M'busa Wa SDA Watula Pansi Udindo ..Litangotukuka Lipoti ... Ichi Ndichifukwa Chake

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 янв 2025

Комментарии • 230

  • @JeremiahHunga
    @JeremiahHunga 25 дней назад +25

    Thank you pastor Nyirenda to resign from this commission of inquiry

  • @AsiyatuPhiri-o5z
    @AsiyatuPhiri-o5z 12 дней назад +2

    Thanks our pastor TY Nyilenda for doing that.

  • @GeorgePatels-go7wj
    @GeorgePatels-go7wj 23 дня назад +7

    Thanks very much my pastor TY Nyirenda ,munachita bwino kuzisiya zimenezo pitilizani kulalikira uthenga wabwino anthu apulumutsidwe

  • @FrancisYesaya-w1b
    @FrancisYesaya-w1b 24 дня назад +3

    God bless you Mr nyirenda

  • @StevenJalifu
    @StevenJalifu 23 дня назад +8

    Kupanga expire mapepala sikuti ubongoso wapanga expire

    • @SidnChisanga
      @SidnChisanga 13 дней назад

      Exactly bruh

    • @SidnChisanga
      @SidnChisanga 13 дней назад

      Kod iwowo sankamuona kut ma paper Ake anapanga expare? Or zilichoncho iyeyu experience analibe

  • @TiyamikeMatias
    @TiyamikeMatias 12 дней назад

    God bless you Mr nyirenda to resigh

  • @TakalaniGlenda
    @TakalaniGlenda 20 дней назад +4

    My question is, where is the report from Chilimas family doctors?

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 18 дней назад +2

    Amachita bwino anyirenda kutula pansi nditu

  • @WisdomMsuku
    @WisdomMsuku 21 день назад +4

    M,busa uyu ndiwa satanic ndichifukwa chiyani amakonda ndare,ife mpingo wathu wa SDA samarora mpingo kuyenda ndiboma

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 25 дней назад +13

    M'busa weni weni oopa Mulungu mu choonadi anadziwa kuti mwazi wa Chilima usamukhudze akudziwa ndpo siku lina adzaulura choonadi bola moyo timva zambri sikunati

    • @HappyMajo-l3q
      @HappyMajo-l3q 25 дней назад +1

      Ndikugwilizana nanu

    • @Ackim-bq6ot
      @Ackim-bq6ot 25 дней назад +2

      Wadya kale ndalama palibe chomwe anganene

    • @BatChingoli
      @BatChingoli 24 дня назад

      Uyu watuluka atadya zaweni pamene Namiwa adachola ntchito isanayambe. Kodi akuuza ndani zotulukaku.

  • @courageouslondo1986
    @courageouslondo1986 25 дней назад +14

    Anafela mundege chabwino.chinawapha ndichani? Pot inali isanagwe?

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 25 дней назад +8

    That's bull shit , how can expired useless paper igwetse ndege ? Amayendetsa ndi munthu kapena pepala ? Nonsense

  • @ABOOBAKRIDRISSA
    @ABOOBAKRIDRISSA 24 дня назад +3

    Mapepala anapanga ex pure Kom oyendesa sanapange ex pure

  • @GovernorGeorge-r5n
    @GovernorGeorge-r5n 17 дней назад

    M'busa wa mnzeru kwambiri God bless you him

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 20 дней назад +1

    Ndipo chakwela iweyo iweyo ayi mulungu yekhayo akupase moyo wautali usazafe ayi uzagoosowa kt ziii

  • @McnovanceDaud-w6y
    @McnovanceDaud-w6y 3 дня назад

    President wa SDA mpaka kulowelera za ndale why koma

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 6 дней назад

    INU MBUSA WATHU SDA MUDACHITA KUTULUKA MUDACHITA MOSAMALA NDONDOMEKO ZAMPINGO,MWAONA ZOTSATIRA ZAKE ZOCHITSA MANYAZI.INE MBALE WANU MU UZIMU.

