BON KALINDO WAFUNSA FUNSO LERO PA 22 AUGUST KUTI MATAMA ONSE AJA KANI AMATHASO KUKWERA NJINGA?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 27 окт 2024

Комментарии • 154

  • @linley8719
    @linley8719 2 месяца назад +3

    I never miss your daily talks. Keep on being REAL. MALAWIANS need your voice and eyes. Malawi tavutika for too long. Yet we are a country full of human resources with HUGE POTENTIAL AND LOVE FOR OUR COUNTRY❤

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад +11

    The DC ❤❤❤❤❤ bon kalindo mwana woyipa kwambiri

  • @EneyaKakhobwe-tq3uy
    @EneyaKakhobwe-tq3uy 2 месяца назад

    Ng'alulayizeshoni booooooni kalindoooooo the DC

  • @GRAYJUMAHPHIRIE-n3h
    @GRAYJUMAHPHIRIE-n3h 2 месяца назад

    We all love you Mr Dc

  • @SherryJiya-c1u
    @SherryJiya-c1u 2 месяца назад

    Ulemu wanu honorable kalindo friend from liwonde

  • @anicakandiado
    @anicakandiado 2 месяца назад

    Ndipo iyeyu chomwe waona cha nzeru nkukayendesa njinga ku German? Asayendesa kuno njingayo bwanji? Ndiye ife zitipindulira chani zokayendesa njinga ku German pomwe kuno akungotigwetsera kwacha ife nkumasauka?

  • @EmmanuelZiba-qz6ug
    @EmmanuelZiba-qz6ug 2 месяца назад

    Am watching you from Lusaka Zambia 🇿🇲🇿🇲 kucharo 🎉🎉

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 2 месяца назад

    From Mozambique to Zimbabwe antill Germany how much did he spend muzipatala mabedi, mankhwara mulibe mzimu wothandiza anthu wovutika alibe, koma ziwani zoti nthawi yimasitha.

  • @linley8719
    @linley8719 2 месяца назад +1

    You are the BEST🌺💜🙌🏽💯🥇

  • @moyo77777
    @moyo77777 2 месяца назад

    Very true sir

  • @brianjames211
    @brianjames211 2 месяца назад +1

    Bon Kalindo ambassador given to poor Malawi from heaven for free.. Go Go Go

  • @wendyphiri9747
    @wendyphiri9747 2 месяца назад +1

    😂😂😂😂😂

  • @RabsonMwanza-d6m
    @RabsonMwanza-d6m 2 месяца назад

    Mizimu yonse 9 ikumuona mr chikangawa

  • @LeahChibwana
    @LeahChibwana 2 месяца назад

    Kikikikikiiiii koma Amoyaaaaa matong'aluratu!!!!

  • @LysonKumwenda-v1m
    @LysonKumwenda-v1m 2 месяца назад +3

    😅😅😅kulibe even company yopanga thabwa ya ndege 😂😂😂😂😂😂😂these is word make mi following u bon kalindo

  • @chancymkwanda-s4b
    @chancymkwanda-s4b 2 месяца назад

    Uyu ndi dolo koma vto sakambako momwe aphuzitsi akuvutikira....mphuzitsi kuchitidwa promote February koma mpaka PANO osasinthiridwa malipiro

  • @cacksygustarf6260
    @cacksygustarf6260 2 месяца назад

    DC❤

  • @happynyirenda8790
    @happynyirenda8790 2 месяца назад

    Zooʻna zoona man good speech

  • @MysonJussah
    @MysonJussah 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂 Ndege ya Manu kkkkk

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 месяца назад

    Kodi a Peter Mutharika angakwela njinga???? Ako ndi kachinyamata nsanje ikuphani,,,,ufuna udindo wauponda palibe udindo wako Bon kalindo vuto ulibe ivini JCE koma ukufuna udindo

  • @GodblessChikwakwa
    @GodblessChikwakwa 2 месяца назад +1

    😂😂

  • @LeonardDavid-tc5iv
    @LeonardDavid-tc5iv 2 месяца назад

    Push Mr kalindo

    • @MysonJussah
      @MysonJussah 2 месяца назад

      😂😂😂😂 Ndege ya Manu

  • @RabeccaChipeta-x7i
    @RabeccaChipeta-x7i 2 месяца назад +2

    Komartu amanena zoona dc mpamene tikumunyoza tidzAmkumbukila ndithu

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 месяца назад

    Funso,,,,,kodi a Peter Mutharika angakwele njinga???

