Pastor Kuyankhulapo Za Mai Brenda Omwe Aombeledwa Ndi Wa Police

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 янв 2025

Комментарии • 50

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 13 дней назад +5

    Point of collection picture mwayi kayo ndi ya mayi Navitcha MayiBrenda ndi awa kikiam wishing mayi Brenda a quick recovery ❤ and get well soon 🎉❤

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 12 дней назад

    Free advise and proud of you pastor Shumba always

  • @EmmanuelSambani-g2g
    @EmmanuelSambani-g2g 13 дней назад +3

    Go ahead pastor Shumba go deeper and deeper.

  • @BernardChikopa
    @BernardChikopa 13 дней назад

    Amen Bishop continue tell us only true factor's.....

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 14 дней назад +1

    Yes 100 percent ndipo apenga azelezeka, ndi mitu yopanda design apengatu, kodi kasongo wachilima uja wakudya zake alibe mlandu wapanga register

  • @HawaHussein-o5k
    @HawaHussein-o5k 13 дней назад +1

    Pastor zikomo ambuye akudalitseni akupatseni moyo wautali my comrade ambuye atithandize

  • @BrotherLester
    @BrotherLester 11 дней назад

    Well done

  • @BrendaKazembe
    @BrendaKazembe 13 дней назад +1

    Amen Amen

  • @GiftMatiki-q7s
    @GiftMatiki-q7s 13 дней назад

    Pastor shumba God bless u

  • @BobJoshua-q5n
    @BobJoshua-q5n 13 дней назад +1

    Ufiti wakula kwambiri ku MCP

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 13 дней назад +1

    Mayi Brenda Mulungu amange bala lanulo Masalimo 147:3

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 13 дней назад

    Tima kunya dilani pastor shuba we love youuuu

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 14 дней назад +1

    Tikufuna maina onse a apolice amene anali pa ntchito.Mai Yolamu utiyankhe mwachangu.Apo ayi tikubwezera kwa iye ndi omutuma.

  • @HawaHussein-o5k
    @HawaHussein-o5k 13 дней назад

    Ameen ndipo ameen kumwamba mulandile ulemu langa ndi pemphero ambuye atiolotse manja mwa pharaoh

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 13 дней назад

    Pastor shumba timakunyadilani coz munanena chilungamo ..mcp sakuchita zinthu zabwino ai

  • @GiftZande
    @GiftZande 13 дней назад +1

    Eeish źayambikazo ndimatelazi amenewo zenizeni zikubwera😭😭

  • @BobJoshua-q5n
    @BobJoshua-q5n 13 дней назад +1

    Osaiwala mau a Chakwera kuti adzalolera kukhetsa mwazi

  • @NickUpoche
    @NickUpoche 13 дней назад

    Pastor tiyamike uthenga wabwino ndipo musafooke,ndipo ndizoonazake,wa police uyuyu khope dzina lake talidziwa ndipo boma likalowa lina,uyuyu tilinaye

  • @FridayH.pontio
    @FridayH.pontio 13 дней назад

    Wa police ameneyo wakhoza anthu amenewa azolowera akagenda a police ndi nduna anthu akudziva kuopsya zd ndie palibe ameneyo ndi mzimayi opusa amazitenga ndan pakati pa gulu

  • @AlicePondani
    @AlicePondani 13 дней назад +1

    A chule alemba Mmadzi

  • @YasmeenYalabi-e8g
    @YasmeenYalabi-e8g 13 дней назад

    Timakunyadilan pastor shumba

  • @katalamajames4947
    @katalamajames4947 13 дней назад

    Ameneyo tithana naye dpp ikatenga mboma ameneyo police yake anakaphuzira kuti panyini pamayi ake pamtumbo pabambo ake tizaonesa ameneyo

  • @BrightonMkandawire
    @BrightonMkandawire 14 дней назад

    Amen shumba

  • @StuartMtambo
    @StuartMtambo 14 дней назад

    Amen and amen

  • @MaxfordWasili
    @MaxfordWasili 13 дней назад

    ❤❤❤❤

  • @RichardHetekere
    @RichardHetekere 12 дней назад

    Kodi wa police ameneyu Ali kuti?

  • @GladysMagadi
    @GladysMagadi 13 дней назад

    Ndipo 16 September kwataloka pastor shumba muno ndimung'anjoyamoto

  • @khwimaBanda-s3u
    @khwimaBanda-s3u 13 дней назад

    mzinenaso kut adpp nawoso ankapanga zomwezo adachosedwa nabuso mwayamba zomwezo muchoaosedwa

  • @DetterYasin
    @DetterYasin 14 дней назад

    Pitilizani pastor, kutizindikilisa

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 13 дней назад +1

    Honarable president Muluzi did say don't vote MCP we goona suffer , but we didn't listen , history is the best teacher

    • @laurentbutao4084
      @laurentbutao4084 13 дней назад

      Nobody voted for MCP, People's mind was voting for Tonse Alliance.

  • @SamuelWyson
    @SamuelWyson 13 дней назад

    Apa nafenso tiyambe kupanga za apolice because timakhala nao mmakomomu nyumba zao tikuzidziwa,A malawi tisapuse atitora

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 13 дней назад

    Ndipo zoona akwantere alibe nzelu

  • @YusufMtendere
    @YusufMtendere 13 дней назад

    Kodi anakazinda,nde kuti chipolopolo chinakafikila mmimba muthu anakaluza moyo,kulakwa koma

  • @EsnartTione
    @EsnartTione 14 дней назад

    Pastor abwatetewa kwao ndikupha ndikuononga

    • @patriciamagawa1036
      @patriciamagawa1036 13 дней назад

      Ambuye akukhululukile uzindikire kuti miyoyo ya anthu ochuluka ali pamavuto azaoneni chifukwa cha boma la mcp shame on you kumasapota zoipa zomwe xikuchita mdzikoli

  • @JessieMbewe
    @JessieMbewe 13 дней назад

    Koma ndiye mulungu sangolore kuti athu azingofa njala

  • @swadikimbwana7680
    @swadikimbwana7680 13 дней назад +1

    M.C . P yatha basi siyizalamulanso in Malawi basi Boma yakhaza . M C P will be completely. fall and demise the same UNIP had finished in Zambia

    • @CathrineRamseyJafaal
      @CathrineRamseyJafaal 13 дней назад

      Ndipo ili mbewu kungoyikazinga ndikuiponya mmadzi isazamelenso mcp chipani cha nkhanza

  • @ChrissyScot
    @ChrissyScot 13 дней назад

    Zoona

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf 14 дней назад

    Mau mau

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 14 дней назад

    futhi 500 tausand sigwilla nshito nkushokella nku DPP utm afood UDF MCP tingophana Bas

  • @Bernarddavide-e1o
    @Bernarddavide-e1o 13 дней назад

    Abwatere go

  • @AnniePetro
    @AnniePetro 13 дней назад

    Akunama

  • @PromiseChanza-q9j
    @PromiseChanza-q9j 14 дней назад

    Abusa osati abwamtere kkkk

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 14 дней назад

    Zikayambika musathawe

  • @StuartMtambo
    @StuartMtambo 14 дней назад

    Taonga

  • @FridayH.pontio
    @FridayH.pontio 13 дней назад

    Kma uyu ndi busa wanj kma wa afiti mwina