YAPHEDUKA NDIYETU KULI KUIFOTOKOZA MWAMVEMVEMVE EISH

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 3 дек 2024

Комментарии • 122

  • @JailosIsaac
    @JailosIsaac Месяц назад +13

    Back to the sender
    Keep calming yourself Mr B kalindo from Njedza village ♥️ you are absolutely doing the tremendous job oipa onse Mulungu adzawaika pa mbalambanda No secret under the sun

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l Месяц назад +2

    Powerful message Mr mphepo Billy malata ndi mbuzi yamunthu

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Месяц назад +4

    Billy Malata 😂😂😂😂
    ADAD ali Ku ntchito kuli kokupha Anthu Ku Chikangawa.
    " Chachikulu Chi Bvumbwe chotantha patsekera"
    Malata ndi Mzako Khombe mudzalithawa Dzikoli .
    Weldone Pangolin Mphepo
    Straight talk.
    Stay safe ✊✊
    Stay blessed 🙏🙏
    God Will protect you.

    • @ADAMSONGONDWE
      @ADAMSONGONDWE Месяц назад

      Let's go back to the original love

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i Месяц назад +1

    Powerful message from my big brother 🙏 ulemu wanu big brother we trust you mr mphepo god bless you 🙏 🙌

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata Месяц назад +2

    God is with us,
    And also bless you brother Mphepo your salute ❤❤

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe Месяц назад +3

    Oimba mpaka 10 at kuti akope anthu 😅😂 kupepera kusowa mfundo. chifukwa anthu stingakopeke ndizimenezo,anthu Pano tinasukusula akungotaya nthawi yawo. Mmalawi Panoakutsata chilungamo

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses Месяц назад +6

    Ndipo machine aja muzakhumudwa asakugwira ntchito tsiku la mavote, ndi pamene musaziwe kuti mulungu si munthu kkkkkk.

    • @jowiemhango5058
      @jowiemhango5058 Месяц назад

      Ndipamene adzakhala kut alibe option koma kuwelengela mwa manual basi 😂😂😂

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Месяц назад +4

    koma comrade Mphepo mpaka wa kholingo ngati chidyansomba 🤣🤣

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 Месяц назад +2

      😅😅😅😅😅😂😂😂game yabwanji imeneyi yabayatu kikikikiki

  • @Joe-h9v
    @Joe-h9v Месяц назад

    Malata ndiwe opusa kobasi nyani wachabe chabe mutu wawukuluwo😂😂😂

  • @MerryWayson
    @MerryWayson Месяц назад

    ❤❤❤❤ Mr Bone Kalindo

  • @HamzahMiles
    @HamzahMiles Месяц назад +4

    😢 Vuto la mcp anatengana athu onamizila kuti nda azibusa, koma zili zigawenga heavy

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c Месяц назад +1

    Mbambande Mr Mphepo another pangolin may Allah bless you

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis Месяц назад +2

    MCP chipani cha mbuli cha ma savegi

  • @AchiwaNikisya
    @AchiwaNikisya Месяц назад +1

    Good work my comrade

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i Месяц назад +7

    Oyimba mpaka 12 mcp band guys this government nonsense government 🙄 😒 savages people's minds

  • @RaphaelMaunde
    @RaphaelMaunde Месяц назад

    Bravo Mr Mphepo💪

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu Месяц назад +4

    Koma ndiye ziyalutu che Malata shame on you 😂😂😂😂😂

  • @NessiCanada
    @NessiCanada Месяц назад +1

    Zoonadi uchitsiru sagawana😅😅😅

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson Месяц назад +2

    Amumangetu basi komanso The DC atsegule mulandu kwa kapolo ameneyi woipisa dzina la The DC wayaluka uyu gwape

  • @EnriqueLemitton
    @EnriqueLemitton Месяц назад

    Mr mphepo Kodi mumamwa madzi wosambitsila malilo?

  • @HaroonAbdulrazackKazembe
    @HaroonAbdulrazackKazembe Месяц назад

    Ikathere ku wire 😂😂😂😂

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 Месяц назад +1

    More fire comrade osaopa osatopa osafooka Allah alipo comrade

  • @AustinBottoman-x1y
    @AustinBottoman-x1y Месяц назад +4

    Munthu uyu amatumidwa nd a MCP omweo kut azipanga izi

  • @AustinTwaya
    @AustinTwaya Месяц назад +2

    Oyenda ndi lupanga adzaphedwa ndi lupanga pake lomwelo

  • @AnaLourencokan
    @AnaLourencokan Месяц назад

    Bravo...Aise❤

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc Месяц назад +3

    More 🔥🔥💪💪 comdrate mphepo 😅

    • @TakondwaSulani
      @TakondwaSulani Месяц назад

      Koma anthu amcp akupanga zinthu

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 29 дней назад

      Bigy inuo, ntanyiwa, BM, brah salo komanso kalindo mupange zoti chisankho mcp isadzabele tatopa nazo zisilu zimenezi

