DR CHAKWELA AYANKHULA MOSAONA NKHOPE 🤔🤔🙌🙌8 August 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 окт 2024

Комментарии • 301

  • @FungulanReuben
    @FungulanReuben 2 месяца назад +22

    Bwana, muntengo mulimo musika posachedwapa , tikukudikilani tili pansi pantengo pano,

    • @lysonkaselema7321
      @lysonkaselema7321 2 месяца назад +1

      Kkkk chibonga chili mmanja

    • @Santo-B
      @Santo-B 2 месяца назад

      😅😅😅​@@lysonkaselema7321

  • @LloydPhiri-d6f
    @LloydPhiri-d6f 2 месяца назад +3

    Nice speech to those who have right heart .
    Don't hate someone on what you don't have it's evidence.

  • @allahslave7177
    @allahslave7177 2 месяца назад +14

    Chipani chakupha with a president with flowering speech but without action

    • @jestinanamkonda1495
      @jestinanamkonda1495 2 месяца назад

      Nsanje too much enanu

    • @allahslave7177
      @allahslave7177 2 месяца назад

      @@jestinanamkonda1495 ngati mmutu mwanumo muli mwa bwino bwino mukutha kuvomereza kuti ndi zoona , unless otherwise

  • @ChifundoGoster
    @ChifundoGoster 2 месяца назад +1

    Kulankhula kwa nzeru. Lord have mercy on you Mr President

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 2 месяца назад +11

    Ummmm atsogo chipani cha mcp sichinalowepo m'boma koma tonse alliance mongokonzapo😂😂😂

    • @Angel-dt6oe
      @Angel-dt6oe 2 месяца назад +2

      Auzen asachite. Matama😂

    • @MahamudKambanje
      @MahamudKambanje 2 месяца назад

      Kkk saziwa kut chipanda Chilima uja sakadalowa

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 2 месяца назад +4

    He has done this because of the broadcast of the kwagwanji program.

  • @LameckDanken-tm4rt
    @LameckDanken-tm4rt 2 месяца назад +1

    Wise speak 😊

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 2 месяца назад +7

    For the First time in History, respect to the speech writer.

    • @emmax9101
      @emmax9101 2 месяца назад

      Ineso ndadabwa nazo 😂😂

    • @amoschataika7440
      @amoschataika7440 2 месяца назад

      @@emmax9101 Kkkkk koma wayankhula bwino kwambiri.

    • @InnocentMtafya
      @InnocentMtafya 2 месяца назад

      Mostly the narrator knows what he is..

    • @gradsonmayira9336
      @gradsonmayira9336 2 месяца назад

      😂😂😂 speech writer 😂😂 ndi dolo

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk 2 месяца назад +1

    Thanks Mr pr speach ya mphanvu kwambir

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 месяца назад +1

    Follow up from Robin Island CapeTown, this is how a leader must be, not to soult someone , this is what we want, to love one another in warm heart of Africa

  • @BladesBullets-pu5uw
    @BladesBullets-pu5uw 2 месяца назад +7

    Apa ndipomwe ndakhulupirira kuti Sarawa kwawo nkulankhula, nanga anthu omwe amagawa ndalama akuwadziwa nchifukwa chani sanawaitanire kumbali. Angofuna kutamika pamaso pa anthu.

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 2 месяца назад +8

    Linda madzi apite kenaka udziti ndadala chikhla mcp njowina si bwenzi kuli zisankho don't forget mwamuna nzako mpachulutu😅😅😅😅😅😅

  • @FWhite-w3l
    @FWhite-w3l 2 месяца назад +5

    Palibe yemwe akukufuna mr chikangawa wakupha mfiti wasataniki unapha chilima ndi anthu 8 komanso unapha kasambala unapha sidiki miya

  • @danielmagwaya1074
    @danielmagwaya1074 2 месяца назад +8

    Mfiti imadziziwaka kuzibitsa mu dzina la mulungu bwanji

  • @giftjamali8204
    @giftjamali8204 2 месяца назад +3

    Ndine wa DPP but speech iyi nkukuyi walakhura bwino kumbali yachipani chawochi koma kukhani ya dziko ndine wa DPP

  • @kondwanivyalema9449
    @kondwanivyalema9449 2 месяца назад +15

    Mwazi wa Chilima ukukantheni munapha munthu wosalakwa anthu oyipa inu

    • @Aqiec09
      @Aqiec09 2 месяца назад

      Unapha ndiwe chilima only if you have proof we can support the truth

    • @bisweckchimphamba8497
      @bisweckchimphamba8497 2 месяца назад

      If you support the truth ,where is a report of his accident?