  • @Janaphiri
    @Janaphiri 24 дня назад +4

    Namiwa ndi Nyirenda anatula pansi Inquiry isanayambe.
    Thanks so much

  • @MartinNice-z9n
    @MartinNice-z9n 16 дней назад +1

    Anasiya chifukwa choti munali chinyengo

  • @RosePhiri-n8q
    @RosePhiri-n8q 25 дней назад +2

    Aliyese adachita kafukufuku wabodza payifa yachilima adziganizile ali iye olo mwana wake zamuchitikila mmmmmm amalawi kukonda ndalama koma azathu adataya miyoyo chifundo muzikhala nacho chakwera ndiwa kupha basi

  • @BerthaMkwinika
    @BerthaMkwinika 25 дней назад +3

    Kwaikika kwamunthu kufa kamodzi kenako chiweruzo

  • @ShantelMuwelah
    @ShantelMuwelah 3 дня назад +1

    Kuyinji tv

  • @AbabaBis-bk1ub
    @AbabaBis-bk1ub 25 дней назад +2

    Chikangawa,malawi sidzaiwala pa 10 june

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 24 дня назад +1

    Report ilili ndilopusa kwambiri chifukwa lakanika kuyankha mafunso mmalo mwake labweretsaso mafunso ochuluka kwambiri, tangoganizani akuti anthu aja adafa ndege isadagwe nde adafa ndichani? Chinaso report yoyamba yopusa ija idafotokoza kuti anthu aja adamwalira chifukwa chakuvulala kwambiri ndi kugwa kwandege,nde ndikufunseni amalawi olo mutakhala kuti simunapange chiwembu chilichonse koma ndi zopepera zomwe zili mmaliportizi muganize kuti chani?? Mudasewera game yopusa manyi akutherani chifukwa mzimu wanthu ndioopsa,ndipo be careful chifukwa Mulungu akukudziwani tsiku ndilimodzi.

  • @SteveniIvuta-x1q
    @SteveniIvuta-x1q 13 дней назад

    Koma guys chilima anapitadi 😭😭😭😭😭😭

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 25 дней назад +2

    Abisa zambiri ndie iyeyo sakugwirizana nazo eeeeee Koma ziliko ndithu

  • @ZexPetrol-tl4rf
    @ZexPetrol-tl4rf 24 дня назад +3

    Chonena tilibe angatimange 🙏

  • @DorisKanyang2607
    @DorisKanyang2607 20 дней назад

    God is good

  • @jameskasowa6790
    @jameskasowa6790 25 дней назад +2

    Iiiih Mr Nyirenda mwachta bwino kobasi koma how come Inu mudzpanga nawo zmenezo?

  • @GrayJailosiVelemu
    @GrayJailosiVelemu 4 дня назад

    😊😊

  • @HarveyYawandaChirwa
    @HarveyYawandaChirwa 25 дней назад +5

    Ndipo ineyo za lipoti imeyi palibe chimene palibepo chanzelu sindikunva nzimenezi ,chilima anachita ku phedwa basi

  • @Samkay66
    @Samkay66 23 дня назад +1

    Kkkk mpaka KaNyimbo pompo dii kkkk

  • @BranzeorMagwira
    @BranzeorMagwira 23 дня назад

    Only God Knows😢

  • @JohnSemu-c3h
    @JohnSemu-c3h 25 дней назад +3

    Ndege imanyenyeka ngat scrap choncho?? Komatu patsiku lotsiriza kuzakhala kuyaluka

  • @HashmHameed-qq4fj
    @HashmHameed-qq4fj 25 дней назад +1

    Ili ndi bodza a commission enquiry chilima anachita kuphedwa bwanji anakhala nthawi yambiri azanapite kukaona maliro a president wadziko mpaka kucha chifukwa chani angothenga black box ayike poyera anthu aying'alure

  • @JabesiNason
    @JabesiNason 24 дня назад +2

    Vuto lomadikirira ma results a inquiry muli kale ndi mayankho anu,,,, ingopitani pa ground mupange yanu commission of inquiry muzitiuza zochokera ku kafukufuku wanuyo osati zongolota mukakhuta ndalama za mabungwezo,, mbuziiiiiii

