Good concept 👍 big up to all performers,,, it has been sounding beautiful from the start..... Keep on coming with other teaching , advising, warning n entertaining ideas just like this 🔥🔥🔥
A very good concept, however it needed a warning to medical personnels not to get involved to such acts pang'ono, or kumapetoko ka langizo kameneko kamafunika kwambiri coz kuchipataku may be zimachitika in one way, orelse akanangomwalilira kunyumba kuja ndi Traditional doctor uja, it would have matched with the ending..... my views
Kkkkkkkk iyi yokha guyz eeeeeee ndiye mwapha mkuchita kukhumba kuti ikanakhala ya ola lathunthu ndithu........Jabilu, Mulelemba, make Maili, Kankhani, and mwini wake Mandota muli super guyz respect
Kkkkkk eshhh keep gud working brother mandota komas Mlelemb suzath thanks guys u made my day since we lost ur legends ISECK and jakob madoth unateng malo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mumakwana guys mlelemba ndiwe katundu mwana wamtonga from uk keep it up
Mlelemba my favorite...big up Mandota🔥
😂😂😂kwa amenene tikuwonerabe 2024 tipatseni like
😂 😹 🤣 😂 🤣 Komatu
Tisiya kubwerekana ndalama.
This girl called Ma Mayili she’s so best in acting I mean best actress🔥❤️🙌
Waojo bulasa ngani jine big up those who dont apreciate your work are just burukenges bro
Eish Mandota usazafe uzangophululuka phrrrrrrruuuuuhh🤣😂😂😂
Mumayitha ankolo 😆😆😆😆 thanks for bringing mlelemba madala
Chemandota ndi galu kwambiri 😂😂😂😂😂
Welcome back ma maili...u are my favourite in this
The good one 🤣🤣🤣🤣utenda wakula mpaka mundu kumuyendeza waphazi🤣🤣🤣🤣
Good concept 👍 big up to all performers,,, it has been sounding beautiful from the start..... Keep on coming with other teaching , advising, warning n entertaining ideas just like this 🔥🔥🔥
Aubrey Matiki is on a different level 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
😂😂😂mandota bwezani ngongole😂 koma episode iyi nde yandiwaza🔥🔥
Ma actor nonse plus make Maili ndinu madolo. Eee Mlelemba kukakamila🤣🤣🤣🤣
nice bro munasowatu mwabwera ngt coming inuyo mandota born again respect to u
Ma Maili is briant. Get your flowers. The whole act is awesome. Big up. Waiting for more
Kkkkkkkk mandota ur best act😅😅😅
Ukukomesa Malawi koma zikuvuta sapot broo ndinu 1
Kkkkkkk mandota you're best actor bro umandivesa kukoma
Angelo avala chani ngati mwamwaliradi komaso Angelo Gabriel pano alikuti😂😂😂😂😂 only these two questions from mlelemba make me lough
Eeeee mlelemba si munthu wamba kkkkkkkkk
Ati palibe zokwela kabaxa povaya ku chipatala uyenda yachimuna ❤😀
Muleremba eeeeeeish I don't know how I can say big up u r so brilliant
This is very awesome! Mlelemba n Che Mandota more faya
Munthu wakulu mulelemba 😂😂😂😂😂😂😂
Koma maliro awawa anali obebesatu🤣🤣🤣🤣🤣we need such honesty maliro walira yekha mkazi
💗💗💗💗💗🇲🇼🔥🔥🔥🔥🔥 more fire mandota squad... I loves you
Kulowa mu libokozi uli nd moyo zisopweka🤣 well done👏👏
Mandota you're the best wish to meet up with u bredah ulemu wenu mmwejo lafuzi yu tumachi
Mandota bwezani ndalama za ngongole🤣🤣🤣🤣
Big up🥰😘😘🥰 next time ndizakunjambuleni ndi ine ndthu for free🥰😘🥰
Ngongole kumaona kotenga 😂😂😂😂
Akudwala chani, akuti akudwala zonse🤔😅😅😅 safe container.
Takufilani ndithu
What an interesting comedy ever, big up guys. Koma ndmada nkhawatu ndmaona ngt wamwaliriratu mandota kkkkkkk
😂😂😂😂
Nice one with your manager that's a great act🔥🔥🔥
Taphunzirako as well
Big up Mandota kmano pliz pliz mwayazo nde ai zsiya kukoma sopano, macheza olowa m'bokosiwo ai Che Mandota
This is nice, keep up the good work,
A very good concept, however it needed a warning to medical personnels not to get involved to such acts pang'ono, or kumapetoko ka langizo kameneko kamafunika kwambiri coz kuchipataku may be zimachitika in one way, orelse akanangomwalilira kunyumba kuja ndi Traditional doctor uja, it would have matched with the ending..... my views
Mumakwana ...mudabwera kudzakhala inuwoo✌️🤣😂😂😂
Iweyo ndi more 🤣🤪💯 mandota umakwana
You are number one che mandota since I started watching you eish non stop laughing 😂😂😂😂
Okwenya ngongole akhale mlelemba hahaha
Kkkkkkkk iyi yokha guyz eeeeeee ndiye mwapha mkuchita kukhumba kuti ikanakhala ya ola lathunthu ndithu........Jabilu, Mulelemba, make Maili, Kankhani, and mwini wake Mandota muli super guyz respect
Big up guys, well organised everything completely good, mandota ,mlelemba and all crews guys musazafe muzangosowa
Well organized indeed anthuwa ndi a goat 🤣🤣🤣
This is funny, anyani mpaka kutenga fridge
The whole cast was on fire!!!
