amanena zoona koma pali zina amanama uyu amatenga zamuutu mwake

    • @SlindiryLoveness
      @SlindiryLoveness Месяц назад

      Ndiye mumaseka nkhani or zina ndizaboza basi zonse tizivomeleza mwatani kodi ana apeter nonse basi mitu kusokonekera sitonse tikusangalara ndi peter wanuyo azathu akumwela mukufuna zonse zikhale zanu mumene boma wanatenga wapakati basi zinakupwetekani sopano ife akumpoto tipanga bwanjinkalindo nayeso ndi wa dpp ndiye alankhura chani chabwino cha mcp kpma zabwino zomwe boma likupanga wakuziwona koma kwayiye mimva palibe chabwino chimene likupanga boma ndiye basi tonsefe tizite inde bwana pamene zina tikuziwona zabwino zomwe boma likupanga shame on you

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Месяц назад

    Nkona anadwara

  • @MADALITSOKALUSA
    @MADALITSOKALUSA Месяц назад

    Bon kalindo ukunama achakwera sakunamizidwa ngati mmene amanamizidwa adad anuwo adad anuwo anakalamba ife sitikuwafuna zimene mukunenazo ndi zipani za lomwe kumpoto kulibe kulibeko zipani za lomwe muyiwona nyekhe😅😅😅

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift Месяц назад +1

    Ati agula Dan luu 500 milion,chikhariren athu akudya chitezi mm

    • @TiamikeMbalati
      @TiamikeMbalati Месяц назад +1

      You see ndeakuyembekedzera kuti Mulungu akhale chete never

    • @jameschiwanga
      @jameschiwanga Месяц назад

      Inu AWA NDI aboza AWA inu osakhulupilila zilizose​@@TiamikeMbalati

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi Месяц назад

    Dpp sidzalephela zisankho chifukwa lozani zanuyu amugula ai, osauka tonse tikudziwa amene tikimufuna.

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w Месяц назад

    Akalindo mulibe nzeru

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Месяц назад

    Anthu Akuda kumuvotela munthu kumuika paulemelelo inu ndikumadya chitedze.
    Ma MP Nyumba zomwe akumanga komanso magalimoto akugula ndi vote yako,
    President Ulemelelo alinawo onse uja ndi vote yako.
    Yet iwe ovotawe ndiwe osauka kwambili.
    Siyani kuvota zitsilu.

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma Месяц назад

    Iweyo ukamati amalawi ambili ngat ukudziwa kut mudzawina mukuvutikilanji dikilani

  • @TyconSululuwa
    @TyconSululuwa Месяц назад

    Abalalika ndipo akuganiza kt kugula anthu kuwapindilira , nthawi yathaaaaa

  • @EleosJari-s5r
    @EleosJari-s5r Месяц назад

    Kma yaaa

  • @jimmywhitecollins
    @jimmywhitecollins Месяц назад

    Palibe chomwe akunena boma ndilomweli 😅

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma Месяц назад

    Kodi ngat muthu walowa mukunena zonama inu bodzaloseli tatulukila Ifé simudzathetsa.mavuto athu aaaaaaa tatopanazo zonamazanuzo

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Месяц назад

    Ananena Chakwera yekha ku conversation kuti mutsogoleri wogula anthu ndikuti utsogoleri mulibe ndichizete

  • @JacksonSquare-us4bf
    @JacksonSquare-us4bf Месяц назад

    MCP ndi ma vampire 👹👺🦀🦞🐦‍🔥🐞

  • @giftsululu4274
    @giftsululu4274 Месяц назад

    Sapota wa dpp sasowa

  • @TiamikeMbalati
    @TiamikeMbalati Месяц назад

    Kd or atamugula Danyo Daniyo ndi Mulungu ndamene atapangise kuti chakwela awineso chakwera akuchokatu pampando or atagula oyimba onse zikomo koma chakwera akumuchosa pampando ndi Mulungu osadera khawa

  • @macksonmkandawire5718
    @macksonmkandawire5718 Месяц назад

    Winiko kkkk umphawi wavuta kwambiri

  • @EleosJari-s5r
    @EleosJari-s5r Месяц назад

    Kma wa nzeru ndi wa nzeru et

  • @user-cg5ml7ym4v
    @user-cg5ml7ym4v Месяц назад

    Dziko lathu ili manja mwa agalu

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 Месяц назад

    DPP woyeee

  • @ShammyBlessingsChisinga
    @ShammyBlessingsChisinga Месяц назад

    Umbuli okhaokha thoo munthu kulowa chipani ndiye kuti wagulidwa ? Osamazilimbisa mutima Apo mavoti apunguka basitu Apo ngati munali anthu ten kwachoka mumozi muziti muli ndi ten yomweo 😂😂😂😂 Apo ndi nine ndeye DPP musamalise kwambiri pamenepo inuo mukamaziona zopanda ntchito anzanu zikuyenda pakandafunda padajiwisa galu!!!?