    • @AbdulNyambi
      @AbdulNyambi 24 дня назад

      Machendiyako mwana wasatanawe

    • @mishecksipolo7153
      @mishecksipolo7153 24 дня назад

      Mwana wang'ona iwe Kuala chete.udawonapo ngozi Yopanda magazi? Fotseki

    • @RemitterFlik1130
      @RemitterFlik1130 24 дня назад

      Mwana wa bakha ameneyu ndithu iwe umayidziwa ngozi iwe mutu ngati kamwala kokulungila nyumba

    • @veronicagullo9373
      @veronicagullo9373 24 дня назад

      Aaaaa nanuso muli ndi lanu tulutsanitu

  • @BrightDindi-c4j
    @BrightDindi-c4j 24 дня назад

    Kuganiza mozama, Rev Nyirenda

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 25 дней назад +1

    Dzikulilenji dzianan'gomba dzokwera patsrkera polemba ndi kunena bodza lotereri .

  • @RichardThera-i1p
    @RichardThera-i1p 25 дней назад +1

    Sinkhani yosangalatsa wanthu koma kafukufuku!

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 24 дня назад

    Yomweyo galu iwe Chikangawa party usampatse ndi mpatsa 😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂

  • @mutumwathongethonge7892
    @mutumwathongethonge7892 21 день назад

    Do not trust pastors today

  • @GiftMapirah-uu7tc
    @GiftMapirah-uu7tc 13 дней назад

    Anafa bwanji ndege isanafike pasi,anathimisa phone ndindani amafunika afotokoxe bhobho mmene inaximila phone

  • @PhlipsPhi
    @PhlipsPhi 23 дня назад

    Pastor Nyirenda amaopa mulungu.

  • @WelingsLongwe
    @WelingsLongwe 25 дней назад +1

    Enawa ukadaulo mwina alibe kukhala president wampingo amatumukila anthu wosiyanasiyana ndiye ngati Ali munthu wowopa mlungu wosogozedwa ndi mzimu woyera akamabwera poyera kufotokoza zimene anatulukira chifukwa woyera mtima sachita Matha ndi anthu ndiye inuyo kafuseni chifukwa chimene anatulukila
    Munthu kugwa kuchoka mumwamba anatha kumwalira akadali mmlengalenga ndipo zoti siyinayake ndege anafotokoza zifukwa zake Malawi tayiwalani za imfa tiyeni muzipanga Zina Kodi kanuko kulibe anamwalira ndangati amene mukadali kuwalira mpaka pano
    Inu muli ndi umboni kuti anaphedwa kapelekeni umboni musatinyase kunja kuno anthu tayamba kulima mvura tayamba kugwa ngati mulibe zochita bwelani ku mudzi tizizalima tithese njara

    • @KinosiKameta-ud1ps
      @KinosiKameta-ud1ps 25 дней назад

      Aaaaa

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 25 дней назад

      Forsake wena....timalira......chifukwa anthuwa munachita kuwampha😢😢😢😢

    • @JaneBanda-ht4ve
      @JaneBanda-ht4ve 24 дня назад

      Anthu inu mukufuna mukwilire chilungamo eti? Angella ananena kuti report amayenera kulemba ndi Patricia Kaliati, Odala ndi Angella. Mulandu wa Patricia Kaliati uli ku court, akayamba kuuzenga timva chimene ndegeyi inachita ngozi ndi kufa anthu onse. godfather anawauza Mai Kaliati ndi Angella kuti amuwuze Chilima asakwele ndege asanapasane moni wamanja ndi a President Chakwera ... Kuli nkhani ku court, zonse mukunamizira Chakwera izi nzabodza, nkhani ndi yoti UTM amafuna kupha Chakwera kuti Chilima atenge mpando, mwatsoka anaphophonyesa chizimba

  • @Eqrah-hj2nu
    @Eqrah-hj2nu 17 дней назад

    MCP iquary kumalawi mkokoma

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 25 дней назад +2

    Aaaa agalu a mcp awa lipoti la bodza chingomo ndichoti akufuna kuwaseka AMALAWI pakamwa thas why akunenaso kuti aliyetse anene kuti chilima anachita kuphedwa amangidwe kkk Anya nayo a mcp

  • @WalledgeChimphungu
    @WalledgeChimphungu 16 дней назад

    Ndekuti expired ya license ndekuti woyendesa nayeso adapanga expire kapena amankhala kuti waiwala tchito yake
    Chidawampha mu dege nchani