    • @leoleonard2103
      @leoleonard2103 2 месяца назад

      Zowonaa

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 2 месяца назад +2

    Uyu ndimwamuna eeh….koma opposition mulimba? Well said your Excellency 👏🏾👏🏾

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 2 месяца назад +1

    Ukunama mphwanga chakwela u will never win again,uiwale

  • @yosefemichael7588
    @yosefemichael7588 2 месяца назад +1

    Strong voice Mr president

  • @LuciusScott-h7b
    @LuciusScott-h7b 2 месяца назад +1

    True

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад +2

    Mwayankhula bwino koyambirirako, koma kumapeto mwayankhula mbwereraa.
    1.Simukanawina kupanga Chilima kutiuza ife kut tikakuvotereni.
    2.Zokuti mipando ndiyosirana mwangoyankhula koma inuyo simumafuna kusira ena, thus y mumayankhula Chilima alipo kut muzayimira 2025 ngakhale mumaziwa kut munagwirizana zozasinthana.
    2.

    • @RejoiceKamanga
      @RejoiceKamanga 2 месяца назад

      Iiiiii zoona ndithu sakuganiza komwe uyu.

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h 2 месяца назад +1

    Kuyankula kwabwino km mene mwayankulilamo mutangoyelekeza kutsitsa katundu kmso m'msokho mmmmm mungawineso 2025 km ngati simutelo kkkk kaya

  • @RichardlawyerPatrick
    @RichardlawyerPatrick 2 месяца назад +7

    Iwe ndi zikhale ng'oma wakoyo muzavotane paubale wanu osadanda 😂😂😂

  • @LazarousNamakhwa
    @LazarousNamakhwa 2 месяца назад

    Feteleza k200 000
    Chimanga k65000
    Mchele 2000
    Mankkwala muzipatalamu mulibemo Pali chifukwa chovotela mcp apa

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 2 месяца назад +1

    Zowinazo ndiye aaaaa ayiii. Dzikolino kungowinanso MCP 🐊 dziko lathela pomwepo

  • @TressLuka
    @TressLuka 2 месяца назад +2

    Uyudi ndi oyipitsitsadi 😎🇲🇼

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 2 месяца назад +2

    Why don't you allow people to compete with you as president?

  • @nelsonsikwese5952
    @nelsonsikwese5952 2 месяца назад +3

    Nice speech Mr president

  • @aubreykamwendo4315
    @aubreykamwendo4315 2 месяца назад +1

    Zowinazo ndy eeee mukutinamiza ngt sipakhla kubela

  • @SABANLOWE
    @SABANLOWE 2 месяца назад +1

    Nice speech

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c 2 месяца назад +1

    Usatinyase chikangawa ife tikufuna liport landenge bas

  • @AbdullahaziziAmoswalala
    @AbdullahaziziAmoswalala 2 месяца назад +12

    Zowinazo nde zokaikitsa boss 😂😂😂

  • @georgemsowoya6525
    @georgemsowoya6525 2 месяца назад

    Our president has failed us malawians....the confidence of malawians has gone in vain.....tel us what good have you done?

  • @InnocentMtafya
    @InnocentMtafya 2 месяца назад

    Ansanje aphulika ,abwana amadziwa kuyala nfundo,sizachibwana akumachita enawo ngati ana a primary ang'ono achambanso ine sinpanga nawo ayi,abwana konzani dziko mosanyengelera wina oononga mindset ya ana ndi anthu opanda look sharp...power hungry siyiathandiza.

