provoice kadandaula pa zomwe kell kay wayakhula pa live yake🙄

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 окт 2024

Комментарии • 15

  • @YoungScott-p7e
    @YoungScott-p7e 10 месяцев назад +1

    Ndinu nose amuna nokhanokha please khalani pansi mukambirane,osamasungirana mangawa chonde,we all love you guys

  • @EliasKamanga-y8l
    @EliasKamanga-y8l 8 месяцев назад

    Ineso ndi fan wako

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 10 месяцев назад

    Don't warry breddh iwowo akudziwapo kanthu

  • @AlexNchessie
    @AlexNchessie 10 месяцев назад

    Ukukhala ngati ukumukakamilatu Kuti muzicheza, move on bro

  • @ChifundoSikelo
    @ChifundoSikelo 10 месяцев назад

    Zalowaso matama mayankhulidwe Ako aise .... Uko usatitheleso bundle

  • @RhodaKalumbi
    @RhodaKalumbi 10 месяцев назад

    Naye Kelly mesa ndi opemphera chosungilana mangawa ndi chani

  • @phillipibandah9560
    @phillipibandah9560 10 месяцев назад

    Makape inu
    Akulukulunu mukabifana

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 10 месяцев назад

    Move on bro

  • @KeraMkandawire-pn5lx
    @KeraMkandawire-pn5lx 10 месяцев назад +2

    I don't usually do this, but ndamvetsera bwino mavoices onse awili all what I see is Provoice you New your friend was down he really needed you that time kwabasi And your silent was not good because you were supposed to be one of his comforters. And to Kelly blocking the person for long it's not a solution but dialogue it is, because that's when you enlighten each other voice out everything.

  • @VituIshmael
    @VituIshmael 10 месяцев назад

    Too personal

  • @CarolinaYusuf
    @CarolinaYusuf 10 месяцев назад

    Amalawi kumwamba akatikhazika pansi mwambo wachiweruzo usanayambe

  • @Ruth-y5q9n
    @Ruth-y5q9n 10 месяцев назад

    Chizungu kuphatikiza ndichichewa amalawi umbuli suzatitheladi Ngati mwabwela ndichizungu pangani zachizungu Ngati so mwabwela ndichichewa chimodzimodzi Kodi sukulu yophunsisa zilankhulo Za mix chihewa ndi chingelezi ilipati Pati kumalawi Kuno ndimafuna nditaiziwa pamene ili Koma zili apazi ndi zadziiii nzako Kelly nayenso wakamba zadziiii guys Choti mudziwe mukamapita kuusataniki kwanuko simumabwela Pano ndikufotokozela athu Kuti mukukalowa zausataniki Koma zikayamba kukunyelelani kumeneko mumabwela Pano ndikumati fefe kagweleni uko nonse ndimbalame

    • @jonasbanda5605
      @jonasbanda5605 10 месяцев назад

      Aaaaaaah ndiwe kape eti sudziwa kut ku xul za malawi timaphunzira ngezi ndi chichewa

    • @NathanMaunda-dz8gc
      @NathanMaunda-dz8gc 3 месяца назад

      Naweso xool imene amaphuzitsa kusalemba bwino ndiiti mmalo molemba chichewa walemba chihewa