USAUVER S08E08 MATABWA

Поделиться
HTML-код

Комментарии • 269

  • @ibrahimtutini5862
    @ibrahimtutini5862 Год назад +13

    Koma patricia ndi chiyambwe😂 chinachake amwene. anamukwatila uyu anawina ❤😂machine 😊

  • @Blavk-ic3
    @Blavk-ic3 Год назад +8

    @Piksy Tv. Mwatilakwila koma. 10 minutes siyokwanila😂😂😂😂 FIRE

  • @alinafemakandanje4687
    @alinafemakandanje4687 Год назад +3

    Koma Edo Edo 🙌😂😂😂🙌🙌🙌 uyuyu ndi🔥🔥 big up guys zili nyatwa Heve mukutimvesa kukoma 🔥

  • @SaeediAssedi
    @SaeediAssedi Год назад +1

    Munatengana odziwa nokha nokha...mulibemo mbola ayi...fire fire

  • @henrykankhokwe6652
    @henrykankhokwe6652 Год назад +4

    Ngozo kayimbo kakumapeto ndi sangie kaja katuluka lit🎉🥳

  • @tamandabanda909
    @tamandabanda909 Год назад +8

    Patricia never dissapoint 🤣🤣🤣🤣

  • @emmanuelmkuliwa1892
    @emmanuelmkuliwa1892 Год назад +4

    Akuti "Iwe Jede"🙌🏾🤣🤣🤣

  • @janemalama8433
    @janemalama8433 Год назад +1

    Belita, edoh , ntebe n Patricia iiiih magaye muli mwalaaaa🔥🔥🔥🔥❤️

  • @blessingskutchuwi8635
    @blessingskutchuwi8635 Год назад +1

    Awa Matabwaaaaaaaaaa koma ndasekaaaaaatu heavy....😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Chi ngaaaaauuuuuzaaaauuuuu on 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @crazynathan
    @crazynathan Год назад +2

    I am the first one to watch here

  • @VictorChinulaachebe
    @VictorChinulaachebe Год назад +1

    Ndunyemereni zingati Neba😂😂😂

  • @princejayhauledh3980
    @princejayhauledh3980 Год назад +2

    Koma ma minutes akumachepa guys, we love it

  • @blessingskutchuwi8635
    @blessingskutchuwi8635 Год назад +1

    Ashadoooo tizipanga Handleee....

  • @favornjolomole7756
    @favornjolomole7756 Год назад

    I love them all, they all portray unique characters 😂❤️

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 2 месяца назад

    The confidence from the Bar man❤❤

  • @vitumbikomphepo5237
    @vitumbikomphepo5237 Год назад

    Fire fire 🔥🔥 Patricia ndi one

  • @mechanicvin2921
    @mechanicvin2921 Год назад +1

    I saw belita kubalaka 😮

    • @mwaisambani1849
      @mwaisambani1849 Год назад

      Monday eti kkkkk ndie osandiyakhula bwanji??

  • @dimitabapu1097
    @dimitabapu1097 Год назад +2

    Men will be Men kuikilana kumbuyo Neba wa Mtebede siyamasewera😅

  • @serahmsuku3291
    @serahmsuku3291 Год назад

    Koma Patricia ndi nkhan zina😂😂...ndamusowa Albert koma❤️

  • @tazmeenmdals9904
    @tazmeenmdals9904 Год назад +1

    😂😂😂😂😂😂😂Koma sangie anakonza😂😂😂😂 this made my day

  • @ApatsaChikoti-fu4vg
    @ApatsaChikoti-fu4vg Год назад

    Nde mwati tidikileso next week or mwina mutulusa kena kati mwa week,,coz akaka nde mwakafupikisa heavy

  • @FlausyMijoya
    @FlausyMijoya Год назад +1

    Gani please 😂 ati akusanjiken

  • @zeliciachisale464
    @zeliciachisale464 Год назад

    Mwetu mwetu ngozi ndimatabwa akazi wanzako😂😂

  • @blesssyneck3677
    @blesssyneck3677 Год назад +1

    Komatu bar man ananena kale kuti iyeee cinsisi samapirira amakaulula 🤣🤣🤣
    Mwayamba kusisa ma mins aja kod afika pa 10 yokha basi!??

  • @preciouschagunda144
    @preciouschagunda144 Год назад

    Matabwa eti big up to Edo pati iwe unabwera aise 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @veromalawi8768
    @veromalawi8768 Год назад

    AEdo inuyo NdI one , good plan 👍

  • @hopeskafumbi2246
    @hopeskafumbi2246 Год назад

    Wow Edo kukwana guys keep it up akuti awo ili thako Kodi? Amwene simukuona kkkkk, I love you guys ❤❤❤❤❤❤❤amowa Aja akuitha koma guys chonde uzikhaladi mowadi akumasukatu malankhulidwe amvekele ndikumudziwa kale wapana ameneyi kkkkk

