I have been following you on Facebook, and today thought of checking your channel, I must admit, you are extraordinary, I love the follow of your stories, I watched some episodes with my Granny, he loved you and he said " dyomba dyangu adyu" 😂😂 sending you so much love from Mangochi, pesi Nyasa 😀
Aaaaah apa 2222 yakulowanitu apa Mwamusunga mwana bwinobwino kut malowolo adzayende bwino mwampereketsa pa K5.00😂😂😂😂😂😂 Chemandota phuma, Chiphwanya mabodza. 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Big up Big Boyz 🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkkkkkkkk ndiye mwati anthu 4 ngwangwa ndi chikwanje 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Today it is my first day watching this comedy and I'm already in love with che mandota
I have been following you on Facebook, and today thought of checking your channel, I must admit, you are extraordinary, I love the follow of your stories, I watched some episodes with my Granny, he loved you and he said " dyomba dyangu adyu" 😂😂 sending you so much love from Mangochi, pesi Nyasa 😀
Che mandola,mwaimilira Malawi pakali pano interms of comedy,big up
🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼 Mandota umagona Uli mu mkanjo ndi jacket 😂😂😂😂
Muli bwino guys.che mandota muli bwino you made me smile this morning
Kkkkkkkk mwabebesa inuyo 😃😃
MAndota team I follow you gyz
Eeee bas inu ndimadoro mumatha keep it
Bwana mandota ndi bwana chipwanya keep it up mumativetsa kukoma,anganga ajabilu mumaitha,anthuwa ndiokonda ndalama ngakhale malolowo amapanga choncho hahahaha lavusi olo gayezi, achipwanya tikumane pantaja bwa kkkkkk
Kikikkikiki plus hahahaha 😹😹😹😹😹 brilliant .mwagulitsa n dzukulu ndi five kwacha .
Fantastic combination following from Capetown balaka young man
Homie
Nice comedy love this👏❤
Number 1 combination ili bhobho kwambili
Mandota ndiwq kemesi serious 🤣🤣🤣
🤣🤣chemandota vuto lako ndichan kwen kwen u ankolo umeneo nde wabwanji,,,,
Ndiye mwati tilipo 4 kkkkk
Ntchito yabwino ndithu guys...
Kodi Iwe mesa chilima anakugulira Mano alikuti mwina sanali size yako
Ati mwaonekera 🤣🤣🤣🤣🤣 l know someone uncle can do this
Kkkkkkkkkkkkk Mwakumana Ndi tsotsi😅😅😅😅
Kkkkkkk 😂😂 kupeleka mkazi pantengo wa 5 kwacha koma guys khalani serious vuto phuma mandota 🤍🤍🤍🤍
Mumatha inuwo basi palibeso wachiyawo wangalusa
Mandota mupakana kupisila mukanju Ndakomoka
Nawe mumavuna kukuliza ngani uli in ndalama bwanji
Koma ndiye simofika mwawukali, money talks
Komatu apongoxi anga kkkk zili bwino une
Mmakwana madolo 💪
Munabwela mesa chemandota 🔥🤣🔥
Mbuya,mwapweteka😂😂😂
mumpasa bwanj biscuit biggy sakwanisa kutafuna
🤣🤣🤣
Pakabaza paka kunja kkkkk love you guys
Kkkkkk ndilowe ndi mad case
Kķkkkķk koma ineitu akulu akulu ibwele part 2 😂🤣
Kkkkkk wapita mtsikana pa 5 kwacha, achiphwanya akuti talemera tili ana kkkkkk mumatha guys
Kkk mumpanga mincemeat bwanji mwachedwa basi, koma nde mwabesa bwanji K5 😂
Tapeleka mkasi pa 5 kwacha 🤣🤣🤣🔥🔥🔥
Mwapeleka. Mkaz kamba ka. 5.kwacha kkkkkkkkk guy khalan srs 😂😂😂😂 mukacedwa mupeza nganga wapeleka. Mimba
Kkk🤣🤣🤣 mkazi wapita ndi k5
So fantastinc
Mmakwana
😁😁😁 che mandota I love this guy
😂😂😂😂😂zinapita ndi idi amin
Umatha aise mandota machinga simasunga kape
Mandota iweyo adha!! 😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkkkkk km mandota uyuuuuuu agreement😂😂😂
Chimphwanya Uli ndi maboza
Lero mwabwera bwino apa 12 minutes ndaikonda?
