Bodza akuti iwowa abusa MM anali mkati mwakasupe wamadzi koma ukakamiza chule akuthawa mmadzi mom amakhala ataona njoka mmadzi mom, he means that he him escape the serpent. Tell people the truth.
Please 2025 vote for pm plz kuzabayizika yayo plz kumupoto kwi2 uko plz ,Only pm can rescue us, and plz brother tell us about vote here in SA how didi it go ,I wish DA could win.
Km ine ndili ku south Africa chaka cha mawa ndkubwera kuzavota kumalawi ndpo chakwera uyu sindkumufuna ndizavotera adad tikufuna nsima ife feterez ndamene timafuna❤
Ndiye ku Zambia Mozambique Tanzania anakweza ndi chakwera kod tiziti ndivhiyani mumanganiza athunu or apm akanakhalapo akanakwera anakwera dziko lapasi
Even panopa ku Jon kukuwawa chifukwa chachibwana awa akutcha apuledetiwa e.g fertilizer in 3 ago 100 thousands amagula 4 bags koma pano just the period of 3 years zikufunika kutumiza 500 zowawa kwambiri.
We miss you bakili muluzi tv, it's been two days without you😢
I hope he is okay asatipheleyi
Timuikize mumanja mwa ambuye
Amene simunva chitumbuka akuti, Chakwela ndi Chule, Chilima Ndijoka
😂😂😂😂😂
Kakakakak mmmm
Bodza akuti iwowa abusa MM anali mkati mwakasupe wamadzi koma ukakamiza chule akuthawa mmadzi mom amakhala ataona njoka mmadzi mom, he means that he him escape the serpent. Tell people the truth.
Kkkkk inbox me please
Hi boss we miss you y are quite
Dpp is only our hope especially APM the best man
Palibeso wina
We need back our guy 😭😭😭
Please 2025 vote for pm plz kuzabayizika yayo plz kumupoto kwi2 uko plz ,Only pm can rescue us, and plz brother tell us about vote here in SA how didi it go ,I wish DA could win.
APM ❤
I wish you a safe and happy and good life boss
Apm My vote
Powerful message 🙏
Thank you brother kk
I already miss the nice voice
Perfect one
Big man B muludzi TV 💪💪💪
Kodi akulu anakumangani 😢😢 mwasowatu tikusowa nkhani zeni zeni chonde wonekani😢
Brother usasiye kuyika mavideo awa amve kuwawa pomwe tikupita ku mavote next year.
Ku Malawi anthu amadalira nsima sopano ngati fetereza akudula anthu otsaukafe tipanga bwanji? Mumidzi muli azigogo okalamba angagule? Mulungu akulangani ndithu pulezidenti wakuba Chakwera mbuzi ya munthu
Big up brother man!!
❤❤❤Ulemu wanu big
Adad woyeeee
This good speech
Big up raster
Zoonadi ifetu tivotera Dpp kapena Udf basi
😂 tilipambuyopo
Or kuno kumpoto ndi chihana ndi peter basi
Best TV ever
We miss you bakili muluzi TV when you stay two days no any updates we are very worried..... You make us happy always Mr bakili tv
APM vote 🥰
Powerful 👊 👊
Big man Peter
Hie Mr new presenter. Mukanakwezako mawu kuti tizimva bwino. My phone is at maximum volume but still am struggling to hear clearly.
Peter mutharika akatundu
Best TV
Apm awina posakaikanso ayi.anthu momwe mumkamuvotera chilima ndikumat mfana oganizo booh ogonaniza mopusa bas and ndichitsilu kwambili anapusitsa mbuli zinzake zomwe anamvoterayo zianyani zopanda wisdom from GOD.kukavotera anthu makape ngat amenewa bas.amalawi ndife opusa kwambili tinapusitsidwanso ndi azitsogoleri ampingo ndiomwe amati tikawavotele mbalamezi zitsilu zachabe chabezi mxiiiii.