  • @lusunguhkayira6924
    @lusunguhkayira6924 Год назад +1

    Koma belita sanati...😂😂😂

  • @yankhochimwaza7925
    @yankhochimwaza7925 Год назад

    Eddo wandiwazaa shuwaa😂😂😂😂
    Patricia it's for me

  • @moniquepeachesmasi3474
    @moniquepeachesmasi3474 Год назад

    Ngozo iweyo unapeza aise🤣🙌🏽

  • @perealackson9879
    @perealackson9879 Год назад

    Ndapanga note kuti boys yonse ikumalenga kschibwibwi except ngozo haha

  • @ReginaMuha
    @ReginaMuha Год назад

    Its patricia for me😂😂😂😂 khani simamuthera😂😂

  • @rosinankhoma7820
    @rosinankhoma7820 Год назад +1

    Ganizani is de best actor guys😂

  • @angellamsewa640
    @angellamsewa640 Год назад

    😂😂😂😂😂 matabwa omwewo😂 i love Patricia mwee

  • @MilcentMchawa-iw3ve
    @MilcentMchawa-iw3ve Год назад

    Beautiful episode, love the sound track ❤️

  • @chrispinebanda7389
    @chrispinebanda7389 Год назад

    Chenkope I like his role in the video

  • @macksonchimalizeni44
    @macksonchimalizeni44 Год назад

    ❤ ati kukhala bar man mkulimba mtima 😂😂😂

  • @siskanyirenda
    @siskanyirenda Год назад

    Edo ndiye waitha amazolowela anthu amenewo Kuba ndi kupha anthu osalakwa

  • @bestonchimbuziphiri9400
    @bestonchimbuziphiri9400 Год назад

    Iyiyi mwatibera nthawi 🤣🤣🤣 Sizoonayi izizi…

  • @gophylgmw
    @gophylgmw Год назад +1

    Patricia ndi fire😂😂😂

  • @XclusiveRam
    @XclusiveRam Год назад

    Ati ali ndi chithako choposa ine eee koma chilungamo chake😂😂😂😂

  • @wysonnamaona6497
    @wysonnamaona6497 Год назад

    Koma za pa week kamodzi ngati ku church zi..... Aaaaaaa

  • @kondwanimaxwell578
    @kondwanimaxwell578 Год назад

    Zili bwino kwambili pa koma neba wa mtebee alibwino😂😂😂link ya nyimboyi tigaileni

  • @vandaichande8294
    @vandaichande8294 Год назад

    Mmmh koma lero nde mwaimana nthawi bwanj ❤❤😂😂

  • @kestonchikaonda1460
    @kestonchikaonda1460 Год назад +1

    Hahahaha man Mwabwera ndiina😂😂😂😂

  • @ChristinaMvula-
    @ChristinaMvula- Год назад

    Iwe jede😂😂😂😂😂ukundiziwa ndimadana ndizopusa😂

  • @grivinzamumtima8640
    @grivinzamumtima8640 Год назад

    Mwayamba kutionjezatu, atleast 20 minutes aaah

  • @XclusiveRam
    @XclusiveRam Год назад

    Mukatulutsa kumaponya ka link pa FB enafe timaiwara. Mwatani kodi?😅

  • @PhillipChauma
    @PhillipChauma Год назад

    Ati ukangondiona uzingosekelera 😂😂😂 Patricia ndakatundu🔥🔥🔥

  • @KhadijaCharles-i4g
    @KhadijaCharles-i4g Год назад

    Mwayambiranso kutumiza timavidiyo tatifupi 😢😢

  • @dancenmilos4356
    @dancenmilos4356 Год назад

    Aka nde katisiya mmaleretu😮

  • @williamsmhango3385
    @williamsmhango3385 Год назад

    Akusanjikeni ameneyo, akusanjikeni ndi manja

  • @MayesoChilongo-j6v
    @MayesoChilongo-j6v Год назад

    M'busa Ntebede Jebedaya😂😂😂😂😂😂

  • @Afropino1417
    @Afropino1417 Год назад

    Moto unandi 🔥🔥

  • @ellensaka5883
    @ellensaka5883 Год назад

    Aaaaa too short ngat isathe😂😂😂😂😂😂😂😂magaye keep the fire burning ❤

  • @lusunguhkayira6924
    @lusunguhkayira6924 Год назад +1

    Oh wow.. the barman..😅🎉😂❤

  • @samanthagausi6342
    @samanthagausi6342 Год назад

    Mukusangalala muli mwetu mwetu 😂😂😂😂😂😂😂

  • @chisomotolani1186
    @chisomotolani1186 Год назад

    Patricia ukhale mzanga basi 😂😂😂😂😂😂😂 walinyumwa thako

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk Год назад

    Koma a piksy mwachepesanso nthawi ija amatero nanga plz

  • @jeanmaele3528
    @jeanmaele3528 Год назад

    Eehhh man Edo mwampereka nzanu

  • @johnlufai2665
    @johnlufai2665 Год назад

    Kakumafupika.. mukumatisiya mmalere

  • @MoreenKanyenda
    @MoreenKanyenda Год назад +1

    Ngauzo and patricia my favorite❤

  • @CharityColletta-td3ls
