Malawi first the people's first!!!,we can find pure diamonds without friction,let's go under friction so that we can find pure diamonds!!!.World belongs to the clever and strong pipo,Malawians let's be strong and very courageous courageous!courageous!
Uyu koma anafa kale samaopa ayi olo atazunguliridwa ndi asilikari achakwera .samaopa ayi koma uyu ndichisuro chosapindika 😂.uyu ndi ddengourous child for sure .wangoyamba kununkhatu
Keep it up abro,,God to guide n protect yu wherever yu go n whatever yu do n also the blood of Jesus Christ to cover yu from head to bottom n the whole body ,,God to keep yu under HIS canopy in Jesus christ name
Malawi first the people's first!!!,we can find pure diamonds without friction,let's go under friction so that we can find pure diamonds!!!.World belongs to the clever and strong pipo,Malawians let's be strong and very courageous courageous!courageous!
We need people like you kalindo,only legends know that your doing a good job pachilungamo suzasuntha,ifeso tizafera flag imeneyi
Malawi first ❤❤❤❤ big up brothers and sisters
Mulungu akudalitseni, kulila kwa amalawi mulungu akulandileni Ameen
Mademo anthu 4 basi zachibwana zokhazokha
Figure ya wanthu ilibe ntchito,koma uthenga omwe munthu wapereka
We want change things are not working to be honest. Kalindo wooooooeeeeeeeee 😂😂🔥🔥🔥🔥
Zaziiiiii
Blantyre The most loved city in South Nyasaland
Mvuto lako kalindo zi2 za clious ukulowetsa drama😂😂😂
Koma winiko ngati ndi chamba chikuphweteka😂😂😂😂😂😂😂
More fire malawi first 💪💪 Kom Mai akuyimika mkonoyo akundiwaza 😂😂 akhale adzanga😅
❤❤❤❤
Malawi first keep it up the good job❤❤
Zokongola Bwanji 💪👉🇲🇼🇲🇼
Our own pangoline the DC ❤❤big up all demonstrators mwatiyimirira mtima umakhumba km tatalikira .
Uyu koma anafa kale samaopa ayi olo atazunguliridwa ndi asilikari achakwera .samaopa ayi koma uyu ndichisuro chosapindika 😂.uyu ndi ddengourous child for sure .wangoyamba kununkhatu
Ndipo uyu ndee anamaliza macheza
beautiful drama
God have mercy on Malawi 🇲🇼 🙏
Koma anthu ndi zitsiru kkkkk, MOTi akukhara busy ndi zopusa . Taona ma demo ife osati zamowa izi .
This Malawi first fighting for real
Keep it up abro,,God to guide n protect yu wherever yu go n whatever yu do n also the blood of Jesus Christ to cover yu from head to bottom n the whole body ,,God to keep yu under HIS canopy in Jesus christ name
Ameñ
True
True
Police akuiona ngati yamao, The DC booooooon kalindo mwana oopsa kwambiri 🎉🎉🎉
The Dc chibooooon kalindooooo🔥🔥🔥🔥🔥kuti buuu
❤❤❤❤ADALA ABAMBO MUMAKWAKWANA INUYO MUMATIYIRILA THE DCEE
Well done malawi first indeed chakwela achoke
I love this 💗💗💗💗💗 chakwera akagwele uko
Good job more fire 🔥🔥🔥🔥
Mpaka winiko amakomoka 😂😂😂😂😂 Ndye.....
Mulungu akutetezele kalindo antill governments changes
Ukali 😊😊😊
Mr Bon kalindo🎉🎉🎉🎉 never give up let's go💪💪💪💪💪💪💪👍👍👍👍
Malawi first wooooooooye go komkoooooooo i like you guys
Ndizoonadi ife sitinalembesedi ndiye tivota bwanji
❤❤❤❤😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 booooon kalindo more 🔥 fire
Bon umakwana pitiliza kutelo mpaka Malawi abwelele mchimake😂
Power to the people, amalawi tiyenela ti vote,olo lD palibe.malawi,wthu uyu.achekwela,2025achoke.
