ZOMWE A KALIATI NDI ANJAWALA AYANKHULA 6 November 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 6 ноя 2024

Комментарии • 30

  • @CAROLYNMALUNGO
    @CAROLYNMALUNGO 11 часов назад +2

    Nduona kuti Kaliati can be a nice boss

  • @ChawezChinkhuntha
    @ChawezChinkhuntha День назад +3

    First time seeing madam Kaliati not putting duku❤😅

  • @YohaneNthala-n9p
    @YohaneNthala-n9p День назад +6

    Ikani number ya Airtel money tikuthandizeni rimodzirimodzi

  • @ModreckKamiton
    @ModreckKamiton 19 часов назад +2

    Komatu muzidziwa kuti dongosolo lose momwe mumayendetsela pa program yofuna kupha a chakwela zaululuka uku

  • @lingstonenagoli7729
    @lingstonenagoli7729 День назад +3

    first person to watch

  • @LemsonManyowa
    @LemsonManyowa День назад +3

    Anthu Andale ndi inu osekesa

  • @chisomobelekanyama
    @chisomobelekanyama День назад

    Coordination in all aspects be it Central Committee or National Executive Committee (NEC) is paramount.Bravo for the outcome of the meeting

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw День назад

    Aaaa ndikuona ngati Cathy sadalakwitse masiku mwaonjezera chifukwa cha Dr Usi?.

  • @LydiaMushala
    @LydiaMushala День назад +1

    Manganese nde akupeperetsani muzalira ndithu😢

  • @zencoczimbiri2262
    @zencoczimbiri2262 День назад

    Ausi ndi anjawala Ali pamozi, Koma akweni chonde limbani kusunga ana amalemu saulosi asabalalike
    Muli njoka mu UTM 😂😂😂😂😂😂

  • @zencoczimbiri2262
    @zencoczimbiri2262 День назад

    RSA Koma AAA fisi ndi fisi
    Koma chenjerani , khola la utm muyenera kumanga molimba chifukwa ndikuwona Ku balalika mwaa

  • @LongweWily-x4k
    @LongweWily-x4k 3 часа назад

    Nice

  • @WillyMajiya
    @WillyMajiya День назад

    Good move...Dr Kabambe mukhaliseeeee together with Dr Patricia Kaliati

  • @JasonMailos
    @JasonMailos День назад +1

    Hot 265 simawilingula kwambi, mmangopeleka mutuwo basi, kumakosana akayamba kufotokoza amaonesetsa afotokoze hafu yanganiyo , Kande mkumavetsalaso chani

  • @TonyMhone
    @TonyMhone День назад

    Uyu Manganya uyu tichenjere naye akhonza kukhala chida chosokonedza UTM chipani chathu chokondedwa.

  • @StanleyMakungwa-t6f
    @StanleyMakungwa-t6f День назад

    No ya mpamba, bank or Airtel money ya UTM plz

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda День назад

    Utm muri zvipingirizvo zvakawanda,

  • @StanleyMakungwa-t6f
    @StanleyMakungwa-t6f День назад

    Tikamava choncho ife Kuno kumuz takondwa ndipo zilibwino

  • @gracemaluwa4674
    @gracemaluwa4674 День назад

  • @ChipiliroKasakula
    @ChipiliroKasakula День назад

    Mmmmm politics yoooh 🙌

  • @JemusRonald
    @JemusRonald День назад

    So my question my kaliati are you married

    • @TiongeChilongo-j4f
      @TiongeChilongo-j4f День назад

      😂😂😂😂😂 you want to marry her

    • @JemusRonald
      @JemusRonald День назад

      @TiongeChilongo-j4f because I say she is too much power like mn llove you mama god burns you get mor power

  • @zencoczimbiri2262
    @zencoczimbiri2262 День назад

    Pali Moto apo...

  • @SymonMwingitsa
    @SymonMwingitsa День назад

    100

  • @MatikiMatiki-r7c
    @MatikiMatiki-r7c День назад

    Mu umodzi muli mphamvu