Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Ndi zopweteka komano munthu sungabeleke ana 9 mkati mwa mavuto.
Very sad story zandikhudza ndithu😢
Ana 9 onsewo achani,ndiye kuti zilibwino ameneyo
Ndi mtundu wanji wa muthu iwowo ndi chichewa chawochi
Mulungu kumwamba titetezeni 😢
Very sad history is best teacher ❤❤❤
Mmmmm zopweteka
Munthu zinthu sizikuyenda bwino ndiye chokhalira ndi ana 9 onsewo achani??
Mmmm zoopsa Kondo sayabwino
Mulungu amateteza brother
Koma guys mmmmmmm tidzipemphereranso dziko lathu kuti Chakwera asadzabwerense nohondo ,nkhondo si zithu ,ndi ukapolo ,ife ndife ana ku Malawi sitidziwa nkhondo, komanso Mulungu akudziwa kuti nkhondo yathu ndi njala yomweyo basi ,Koma zokhalira kumathawa kugona mthengo sizowona Mulungu amatikonda ,Malawi timapemphera
Mulungu bwelani sanga dziko layipa eshiiiii
Nebati alicki 4:53
burundian uyu siwakumalawi😮
Anthu mulipa mavuto ndempaka ana 9 ,nonses
Zi😅
Nebati alicki
Very said
Anthu inu ngati mukufuna kuti chakwerayo achoke pitani paground osamangoti pa 16 timuchotsa pamenepa chovotera ulibe simungamuchotse ndi ufiti ayi akuyenera kuchotsedwa ndi vote
Nkhondo si yabwino by all means
Apa zaqoneselatu kuti Ntambo uja siwakumalawi
hahaha😂😂😂😂
Mmmm mpaka Ana 9 mavuto osewo😢😢😢
Mulungu ali nanu ndicholinga mbabo nkhani yowawa kwambili siku lina muzasangalala
So sad
Sad
Zovuta kwambiri
Anthu awa amaswana paka ana 9 eeeee
Munthu ulibendalama chomabelekelaso ana 9 ndichani
Ndizimene akuzifuna chakwela pa 16
Koma dzikoli abale
Eee 9? Ok God is good poti muli moyo
Very sad
Zachisoni
Muyiona 16 September
Don't say that bro..but instead keep praying
Very Sad