CDEDI PRESS BRIEFING LIVE - “LIPOTI LOPANDA PAKE, TULUTSANI LIPOTI AMALAWI AKULIFUNA LERO - NAMIWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 16 дек 2024

Комментарии • 28

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 6 часов назад

    Kuchoka kwa Namiwa mu inquiry anachita bwino bwenzi atampaka coz iye ananena kuti inquiry ikhale openly , azibale, achipani akhalemo koma a mcp anakana chifukwa akudziwapo kanthu .Bravo Namiwa God be with you

  • @CynthiaLiviel
    @CynthiaLiviel 3 часа назад

    Namiwa Mulungu Akudalitsen ukapatsa Moyo wautali

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 9 часов назад +1

    Ambuye akumva ndithu ndipo tsiku lina azayankha mapephero Awana ake . Mabvuto onsewa ndi chilima ndi ntambo Ambuye awaone ndithu .anthu eight omwe anafa osalakwa aja azibale awo akulira daily kufera za Eni ake nnnnh

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 7 часов назад

    Namiwa afunseni kuti chimwendo anakanika kukwela ndege why? President, General , kunkuyu ananena zosiyana

  • @GersonMadikhula-n9x
    @GersonMadikhula-n9x 9 часов назад +1

    Namiwa you are brilliant Man and keep it up by acusing what ever is wrong, open our eyes and put Malawians in a right path,, I would happy if you could just stand in political side in order to govern and save Malawi in one side, please

  • @PeterDavid-k4g
    @PeterDavid-k4g 7 часов назад

    Kkkkkkkkk mkwiyo kuti mudatuluka ku state house????

  • @ntombiunice8637
    @ntombiunice8637 8 часов назад

    Fisi amaneyo bwanji anathawako

  • @MphindiraChimwemwe
    @MphindiraChimwemwe 8 часов назад

    Choonadi amalawi akuziwa asatitenge ngati ife zitsiru ayi

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 8 часов назад

    Exactly mr namiwa atiwonjeza chakwela ndi azake

  • @vincentmatemba1659
    @vincentmatemba1659 8 часов назад

    Vuto ndiloti a malawi ndife opusa sitichedwa kuiwara zikachitika amangoti basi zatha

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 9 часов назад

    Namiwa mulungu akhale nawe poti umanena chilungamo

  • @MikeligsonPhiri
    @MikeligsonPhiri 9 часов назад

    Namiwa umakwana

  • @VioletMbale-o4y
    @VioletMbale-o4y 9 часов назад

    Am confused ine please zikut bwanji? 😢

    • @MervinKandoje
      @MervinKandoje 8 часов назад

      Who expect you to understand? 😂

    • @VioletMbale-o4y
      @VioletMbale-o4y 8 часов назад

      @MervinKandoje you of course 🤣🤣🤣 ndimayesa report latuluka kale nde namiwa akuti report lina nde liti?

    • @MervinKandoje
      @MervinKandoje 8 часов назад

      @@VioletMbale-o4y people like chose to praise politicians even if they are underperforming or telling lies you always stand by their side so expect such people to understand the truth is just wasting time

  • @vincentmatemba1659
    @vincentmatemba1659 9 часов назад

    Anamiwa inu ndi munthu wamkulu mumalizindikira boza nsanga kuti uyu akunama

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 9 часов назад

    Awa ndi a chitsiru anakuyikamo momuja munathawa nokha pano anzanu atulusa report mukususanso

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 9 часов назад

    Palibe chanzeru ndikunva ine apa

    • @alicemalika677
      @alicemalika677 8 часов назад

      What do you mean Malawian we are praying for the beloved country MALÀWI

  • @MphasoChirwa
    @MphasoChirwa 9 часов назад

    Namiwa ndiwe Garu kwa basi ,chifukwa chani unachokamo ,Garu iwe

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx 9 часов назад

    Zikolomvesa chisoni

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 9 часов назад

    Ichi ndiye chidzete chenicheni. Kuchiika mucommision nkuthawamo pano akuti report ndiyabodza

    • @alicemalika677
      @alicemalika677 8 часов назад

      Chizete ndiwe one mbale wanga anaphedwa nawo ndipo tikupempherà Mulungu akumva

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 9 часов назад

    Report ijadi ine ndmaziwa kut chakwera analinayo kale

  • @RilJacksy-w5t
    @RilJacksy-w5t 9 часов назад

    Kona musayiwale kut mayi yolamu munawapatsa 48hrs pano zili pati

    • @MemoryZiyaya
      @MemoryZiyaya 9 часов назад

      Mesa dziko lilimmanja mwa chipani chawo ..ndeangave zamunthu..😅😅😊
      Azimai angapo eeish