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 2 месяца назад +1

    The dc is very strong man in malawi athu amenewo ndi amene tikuwafuna ku malawi zigawo zonse zakumalawi

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 месяца назад

    A Bon kalindo alibe fundo ndinasiya kale kuwanvela palibe chimene ma data anga akutengapo pa Bon kalindo

  • @mikelnorthern1911
    @mikelnorthern1911 2 месяца назад +1

    Kikikikikk😂😂😂😂😂😂😂 matama a vera

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx 2 месяца назад

    We are with you the DC

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 2 месяца назад

    Umakwana boni kalindo❤❤❤

  • @ChikumbutsoAntony
    @ChikumbutsoAntony 2 месяца назад

    The DC

  • @SHDRECKMALINGAH
    @SHDRECKMALINGAH 2 месяца назад

    Koma inuyo nda nyoooooodiiiiiii big up

  • @imraankambalame69
    @imraankambalame69 2 месяца назад

    Koma ambwiye chemuruphale 😅😅😅😅😅 iyayizikomo ambwiye

  • @JosephNambazo
    @JosephNambazo 2 месяца назад

    We just have a president but not leader like it or not i don't care

  • @WysonAnton
    @WysonAnton 2 месяца назад

    Kkkkkk uku ndy kung'alura 😅😅😅

  • @BosscoReston
    @BosscoReston 2 месяца назад

    Kkkkkkkkk km bon kalindo
    Umakwana koma

  • @CharlesMateya
    @CharlesMateya 2 месяца назад +1

    Yes maka yamdzio muibweleze

  • @VitumbikoTembo-b3m
    @VitumbikoTembo-b3m 2 месяца назад

    Simatama koma ndi nthawi akuyendamoyo ikuwoneka ngati matama

  • @PatrichaGolia
    @PatrichaGolia 2 месяца назад

    Umakwana do ❤❤❤❤❤

  • @LucyEndmond
    @LucyEndmond 2 месяца назад

    Kkkkkkkkkkkk koma ndaseka

  • @ArnoldChimtengo-c9z
    @ArnoldChimtengo-c9z 2 месяца назад

    The Dc mwana mulanje

  • @NaomiMagoha-uw7rm
    @NaomiMagoha-uw7rm 2 месяца назад

    Bt kumvetsa chisoni madera ena like Bangwe anthu kumamwa madzi apachitsime ngati simtauni

  • @ubs7030
    @ubs7030 2 месяца назад

    Iwe ndiwe chitsilu wava: usamanyoze chakwera, munthu amayenera akugwila ntchito.

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON 2 месяца назад

    Kuwononga mitsonkho yathu kumakwera njinga ku Italy koma umbuzi siyachikumba yokha iyiso ndimbuzi yeniyeni Mr chikangawa chakwera 😅😅😅😅😅😅

  • @EphraimNaveya-hz1du
    @EphraimNaveya-hz1du 2 месяца назад

    Chikangawa ndiwochitisa manyazi kenako azakamukweza wilibala zaziiii

  • @connexkathala
    @connexkathala 2 месяца назад

    BON KALINDO NDI KAPE UYU MXEEE

  • @TaweniChavulaKamwendo
    @TaweniChavulaKamwendo 2 месяца назад +1

    Boni kalindo puliz tandisiye ine chonde 😂😂😂😂😂 ndatopa nkuseka ine

  • @SamNkhomo
    @SamNkhomo 2 месяца назад

    Dyela azisongoleli

  • @CosmasBanda-ls8og
    @CosmasBanda-ls8og 2 месяца назад +3

    Kumalawi kuno nsanje idzatipha kwabasi, kudzikonda ndi ndi kudzikundikira, chavuta nchiyani munthu kukwera njinga aaaa

