Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Well said
Amen fathermau achilimbikitso tinali munthawi yankusadziwa ndipo mulungu adatilekelela
Powerful massage and 🙏 chilichose ....sichikuyenda....ndipo tawonanyekhwe😅😅😅😅😅
Powerful message
Apapo ndiye mwabwela so pano abusa mulungu akhale nanu ❤,, God bless you
Ambuye mutikhululukire amalawi father god bless iu muzitiuza zoona ma Church kuti timasuke tipemphere dziko l lathu
Lord have mercy
Ulaliki wabwino father
Amen 🙏 son of God 😭😭😭😭😭
🙏🙏
Kodi umeneyu ndi ulaliki kapena campaign 😂😂
Nanga choncho mu Chechi ana anjoka pembedzani mafanowo
Amen 🙏
kodi akatolika panopa makalata simuntha kulemba?mapepala mulibe?kapena ballpoint??tell me if it an envolop then ndikugulireni
Komanso achakwela.khalani ndi umunthu pangani re-sign pliz pliz pliz
Amen
Pamenepo timati kumva nkhwangwa ili mmutu. Munaonjeza ma bishop kufuna ung'onoung'ono apa mwalapadi nanga simphatso akkhristu sakupeleka mokwanila.
Mwakamba bwino koma sindinamve mawu opepesa ..mukanakhala wina mukanayamba ndikupepesa kwa anthu omwe munawasocheletsa😂
Kod ndindana makamaka
Mwachita manyazi lero! Munali nawo mu team yothamangitsa DPP inu, lero mwaziona
Mawu mawu
President wathu tinamuthandiza kwambiri koma lero akutipanga chipongwe.........Mulungu mutisogolere
Koma ndiye,
Aloma ndi anthu adziko lapasi ndifukwa amalimba zadziko ndi ameneso atadzabwetse 666 ndikuwononga ziko chipulumutso palibe
Chakwera ngat samatamba amangouluka dziko lonse kumuika PA map Ai fekisi
Vuto la aMalawi mavuto timachita kidziitanira
Wasembe uyu ndikatundu
Medicine after death
Mau achilimbikitso,zikomo pozindikira kut munatisogolera kolakwika komanso vuto sindinu ai vuto ndi msogoleriyo pozikundikira
Ame 🧎♂️🙏🙏🙏
Tinamulakwira mulungu Koma panopa tikupempha mulungu Kuti atikululukire Satana anatinamiza Koma tachimina ndithu Malawi sali pa bwino tili pa moto
Sure, Mulungu atikhululukiredi zinthu sidzili bwino.
Amen ❤
Well said
Amen fathermau achilimbikitso tinali munthawi yankusadziwa ndipo mulungu adatilekelela
Powerful massage and 🙏 chilichose ....sichikuyenda....ndipo tawonanyekhwe😅😅😅😅😅
Powerful message
Apapo ndiye mwabwela so pano abusa mulungu akhale nanu ❤,, God bless you
Ambuye mutikhululukire amalawi father god bless iu muzitiuza zoona ma Church kuti timasuke tipemphere dziko l lathu
Lord have mercy
Ulaliki wabwino father
Amen 🙏 son of God 😭😭😭😭😭
🙏🙏
Kodi umeneyu ndi ulaliki kapena campaign 😂😂
Nanga choncho mu Chechi ana anjoka pembedzani mafanowo
Amen 🙏
kodi akatolika panopa makalata simuntha kulemba?
mapepala mulibe?
kapena ballpoint??tell me if it an envolop then ndikugulireni