BON KALINDO 29 JULY 2024 KUPONDA MAKOSI PA MONDAY

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 сен 2024

Комментарии • 57

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c Месяц назад +8

    Opposition pitani ku court tizavote kopanda I'd,

    • @KingfrahMachado
      @KingfrahMachado Месяц назад

      Zikufunika ziterod cause mavuto atikwana kuno kumalawi ❤

  • @SabitSamohgruva
    @SabitSamohgruva Месяц назад +2

    Manganya yudas kkkk😂😂😂😂😂

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Месяц назад +2

    Exactly udasiso mu utm yemwe anapeleka mr chilima ndi Michael usi

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Месяц назад +2

    Ankolo cha Bon, awopositioniwa ngamantha akuwopa kumangidwa ndikuphedwa, tatiyeni inuyo ndife tikamang'ale kukhoti ponena kuti tizavota ngati mmene timkavotera kale , awa awopositioniwa satithandinza olo mpang'ono pomwe anama,,,,,,,, nde

  • @ThompsonMakwakwa
    @ThompsonMakwakwa Месяц назад

    The DC

  • @NadeemKhan-sh9js
    @NadeemKhan-sh9js Месяц назад

    Tiyenazo osasiya amenewo

  • @FanuelSoda
    @FanuelSoda Месяц назад

    The opposition is not constructive

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa Месяц назад +8

    Ndukumvera kuchokela kuno ku nakonde border ❤

  • @lovenesskampira
    @lovenesskampira Месяц назад

    Ndizoona za NRBzo

  • @LuckiaMichongwe
    @LuckiaMichongwe Месяц назад

    Moyo ndiwovuta,

  • @ConnexMtika
    @ConnexMtika Месяц назад

    Zoona MCP nfiti yopha anthu

  • @YNOTGEORGE8
    @YNOTGEORGE8 Месяц назад

    ❤❤❤❤❤

  • @EllenThunga-wb5cs
    @EllenThunga-wb5cs Месяц назад

    Umaitha DC

  • @JonaZimpita
    @JonaZimpita Месяц назад

    Iwe chistilu kwambili uziti pulezinti wa alomwe

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi Месяц назад +1

    Opposition siili serious fuusitopo inu Mukungo inu mukuwona kuwachenjeza

  • @StevoZimba
    @StevoZimba Месяц назад +1

    Opposition wake up please help Malawi

  • @Fredoh10
    @Fredoh10 Месяц назад

    Ing'alure ase ndi nthaw yako 😅 7:54pm

  • @Mustafaaliki-tr2kv
    @Mustafaaliki-tr2kv Месяц назад

    I am waiting from Cape town South Africa best tv❤

  • @SherryJiya-c1u
    @SherryJiya-c1u Месяц назад

    Respect from fire Rose empress from liwonde

  • @GeraldChisokeza-er5cf
    @GeraldChisokeza-er5cf Месяц назад

    Koma a Kalindo ndi Fire.The DC Deadly Child

  • @FrankMulela-qt1wi
    @FrankMulela-qt1wi Месяц назад +1

    Exactly 💯 %

  • @user-js6xn9qj1r
    @user-js6xn9qj1r Месяц назад

    President wathu wathu iwe 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @DarlingtonChaura
    @DarlingtonChaura Месяц назад

    Listening from linthipe

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Месяц назад

    THE DC'S MWANA WOOOOPSA KWAMBIRI AKHALISE MALAWI CHILUNGAMO CHIYENDE NGAT MADZI.

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani Месяц назад +6

    Anthu andale ndi oyipa sibwino ....kumavela kalindo amavutika kudziunikila koma sidziva

  • @user-fc4ky5vu7m
    @user-fc4ky5vu7m Месяц назад

    THE DC Mwana wovuta kwambiri

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Месяц назад

    Iweyo ndikatundu timakunyadilan 🎉

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Месяц назад

    KOMATU DC NDIYE AKUCHENJEZA KOMA KUSAMVA KWA ANTHU OSUSA ALI NDWIIIII CHONSECHO AKUFUNA KUZAVOTEREDWA ZAUSIRU BASI, IWOWA NDAMENE ADZATIPWETEKETSE 2025 CHIFUKWA CHA KUGONA TULO

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali Месяц назад

    The DC ❤❤❤

  • @ThomasMlowoka
    @ThomasMlowoka Месяц назад

    The DC🔥🔥🔥

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn Месяц назад +1

    A opposition apatsidwa ma billion a ndalama agawana

  • @user-ju9gj1yk6c
    @user-ju9gj1yk6c Месяц назад

    Zimvere mtolo a opposition. Wake up and perform

  • @DarlingtonMalikebu
    @DarlingtonMalikebu Месяц назад

    Zoona kalindo zili kawale ndithu bwana

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Месяц назад

    Komaso opposition mukutikhumudwitsa simuli work up pls

  • @modestamhango7737
    @modestamhango7737 Месяц назад

    MP wathu wa Zomba Chingale wagulidwa ndipo zokhumudwitsa kwambiri.

  • @MarkinaJohn
    @MarkinaJohn Месяц назад

    Team DC

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Месяц назад

    Ndikubwera ndizavote Chaka chamamwa

  • @Emmanuelsuman
    @Emmanuelsuman Месяц назад

    Katundu iweyo

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Месяц назад +1

    Watching from S/A Bhoni kalindo

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Месяц назад +1

    Redson munlo wamwalira 😢😢😢😢😢

  • @JustinMwananaphirih
    @JustinMwananaphirih Месяц назад

    Cool

  • @SamzyTimechisaleh
    @SamzyTimechisaleh Месяц назад

    😂😂Iwe anakonza

  • @sulleahmnyimbili1362
    @sulleahmnyimbili1362 Месяц назад

    🙏🙏🙏

  • @user-tl8pe5ge6l
    @user-tl8pe5ge6l Месяц назад

    Kuitenga ndalamayo koma vote ili mutima ku vote mcp ndiye kumbesatu

  • @MustafaMachika
    @MustafaMachika Месяц назад

    Opposition sili bho

  • @dytonmoyo4629
    @dytonmoyo4629 Месяц назад

    🔥🔥🔥🔥

  • @violetpotani
    @violetpotani Месяц назад

    Kwacha bwa?

  • @DALITSOMOENDAPATHERETUMoendapa
    @DALITSOMOENDAPATHERETUMoendapa Месяц назад

    eeeee.