  • @LimzeySande-b9n
    @LimzeySande-b9n 13 дней назад

    MCP inapha anthu

  • @JohnSemu-c3h
    @JohnSemu-c3h 25 дней назад +7

    Komatu wina azathamanga ngat wapenga misala

  • @SamuelKhumbiwa
    @SamuelKhumbiwa 22 дня назад

    Chinsinsi mnchake Cha yehova,apatu zkuvutabe kubisa chomwe chinafela anthuwa.akupitiliza kuziluma luma,anali atafa ndege isanafike pansi chinachitika ndi chani? Anthu onse anafa umbon zot anafa isanagwe umbon umeneu autenga kt? Pot black box akt inalibe, munayikidwa poyizon kt zonse zisaziwike Amalawi anthuwa azigwilisa okha ndichifkwa chake Abusa ndi Anamiwa ataziona kt palibe chilungamo anatuluka kuopa sambi

  • @StanleyChamasowa
    @StanleyChamasowa 25 дней назад +1

    Mboliyake chakwela akamange amake munthu okupha oyipa anapha chilima

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 25 дней назад

    Ziko la Malawi kukhala maiko ena,mr chakwela,anganatula, kapena kuchotsedwa, ntchito koma chifukwa amalawi fe ndife ogona kuchokela munthawi ya weletsiki mpaka kamuzu kukhala president wa Malawi,mukuputsa mwathu momo mpaka ku democracy wooooooo

  • @thomphalavi5027
    @thomphalavi5027 25 дней назад +1

    Analakwitsa PA chiyambi kulowa mugulu ili

  • @NtakumbaNtara
    @NtakumbaNtara 24 дня назад

    Sda my vote ❤❤❤

  • @HalimaMussa-j6t
    @HalimaMussa-j6t 24 дня назад

    Muli mafuso osowa mayankho only got knows the best
    Mulungu sachedwa safulumila chouluka chizatela

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 23 дня назад +1

    Ada nyerenda anthu akuwongani

  • @BlessingsJulio-v5x
    @BlessingsJulio-v5x 17 дней назад

    Mene ndege imanyamuka muja imaonetsa expire wa pilot? Zoputsa basi osamanena chilungamo bwanji

  • @ALIEMUHAMMAD-yb4lr
    @ALIEMUHAMMAD-yb4lr 24 дня назад

    Chilima adachita kuphedwa boma lisamanamize anthu ndipo ine sindikuopa

  • @EphraimChinkhwangwa-vw7gg
    @EphraimChinkhwangwa-vw7gg 17 дней назад

    Kma inu mungalamule kuti a police amange wina aliyese ine kwanthu ndi kwa malembo apa tisaname kalipo biyeni akukudikililani kumwaku sure

  • @MartinNice-z9n
    @MartinNice-z9n 16 дней назад

    Chakwera akudziwapo kathu kmso chimwendo

  • @DorissLongwe
    @DorissLongwe 25 дней назад

    munachta bwno kuchokqmo mr tony Nyirenda

  • @LinlyMathewe
    @LinlyMathewe 25 дней назад +2

    Nde kuti anaona kuti chilungamo palibe monga munthu wa mulungu

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 18 дней назад

    Abusa mumakwana anyirenda

  • @PatumaCassim
    @PatumaCassim 25 дней назад +6

    😂😂😂😂😂kupanga exmpire kwa mapepera oyendesera ndege zigwilizana bwanji ndikugwesa ndege 😂😂😂😂 iiiiiii kuseka pakamwa anthu kudalira police 😊

    • @MaggieMasiano
      @MaggieMasiano 25 дней назад

      Eti abale inu

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo 25 дней назад

      Abale abale ndiyankhulileni mmmm

    • @ceciliasokoh3779
      @ceciliasokoh3779 25 дней назад

      Ndipo inu

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 25 дней назад

      Padziko lapansi palibe chisisi,, zonse zizaululika ufumu okubawo ukazatha,,

    • @JeremiahNgwira
      @JeremiahNgwira 25 дней назад

      Vuto anthu inu ndi Umbuli, mukuwona ngati kuyendesa ndege zili ngati kuyendesa galimoto?