    @CharityColletta-td3ls Год назад

    Patricia anabwera ndi mor🙌🙌🙌

  • @risingabove47
    @risingabove47 Год назад

    Koma a Edo 😂😂 kungopeleka basi

  • @wentozpombe9516
    @wentozpombe9516 Год назад

    Koma patilishayu eeee 😂😂😂😂😂😂

  • @FatimaSaidi-mz8fi
    @FatimaSaidi-mz8fi Год назад

    Gyz mukulakwisatu tipaseniko nthawi makosanaaa😂😂😂

  • @marymwantende7284
    @marymwantende7284 Год назад +1

    aNgozo ndopililaa ehh milandu daily😂😂😂😂

    • @rajabfrank2785
      @rajabfrank2785 Год назад

      kkkkk eeee komanso milandu yake ya serious😂🤣😂

  • @daviemindozo2933
    @daviemindozo2933 Год назад

    Ganizani mpaka chizungu 😂😂😂

  • @PercyChambwinja
    @PercyChambwinja Год назад

    Gan team chisokonezo kkkkk Edo big up

  • @DanielKaliati
    @DanielKaliati Год назад

    Title ya nyimboyo tipatseni tingaipeze bwanji

  • @manuelmbinju7105
    @manuelmbinju7105 Год назад

    Ma guy kodi pakati anapita kumudzi

  • @kondwanimakumba5778
    @kondwanimakumba5778 Год назад +1

    Belita😂

  • @leunardopaulo1917
    @leunardopaulo1917 Год назад

    Eee koma a yedo mumakwana anthu akuonjeza zopusa

  • @tonilipenga
    @tonilipenga Год назад

    😂Patricia please🤣🔥aty munthu alindi matako ake kuno

  • @tiyamikeemmanuelkabanga4105
    @tiyamikeemmanuelkabanga4105 Год назад

    Ati Ngauzo amayang'ana chan😅

  • @Clifton1993
    @Clifton1993 Год назад

    Mai ngozo awona matako

  • @ClementChisale-wl9xi
    @ClementChisale-wl9xi Год назад

    Mwationjeza mpaka 10min😢

  • @debbiekalima4541
    @debbiekalima4541 Год назад

    ati ukundiziwa nd adana nd zopusa🤣🤣🤣

  • @simeonkhamwaha8529
    @simeonkhamwaha8529 Год назад

    mwalamwala kom minutes aaa zikukhala bwanji

  • @kennethchikwenga8434
    @kennethchikwenga8434 Год назад

    Kod basi sikutuluka ma episode ena??

  • @joycesuluma5996
    @joycesuluma5996 Год назад

    Komanso banja la angozo😂😂😂😂

  • @harrisonmanyika3087
    @harrisonmanyika3087 Год назад

    Edo kumeneko ndiye kukhala osamasekelera anthu akhalidwe loipalo

  • @laisibukumatelesi1586
    @laisibukumatelesi1586 Год назад

    Komatu aunt pat😂😂😂🙌🙌🙌🙌

  • @redsonmuhuwah3490
    @redsonmuhuwah3490 Год назад

    Ganizani🙌🤣🤣🤣

  • @MphatsoChangata-zj5iy
    @MphatsoChangata-zj5iy Год назад

    Maneba ena akati akubhakire ngati ndiwe wakwao

  • @ZionneChidali-f7h
    @ZionneChidali-f7h Год назад

    Can i have this song pls

  • @SusanneKamwendo
    @SusanneKamwendo Год назад

    💥🔥🔥kma too short

  • @phunzirozilinde8530
    @phunzirozilinde8530 Год назад +1

    Lavuta ndi thako Patricia😂😂😂

  • @constantinechimodzichiwaul6907

    aah eddo kuaykhula gati chipagano chakale
    🤣🤣🤣

  • @vincentmwenenguwe8549
    @vincentmwenenguwe8549 Год назад

    Yafupika bwanji, kungotilawitsa

  • @ilanathema
    @ilanathema Год назад

    😂😂 matabwaa awaa

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 Год назад

    😂😂😂😂 nadziwa kuti nkhani imeneyi ikathela kuwaya

  • @lawrencekwilasha4951
    @lawrencekwilasha4951 Год назад

    Apaaa nde mwatipwetekatuuuuu aaaaaah

  • @taongachibwana9713
    @taongachibwana9713 Год назад

    Komatu nthawi ikumachepa aaa

  • @TisungeAkimu-n3m
    @TisungeAkimu-n3m Год назад

    Big up guys, angozo ati ili ndi thabwa hahaha 😂

  • @mikephakila
    @mikephakila Год назад

    Inu mukutimvetsa kukoma kumalawi kuno

  • @bernadettechoma
    @bernadettechoma Год назад

    Ili sithako????? 😂😂😂😂😂😂😂😂🙌

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 Год назад

    😂😂😂koma ndaseka Patricia 😅😅nsanje lmeneyo

  • @thocolate
    @thocolate Год назад

    Yafupika bwanji😂

  • @clementkanyangwa5460
    @clementkanyangwa5460 Год назад

    10 minutes yokha, mwatisiya mmaleretu apa.