Nandikonda Mbuye - The Morning Star (Official Video)

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 2 дек 2024
  • Lyrics
    Verse 1
    M'mene ndinayesedwa, Ndinagwa mu uchimo,
    Yesu nandiombola 'ne,
    Nanenanso mau "pita usachimwenso",
    Nandikonda, nandikonda Mbuye.
    Chorus
    Nandikonda Mbuye, nandiwombola ’ne,
    Ndiyenera nane kumukonda,
    Nditame mwazi wokhetsedwa pa mtanda,
    Nandikonda, nandikonda Mbuye.
    Verse 2
    Kweza maso m’mwamba uwone chikondi,
    Yesu na-fera pa mtandapo ooh,
    Gonjetsa tchimo podalira mwa Yesu,
    Nandikonda, nandikonda Mbuye.
    Outro
    Nandikonda Mbuye, nandiwombola ’ne,
    Ndiyenera nane kumukonda,
    Nditame mwazi wokhetsedwa pa mtanda,
    Nandikonda, nandikonda Mbuye.
    -----------------------------------------------------
    Recorded by: The Morning Star, Kawale, Lilongwe, Malawi
    Audio Prod. by: Recall, Kuimba Mwamphamvu Studio
    Video Prod. by: Hope Channel Malawi
    -----------------------------------------------------
    Share this video:
    • Nandikonda Mbuye - The...
    Subscribe for more videos:
    / @themorningstar-mw
    -----------------------------------------------------
    Connect with us (subscribe and follow):
    Facebook: / themorningstarsingersmw
    Instagram: / themorningstar_mw
    Whatsapp: whatsapp.com/c...
    Spotify - spotify.link/E...
    E-mail:
    themorningstarsingers@gmail.com

Комментарии • 18