    • @ussimasi2458
      @ussimasi2458 2 месяца назад

      kaya kkk

    • @miccah81
      @miccah81 2 месяца назад

      Eti abale 😂😂 zinazi umangozindikila data yapita pachabe ndizinthu zozizila

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 2 месяца назад

      Muli ndi vuto ndinu anthu akupha inu

    • @miccah81
      @miccah81 2 месяца назад

      @@Eric-gb9ms iyi ndi social media akulu, osamapusa nazo

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 2 месяца назад

      @@miccah81 l don't care about social media bro the guy is talking the truth vuto anthufe timadana ndichilungamo

  • @MustafaLoyd
    @MustafaLoyd 2 месяца назад

    Ati what really happene wa chani😂😂😂😂😂😂 iwet ndiwa ntopola😂😂😂😂

  • @violetpotani
    @violetpotani 2 месяца назад

    Vuto utsogoleli wa matama, wamata 😅😅😅😅nthawi yolandira ndalama yo chonde a kalindo mudzandikondole😅😅😅, vuto kudzimva akamayenda ngati sanamweko madzi apachitsime

  • @raymondjustin1779
    @raymondjustin1779 2 месяца назад

    Kodi ameneyu ngotani? Chomwecho anthu abandu kuno amawalipitsa nsonkho

  • @CharlesBanda-pm2oe
    @CharlesBanda-pm2oe 2 месяца назад

    Boni kalindo chitsiru chamunthu,kuphatikizapo omwe amachemerera munthu wamisala,

  • @josemasiye3512
    @josemasiye3512 2 месяца назад

    Kalindo 🔥

  • @JosephyChisoni
    @JosephyChisoni 2 месяца назад

    Mboni kalindo winaso ndi umbuli sopano, mvuto simukisiyanisa zabwino ndi zoipa mukungofuna kutchuka bas

  • @jonaolex6221
    @jonaolex6221 2 месяца назад

    Osauka nzako ndani galu iwe uli mu hummer ...mabodza basi

  • @RichardDickson-bb6tc
    @RichardDickson-bb6tc 2 месяца назад

    Apa ndiye wationjeza nkuluyu

  • @FiskaniLungu
    @FiskaniLungu 2 месяца назад

    😂😂😂😂 dziko lotii even thabwa ndege lilibe😂🤣🤣

  • @SiboNkundi-hm1si
    @SiboNkundi-hm1si 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂😂 auze Bon

  • @MalonzoMazombwe
    @MalonzoMazombwe 2 месяца назад

    Hon kalindo tikuyamikireni, ntchito yanu yoimilira amalawi osaukafe mukuigwira, ndipo mwainu mulibe dyera.. mmbuyomu achina Ben longwe anaesetsa kukuonongerani mbiri kuti mumalandira ndalama kwa andale, koma ife amalawi tinapeza umboni kuti amakunamizilani.

  • @HafjulBari
    @HafjulBari 2 месяца назад

    What kind of president playing like that so which means he don't think about country why he's going to playing like that no no we must think guys his playing so much

  • @MackChimbageto
    @MackChimbageto 2 месяца назад +1

    Ndipo palibe fundo apa zamisala Basi zayamba relo pule kuenda pa kovoi

  • @OscarKathumba
    @OscarKathumba 2 месяца назад

    Ina ndi sanje naye kapolo uyu,, ukhala 5 years Ina ukutulutsa audio, MCP my vote

    • @samchibenene4458
      @samchibenene4458 2 месяца назад

      Yeah akhalira dzimenezi 😂😂😂😂

    • @MarkGonda-qr4vm
      @MarkGonda-qr4vm 2 месяца назад +4

      Enanu umbuli ndiumene wakula sindimakudabwani chakwela sitsogoleli sakudziwaso chimene akuchita