  • @JohnKaudzu
    @JohnKaudzu 2 месяца назад

    Good report imafunika osat kumazinamidza

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 месяца назад

    Chakwela yomweyo misewu palipotse town ya Lilongwe yikukwela modetsa khawa abwana tchito mwayiyamba bwino kwambili chatsala kusitsa fertrazer kuti adzipedzeka palipotse Kuti chakudya chikhale palipotse mu malawi,, MCP hoyeeeee wina afune kaya asafune yilamulilanso 2025

  • @AsimenyeMwalwanda-kh8ir
    @AsimenyeMwalwanda-kh8ir 2 месяца назад +4

    Ife tinavotera chilima osati iweyo uthokoze utm

  • @TRIPLE-w1s
    @TRIPLE-w1s 2 месяца назад +1

    Kkkkk zowinasokhazo Kaya mwina😊

  • @RichardlawyerPatrick
    @RichardlawyerPatrick 2 месяца назад +7

    Ife sitikukufunan bambo😂😂😂😂

    • @InnocentMtafya
      @InnocentMtafya 2 месяца назад

      Ndiwe opusa ukuona ngati iwe ungafunidwe Ndi munthu wankulu ,gwiritsani brain zanu bwinobwino not these stupidit comments...

    • @godricktsakama3954
      @godricktsakama3954 2 месяца назад

      Uziti ine osati ife ngati takutuma

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 2 месяца назад +3

    Ayi chipanda chilima bwana simukanakhala president ndichifukwa mwamuphaa eti

    • @InnocentMtafya
      @InnocentMtafya 2 месяца назад

      Nanga popanda bwanawa Ndi pure evidence yao ,nthawi ya Presidential electoral case bwezi mutawina panokha,? History is not forgotten at all, nthawi inafika kuti bwanawa akhale pampando after so much struggle some which are questionable in my brain until date.. NICE SPEECH our head of state ✊✊✊✊✊✊✊✊✊✊✊✌️✌️✌️✌️✌️✌️✌️

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s 2 месяца назад

    Munalowa mboma chifukwa cha Dr Chilima munapha uja panokha mwakhala mukulephera and utm yomweyo ikutulutsani mumbomamu ndipo mudzalira ching"ang'azi next year

  • @Blessingskanyinji-x7s
    @Blessingskanyinji-x7s 2 месяца назад +1

    Mumene kwachera lero masiku akupita muziweso kt munawina chifukwa cha skc kopanda apo somukanawina manyazi bwaaaa😢😢

  • @jameschibwana2751
    @jameschibwana2751 2 месяца назад

    "Actions speaks louder than words."

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 2 месяца назад

    Koma uku after convention imeneyi kukhala ma exodus "mark my words"

  • @Yanjanani
    @Yanjanani 2 месяца назад +3

    Km ameneyi ndi galudi et? Dr Ch sindimaliza angandidyetse ng'ona😂

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo 2 месяца назад

    Dzikomo kwambiri a President chifukwa cha mau anu.
    Dzikomo kwambiri a khoti polora aliyense kuvoteledwa.
    Funso. = Kodi omwe analetsedwa aja. Angapambane bwanji popanda kupanga Complain?
    Popeza mwatiuza nokha a President kuti ambiri a ononga ndalama zambiri kukopera anthu. Khoti enawo lisanawavomeleze
    Dzikomo a Khoti.

  • @FahadiFalaji-q8y
    @FahadiFalaji-q8y 2 месяца назад

    Mbavayo

  • @SinoliyamuBanda
    @SinoliyamuBanda 2 месяца назад +1

    nice big

  • @simonejose8925
    @simonejose8925 2 месяца назад +2

    ZIKOMO MFUMU LA FUKO LA MALAWI AMBUYE AKUDALITSENI NDINE MWANA FELIX THOMUSEN TEMBO NSANJE SOUTH CONSITUENCY NSAMBA POLING CENTER

    • @clementmahoka6287
      @clementmahoka6287 2 месяца назад

      introduction imeneyi bwanji? mukuyese abwera kuzakuonani kkkkkkk

    • @TheresaMuthowa
      @TheresaMuthowa 2 месяца назад

      Kikikikikikkkkkk

    • @TiyanjaneMkwate-we8gu
      @TiyanjaneMkwate-we8gu 2 месяца назад

      Mwazipanga introduce bwino ndithu, maluzi omwewa kapena ndipeze loyer?

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 2 месяца назад +3

    Saulo chifunga chikangawa chakwera

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 2 месяца назад +3

    Kutipula paground nde kubako

  • @CharityChirwa-t1e
    @CharityChirwa-t1e 2 месяца назад +1

    Zikomo andevu zamwayi mwayuka mawu nkamwa achakwela kuti ayakhuleko zogwilakobmutu khakhale amangoyakhula zoti sizingatheke amenewo ndiwo Mr chikangawa 😂😂😂

  • @JonathanZaithwa
    @JonathanZaithwa 2 месяца назад

    Moto kuti buuuuuuuuuuuuuuu sakufuna akhale 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2024 bomaaa

  • @RejoiceKamanga
    @RejoiceKamanga 2 месяца назад

    Sindikutha kuvesa mnthu wamulungu samakhala ndi nitima chonchi. Ndilibe zoyankhala zambiri ayi kma my last word is. Mkuyenera kuziwa nthawi yamulungu. msapusisike ndi chuma ai. nthawi yatha izi mzazisiya ndizikoli simuzanyamula. I can see it. This is challenge speech.