  • @JamiraJamirashaime
    @JamiraJamirashaime 19 дней назад

    😂😂😂😂 La40 😂😂😂😂

  • @mwayiwawontawanga3969
    @mwayiwawontawanga3969 Месяц назад +1

    Inu a MCP pamenepo ndipomwe mutadziwe kuti zakuvutani.... ndipo ma vote mwabela anja ziwani kuti zavuta kwabasi 😂😂😂

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l Месяц назад +2

    mmmmm mulungu sachedwa safulumila eee koma dziko lamalawi ayi ndithu

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Месяц назад

    Wagwidwa ufiti 😂😂😂 ili ndi dziko aise

  • @PatienceMphuche
    @PatienceMphuche Месяц назад

    Kholingo ngati chidya nsomba😂😂😂

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu Месяц назад

    Amene anga muone ameneyu malata yu andiperekere chikhofi chachikwanje😊

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Месяц назад +2

    Boma ili linapita ndi Chilima pa 10 June 2024.

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Месяц назад +1

    ine ndakhala ndikunena kuti uyuyu uyu la 40 lizakwana 🤣🤣

  • @ElizabethMwale-z3s
    @ElizabethMwale-z3s Месяц назад

    Ndiye muziti waphedwa ku ndirande uja koma ndi a dpp, si zitsiru zanu zomwezi zi a malatazi, chipani chochititsa manyazi. Apolice amangenitu athuwa si mumamanga anthu osachimwa, komatu mukaweruzidwa ndiiithu patalike pafupike Jesus is there waiting for YOU

  • @LumbaniNeba-d9n
    @LumbaniNeba-d9n Месяц назад +1

    God is with us

  • @EsterManiya
    @EsterManiya Месяц назад +3

    Komatu achakwerao amati ndabusa kod abusa simudawerenge baibulo kut sipadzakhra chinsinsi PA dziko lino lapansi nde kkkkkkk akadzachitabe ati zisinsi kkk oky nduwavesesa ayiwara

  • @FelixAaron-jm3ui
    @FelixAaron-jm3ui Месяц назад +1

    Actually ineo pali anthu angapo omwe amandibowa ku chipani cha MCP sure, Billy malata, Chimwendo Banda, Zikhale Ng'oma, Moses Kumkuyu,, etc 😢

  • @MAPANGAORIGINAL-w4y
    @MAPANGAORIGINAL-w4y Месяц назад

    Maratayi ndgaru sure ndakaika ngat sanakaphe nawo achina chirima aja kuchikangawa kuja

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Месяц назад +1

    Aaa koma MCP nyasi dzachipani ndale dzachikale idziii MALATA NDI MCP YAKEYO NDI GALU KWABASI

  • @VitumbikoShonga
    @VitumbikoShonga Месяц назад

    Mmmmmm galu ameneyi

  • @louisgolden
    @louisgolden Месяц назад +2

    Amaziziwa a MCP ndi munthu wawo uyu

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 Месяц назад +1

    vuto a MCP akugwiritsa khalidwe lawo lomwe ankapanga kamuzu banda koma ayiwara kuti lero anthu ndiwozindikira zasiyana ndi ndi nthawi ija

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v Месяц назад +2

    Chimwendo banda ndi chakwera anthu oyipa inu lero ndi chisuru chanucho mwayaluka

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman Месяц назад +1

    Inu ngat umboni ulipo osakamponda bwanji chilungamo kulibe bro kuno 50,50 bs

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 29 дней назад

    Mcp olo itagula oyimba onse mmalawi 2025 sikuwina akafunse ku botswana ndi ku america mbuzi za anthu APM akubwera

  • @RhodrickChauluka
    @RhodrickChauluka Месяц назад +1

    Poti zonse ndizisiru zokhakha

  • @mwayiwawontawanga3969
    @mwayiwawontawanga3969 Месяц назад

    Thanks god masiku osiliza chinachilichonse chizakhala poyela

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy Месяц назад

    Km kuno Galu ujah wagwidwa kuno zamanyaz 😂😂😂

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola Месяц назад

    Billy Malata kkkkk zakuvutani

  • @Felie-p7l
    @Felie-p7l Месяц назад +1

    Ambuye akudalitse bro timakuimililani

  • @EmmaEmma-q4u
    @EmmaEmma-q4u Месяц назад +1

    Km ndye mwa wathila mphepo tu mwa dzina lanu anthu awa kuipa koyamwila kwa kamudzu Ai matchini amenewo dzina LA yesu asazagwile tchito

  • @Joe-h9v
    @Joe-h9v Месяц назад

    Koma malata zelu ulibe nyalungwe weniweni tikuponda mudzimu mcp ngati simumanga tipita kunsewu muwonaso