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er Месяц назад

    Komanso ndalama ndi tsatana basi.a dan lu mpaka kulowa mcp😢😢komano adzavotera adad mopandanso kukayikira

  • @macksonmkandawire5718
    @macksonmkandawire5718 Месяц назад +2

    Marry chilima abweleso ndi boza la mamuna wake

  • @macksonmkandawire5718
    @macksonmkandawire5718 Месяц назад

    Azilima Ku mpoto bwanji sitidya chitedze

  • @ChimwemweKamanja
    @ChimwemweKamanja Месяц назад +2

    Umakwana Kalindo

  • @GIFTPAUL-c9s
    @GIFTPAUL-c9s Месяц назад

    Iwe ukhalira yomwe yomabwebwetayo😅😅😅😅

  • @OmexMasikoya-q2h
    @OmexMasikoya-q2h Месяц назад

    Waying"alura tsopano Kalindo

  • @MadalitsoIbrahim
    @MadalitsoIbrahim Месяц назад

    Dan Lu akukayimba zokupha chilima

  • @jacquelineboya9529
    @jacquelineboya9529 Месяц назад

    Za mery chilimazo ukunama bon kalindo😅?mery mwini wake anakana kuti sakufuna ndale nde anthu achita kumumanga chingwe? Khalani pheee ku UTM kutuluka mtsogoleli mbambande akazawina mery chilima azamupasa ntchito not kukhala president

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 Месяц назад

    Mboli yamako cadet wa dpp, ngati Dan Lu wagulidwa ndi mcp inu dzitsilu dza dpp osagula anu bwanji, nkhondo ilipo lomwe tithana nanu nyelo zanu

  • @andreakalambula7723
    @andreakalambula7723 Месяц назад

    iiiiii mcp ndilibe nawo mau

  • @ALEXSUBME67
    @ALEXSUBME67 Месяц назад

    Iwe nde ndani what have you done for Malawiu

  • @ALEXSUBME67
    @ALEXSUBME67 Месяц назад

    Za usilu basi inu

  • @WilbartMilezo
    @WilbartMilezo Месяц назад

    Chastity garu

  • @YoungsonmSimkonda
    @YoungsonmSimkonda Месяц назад

    Kalindo wazionesa kut ndwe wa dpp

    • @MalidadJaffalie
      @MalidadJaffalie Месяц назад

      Ndipo chilungamo munthu sangalemekeze prisdent osamphunzila

  • @YoungsonmSimkonda
    @YoungsonmSimkonda Месяц назад

    Mkuchedwa ndzimenezo akalindo

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 Месяц назад

    Dan lu ndi ndani so mu ndale achoke kumene

  • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c
    @GladysndilimbiraBonongwe-g6c Месяц назад

    Mcp ndalama zomwe Ali nazo ndi zogulira Anthu basi

  • @HalimaShafie-q9k
    @HalimaShafie-q9k Месяц назад

    Kalindo alibe chipan palibe ku zionesa kuti ndi wa dpp galu iwe

    • @hantosidira8720
      @hantosidira8720 Месяц назад

      Kalindo ndiwa DPP mukufuna mtinamize

    • @SlindiryLoveness
      @SlindiryLoveness Месяц назад

      Inuso munthu mukumuwonelathu kalindo kuti alimbali ya dpp ndiye lero mukukana bwanji

    • @HalimaShafie-q9k
      @HalimaShafie-q9k Месяц назад

      @@SlindiryLoveness iweso ndi wa mcp

  • @Daniel-cf4tu
    @Daniel-cf4tu Месяц назад

    Akalindo zilakhula zanu sizomanga or athu ena amakhalila kukuombelani m'manja koma zolakhula zanu ndizokhuza khondo wy?

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma Месяц назад

    Koma zoonadi tsilililose kumagotiuza khani zosokoneza athu bas ineyo tiludikila yesu bas zanuzo tatopanazo aaaaaaa apazaoneka kut mukunama tsopano

  • @ChisomoNthukwa
    @ChisomoNthukwa Месяц назад

    Koma zodabwitsa kut mukupanga izi ndinu alomwe okhaokha bwanji chikukuwawani ndichani asiyeni azani apange mbali yawo kupusa basi kuzikonda