  • @xadrequejohnsantos9188
    @xadrequejohnsantos9188 2 месяца назад

    Good man

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 2 месяца назад

    He's very good on speech, koma kutsatira zomwe anena ndikomwe kumavuta

  • @CELECTRICALCHILOMOH
    @CELECTRICALCHILOMOH 2 месяца назад

    Well speaking Mr president ❤

  • @MadandoChannel
    @MadandoChannel 2 месяца назад

    Alex major is the only one mcp can change than even a chakwera 😂

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 2 месяца назад +2

    Koma gwenembe aaa

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 2 месяца назад

    After kuchita Ndale za usiku then the path is cleared, someone is buried 7 feet under as we speak.

  • @EviChio
    @EviChio 2 месяца назад +1

    Ndiye mudzikonze nokha. Chifukwa inu a MCP mukugwilitsa ntchito ndalama pofuna mpando

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад +2

    Mr chikangawa fundo mulibe zowina muchonse inu palibe mapwala ako akukunamiza chifukwa umaba ndikumapasa uwonaso chaka chamawachi

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад

    Zikhale ng oma ukumva kumene uliko akukusambilatu manja ineyo chipani changa chosapota bakili muluzi TV koma chakwera lero ndakukonda wayakhula mwazeru

  • @MpapiParadise
    @MpapiParadise 2 месяца назад

    Galu ameneyu uchitsiru udamuyanja - zoti idali ncp sakuziwa mmmm

  • @CHIMWEMWECHILUNGA
    @CHIMWEMWECHILUNGA 2 месяца назад

    Zadziii kodi amphawife nde dzida zanu,tinalakwa kukhara anthu osauka bull shit, kodi mmesa tili mu tonse alliance MCP ndekuti chani

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад

    Chakwela machende ako wamva panyo pako iwe tikuwona next year mbuzi ya munthu mfiti yayikulu

  • @MasekoKalimanjira
    @MasekoKalimanjira 2 месяца назад

    Bwana tili pambuyo panu,boma iloooooo😅🎉

  • @ThokozaniDavismlamba
    @ThokozaniDavismlamba 2 месяца назад

    Chikangawa woyeee!!

  • @Kachimera
    @Kachimera 2 месяца назад

    Amene analemba speech iyiyi nd goat😂

  • @MadandoChannel
    @MadandoChannel 2 месяца назад

    😂😂😂😂We are a disgrace as Malawians political parties will never ever develop Malawi.

  • @ErnestManda-iz2sr
    @ErnestManda-iz2sr 2 месяца назад

    Garu iwe kipusa kwako chimutuu chaoko

  • @DanielNamate
    @DanielNamate 2 месяца назад

    MCP mpaka Yesu azabwera ikulamurabe. Wina afune kaya asafune koma boma ndilomweri mpaka kale ndanena ndanena.

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 месяца назад

    Ine monga president wakupha anthu😢😢

  • @JohnBanda-k5y
    @JohnBanda-k5y 2 месяца назад

    Bwana amkaka akukunamizani bola mukanamusiya biyeni apa mwatsekula maso Malawi kuti chipani ichi mchamagazi

  • @CellinaNgolingoli
    @CellinaNgolingoli 2 месяца назад

    Tasauka kale chifukwa chaiwe chakwela bolani mubwelele ku tchalitchi konkuja tatopa nanu inu ndi chisanzo choipa mwapha chilima

  • @FridayKapito
    @FridayKapito 2 месяца назад +1

    Lero apresident mwayankhula zamphamvu kwambili

  • @yakiduidi5752
    @yakiduidi5752 2 месяца назад

    Bola kunyoza pomwe iwe unawinila kupha anthu komaso mademo ndi chisilu kwa basi imeneyo ukuti fundo kodi mesa uayambisa kunyoza ndi iyiweo

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 2 месяца назад

    Kuwerenga or kuyankhula??