Akuti kumpanga soya pises
Hahahahahaha mumakwana makosana
Kķķkkkkk ndalama ndizina yasitha nkhani ija
Kkkkkkk a chimphanya akuyambisani ma boza a Che mandota
😄😄😄kukonda Ndalama 🙌🙌🙌
🤣🤣🤣🤣🤣🤣...kwachema 💥
You are best come
Hiii kutengeka Che Mandota ndi mzanu Chiphwanya 🤣🤣🤣 nganga Jabil akusewerani kkkk mwana nde mwapeleka🤣big up 😍😘
Unavapo kt airport ili ndiii matope
Moçambique
Nice 1!! Keep it up...#Talemela
This is nice but next time the director azachotse ma guy amene amaonelera kuti zisamadziwike kwambiri that ndi comedy
Tinayesa zimenezo and thats the best we could do.....anthuo sanali ochepa nde kuwachotsa ose sikunali kophweka
@@CHEMANDOTACOMEDY alright boss Mandota apopo ifeyo tafesesano ifetu we nyadira you
salute muthu wamkulu
😂😂😂😂 iwe ndi adolo
Mumakwana guys
Tionere zimenezi bas 🤣🤣🤣🤣
Kudikira part 2 ine pheee .
Make sure pamasamakhare anthu owonerera
Kkkkkkk ife sitimapanga sapaground ife ndi ama airport 🤣🤣🤣🤣🤣 mmakwana guys
Nice
Ziliboh
Mandota kukonda ndilama
mumaitiimilila che mandota
Madota ndili ndi game ndipase namba yako tilakhulan pa WhatsApp
Kkkkkkkk wabesa mzukulu
Kkkkkkkkkk umakwana mandota ndi jabilu
Iwe ndinu adolo?🤣🤣🤣🤣
Tilipo anthu 4 😂
Musapedwatu sindu sa sii..
YOU'RE LENGED DUDE
Best
Hahahhaha komatu clue iyi🤣🤣🤣😂
😂😂😂😂 vuto lopanga ant corruption beulo
Soya pieces yomweyo
Kkkkkk guy's Mandota group
Kkkkkkkk gys mumath daily
Team mandota💥💥
😅 😅 😅 😅 😅 😅 😅 😅 koma muli serious
Chemandota ni one
Amamwa zithu azangokunamizila kupha munthu🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂😂 agogo koma akupepelesano 🙆
Aaaaah apa 2222 yakulowanitu apa
Mwamusunga mwana bwinobwino kut malowolo adzayende bwino mwampereketsa pa K5.00😂😂😂😂😂😂
Chemandota phuma, Chiphwanya mabodza. 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Big up Big Boyz 🔥🔥🔥🔥🔥
Kukunyadilatu ine mandota
Katswiri mandota
Wawo
😅 😅 😅 😅 😅 Kma ndasekaaaaa
Haha haha haha haha😆😅😆😆😆😆
Kma chemandota wachiyao mmm ndalama izakupha ndithu money talk
Mandota
Mumantha guys keep it up
Hahahaahahaah koma yaaa
Tilemera tili Wana kkķkkk
😂😂😂😂 mwabetsa mzukulu
Kkkkkkkk 😂😂😂 waguliza chisukulu
So funny Che-Mandota
Kkkkkk mandota puma kkkkk
Hhaahahahaha Chiphwanya iiiiiiiiiiiiiiii
Inuyo mumatha ma guys. Keep up