Koma nacy chilungamo umachiziwa koma anagulukunyinda sakumva ndipo astsogoleri awa awumisa mutima kuposera falawo koma siku likubwera adzaziwa kuti Mulungu ndiwopambana oa nzose misozi ya amalawi singapite pachabe.chiteze akudya adzathu Mulungu akuona ndipamene wina akutenga ma thousand a anthu ulendo ku unga
Been here since day 1. Nancy my love ❤😂😂😂...lero wakwiya zenzen 😅
Page iyi ndimayikobda ngati bakili TV
Mmang'alula zenizeni simmawopa ayi
Iwe Nancy ndie ndikumagwilizana nawe kowoooopsya live aziyamika kuti Mulungu si munthu
More 🔥🔥🔥🔥 Nancy
You are number 1
Auze Nancy anthu osamva amenewa angofuna kuzilemelesa Iwo ndi azibale awo kmso ana awo kuwaiwala anthu omwe anawaika pampando ndipo adxafadi imfa yowawa
I don't miss any episode 😂😂😂
😂😂😂😂kooooopsaaaa koma Nancy
Nancy ur number 1
Koma Nancy umango booleza umandisangalatsa😂
I have never seen President opusa ngt uyu sangatumizeko ena kut akamuimilire?
🤣🤣🤣! Koma nancy ndizoona anthu akeo aaah koma asatana amenewa ai zikomo zosawakhuza olo nkomwe
🔥🔥🔥🔥
😂😂😂😂koma nancy amameza malovu poyakhula kkk
Nancy is here again. Lets Comment, Subscribe, like and share. Love you all!!!
Nancy kma Uli ndi Loyah 😂😂😂
Chekope ulem wanu bwana
😂Koma Nancy chilungamo amachinkhutura
Eeeee koma mmmmm zooopsya ndipo anthu zeru zatha koma ngati chili chikuwawe mmm ayi
😢😢
😂😂😂😂😂 Nancy chimene umandisangalasa ulindichilungamo Moyo mwako
Koma Nancy uli ndi loya? Ayi zikomo
Atsogoleri athu awa nawomsooo
Kkkkkkkk nawonsoooo
Kkk-oh-oh-wooopyssyaaa😂😂
😂😂😂Ali ndi dyera nawonsooooo
To be honest manyaka okhaokha
😂😂😂 komatu nancy nawe siku lina ustabwele poyela anthu azakuone
Nawe usanakhale angati bakili mulusi tv ozaoneka nayeeeemso
😂😂😂😂💙💙💙
Nancy iwe sikunache😂😂
Pompanopa Nancy akhala lawyer wa amphawi ife kuno taponya kale vote kkkkkkkk
Nancy awuze achina sonda mfiti yaikazi kkkkk 😂😂😂
kkkkkk tayenda bwino
Vuta la chakwera ali kunja kwa boma wachinda kwambili agalu ndi chifukwa pano mutu sukuyenda
Asambwaze Naaaaaaa
Ati pamene pali njira Mulungu amayika njira
Nancy usakidwa 😂😂😂
Chifukwa chamantha ngat awa ndichifukwa chake andalewa samatiopa popanga zinthu
@@charleshenderson70 mayaz ngat ine ndiwamantha
😂😂😂😂😂nancy nayeso
Koma nacy chilungamo umachiziwa koma anagulukunyinda sakumva ndipo astsogoleri awa awumisa mutima kuposera falawo koma siku likubwera adzaziwa kuti Mulungu ndiwopambana oa nzose misozi ya amalawi singapite pachabe.chiteze akudya adzathu Mulungu akuona ndipamene wina akutenga ma thousand a anthu ulendo ku unga
Nancy uzimezelako malovu😂😂
😂😂😂😂😂
😂😂😂😂
🤣🤣🤣
Kkkkk Nancy tsopano
😂😂😂😂