BON KALINDO LERO PA 22 JULY 2024 |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 сен 2024

Комментарии • 37

  • @lyiemax
    @lyiemax Месяц назад +5

    Powerful speech and strong advice from our beloved president, the Dddddd Cccccc ❤❤❤

  • @user-mk7fh5ml8s
    @user-mk7fh5ml8s Месяц назад

    Good speech mr kalindo❤❤❤.but chakwera vuto ndi mphawi Ndiye akuona ngati kuti akatula pansi udindo asauka.Sinanga umphawi unamphweteka kwambiri.

  • @juniorpeter2285
    @juniorpeter2285 Месяц назад

    Good advice... 🔥

  • @kanjibamumba4963
    @kanjibamumba4963 Месяц назад

    The D.C BORN KALINDO!!!!!!!!! ZAMBIA HERE LUSAKA

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft Месяц назад +3

    Achinyamata anzanga tiyeni tisegule maso ,osamaimbira mmanja zisilu let's be wise and open our eyes 👀

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Месяц назад

    Aaaaaa kodi mtsikana iwe kalindo ulipo uasatisokosere mutu wokhala Ngati mbinawo galu 😅

  • @MaxwellBanda-xd6oh
    @MaxwellBanda-xd6oh Месяц назад

    Power massage and power unity

  • @AbdulrahimoMassamba
    @AbdulrahimoMassamba Месяц назад +2

    More 🔥.

  • @user-lr2wx5xd9d
    @user-lr2wx5xd9d Месяц назад

    Strong voice

  • @PSTPerivoli-xd1ot
    @PSTPerivoli-xd1ot Месяц назад +2

    nanga mmene zililimu palichifukwa chovootera muthalikaa?

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Месяц назад

    Boooorn kalindo

  • @MaxwellBanda-xd6oh
    @MaxwellBanda-xd6oh Месяц назад

    Mr boni kalindo tikudalira inu

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane Месяц назад

    Ndipo ndizoonadi tilipo ambiri tinachokako ku Malawiko khani kulibe ndalama pano tili ndi zaka 7 panopa mu Botswana timafuna kubwera kumeneko koma kwacha yakeyo 😂😂

  • @FaithTricia-q5d
    @FaithTricia-q5d Месяц назад +1

    Ndipo zoonad sukunama the DC woyeeeee

  • @user-ih7li3im4s
    @user-ih7li3im4s Месяц назад +1

    Iweyo ndiwa mfundo kuposa manganya sure

  • @DannyDaka-sn2fj
    @DannyDaka-sn2fj Месяц назад

    Ndimalondola khani za bon kalindo nkhani zimandingila mtima koma video ndiimozi naimozi?

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Месяц назад

    Munyamata opusa ndi amene akulandila 2000 ndikuononga chilungamo wachinyamata opusa ndi amene akusangalala ndi ngongole yomwe singamupindulire . Tachinyamata sitikufuna kupita kumaiko akunja tikufuna ziko lanthu mukhale ntchito tizigwira muziko mwanthu tiyeni tizuke . Opposition wamphavu kumalawi ndi DC tantiwa bakili TV kalua game changer munyanyiwa . Anthu inu muyambise chipani kumalawi kuzasintha simukufuna kubera amalawi komaso mumayima pa chilungamo. Osagulidwa ndi ndalama ngati ena.kuti president wako wamwalira mosaziwika bwino iwe 7 days ndikulandira udindo pali zeru

  • @Costance-nf7ue
    @Costance-nf7ue Месяц назад

    Manganya alindinzeru chisilu cha munthu chimenechi chopanda mfundo fotseki

  • @PaulKanyoza-bi4xi
    @PaulKanyoza-bi4xi Месяц назад

    Uthenga wachilimbikitso ndipo watisegula maso

  • @user-sw8bb3iz7x
    @user-sw8bb3iz7x Месяц назад

    Viva kalindooooo

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Месяц назад +1

    Abon kalindo.....point of correction;Chilimatu sanali munthu wabwino ndipo balibe chabwino chomwe anachitira amalawi...km a malawi akuonetsa kut ali kumbuyo kwake chifukwa cha mmene adaphedwera ndi MCP..Km musanene kut akanasintha zinthu...he was the worst

  • @CosterMustafa
    @CosterMustafa Месяц назад

    The DC please kapangeni mademo lero kumangochi chifukwa chakwera walawila lero kumeneko akut akuyendara mmafamu kumeneko Ky akufuna chani😂😂😂😂Ife ctikufuna the DC ndipo pelekelani micro foni kumeneko mutiuuze zosatila💪💪💪

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Месяц назад

    The Dc bon kalindo good Messnge ❤

  • @user-ns2po8ng5k
    @user-ns2po8ng5k Месяц назад

    Bravo No Retreat No Surrender

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Месяц назад

    Kudziva ndi kudzikuzi ndi kulalatila ena chifukwa cha ntchito yomwe umagwila zimangosonyeza umbuli
    Pa ntchito yakoyo, uyembekezele zinthu ziwili pa ntchito yakoyo kuchotsedwa kapena kufa,,,

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Месяц назад

    Perfect talk the DC.

  • @user-ln5hw7dn9g
    @user-ln5hw7dn9g Месяц назад

    Let's open our eyes guyz

  • @InnocentMedison
    @InnocentMedison Месяц назад

    Apo walankhula mosaopa

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan Месяц назад

    The DC...💓

  • @EviePhiri
    @EviePhiri Месяц назад

    Dolo kwambiri

  • @LatifBeni-e6z
    @LatifBeni-e6z Месяц назад

    ❤❤

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli Месяц назад

    Zoonadi Amfumu

  • @Vascomw
    @Vascomw Месяц назад

    T̈ḧë DC

  • @Vascomw
    @Vascomw Месяц назад

    K̈ẅb̈r̈ l̈ïv̈ë

  • @CatimboJosé
    @CatimboJosé Месяц назад

    Zoliboh

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon Месяц назад

    The deceeee