  • @DalitsoGoliath-m2y
    @DalitsoGoliath-m2y 24 дня назад

    Choonadi chidzaululika pangatalike maka kma tsku lina chidzabwela pambalambanda

  • @gladysmanthimba7851
    @gladysmanthimba7851 24 дня назад

    Zikomo kwambiri abusa mwachita za nzeru

  • @MagieJames
    @MagieJames 15 дней назад

    Awina pobera mavote galu iwe

  • @TNMMobigo-k4w
    @TNMMobigo-k4w 24 дня назад

    Mulungu apitilize kukutsogolerani abusa pokuzindikiritsani choonad pakuti tonse tidzapira ndipo taona kudzati ziiiiiii!!!

  • @Felix-i7b1j
    @Felix-i7b1j 24 дня назад

    Ife timadabwa kuti kodi abusa apambana mmayesero apatsidwa pofuna kusankha pakati pa choonadi ndichabodza, koma abusa agonjetsa bodza alondola choonadi zikomo

  • @ChuluMsounds
    @ChuluMsounds 25 дней назад +1

    Well done Mr nyerenda

  • @chimwemwechimwanza
    @chimwemwechimwanza 25 дней назад +1

    A nyirenda ulaliki wanu umatisuntha mwachita bwno bigy

    • @fosternyirenda-wo4eb
      @fosternyirenda-wo4eb 24 дня назад

      Am the one ,ndimasuthidwa ndithu.mot nditamva kut nawoso Ali mkafukufuku obisa ,ndinakhumudwa nawo .koma pano am so happy

  • @YusufNdege-o2u
    @YusufNdege-o2u 19 дней назад

    Zikadakhala zamtendere sakadaleka

  • @MauriceFrank-g6v
    @MauriceFrank-g6v 25 дней назад

    Simunalakwisa pastor

  • @YusufNdege-o2u
    @YusufNdege-o2u 19 дней назад

    Ngat anafa isanagwe mchiyani chidawapha?Nanga nkhani za transponder zinayenda bwanji?

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy 25 дней назад

    Chakwera ndiyemwe anapha anthu onsewa,, why akufuna kuti tikhale chete,,chimo limadzuza uziwona ili ndidziko ndipo mulungu ndiye mboni,,,,

  • @MacdonaldMajohn
    @MacdonaldMajohn 25 дней назад +1

    Chakwera ndi Chimwendo udzingopanga zakongresi osati kumaikapo apolice ndalama dzanu mukudya nokha dzokubadzo lero apolicewo malipiro awo akuthera thumba lachimanga mwalowa inu mboma mwawakwedzera ndalama dzingati ?ndiye soap wakwera kangati,mafuta ophikira akwera kangati?umbuli ndiwomwe ukulamula malawi ,,malipiro ndi omweaja koma chilichonse chinakwera ndiye apolicewo alinadzo dzochipa kuti iwo adzikumvera dzopusadzo mmalo mokwedza malipiro awo kuti adzifikira katundu wodurayi ukuwatuma kuti adzimanga anthu iwe bwanji osamanga wekha ngati ukuona kuti munthu samavuta kumanga ndi ndalama dzakozo wayesa ndi agalu

  • @ListonePazani-is3ot
    @ListonePazani-is3ot 25 дней назад

    Analakwitsa kutuluka muguluro chifukwa timaona kt iyeyo ndimunthu wamulungu amene akadanena chilungamo mosaopa dziko lapasi,moti apapa sitidziwa Zoona .

