Timayambira yakapalasa,kenako njinga yamoto,mkukagula galimoto umakhala wadziwabe zingapo kmno direof youth akadatika opanda opikisana naye bola kaliyati ali ndi experience pa position imeneyi inde ndi maganizo abwino km fredo wafulumira kwambiri.
Mzotheka osam'phweketsa taonera Traore waku bukina faso 34 years old....2 years yokha dziko kusinthiratu....he has the spirit of SKC titha kuona ngat kutulo atatukula malawi uja in just a year but we are so blind to see it....chomwe chinatilowa mmagazi a Malawi ndi chakuti timakhulupirira kuti president amakhala ndi zaka 70 going up....taesa kokwanira for more than 60 chilandilireni ufulu palibe chikusintha..let's try fresh brain
Wow I wish him all best bec this readers no one like him since 1994 up to now nothing change our country bec same readers who up an down political party's never mind our people so wish this young man can take new Malawi 🇲🇼 future please God 🙏 protect our country 😢emen
Kuno ku malawi sitifumaso ma president aziti ndi ma Doctors and Dr for who ? Aise Fredokiss limba mtimba chabe kumeneko ndikumene ndikutamba kuziwa kt mawa uzakhala president sungawine thawi yomweyo ai ai koma naweso khala pamndanda wa president,2035 uzayima
Pls tipange sapoti mfanayu .anyamata azake akukwanitsa kuyendetsa maiko awo ndiye iye chingalepheletse ndichani ❤❤❤
Now I know where am going my vote may the good lord protect you
Amalawi ndife mbuli fredo alibwino nkhalamba zonse zikukanika bola wachinyamata tione kusintha❤
Better this one I love you big man
Fredokis. My vote big up bro I salute you Sir, you deserve this position Osatopa, Osaopa komanso Osafooka
Fredokiss my vote 🎉
Mwaitha iyaaaaa tikufuna Nyamata Ife ❤❤❤❤❤💃💃💃💃💃💃💃💃💃
My bruh dont worst your cash, 4 now nothing much, u wll see wht wll happen APM my vote
Am behind you ntchana 💪 nice move
I like this too and i will vote with power and confidence
Its time for change?
Ok takulandi aphwanga tikazionela konko good bless you amfana
Zolowa zi bwana anyway we all have ambitions but it s too early for him
Zibwana poti ndiyeyo koma munakakhala inu amalawi nsanje izakuphan
Big up youth leader am your suporter
ambuye akufungatire munthawi zose ndimapemphero thanks fredokis takurandira
Eee anaganiza bwino kupikisana nawo koma osati mpando wake umenewo ayi sindikudziwa abale ena mpandowo ndiwaukulu kunali kwa bwino apikisane nawo wa achinyamatawo kapena kungoyesaso VP mwina mwake
Akapeleka 20 million ee taking a risk osati masewera eee how old z this famous young man?
Wishing Fredoks good luck💯
Timayambira yakapalasa,kenako njinga yamoto,mkukagula galimoto umakhala wadziwabe zingapo kmno direof youth akadatika opanda opikisana naye bola kaliyati ali ndi experience pa position imeneyi inde ndi maganizo abwino km fredo wafulumira kwambiri.
Very true adakali mwachibwana bwana ndithu
Maganizo awa obwezera mbuyo lets wake up
I think he should go for vice at the moment so that we see how matured is he
Umakwana boss take my vote❤
All the best
My vote
Ku UTM tikachita zibwana potha zaka 5 chipanichi chidzakhala chitatha. Masewera too much
Mmmmmmm cadet wa mcp iwe
I wish you all the best my brother i hope one day i will join you Fredokiss
My vote atupele tamutuluka Bas
Time is here now don't wait iam congrats to you brother it's a time for youth to take part in such position
Aaaaa😅 kweni my vote 🔥🔥
Mzotheka osam'phweketsa taonera Traore waku bukina faso 34 years old....2 years yokha dziko kusinthiratu....he has the spirit of SKC titha kuona ngat kutulo atatukula malawi uja in just a year but we are so blind to see it....chomwe chinatilowa mmagazi a Malawi ndi chakuti timakhulupirira kuti president amakhala ndi zaka 70 going up....taesa kokwanira for more than 60 chilandilireni ufulu palibe chikusintha..let's try fresh brain
🎉🎉🎉
Koma ndiyedi mwava
😂
Burkina Faso that guy he was a soldier bro u ca not compare with frdo lol😂
It's good news achinyamata tipushe
Sanafulumile tengani chisanzo cha traore ...komanso senegal ndiana ameneaja.. fredo iponde fada .. mwanaaaaaa
Very true
Chilichose chlindichiyambi good
Bravo freddo....will only cast my vote for him...osati mbava zachikalambilezi😂
ntchana my vote
Wow I wish him all best bec this readers no one like him since 1994 up to now nothing change our country bec same readers who up an down political party's never mind our people so wish this young man can take new Malawi 🇲🇼 future please God 🙏 protect our country 😢emen
Tikufuna ana Ngat amenewa kwambili kwake wosati anawa
Owk no problem ❤❤
Keep it up chana
Ayamba kale ma njenje patelela ngt denje 😮 more fire ntchana
All the best..he's capable to secure UTM
wosawopa maganzo abho amenewo shosho
It's about to support the party
And thats part of democracy ❤❤🎉🎉
Fredokiss bravo more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 2025 Boma aaaaaa WINA WASEGULA KALE M,MIMBA KU STATE 🏠
I think It's not a bad decision, everyone knows that there is always a time but most of us don't know when it's exactly our time, let him try🎉
Nthawi yakwana achinyamata alamulire... Fredokiss my vote 😊
Very true
He will not win. Let him settle for vp at least
Please try to be positive
And who do you think is going to be the president then?
