SKC ANAYANKHULA IZI ZOKHUZA MGWIRIZANO Vs ZOMWE TAMBALA OKUDA ANAMUCHITA👐👐👐👐

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 сен 2024

Комментарии • 15

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 8 дней назад +2

    God you are the only hope to our nation and let your will that has fallen upon us be 😢 Remember Malawi God in everything, let your spirit be revived in every person for better Malawi that will be filled with nothing but Joy and glee❤

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 8 дней назад +2

    John Tembo anakanitsitsa kuti sanapangepo mgwirizano ndi UDF. Panopa taonanso kuti otsatira MCPigs aja akukana UTM. MCP ndi ufiti weniweni.

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw 8 дней назад +2

    Ndinathokoza kwambiri MCP pomutaya mkulu ameneu MkaKa

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 8 дней назад +2

    Chakwela ndioyipitsitsa.

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu 8 дней назад +2

    Chikangawa mtendere siudzaupeza

  • @PatumaCassimu
    @PatumaCassimu 6 дней назад

    😢😢koma ziko ili ai zikomo

  • @GiftChitsulo
    @GiftChitsulo 8 дней назад +1

    Gona ndikuphe bwana munagona kwambili kupanga m,gwilizano ndi MCP siizo akuphanitu mwambi wanu omwe

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala 8 дней назад

    Misozi mason mwanga skc hhhmmmm tsiku Lina chilungamo tizadziwika

  • @TressLuka
    @TressLuka 7 дней назад

    Munthuyu ankanena zoonaditu ndipo mzimu wake unkayenda mu mchilungamo ndi ulosi 😢😢

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 8 дней назад +2

    Koma chakwera siukarowa kumwamba ndiwedi udamupha muzako mboloyako

  • @user-fm7yg5yc2c
    @user-fm7yg5yc2c 8 дней назад

    Mmmmmh koma dzikoli🙌

  • @Betty-fe9ql
    @Betty-fe9ql 8 дней назад +1

    Dziko 😂😂😂

  • @KumbukaniKafatia-cd2hq
    @KumbukaniKafatia-cd2hq 8 дней назад

    Anthu okupha inu

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 8 дней назад

    Mugwa nazo Malawi ndi dziko lina

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 8 дней назад +2

    Komat nthawi ikakwana or ngat umaganiza kwambiri sizimatheka umawonekabe osaganiza coz mmene timamudziwila chilima zot ungamamve izizi then mkumapitilizabe kumayenda ndi chakwera mmmm timadziwilat kut munthu ukamafa makutu amagotha ay. Rest in peace skc