  • @BertharrySecurity
    @BertharrySecurity 25 дней назад

    Olo atiseke pakamwa,Koma aliyese payekha chilungamo tikuchiziwa

  • @georgealabih8979
    @georgealabih8979 25 дней назад

    Chakwera munthu woipa satana weniweni eeeish kupha Vice wake zoona

  • @SudaisAwali
    @SudaisAwali 24 дня назад +1

    Koma guys 😂ationjezeranso mkwiyo😮

  • @MamagMa-r5n
    @MamagMa-r5n 24 дня назад

    Musavutike nazo ku mpingo kwathu sitipanga ndale wina asakunanizeni

  • @ThulaniPrince
    @ThulaniPrince 24 дня назад

    Apo wandisangalasa mubusa wanga chifukwa ndinankhumudwa kwambiri

  • @Hambalisphiri
    @Hambalisphiri 22 дня назад

    Boma la anthu amisala ili asatana

  • @PkKumbokola
    @PkKumbokola 25 дней назад

    Mapepara kupanga expire it doesn't mean she can nor operate

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 18 дней назад

    Ndale nsapansi pano

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 25 дней назад

    Ngati atula pasi udindo anyirendawo pilizi abwenze ndalama zamagazi

  • @MacpharryMilanzi
    @MacpharryMilanzi 24 дня назад

    Muluzi atatenga ulamuliro kuchoka kwa kamudzu anafukula mafupa achina gadama
    Matenje
    Sangala
    Koma nothing was done ndye izi tizingotaya nazothawi tisayembekezere kuti wina azabwera kunena kuti anapha chilima ndi uje never ngakhale chakwera akazachoka palibe azamupeze olakwa pakhaniyi
    Musiileni namalenga
    Ndye mwini kuweruza
    Apa vuto poti chilima anakakhala munthu wamba khani panalibepo apa
    Ndipo palibe yemwe amakoza ifa ndi chauta yekha amene amatipasa masiku okhalira padziko pano
    Koma ngati masiku ako sanathe sungafe zitavuta bwanji
    Inu ndi mboni munthu amatha kuchita ngozi yagalimoto iwe kuiona kumati koma mwatukuka wamoyo umu eeeee watuluka ngakhale kukandika palipose alibe

  • @Moseskhutse
    @Moseskhutse 23 дня назад

    Nkukuyu machende ako galu iwe unapha witika sungayankhule zazeru

  • @IanPearson-o6l
    @IanPearson-o6l 25 дней назад

    ndagaluso nawo a equarery-wo

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve 24 дня назад

    Kafuseni mwana wa pailot uku uzani zonse

  • @khumbotembo302
    @khumbotembo302 25 дней назад

    Wina azamangiwa pa nkhani yomweyi, nthawi ikubwera

  • @JamesLigomeka-en6zx
    @JamesLigomeka-en6zx 25 дней назад +1

    Esh km boma limeneri ok

  • @DavisSeyani
    @DavisSeyani 24 дня назад

    Abusa odziwa kuti kunja kuli Mulungu

  • @Ridisoni
    @Ridisoni 10 дней назад

    Kulinji

  • @NamuthuwasebastianoDaniel
    @NamuthuwasebastianoDaniel 24 дня назад

    Mm mm mm mukuganiza bwanji kuti muzimanga anthu ?????? Mm mm mulungu akuchitileni chifundo

    • @MEGANABIGAILKMNTHALI
      @MEGANABIGAILKMNTHALI 21 день назад

      Mukati mulungu awachitile chifundo akuphawa nde amaliza kupha anthu koma ndikupempha mulungu kuti onse achite nawo monga anachitira ndi nkhondo afarao

  • @madalitsomakawa9708
    @madalitsomakawa9708 25 дней назад

    Abale nyimbozo mmm so disturbing sankhani kuchita chinthu chimodzi.

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 22 дня назад

    Ndege ya 19 people munalowa anthu 9 ndiye idzadza bwanji kuti Chimwendo asalowemo?

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 25 дней назад

    Okondedwa kuwakakhira anthu ena ku imfa sikuchenjera anthu onse omwe akukhuzidwa ndi imfa imene ija mkwiyo wa mulungu awuona ndithu!!!!!!

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 25 дней назад

    Chakwela walemba mumadzi achule awelenga sangamange munthu amalawi panopa anapenya ndimangeni ine ndanena kuti chakwela anapha chilima

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 25 дней назад

    chati delu,chaopsa a TY Nyirenda eeeeish, report ili ndi mbola 😢😢😢

    • @ceciliasokoh3779
      @ceciliasokoh3779 25 дней назад

      Inetu nditangoona abusa awa ndinalimba mtima kuti report likhala bwino ndikaona mmene amagudubukira ndi bible akulu awa mmmmm koma ndalama ndi satana