HOT CURRENT ON TIMES TV 19/05/2024--CHAKWELA AVOMELEZA KUTI ZAMUVUTA TIVOTE LERO LOMWE
HTML-код
- Опубликовано: 18 май 2024
- #numeroyapastorntambabazi0788554028 #malawipolitics #news #duet #march2019 #bongotv #zodiaktv #humour #aford #31march
watch ZODIAk CRUISE 5 WITH MLAKA Malilo part 2 here
• ZODIAK CRUISE 5 NDI ML... - Развлечения
Amandiwaza makosanawa akati aseke😂😂ngati nkhosa zikulira mu khola😅😅😅😅😅
Very nice conversation in this part I like you guys keep up helping malawian people's lives
kodi atati amenyedwa a mcp achakwela angamango yang'ana achipani awo akumenyedwa
Are they Malawians
Made in malawi always very expensive ,
aaaaa inu chokani apa mitu youmayo ndinu mbuzi za mcp asakuziwani ndani
Ndangwiliza nowe kodi chakwera akhoza kutuma anthu mukawateme mmmm ndizosatheka pena kodi amalakhulile kalindo munja ndili mu lilongwe muno ine sindimaopa ndine mwano oopsa amafuna anthu a mu lilongwe atani
Eish
Mmm
Mukhalitsa kwa mcp basi kodi ku kamuzu stadium anthu ankaimba achoke ankafuna otsatila mcp atani bwanji osakambapo imeneyi dpp idali ndi msonkhano kodi a mcp adapita nkumakaimba agogo agogo kodi musamakondele timadziwa ndinu a south nonse ndi anthu ozizindikila kuposa madela ena kodi tizitukuko tikuchitikati bwanji osamauzapo amalawi madzi mangetsi pano bolani
Zimenezo ndizimene ife tikufuna wina asanayambe ntchitoyo muziyamba kukawonamo Kuti asoyamo chani ndichani tatopa ndinyimbo yoti mboma tinapezamo mulibe chilichonse zimenezo ife zikutinyansa
Guys to be honest chakwera walephera and palibe amene angasangalale kut chakwera azakhalenso pampando we r tired
Kodi atola nkhani inu why are you lying to Malawians? President amanena mobwelezabweleza kuti he doesn’t condone violence.
Vuto ndi anthufe we need to take responsibility mtsogoleri sangalondere anthu 20 million tonsefe. Tisinthe tonse pathoka
its in nature of humanism to be reluctant, thus laws are put in place to control the society. European countries and America have stiff Laws to maintain order. However MPs and OPC are our policy makers, so if there is no order in a society we blame the policy makers.