Комментарии •

  • @HastingsJonathan
    @HastingsJonathan 5 дней назад

    Chembonera my favourite

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t Месяц назад

    Mafunso Mbola Jokes,,,siiwedi mtolankhani

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 Год назад +3

    Inu ndi Piksy mumaimba bwino kwambiri ndipo mumakwana, kulekana kwanu kunakhumudwitsa malawi yense, takusowan

  • @chisomophiri2259
    @chisomophiri2259 Год назад +2

    Program yabwino but mr jokes improve your questions 😅

  • @user-ec9om3og2x
    @user-ec9om3og2x Месяц назад

    Iwe jokes sutha kufusa ma Fuso kkkk

  • @chisomogadama4921
    @chisomogadama4921 Год назад +1

    Voice ndendendee nd ngozo

  • @fedson2050
    @fedson2050 Год назад +1

    Very nice 👍

  • @ibrahimchakwana6614
    @ibrahimchakwana6614 Год назад

    Very nice

  • @Kakajkapinga6538
    @Kakajkapinga6538 Год назад

    Izikasiyana p square ma twin
    Even favoured sister inalekana

  • @DivineSyntaxMw
    @DivineSyntaxMw Год назад

    Akuti ukapemphera kwa Mulungu ameneujayo ndi amene amakuuza kuti nkhaniyi utere kapena uona kuti upanga nayo bwanji😂😂🙌

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t Месяц назад +1

    Palibe chanzeru Jokes ukufunsa Apa,,,sukukhazikika pa mafunso Ako,,,Funso loyamba ....mudasiyana bwanji ndi piksy,,,,Koma komwe zapitako kuvwakanyavwakanya basi

  • @isaaczulu6296
    @isaaczulu6296 Год назад

    Nice

  • @joshuakastom
    @joshuakastom 14 дней назад

    a jokes mafunso ake aaaa

  • @jamesjolichi2026
    @jamesjolichi2026 Год назад

    Akanandimanga ndikanaswa mtima wo😂

  • @masautsothomas1946
    @masautsothomas1946 Год назад

    Kkkkkkkkkkkk jokes umudziwe yesu

  • @graciankabena5931
    @graciankabena5931 Год назад +1

    Apa nkhani imene anasiyanilana sindikumvapotu, program yabwino koma mene mukupangira simukukhazikika pa point

  • @joanahwchiwangah9267
    @joanahwchiwangah9267 Год назад

    Jokes nkhaniyi siudaiyambe bwino koma title imenei ndi y ofunika zedi

  • @mussamanda4839
    @mussamanda4839 Год назад

    Iiiiiiiiiiiii mr jokes kukonda kuseka😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @witbridge7611
    @witbridge7611 Год назад

    Koma mafunso ake🤣🤣🤣🤣

  • @Fatima-ck3mu
    @Fatima-ck3mu Год назад

    🤣🤣🤣🤣🤣 jokes amenewo ndimafunso aaaaah uzikhala srs

    • @willsonmzumala
      @willsonmzumala Год назад

      Akulu izi musiye cuz simuziwa poyambira ngankhale mafunso akukanikani mukuchita kuzilidwa zochita ndimulendo that's nonsense

  • @rashwillstech
    @rashwillstech Год назад

    🤣🤣🤣

  • @moosathomas6440
    @moosathomas6440 Год назад

    Jokes be serious

  • @mussamanda4839
    @mussamanda4839 Год назад

    Thumwi🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @ednahndalama6817
    @ednahndalama6817 Год назад

    Muzipelekako mpata munthu azimaliza kuyankhula.. improve on your listening skills Mr jokes

  • @Eliasiwhite-foreveryoung
    @Eliasiwhite-foreveryoung Год назад

    Nkhani yakuba dholar ija mwaiiwalaso