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 месяца назад

    We want report for chilima's death.. ndege inagwa chifukwa chani??

  • @SaleemEid-sr5ph
    @SaleemEid-sr5ph 2 месяца назад

    Musamazinamize zowina azakuvoteleni ndiokhao omwe mugwila nawo tchito abusainu.😂😂

  • @samsamuel9280
    @samsamuel9280 2 месяца назад

    Kodi skc mnamtani?

  • @RennieSomba-xt9zk
    @RennieSomba-xt9zk 2 месяца назад

    Awaiting Chikangawa report after this.

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 2 месяца назад

    Athu ena alibe manyazi nkhani ndi yao koma akuimirira ngati zanzeru ndakhulupiriradi kuti chitsiru sichimakhala ndi manyazi.

  • @HajieMtenje-qm2lj
    @HajieMtenje-qm2lj 2 месяца назад

    Ngatimukudziwa kuti akugawandalama zambirimbiri ozazifusa kuti ma billions amenewa atengakuti bwanji osafufuza

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 2 месяца назад

    Koma ndiye mukunanaratu azanthu mimba zimenezo.Malawi wake yemweyi? Tikuona ngatitu akunja ife athu mukudya bwino.

  • @LewardPatel
    @LewardPatel 2 месяца назад

    Chilima Rest in Peace!

  • @CellinaNgolingoli
    @CellinaNgolingoli 2 месяца назад

    Mwayakhula bwino ife sitikukufunani amwene mupumeko tione zina

  • @GladsonBanda-m3e
    @GladsonBanda-m3e 2 месяца назад

    Chilima anayamba wawinapo Boma dzaphatikizaneni mudzanyenyedwa nose

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 2 месяца назад

    Nzomwe amafuna kuti azilankhula mokhazula Mulungu akuonatu

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 2 месяца назад

    Chipani chimene chimaphunzitsa zipani kaphedwe, kabedwe, tsakho mkhaza!!!!

  • @SandrahPretty
    @SandrahPretty 2 месяца назад +2

    Ambuye mukuchedwa patii zamukatheni muthuyu chonde ..akuyakhula mwatudzu chifukwa palibe chomwe akukumana nachoo ..kumanizen adziwe kut mulunguu Inu mulipo imvan kulira kwathu ovutikafe ambuye tamukathen

    • @SalomyKamnkhwani
      @SalomyKamnkhwani 2 месяца назад

      Mmm pemphero lopempherera mwana wazanu Ili ali wanu mungamve bwaa? Mmm musatero asisi palibe phindu lilonse apa zotsala timusiile mwini wake namalenga adzaweruza yekha🙏

    • @philemontitusnkhoma7740
      @philemontitusnkhoma7740 2 месяца назад

      Indeed, God will visit you with a handfull of punishments

  • @Edwardfulutuna1180
    @Edwardfulutuna1180 2 месяца назад

    Malankhulidwe amene malawi wakhala akuyembekezera kwa zaka zochuluka kuchokera kwa mtsogoleri wa dziko ndiye ndamenewo zikomo a president bola zimenezo zizichitikadi asakunamizeninso ali ku mbuyowo

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 месяца назад

    Munaphelanji chilima chimunthu choipa iwe munalindani inu chifiti😢😢

  • @BeatriceProfessor
    @BeatriceProfessor 2 месяца назад

    Am not mcp member yooo count me out hiyaaa

  • @kellymofo8459
    @kellymofo8459 2 месяца назад

    😂mwapanga chani pa 4yrz mukungogwetsa dziko m,Malo mulitukula munapasana terms panopa mukut muyimaso thats greedness of leadership😢

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 2 месяца назад +2

    For the. first time you. have said something. building

  • @ManuelMalunga-j3l
    @ManuelMalunga-j3l 2 месяца назад

    Following up from Capetown

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 2 месяца назад

    Zowinazo nde mzosatheka uyiwale ase unapha chilima maliro akanali a fresh fiti iwe kumachende kwamako

  • @NTOMBIZANELEFAITHGUSHE
    @NTOMBIZANELEFAITHGUSHE 2 месяца назад

    pamnyopanu achakwera wonani ma massages munya inde takuwonani chikhalidwe chanu

  • @JamesChakwira
    @JamesChakwira 2 месяца назад

    Dr chikangawa