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 2 месяца назад

      Kapolo koma iweyo
      Ungafanane ndi a Bon kalindo iweyo
      Kuvutikaku kukuphetsani ndimaumboniwo Achakwera wo

  • @AhabKazota
    @AhabKazota 2 месяца назад

    A Bon Kalindo, Dziwani kuti nyengo imasintha. Nasuso kwerani yanu njinga

  • @IsaacMashambuza
    @IsaacMashambuza 2 месяца назад

    😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

  • @MustafaLoyd
    @MustafaLoyd 2 месяца назад

    😂😂😂😂nde wat ma MP a kazi 8.8

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 2 месяца назад

    Ulemu wanu Big

  • @CosimassShyman
    @CosimassShyman 2 месяца назад

    Boni kalindo inu mumakwanira

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 месяца назад

    KkK koma Bon

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 2 месяца назад

    Ndipo akanagwa

  • @NtchindiChirwa-l8o
    @NtchindiChirwa-l8o 2 месяца назад

    Chisiru chimandikwana heavy sanje basi ngat uli phawi osangopita kumunda kukalima bwanji

  • @MustafaLoyd
    @MustafaLoyd 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂 nde mwati vuto ma tttaaaaaamah😂

  • @KanyoleKanyole
    @KanyoleKanyole 2 месяца назад

    Zosekhala bwino

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 2 месяца назад

    Zaziii

  • @ubs7030
    @ubs7030 2 месяца назад

    Fuso lopusa limenero

  • @MussaNgoma-r2k
    @MussaNgoma-r2k 2 месяца назад

    Y you got body guards iŵeyo?

  • @JohnGeraid-t3n
    @JohnGeraid-t3n 2 месяца назад

    😂😂😂

  • @JamesDiston-x1f
    @JamesDiston-x1f 2 месяца назад

    Umatisokosela iwe anakumana unduna ndiye utikwanepo apa aliyese amachita matama ndimene wapezela ndi nthawi yake chakwela

  • @CharlesBanda-pm2oe
    @CharlesBanda-pm2oe 2 месяца назад

    Mbuli zimangolira chilichonse zimaganiza kuti munthu akakhala president basi chilichonse asiye aziwaphikira ngakhale nsima,Malawi womvetsa chifundo anthu ozolowera kupatsidwa chilichonse

  • @chrispinembewe363
    @chrispinembewe363 2 месяца назад

    Auze bon

  • @TshepisoNonyane
    @TshepisoNonyane 2 месяца назад

    The DC😂😂😂😂

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 2 месяца назад

    The Dc

  • @MonicaChisemphere
    @MonicaChisemphere 2 месяца назад +1

    Ine uyu amandi bowa sanje thoooo mcp my vote

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 2 месяца назад

      Go ahead
      Why you telling us
      Funk off

    • @jennyx6914
      @jennyx6914 2 месяца назад

      futsek

    • @FelixMachika
      @FelixMachika 2 месяца назад

      Go and mop the lake

    • @MikeMerecah
      @MikeMerecah 2 месяца назад

      Ndie utani chifukwa ndie Ali ndi anthu omkondatu meaning or MCP yakoo singapange mistake yomupha,

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 2 месяца назад

    Wamisala osagenda

  • @AhabKazota
    @AhabKazota 2 месяца назад

    Galu wachiwewe uyu adachita khungu sakuona🎉

  • @dalitsonjewa4868
    @dalitsonjewa4868 2 месяца назад

    Ndibwino kubadwa mphawi kudzafa olemera not kubadwa mphawi kudzafa mphawi 😮😮😮

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 2 месяца назад

    Achitsilu mmalo mothandza dziko akulisya mkumakazendewela njinga koma mmutumu muli nzeru?ma supporter mkumaombela mmanja chonsecho nao akufa ndi umphawi zikutithandza chian iz tangomupatsen kalindo amalize kwatsalaku kuendetsa dzikoli aaaaa