  • @SteveriaNyalugwe
    @SteveriaNyalugwe Месяц назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂koma mundikomola ndi phwete, munthu wake ndi uyu wamkulu mutuyu

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Месяц назад +1

    MCP iyi nduina ina 😅😅

  • @AdaMussah
    @AdaMussah Месяц назад +2

    Kukula koseku alibe nzelu

  • @StuartMatanje
    @StuartMatanje Месяц назад

    Eeee😢😢 koma

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g Месяц назад +1

    MCP ,IYI NDIKHANI YOKUCHENJEZANI NDIPO MULUNGU AKUKUMASULANI TAONANI MUKUPASA ANTHU NDALAMA MULI AZIKHALA MBALI YANU KOMA AKUKUTUKWANANI , ZIKUPHUZISENI KUTI ANTHU OMWE MUKUGURA NDINDALAMA ,SAZAKUVOTERANI CHIFUKWA NDALAMA LERO AMALATA OKUDYA NANU AKUKUTUKWANANI KUKUMVEKSNI CHIKOPA CHABORN KALINDO KOMA MWALEPHERA

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis Месяц назад

    Billy malata vhitsilu chomwa mafzi. Ometela ndevu

  • @ThubsMtambo-b5d
    @ThubsMtambo-b5d Месяц назад

    Anthu adyela awa osalimbana nawo atayeni ali ndi mcp awa kumaona zipani zosapota awa Palibe chomwe angakuthandizeni ife sitimadya u d f

  • @robsonmapeto1911
    @robsonmapeto1911 Месяц назад

    Timawonera Times ndi mibawa sizatudzizo

  • @SmilingCompass-vw5ns
    @SmilingCompass-vw5ns Месяц назад

    Koma murungu atimenyele nkhondo ndiboma ili

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka Месяц назад

    Billy Malata yo amenyedwe

  • @SamsonSelevasio
    @SamsonSelevasio Месяц назад

    Kkkkk galu wachabechabe wagwidwa pansana pake

  • @M.shukriAdams
    @M.shukriAdams Месяц назад

    Ukatamba tamba kumakuchele la 40 lamukwanira

  • @TelezaManyela
    @TelezaManyela Месяц назад

    ngati iwe makata uli dolo bwanji ukanangotsegula fb account yako kuti udzinyozerapo anthu.umafuna kumabisala kumbuyo kwa original Dc,upite naweso ukawapeza ashumba

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x Месяц назад

    Akupangira dala cholinga oimira amalawi mu ubwino amangidwe mulu akuona ndithu

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 9 дней назад

    za manyazii chalu iwe malata

  • @AlexDaniel-y8g
    @AlexDaniel-y8g Месяц назад

    Koma nkhani zake taonani inetu ndinali mmodzi mwa oitsata page imeneyo osadziwa anali nyaniyu ndithu aaaa

  • @AnnaPhiri-b8t
    @AnnaPhiri-b8t Месяц назад

    Kwaoipa onse sazaupeza mtendere

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u Месяц назад +1

    Pakufunika apeleke ndalama
    Pakufunika kukasumila ku khoti

    • @jowiemhango5058
      @jowiemhango5058 Месяц назад

      Ofunika bon kalindo adyepo zake 😂😂😂

  • @JusticeMikondo-i9e
    @JusticeMikondo-i9e Месяц назад

    Koma ameneyo ndi galu kwabasi

  • @MikeTwaibu-i1h
    @MikeTwaibu-i1h Месяц назад +1

    Koma helewuuuuh

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka Месяц назад

    Koma ameneyi woipa kwambiri

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza Месяц назад

    Abilly malata manyazi bwa? Mungopanga zinthu ngati wozerezeka, nde abilly malata nanunso mukalowetu kumene kuli pastor shumba, mwayalukatu apa

  • @christopherMacheso
    @christopherMacheso Месяц назад +1

    Bon apite ku court basi

  • @katalamajames4947
    @katalamajames4947 Месяц назад

    dzoona namachende ameneyu mutu ngati phwala rankhumba akaziwone panyini pamake ameneyu ndiposo pamtumbo pake nkhope ngati kunyini kwankharamba marata

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga Месяц назад

    Bwanji sangamumange ameneyo akudikira chani

  • @louisgolden
    @louisgolden Месяц назад

    Amatumidwa ndi Boma lomwero uyu asatipeperese a Boma

  • @ceciliasokoh3779
    @ceciliasokoh3779 Месяц назад

    Tachioneni

  • @HamzahMiles
    @HamzahMiles Месяц назад

    Kodi Onsewo uyu mumusiyasiya?