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 Месяц назад

    ❤❤❤❤❤❤

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo Месяц назад

    🔥

  • @HalimaShafie-q9k
    @HalimaShafie-q9k Месяц назад

    ❤❤❤ the ddccc❤❤❤

  • @YoungsonmSimkonda
    @YoungsonmSimkonda Месяц назад

    Kod ndwe was dpp

  • @TemboHaswell
    @TemboHaswell Месяц назад

    Ngati ndichoncho zilibwinotu kt a mcp akachite manyazi akaone anthu mene akazazile ku nsonkhano wa dpp

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td Месяц назад

      Iwe ndiye wakamba iwe Malonda ndim'aso kumeneko MCP ingotumiza Wana chakwera sapita wakula ndipamene mudziwe Kuti MCP bomaaa ndilomweli gotani chimwendo oladi Musa akwana tambala Ali ndimoto pamutu wina akalira tiyeni konko tikakhomana DPP imadelera muona Ngati muliku mulanje kayiyambeni mudzadutsa Kuti simu Lilongwe tithana mukuchepela nyawu zathu konzekani tinyape alomwe pobwela kumeneko a police pumani tiombane Kaye apa

    • @CharityMhone-uk9ym
      @CharityMhone-uk9ym Месяц назад

      Mmmm inu Nanu 😮inu akupanga chan chikangawa wanuyo anthu akuvutika

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td Месяц назад

      @@CharityMhone-uk9ym you must work you think things will come before you work thinking about chakwera wauponda chakwera it's just a leader for the money we pay for him to eat by his house not his house but government House almost everything to him zathu zaulele Ku vota tokha ndiye wina WA DPP akuzifuna wadyapo kulibe bomaaa ndilomweli

  • @YoungsonmSimkonda
    @YoungsonmSimkonda Месяц назад

    Kod wabwino ndiuti

  • @KapitoDaire-n1h
    @KapitoDaire-n1h Месяц назад

    The DC

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Месяц назад

    Akalindo ndinu openga inu dan Luu sanalakwitse azikayimbila chinkhalamba chija nindani wazelu angayime kukavotela fundudwa ngati imene ija

    • @AmoTiamo
      @AmoTiamo Месяц назад

      Nawe mutu mwakomo uli misala

    • @GriperZimba-q5g
      @GriperZimba-q5g Месяц назад

      Dani lu ndindani kape malawi wafika poyipa

    • @dalitson3558
      @dalitson3558 Месяц назад

      Pantumbo pako ndi chikangawa wakoyo panyini pamako

    • @CliveChikaphonya
      @CliveChikaphonya Месяц назад

      Bambo Akonso Ndpo akavotero DPP iweyo ndkupusa kwakoko khala choncho

    • @AnthonyZuzePhiri
      @AnthonyZuzePhiri Месяц назад

      mmulibe agogo kod 😂

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg Месяц назад

    The Dc 😊

  • @YoungsonmSimkonda
    @YoungsonmSimkonda Месяц назад

    Zoona zake zit

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo Месяц назад +1

    Mulindi nkhawa mutha munthu wazeru akaona Kuti ukubkwaipa amachoka okha welcome everyone to MCP boma ndilomweli

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 Месяц назад

    Nthawi yonseyi ngat mumadziwa kut Dan lu anamugula, munkalekeranji kunena asanalengeze kut walowa MCP? Ndie chifukwa chakuti lero walengeza yekha kut walowa MCP ndie muzikati aaa ai amugula! Aaa ndinunachitsiru. Ndipo zomwe mukuyankhula apazi ndizopanda nzeru, mesa a DPP-wo ndiamene akumayambitsa nsankho kumanena kut MCP isadzapiteso ku kumwera, zomwe a DPP-wo amayankhula ku phalombe zija, bwanj osadzudzula zimenezijazi ukukanena za MCP? Kod basi umafuna kuyambanitsa anthu dziko muno chifukwa chot ndiwe mulomwe wakumwera? Activi wanji okhala ndi mbali chonsecho umati siwe wandale? Mmutu mopanda nzerumo, anakuuza kut Mery Chilima amafuna u president ndindani? Simupindula kanthu baba ndipo muphulika 😅😅😅😅😅😂😂😂

    • @SlindiryLoveness
      @SlindiryLoveness Месяц назад

      Kungochisiya chitsilu iyo chikungokhalira zomwezi azake aliphe uko basi pakamwa ngati chinakhala nthawi yayitali pamene chinali mwana wosalankhura ndiye chayamba panopa ndale si drama ndizithu ziwiri zosiyana

  • @GIFTPAUL-c9s
    @GIFTPAUL-c9s Месяц назад +1

    😂😂😂 nanuso mukuti abon kando muziona mcp ikuwinaso 2025 boma iloooooo

  • @ChristopherJohn-u5i
    @ChristopherJohn-u5i Месяц назад

    Mwakangalika ndikupanga zaziko lapasi,soka Kwa iye wobwelesa chokhumudwisa