@@BenjaminKamanga-p8wanakayesa kaye u Mp nde akalowe kaye ku paliament akhaleko ndi knowledge but other wise its too fast game
😊😊 I think this this
Alibe fundo yoyo akanyele palibeso chazelu chomwe akuyakhule machende ake 😂😂wangokhuta
A right move, at a wrong time. Have patience boss.....
Tiye nazon bg
Utm ambiri akutengera dyera akalunza azabalalikana
Risk is worthy taking, i dont see any problem here
Mulungu akukhudzeni afredokis zonse za mbuye
Kuyesera mwayi wina aliyense anga wine Ku utm timudapota
Finally my vote
Never give up fredoo
I'm Ur support 💯💪
❤ vote Kwa fled
Wishing him all the best
Big hand 4 him
Ayambe kukhara conserer Kaye, then aziyenda step by step
fire,,,,fire ma bomba eee i can only imagine convetion ya utm izabeba guys 🤣🤣🤣
Good idea
Fredo osaop osafowoka ife achimata ngnganga pa mbuyo pako
We don't force plz, accept ur age first
Vote yanga
Akuchitika ku UTM sopano ndemanyaka 😂😂😂 enieni
Pa ntumbo kwinanako umalizitsa wekha
🔥🔥🔥🔥
Fredo my vote khalamba tatopa nazo viva fredo
Kkk😂😂
Ndipo zikafike mkhalamba 😂😂😂😂
Ine ndikuona kut palibe somati wafulumla sanafulumile alibho my vote Fredo kiss
My vote🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Adadikila
All the best fredo
tikufuna achinyamata basi anthu akulu akulu atikwana kwawo kwatha fredokiss utm moto kuti buuuuu
Chenicheni akufuna chiyani?
Ndamufrira mtchana amakwan wawinakare ameney
DZALOWA BWEMBA KU UTM
Zilibho ayime ❤
Usi kungowina basi chipan chapita Ku chikangawa
Kkkkkk UTM yatha basi
Ntchana Mr president. Anaoneka kuthamangathamanga k 🕯️🕯️ lighting
Mmmm guys penapake zufunika kumaganiza coz kuyendesa dziko sizocheza and kukapanga control chuma chadziko ngati muja amapangira Bingu mmmm sizocheza zimatengera kuti ukudziwa momwe forex ikuyendera otherwise eish dzikoli litilaka basi
Kwalowa zibwana ku utm
You deserve it Fredo osaopa osafooka
Bola pamenepo,
Amange malamba kumwamba kukuyakhula😂😂😂😂😂
Apa ndy kungowina ku conversation ndzakuvotera bas
Tiyenazo man osaopa midalayo ayi zokalamba zimenezo
Koma tisafere kuti ndinyamata ,ilitu ndidziko siteam kapena band, uyu wangokhala chabe ndi moralo koma mfundo alibe let's be serious guys
Dolo❤
I'm with you fredo😂😂😊
it is too early for him he is not deserved to contest on that position
Eeee Fredo walimba Nkandilo
Bro mukanazatsala nachotu chipqnichi mtsogolomu koma zomwe mwayambazi am sure mugawanika bas
Kuno ku malawi sitifumaso ma president aziti ndi ma Doctors and Dr for who ? Aise Fredokiss limba mtimba chabe kumeneko ndikumene ndikutamba kuziwa kt mawa uzakhala president sungawine thawi yomweyo ai ai koma naweso khala pamndanda wa president,2035 uzayima
Mhhhh dziko ndi wathu ake
Big up Bro now I'm 32 but ndinayamba ndikalekale kumva kuti achinyamata alero ndi atsogoleri mawa,which mawa are they talking about 🤔🤔🤔⁉
Even me idont understand the word asogoleri amawa
😂😂😂😂 ndamenewo abwera sopano asogoleli amawawo 😂😂😂 koma ndaseka bwanji
Ndipo uyu ayimile kumene achotse matha achinyamata
Ndiye Poti Pali andu ena njingayo sanagulepo anangofikila kugula galimoto
Wayitha kucheza zaka si mvuto see how bukinafaso is.
Freedo eee mwalimba mtima.
He cant win best way he should for his turn in future
Chana umakwana osafooka