  • @BilliatPhiri-k7n
    @BilliatPhiri-k7n Месяц назад

    Za boza Zeni ife boma ndilömweri la chakwera zanu izo ndi ma boza anuwo

    • @FelixAaron-jm3ui
      @FelixAaron-jm3ui Месяц назад

      Uzimvere chisoni nyapapi wachabe chabe iwe, actually can you mentions 4 reasons what the MCP government has changed in your life BETTER????

    • @HannockMesiwni
      @HannockMesiwni Месяц назад

      Ndiwe wekha wayakha motero ndiwe wovesa chisoni

    • @GraceShaibu-i9d
      @GraceShaibu-i9d 9 дней назад

      ​@@HannockMesiwni iwe ndi chitsilu kwambili kodi mavuto sukuwaona Malawi muno sopo Ali pazingati iwe ndi ngalu kwambili chipani cholempela ichi apangapo chani anthu awa kupanda kuyakhula ukuwona ngati amalawi angawa yakhulile ndi ndani ? uzinganizile ukama yakhula

  • @MwinkhulanaLulu
    @MwinkhulanaLulu Месяц назад

    Amumangetu uyu ngati samanga uyu tipha ngati nkhuku

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu Месяц назад +1

    Iwenso ndi mbola

  • @ChristinaSinoyakapawo
    @ChristinaSinoyakapawo Месяц назад

    Boma la mamafiyaa zovese chisoni

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 29 дней назад

    Iweo billy uli ndi amako? Nanga amakowo ali ndi amawo? Tacioneni cimutu mbuzi ya munthu iweo tithana nawe

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli Месяц назад

    Mmmmmm koma mcp manyaka manyaka

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Месяц назад +1

    Machende ako panyapako patuvi palibe zomwe ukukamba nigalu iwe

    • @WilisonWilliam-d9j
      @WilisonWilliam-d9j Месяц назад +2

      Iwe.umakonda.kutukwan.bwanji ngt.ukuon kt.ukunyasidwa.naxo.osangotuluk.bwanji pagruop

    • @ShinglaiAli-be3yn
      @ShinglaiAli-be3yn Месяц назад +1

      Mulibe nzeru akulu

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u Месяц назад +1

      Iwe nde ndi mbuzi, mwa MA comment onse Ali apawa iweyo ozindikira kwambiri??? Lusifala mwana wa hule panyero PA mako ndi achakwera akowo uwawuzenso pamodzi ndi cabinet yawo galu😢😢😢😢

    • @ArronBenson-g6d
      @ArronBenson-g6d Месяц назад

      Mwana wa hule iwe

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Месяц назад

    UYUYU AMANGIDWE BASI KOMASO NDI CHIFUKWA CHANI SITIKUPANGA MA DEMO KUTI SHUMBA ATULUKE ?

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck Месяц назад

    Osamusiya azolowela kunpusa

  • @NickUpoche
    @NickUpoche Месяц назад +1

    Chi Billy matako ndichichi???

    • @PatricaTchuwa
      @PatricaTchuwa Месяц назад

      Kkkkk.ndipo inu ngati uli umphawi ee zafikapo

  • @HijkkFjkffj
    @HijkkFjkffj Месяц назад

    Tiyen nawoni amenewo bigy 💞

  • @OmarBasheer-v7c
    @OmarBasheer-v7c Месяц назад

    Koma nalero nde billy wazioneratu

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi Месяц назад +1

    Lafote lamukwanila

    • @viennasamuel2976
      @viennasamuel2976 Месяц назад

      Ntanyiwa wabwera kudzayalutsa anthu oipa siizi?

  • @JoelKacheche-x6i
    @JoelKacheche-x6i Месяц назад

    Zonse akubwebweta nkuluyu zaboza zokhazokha,Billy malata anatopa nazo zama propaganda zanuzi,ndichifukwa chake akuwulura zinsisi Zonse mukuchita pa social media, kuyambila limpopo fm,bakili muluzi tv,bon kalindo nonse mumatumidwa ndi dpp Amalawi akuziwa zimenezo pakali pano, komanso Ben longwe naye anakutulukani ndipo wa akonzeka kuwulura chinsinsi chanu chilichonse chifukwa akuziwa madooko anu komwe mumapangira nyansi zanu zama propaganda,ziwani kuti style yanu yama propaganda singakuloweseni kulamulira boma ata!! mfundo mulibe zogwira mtima,kutukula ziko la malawi.Musiyeni Billy malata aziulura umve wa dpp mziko muno.

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane Месяц назад +1

    I can confirm kuti smartmatic machines sazagwiradi ntchito kkkkkkk

  • @robsonmapeto1911
    @robsonmapeto1911 Месяц назад

    Ngati police ili independent chonde uyu akalowe failing which you're used
    Very pathetic

  • @MaxwellPhiri-u9n
    @MaxwellPhiri-u9n Месяц назад

    Palibe chomwe mukukamba abwana Malawians a not stupid we are tired of u