    • @EdwardRichman-zs5pl
      @EdwardRichman-zs5pl 2 месяца назад

      @@Biath-m4b zomwe wayendela kwaife ndizamphindu kwambiri km inuyo mbuzi njinga inuyo simungakwele chifkwa chamatama palibepo zachilengo km umbuli ndiuphawi ndi chifkwa mukuona ngati zolakwika

    • @Biath-m4b
      @Biath-m4b 2 месяца назад

      Mmene mumadyela ifetu tiliku magobo sitimalimbana ndi zimenezo zoti kuli njala mankhwala kulibe zimenezo zikusangalatsa amene dziko akulimva bwino koma kumwamba kudzayankhula

  • @FaysonChimbalanga
    @FaysonChimbalanga 2 месяца назад

    Ndikape bon uyu timachenji taku dpp tampengetsa ndiyekukwela njinga mchifukwa kkkkk koma masala inayi

  • @AcksonSimbeye-pm9po
    @AcksonSimbeye-pm9po 2 месяца назад

    Zikomo kwambiri bwana, mwatiyankhulila ife aku chitipafe ndipo tikuzunzika kwambiri ndinkhani ya mafuta, ndipo kulibiletu mafuta kuno

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад

    Akutherani bandu wakuuzani nindani kuti muvere zaziiiii zopanda nimuchere akuchita bwino kukupasanjinga akuziwa kare kuti ndiwe mbava inde karindo umatiyimira

  • @AyandaPhungula-bg9ql
    @AyandaPhungula-bg9ql 2 месяца назад +2

    Eish anatilodzayo ayi ndinthu adatilakwira ndinthu 😅😅😅😅

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 2 месяца назад

    Iwe karido ngati ulibe chochita tengani khasu pitani kumunda muzika sosa ndiwe mbwewa

    • @moniqb7373
      @moniqb7373 2 месяца назад

      Akupasani zingati? a Mr chikax anuwo?

  • @CathleenMsaya
    @CathleenMsaya 2 месяца назад

    Wayamba kabanza kunja

  • @chrispinembewe363
    @chrispinembewe363 2 месяца назад

    Ndipodi ndi amphawi

  • @JosephNambazo
    @JosephNambazo 2 месяца назад

    Sitikutanthauza kuti a president kukwela njinga ndi vuto ayi koma ndalama zomwe akuonongazo kumayenda ndi anthu ochuluka ku maiko akunjazo ndi misonkho ya amphawi yomwe ikanathandiza kugula mankhwala muzipatala inuyo simukuona nokha pamenepa anthu omwe ali ndi ana sangatenge kandalama kochepa komwe angathe kugulila chakudya ndikumakayendaka juga ayi apa sitikunyoza president but it doesn't make sense for a president leaving his own country and doing rubbish to other countries that's very nasty and not good at all guys be wise before you support this nonsense please

  • @MussaAndreQuenessi
    @MussaAndreQuenessi 2 месяца назад

    Auze the dc

  • @PETERSINKADZIWA
    @PETERSINKADZIWA 2 месяца назад

    Bon Kalindo ndi President wa Amphawidi

    • @EdwardRichman-zs5pl
      @EdwardRichman-zs5pl 2 месяца назад

      @@PETERSINKADZIWA mbali akwanuko osati enafe km mbuzi nu

  • @JosephyKhimbitoni
    @JosephyKhimbitoni 2 месяца назад

    Mavutowa mwawawona lero?vuto mumaganiza zopusa

  • @ArchangelMayesoGift
    @ArchangelMayesoGift 2 месяца назад

    Wamisala uyu

  • @UjEsithrHhloyd
    @UjEsithrHhloyd 2 месяца назад

    😂😂😂😂 koma moyo

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 2 месяца назад

    ukharira yomwey namabwebweta lwe onyooooooo