Charles Nsaku - Mournıng Luck Dube - Part 3

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 3 дек 2024

Комментарии • 19

  • @tobiousnyirenda4570
    @tobiousnyirenda4570 3 года назад +4

    Nsaku, one of the best musicians.... Mumaitha, kuposa zonse muzitamanda wotilengayo

  • @robertchakwira7079
    @robertchakwira7079 2 года назад +1

    Mr Muluzi was realy the president i chose to never vote for someone else but him. NSAKU my ONLY favorite muzician in Malawi

  • @bilalisipikini8061
    @bilalisipikini8061 6 лет назад +2

    Nsaku bwelera Ku Malawi bingu anamwalira peter zangakumange sizikwakhudza, bwekerani uzikaimba nyimbo zanu timazikonda kwambiri

  • @doreenkhembo7718
    @doreenkhembo7718 Год назад +1

    Kd ulipo mwa goti ziiiii

  • @lazaruspias86
    @lazaruspias86 Год назад +1

    Takusowani a Nsaku, tabweraninso nyimbo zanu zasowa.

  • @benitocazota296
    @benitocazota296 7 лет назад

    Kuimba ansaku adasiya,lero akungothawa thawa.Avekere Ali Ku south Africa ena akuti ai Ali m'malawi mumuno kkkkkkkk

  • @WalidWilliam-t4h
    @WalidWilliam-t4h Год назад

    Yaa ney. I got breaking news now sure 😂

  • @yusufjonas5088
    @yusufjonas5088 7 лет назад +1

    Mwasowatu a Nsaku

  • @WalidWilliam-t4h
    @WalidWilliam-t4h Год назад

    Timtame MULUNGU.

  • @edwarddixies3618
    @edwarddixies3618 6 лет назад +1

    Nsaku ndi katundu

  • @nonotamlaz3409
    @nonotamlaz3409 3 года назад

    Nsaku ndi mashini palibenso

  • @delgodutoit116
    @delgodutoit116 6 лет назад

    Chamba tchinakupweteka mwana iwe

  • @noelngwira1113
    @noelngwira1113 5 лет назад

    Kutha kwake kunayambila pamenepa

  • @lazarustembo7398
    @lazarustembo7398 6 лет назад

    Where are u sir

  • @ClementinoAnerio
    @ClementinoAnerio 7 месяцев назад

    Aqui zilibom tumizani só nyimbo zinanso zakale kale

  • @yamikanimdala5955
    @yamikanimdala5955 5 лет назад

    Nsaku kutsindika

  • @brightmpanda211
    @brightmpanda211 7 лет назад

    Ansaku akukhala ngati adatha limozi ndi UDF chifukwa sakuoneka