Ndiwe katundu br God's time is the best,all the best
Voice ya bigy zkutibwaaaa
Guys I miss bakili muluzi tv 📺 where is our best journalist it's been a while
Best Ever TV
Sinnabotepo ulendo uno ndi vote apm my vote
zose zomwe akunena anthu awa ndi chilungamo ndipo chakwera wakhumudwitsa anthu ambiri koma ine chakwera ndinaziwa kuti ndi wankhaza
Peter my vot
Best ever tv dankie
Where is our man bakili muluzi tv we miss you too much
Bakili muluzi please come out we need you this time please 😭😭
Bwana wathu kodi mulikuti imfe tiri wodandawula kwambiri sitikuwona video new one😢😢
3 days now without a video. Bakili muluzi TV are you there?
Lero akulankhulayu nde uti?
amene akuyankhulayu sakukumesa aaaaa
Dzika yokhuzidwa
May the Lord bless DPP and curse MCP. In the name of the Lord MCP shall go down and their place shall never be there.
Amen
Peter my vote 🗳️ ❤❤❤🎉🎉
Mmalawi wa nzeru uyu
Km ine ndili ku south Africa chaka cha mawa ndkubwera kuzavota kumalawi ndpo chakwera uyu sindkumufuna ndizavotera adad tikufuna nsima ife feterez ndamene timafuna❤
Good message ❤Bakili Tv
Thanks for the update on the video
Powerful!!! 💪
Ndiye ku Zambia Mozambique Tanzania anakweza ndi chakwera kod tiziti ndivhiyani mumanganiza athunu or apm akanakhalapo akanakwera anakwera dziko lapasi
A space of 4days without hearing your voice seems like a decade
What next our ears should hear of bro?
Bwana
Where are you it's been 3 days
BM tv takusowani koma muli bwinobwino?
2025 DPP my vote 🎉🎉🎉
Boss tapangani check in mukusowatu, muli kutiko
No any updates for 6 days now are you arrested?
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💪💪
Bakili muluzi tv are you there????
My vote is APM DPP 2025
Koma adha inu sanakupheni?
More fire 🔥 asambiseni anthu oipa
Aise tipatse update kapena naweso waphulitsidwa 😢
But I miss your voice big man
We're is this guy baliki muluzi why quite big man
Rumours has it that it was being run by Ralph kasambala
Thats it
Ku Northern Region please please kubayiza yayi paluvotelaso Chakwela or MP wa MCP.
Thakusowa abro
Kod wakulu mulipo?? We miss you
Tonse Alliance iwona za ANC .Paulendo 2025
APM my vote.
Malawi 😭😭😭😭
Where are you bakili muluzi😢
Zoona ife tikufuna Peter munthalika fertilize wunali wosika mapassport anali osavuta makhwara amapezeka muzipatara amapezeka sugar wumapezeka tatopa nazo mbamva izi za MCP
❤❤❤❤
Koma Bakiri muluzi TV ndayisowa bwanji
Kodi bwana Bakili Muluzi channel mulipo?
Kodi mwini voice mulipo big? Kapena akupezani a MCP aja😢
Koma akuluwa alipo sathatu 2days opanda video ananjatidwa kapena 😢😢😢
Ine ndiye Peter muthalika basi ndimanva naye kukoma muntima mwangamu
Kodi munasiya boss kusakatula history takusowani
Bwana Koma mulipo ziii ameneyu? Plz yankhani
Guys bakali muluzi TV alikut?
Even panopa ku Jon kukuwawa chifukwa chachibwana awa akutcha apuledetiwa e.g fertilizer in 3 ago 100 thousands amagula 4 bags koma pano just the period of 3 years zikufunika kutumiza 500 zowawa kwambiri.
His last video was this i think nyamata wa bakili muluzi tv waphedwa
Kodi bwana Bakili Muluzi TV mulikuti😥😥
Kodi bakili muluzi TV anamugwila sakukutulusa ma letest
Ineso ndikudabwatu kwangoti ziiiii
Maybe the dictator have taken you boss
Let me enjoy today's update 🎉❤
Mulimonsemo koma chakwela asazawinenso 🙏🙏🙏🙏
DPP woyeeeeeeeeee
Osafoka bro BM
Chakwera Timuleke ngwakutangwanika uyo😅😅
Vyakutonda nadi mwee mauka uka yakwa phanana no vision
Chakwera the punisher 😮
Kkkkkkkkkkkl
8 days bro mwatiyiwala2. daily. bundle timagula bcouse ov u bro
Ndipo even chilima asakunamizeninso amalawi anzanga tiyeni ku DPP
Awuze