Nkhani ikhale yoti chakwera achoke coz mavuto onsewa ndi chakwera
umakwa DC booono kalindo ❤❤❤❤❤
Ifetu a kalindo tili pambuyo panu ndipo osalola kupasidwa ndalama amalawi ambiri akuzuzika kwambiri
We like you Mr Dc
Chaka ndi chaka kulira chimanga nacho chakwera for me 😅😅😅😅😅😅
Woooow zoona boma ili linaloweradi mademo lizachokaso chifukwa chaa mademo
Mkangoo the DC
Kkkkkkkkk. Akuti nchiyani? Ozolowera kulandira agalu awa
Keep fire burning ❤❤❤ Born Kalindo
Maine bando yanga ndimaona ngati ndiona ofesi ya NRB ikupsyatu,amalawi ndife abata ndimtendere zedi mlooo🎉
Kkkkkkkkkkkk the dc sazatheka😂😂😂😂
Rest in Peace Bwana Saulos 😢😢😢Tikulilabe
Anthu kulibe a bon manyazi akugwireni
❤️🔥 more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Big up
Powerful 💪💪 ❤❤❤🔥🔥🔥🔥
May God bless
🤓🤓🤓🤓 ndizoona izo
DC ukukhwana tili pambuyo pako osafooka
God have mercy on us dziko siyili bho ili🥴🥴🥴
Osafooka 🎉❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥
Mademo anthu osakwana 100 koma anthu amasowa zochita eti kodi malaeo first ilibe donor kuti aziwapasa ndalama azitipasa aphawife bwaaa
Bon kalindo more fire
The DC ndi moto
Application awa ng'alula akumuona live
Masewera achabe ndalama zachepa mademo sangathandize
Kwende kwende che kalindo ku mangochi chakachi?
Good job kalindo
Umakwana DC
Good job more fire 🔥🔥🔥 the Bon Kalindo
The DC Bon Kalindo Moto kuti buuuuu
😂😂😂😂kma kalindooo
MCP already gone with Chilima believe me
Malawi first❤❤❤❤❤
Mwana woophsa kwambili
The DC🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
We like you Mr Dc 😢
Umakwana a DC ulemu wanu from Mozambique.
Until government intervene our plee
Bwana DC mwadya chamba chachabe😂😂
😂😂😂😂😂😂more fireeeee😅😅
Winiko ndikugulira jombo ya Argentina Canada uzivala Popanga mademo kkkk iweyo umatiyimilira
Yonse bho big man ❤❤❤❤
Umakwana DC keep it up
😂😂😂😂 make Malawi first a party pls winiko
Osatopa boma ili rinawibila mademo tilichotsaso mademo
🔥🔥🔥🔥🔥
The kalindo
Tikufunaso kuno mademo.omwewo Winiko
Chipani cha mcp chidzatopa chonkha kulamulira chifukwa anthu azindikira kuti akalindo akufuna anthu amenyere udindo basi
Izooooooo
Bornkalindo mulungu akuteteze ndi kukudalisa
Ulemu wanu big man bon kalindo
Malawi first 🔥🔥🔥🔥🔥
Akuti zamtudzu 😅😅😅😅😅😂😂😂🎉
👍🙏👌🤩👋👋👋👍
🔥🔥🙏
How can follow muthu wa ku gwa
Winiko km ndi boma palokha
Mulungu wathu sangatisiye boma ili likupita
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 4:57 Chokomoka Chiwiniko chotsilu chamunthu ichiiiiiiiiiii
Keep it up big
Ambwiyeeeeeeee che bon kalindoooo
The 😂😂 D cccxx
More fire Born Kalindo Malawi I follow you
More fire ❤❤❤❤ the DES
Kkkkkkkkklk anthu kuchitakuoneka kuti kulibe nkhwimbi laanthu kkkkkkkk kufuna kutamika basi akalindo
Anthu anatopa ndi mademu
Zaziiiii