WADZIDZIMUSA ANTHU UKU VP NDIKA SURPRISE VISIT ku Chikhwawa District Hospital...atutumuka😂😂😂😂

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 окт 2024

Комментарии • 93

  • @Vinic-f3w
    @Vinic-f3w 2 месяца назад +8

    Malawi needs such heart ❤,,,, continue VP

  • @abangaabanga4677
    @abangaabanga4677 2 месяца назад +6

    I commend this, this needs to be encouraged, please continue, with this kind of mentality Malawi will rise, God bless 🙏

  • @FloridaOssy19
    @FloridaOssy19 2 месяца назад +1

    ❤❤❤❤❤❤ mwayamb bwino a manganya

  • @DeborahHetekere
    @DeborahHetekere 2 месяца назад +2

    This is good development that's the spirit that we need as malawians,,,this is exactly what Late Dr Claus Chilima wanted

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda 2 месяца назад +8

    Zipatala za boma mavuto aakulunso ndomweo. Ogwra ntchto amafika nthaw yomwe akufuna and sayambanso ntchto nthaw yomwe afklayo amayamba wakhala kae akut kupumula then ayambe kugwra ntchto. Imafika mpaka 9 asanayambe ai. Chomwe amadziwa nkutukwana ma patient bas

  • @veronicamalisero2671
    @veronicamalisero2671 2 месяца назад +1

    A VP ndipo muyendele ma office onse aboma,,,....amakhala pa mtambasale anthu awa..keep it up, ,,,....

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l 2 месяца назад +3

    Kkkkkkkkk koma vic wake kashoti

  • @masalinodovu1705
    @masalinodovu1705 2 месяца назад +1

    Excellent Mr VP izi nde zofunikira kwambiri

  • @DinahNantchengwa
    @DinahNantchengwa 2 месяца назад +1

    Proud of you Mr president, zikamatele dziko lathu liziyenda bwino, anthu muzipatsla amataililadi koma akamalombikitsidwa choncho ziziyenda

  • @giftsululu4274
    @giftsululu4274 2 месяца назад +4

    Ku utm''' '' mukuona koma... Mwataya gold

  • @vanalphamphaya3518
    @vanalphamphaya3518 2 месяца назад +1

    Big up the VP continue the good work you started when you were there long time.

  • @nyasavoicebox
    @nyasavoicebox 2 месяца назад

    Good on the Right Honourable the Vice President for being positive. Especially when dealing with the young nurse. Samakalipa koma kulangiza kuti mavuto akunyumba aliyapo iyi ndi ntchito anthu amakudalilani muziyesesa ku bwela ku ntchito on time. Even when dealing with the DHO the conversation sinali yoti ine ndiwonke kuti ndine VP but after reprimanding her he made her feel safe to elaborate on the challenges their hospital and district are facing. Politics aside, this guy may actually care about improving Public Service Delivery in Malawi.

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 2 месяца назад +1

    This is great. ife ogwira ntchito mboma tikugona kwambiri. Ngati sitifuna ntchito titsanzike

  • @AfickDaud
    @AfickDaud 2 месяца назад

    Kukhala ngat madam akunyumbatu Mr Manga kkkk mukuchta kukhalana mmene mukuendamo

  • @Ella13400
    @Ella13400 2 месяца назад +1

    Mr Usi pitilizana mwina malawi akhonzaaa.......

  • @omarlux3434
    @omarlux3434 2 месяца назад +2

    Osafuna.asye ine ndikuva kukoma ndi vp wathu

  • @RiaThomKata
    @RiaThomKata 2 месяца назад

    Well done Mr president

  • @elisaPhiri-k1e
    @elisaPhiri-k1e 2 месяца назад +1

    Ma patient kumvetsa chisoni pogona pamene ndalama zaboma zikungobedwa mmm

  • @HassanMaganizo-im6nk
    @HassanMaganizo-im6nk 2 месяца назад

    Kkkkk kodi limeli ndi sewero lakutiferanji kodi😂😂😂😂

  • @abbasjutasi909
    @abbasjutasi909 2 месяца назад +1

    Iwe nde akuphela kutulo iwe za ndege wachepa nazo
    Good job apule

  • @mayesouldphiri9889
    @mayesouldphiri9889 2 месяца назад

    Iyi ndi tikuferanji ya srs 😂😂

  • @RotNkhoma
    @RotNkhoma 2 месяца назад

    Let's continue mr vp you need to go different department of government9, we need great malawi

  • @brothertonekathyole7349
    @brothertonekathyole7349 2 месяца назад

    Keep it up our VP!

