Fredokiss Wazituluka!

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 3 дек 2024

Комментарии • 15

  • @ReginaMalunga
    @ReginaMalunga 26 дней назад +3

    A fredo mwapanga chn ,mapwala😢

  • @mercymalenga1884
    @mercymalenga1884 12 дней назад

    Kapezeni zina zoti munene

  • @ShillahChisi
    @ShillahChisi 18 дней назад

    Azaime 2030

  • @fraiserkapito-yb2ob
    @fraiserkapito-yb2ob 26 дней назад +1

    Sanalakwitse waganiza mofatsa kuti ayinyamulebe UTM

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge 25 дней назад +1

    Waganiza bho .....maganizo amenewo uzapange 2030

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 25 дней назад +1

    Wachita bwino Fredo umakhwana aise

  • @YusufAjida-t8r
    @YusufAjida-t8r 25 дней назад +1

    Apa ndi pamene freedo waganiza bhoo kwa mbiri Umakwana ndiiwe fana oganiza bho diii

  • @peterbyson6269
    @peterbyson6269 23 дня назад +1

    Mawayilesi akwathu mumalankhula mofuna kusokoneza anthu ... Wachita bwino munthu akuyenela kufatsa adzalamulila basi koma adakali mwana

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 26 дней назад

    A fredokiss bwanji mwasiya😢😢

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 25 дней назад +1

    Wachita bwino ndi nyamata omva za anthu

  • @imranAllan
    @imranAllan 26 дней назад +1

    Wachita bwino fredo

  • @MoyendaMoyenda
    @MoyendaMoyenda 21 день назад

    Top 10 ya mativ

  • @LinlyMatheweKufakwina
    @LinlyMatheweKufakwina 21 день назад

    Aaaa nde wapusisa bwanji muziyamba mwaganiza mukamayamba kulengeza zamabozazo chifukwa anyamata amnzake anachita kumupempha zaziiii kukhuta eti???

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk 26 дней назад

    ❤🎉

  • @MeffaChinomba
    @MeffaChinomba 26 дней назад

    Anthu aphana sure