Che Mandota unandisisimusatu ndimawon ngat so wona kkkkk usamapange zimene so usandifa ndi mtima kkkkkkk
Kumaona anthu owabwereka ndalama mphakana amulelemba kkkkk
Big up elder 💓
Kkkkk Koma mandota your a best actor ma fumu matiki big up Malo akufunika Lilongwe
Palibe emwe amakharadi oipa akamwalira 😂😂😂😂🤣
Mlelemba is a legend, big chemandota mwayatsa moto pa Mw,
🤣🤣😂😂 film in film that's what we call real creativity. I like it mandota the best
Sanakhalepo wabwino🤣🙌
She Mandota mukonse mbiri yanu. Bayizoni Mulelemba zi mundu wozeweleza.
Nice one ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤che mandota❤❤😂😂❤
Mandota ndi wa sirious komaso nkazi wake ndiwolimbikira zedi. Zimenezi ndizomwe zimafunika, osamalekerana popanga zinthu!!
Umu phangala zinakumana kikikiki eeeeh koma naweso Mandota kotenga ngongole kunasowa Chan? 🤣 🤣 🤣 Mulelemba siopanga naye Masewera 🤣🤣🤣
Nice one...day maker che mandota
Nane ndiyambe sewero ndizamtenga mleremba
Ma maili ndi nkazi mbambande coz kukhara ndi mamuna ngat mandota eeeh ndi minyama yayikulu😂🤣
🤣🤣
Wangongole uyu ndi more🤣🤣🤣 thanks Che mandota muli mwala
Mwachena jesi ya fulemus kkk
Eeeeh kuthawa ngongole mwati😂😂
Ahh😂💔🔥ur the best in Malawi aseh
Great perfomance i just like the energy in it🔥🔥🔥big up che mandota
Nice video ulemu wanu 🙏🙏🙏
Ati munene kuti ambuye anatikonda😂😂😂😂
Amulelemba guys.😂😂.Ati ngat wamwaliradi nena angelo lero avala chani😂
Mpaka ndapanga comment kawili 😂🤣ur taking Malawi comedies at higher place 🙏
Unabwera kuzakhala receive ur flowers while u r alive❤
Kkkkkk eshhh keep gud working brother mandota komas Mlelemb suzath thanks guys u made my day since we lost ur legends ISECK and jakob madoth unateng malo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Q
Mwayesesa muli bhoo
Yomweyo big mumatipatsa chilimbkitso
Welcome back mandota, you made my night as you used to do masiku apitao 🤣🤣🤣🤣🤣
You are best comedian here in Malawi big up mandota and crew without you gyz Malawi is nothing
Kodi a inno build sakumapezeka ndi Malo ku Mulanje? Koma ndisaname umantha mandota keep it up
Mukafa muziti bushiri,,, zadara zooo kupanga act izozo muzifusa azanu ku Nigeria ana opusa kwambili
😂😂😂😂😂 Umakwana mulelemba
Big up Che Mandota ayilafusiyu tuu malichi
Nkhani ya Malo ija akufunika Ku Blantyre so tiuzeni machitidwe ake
Utambwali siwabwino,kkkkk...zilibwino ndithu as always
Welcome back tinakusowani big u r the best pano ndikumva kukoma
You r the best we really missed your comedies
Funny guys
I really proud of you Che Mandonda. Umandinvesa chimwemwe Inuyo. 😂😂😂
Umakwanila che mandota
So nice Mr mandota
I can't stop laughing. This is nice
Mwaitha guys ulem wanu ndithu
Ndita ndi Dolo ndinthu ❤
Wow!!!malowo akufunika..BT
Big up bro Mandota.... You always make me laugh with your good comedies 😂😂😍😍
Sikuti tsiku litha asana pepere uyu CHE MANDOTA😂😂😂😂😂😂
U guys muli mwala heavy mumativesa kukoma
Make ma iliii knows how to act... Ndakonda.. BIG UP MANDOTA
This lady acting as Mandota's wife is a good actor.
Mumatha azibambo kkkkk ndaseka nawo
Koma mpaka kupepha number azanu atamwalira inuyo anganga ndi one🤣🤣🤣🤣🤣
Wow! This real acting, big up Che Mandota and team
Mandota u made me happy keep it up
Koma ziribwino guys koma mlelemba plz osamamusiya kupanga naye comedy plz
This one made my day😂
I can't stop laughing 😂 laughing 😂 😂 😂
Njomba waonjo ni moreee