  • @ChifundoChikakwiya-kf1is
    @ChifundoChikakwiya-kf1is 2 месяца назад +1

    😂😂😂 It is promising slowly but let's hope greedy people won't disturb him

  • @fredbmazuwa8066
    @fredbmazuwa8066 2 месяца назад

    VP you have got my thumb

  • @GraceGonani
    @GraceGonani 2 месяца назад +1

    Anthu ogwila ntchito boma amatailila kwambili mwina apa atengelapo mphutzilo😊

  • @ChimwemweDemelo
    @ChimwemweDemelo 2 месяца назад

    Big up Mr vp

  • @KondwaniNguleti-x1q
    @KondwaniNguleti-x1q 2 месяца назад

    Mr VP Usi u did it well 👏

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi 2 месяца назад

    That's my VP ❤❤❤❤

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 месяца назад

    Well done VP usi. Ntchito yofunikira

  • @MacsJafali-d1m
    @MacsJafali-d1m 2 месяца назад +1

    Uyu apwetekaa anthuu

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 2 месяца назад

    Anakapangaso check ku pharmacy ngati kuli mankhwala okuti odwala alandira?

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg 2 месяца назад +1

    Zikachita bwno tiziyamikilako wakulu mwayamba bwno

  • @MenasKaliati
    @MenasKaliati 2 месяца назад

    Uyu ndiwasero basi😂😂😂

  • @TizifaBanda-xn5tm
    @TizifaBanda-xn5tm 2 месяца назад +1

    Civil servant kumakhala ngati ant civil servant.worse ku chipatala it's beyond ntchito.

  • @FestoniehJim
    @FestoniehJim 2 месяца назад

    Izi ndie zalowa sewelo ndithu

  • @BrendaJali
    @BrendaJali 2 месяца назад +1

    Good move

  • @GiftDaftala
    @GiftDaftala 2 месяца назад +1

    Sizikukhala or pangono he can't even afford chilima's footsteps

    • @blessingsmunthali9202
      @blessingsmunthali9202 2 месяца назад

      Understand that Mulungu atilenga mosiana and everybody is unique 😊

  • @GustoAjasi-fl9oo
    @GustoAjasi-fl9oo 2 месяца назад

    😂😂😂😂 ausi anachenjela eee

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan 2 месяца назад

    Zayambika 😂😂 big up mr usi....

  • @MoloiTeboho-x9f
    @MoloiTeboho-x9f 2 месяца назад

    Iwe ma nganya 10pn munthu apanganao cani 😂😂

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda 2 месяца назад +1

    Nurse kukanika kuyankha mafunso a a Usi in English Kkkķk Malawiiiii...bolakotu a DHO 🎉

    • @chigokhalid9420
      @chigokhalid9420 2 месяца назад +2

      Wakwanisa komanso Mbali ina anali mantha plus I think sanaganizile Kut akumana ndi VP

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib 2 месяца назад

    Yalakwa apa...mwachedwa ku vepi a nurse

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 2 месяца назад

    Ine. Ndiye. Ndikalila. Malilo

  • @janemanyamba7201
    @janemanyamba7201 2 месяца назад +1

    Uyu ndiye atithandizadi zoona

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 2 месяца назад

    😂😂😂 Km manganya

  • @TizifaBanda-xn5tm
    @TizifaBanda-xn5tm 2 месяца назад

    Ndawala zikuswedwa eeee

  • @MagretSaid
    @MagretSaid 2 месяца назад

    Mukawaopsezeso ku mapasport uko kuli chinyengo

  • @Marionphuxymw
    @Marionphuxymw 2 месяца назад

    Kkkkkkk kma adaa changa ndichala pakamwa

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib 2 месяца назад +1

    Tikuferanji 😂😂

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto 2 месяца назад

      Ndendende😂😂😂😂😂😂😂

  • @LovemoreVincent
    @LovemoreVincent 2 месяца назад

    Powerful musatsiye

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 2 месяца назад

    New sheriff in town

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 месяца назад

    Zama reform please a vice president yambsnipo before 2025

  • @osmanafadi4801
    @osmanafadi4801 2 месяца назад

    Wamisala anaona ndewuu

  • @AlinafeSolomoni
    @AlinafeSolomoni 2 месяца назад

    Koma akuoneka ngati afika movuta koma ndimunthu ochezeka

  • @clesheinvestments
    @clesheinvestments 2 месяца назад

    Zofunika zimenezo a VP.
    Ma Civil Servants ambiri matama komanso kumalimbikira ntchito, kukula Mtima komanso kudzikonda.
    Akuti ntchito ya m'boma imavuta polowa.
    Achangamutseni ndithu.

  • @Uncle_B265
    @Uncle_B265 2 месяца назад

    Ngati azimaliza ndiyen tione

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 2 месяца назад

    ❤❤

  • @Choicemlw
    @Choicemlw 2 месяца назад

    Mu manifesto a Tonse alliance anati ankadzalowa m'boma anthu azipita ku ntchito 8:30
    Aiwala nthawi yomweyi kodi?

  • @emmanuelkenneth4768
    @emmanuelkenneth4768 2 месяца назад

    😅😅😅😅 well planned

  • @EvanceSteven-u5g
    @EvanceSteven-u5g 2 месяца назад

    Nice

  • @ruthkaoloka4772
    @ruthkaoloka4772 2 месяца назад

    ndi drama kodi?

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 2 месяца назад

    Mupitenso ku immigration mukawonekeleko bwana

  • @LemosBanda
    @LemosBanda 2 месяца назад

    Bola zipipitirire

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 2 месяца назад

    I remember achilima anayambaso chonchi kenako nae alowa mu system...... Hope this will no stop

  • @TamieMbenza
    @TamieMbenza 2 месяца назад

    Kkkkk ine ndimaona ngati sewelotu😂😂😂😂🎉🎉

  • @EmmReece
    @EmmReece 2 месяца назад

    mcp iwinaso bad

  • @ErustusPhiri
    @ErustusPhiri 2 месяца назад

    Malume mukukwana

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 2 месяца назад

    Akuyankhula ngt akupanga tikuferanji

  • @Sinya-r5q
    @Sinya-r5q 2 месяца назад

    Mulunguakupatseni phamvu

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 2 месяца назад +1

    Ngati zenizenitu, nkana unampeleka Bhiyeni umafuna zimenezi.

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto 2 месяца назад

      😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 2 месяца назад

    Ukuoatenga anthu ngati zitsiru USI government ukuti kulibe ndalama koma zomwe akumagawa kumusonkhano akuzitenga kuti?

  • @willieBillschiumbuzo
    @willieBillschiumbuzo 2 месяца назад

    Ipatseni moto a vice ama 10:41 wonjeza kubwera mochedwa kutchito ma nurse akafika ayambe kaye aseweretsa 4n then aziyamba cha ma 9 kugwira tchito

  • @StellaErias
    @StellaErias 2 месяца назад

    Pitilizani bwana azimayi oyembekezela timavutika zipatalamu agalu amenewa amazimva ubwana zipatalamu

  • @BrianBanda-j5n
    @BrianBanda-j5n 2 месяца назад

    ipase moto usi bola osazasitha mukazapasidwa mwayi.......try hard this year 2025 boma....

  • @danielkhinguirossejuliasse6106
    @danielkhinguirossejuliasse6106 2 месяца назад

    ndiye wapanga sewero lamphamvu

  • @HappinessMilanzi-b2m
    @HappinessMilanzi-b2m 2 месяца назад

    Zikuoneka kuti mutithandiza

  • @EmmReece
    @EmmReece 2 месяца назад

    mcp iwinaso

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda 2 месяца назад

    Ma nurse ku malawi osadziwa English Kkkķk km zlko. Usi wayesetsatu

  • @AishaUthman-mg7db
    @AishaUthman-mg7db 2 месяца назад

    😂😂😂😂

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 2 месяца назад

    Ananena kuti asenda aliyense waulesi

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад

    Zandale ziduse uko nawo anthu ogwira ntchito chipatala za boma amapanga matama muzapanadi

  • @MustaffMdogo-c7q
    @MustaffMdogo-c7q 2 месяца назад

    Zapamwamba

  • @FlorenceBillyGama
    @FlorenceBillyGama 2 месяца назад

    Ubwana syndrome inavulaza a malawi ambiri