ZAVUTA BASI .... CHAKWERA AMUWUZA KUTI ASIYE UDINDO WAKANIKA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 8 ноя 2024

Комментарии • 53

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm Месяц назад

    Nice spesh thanks

  • @DannielOnions-fy3dc
    @DannielOnions-fy3dc 2 месяца назад +1

    Nice one thanks keep it up please 🙏 👍

  • @WiliWili-y2d
    @WiliWili-y2d Месяц назад

    ndaikonda

  • @HajiAslam-nd9xq
    @HajiAslam-nd9xq Месяц назад +1

    Omakaka alibe chisoni ndi tundu wa malawi muthu oipa chikangawa

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 Месяц назад

    ine mtima Wanga suvomera kuti chakwera is our president ndi momwe amapangira zinthu zake

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 месяца назад +1

    Vuto ndiloti nyau chilingati chilombo , chakwela ndiwanyau , that means chilombo sichingamve chisoni , chokuba komanso chokupha + mbuli ,
    Chitulepansi udindo ndicholephela , chizikaika dambwe kwao

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 2 месяца назад +1

    Bolaso kujhalabe opanga president mdziko muno,atule pamsi uyu chikangawa uyu.

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 2 месяца назад +1

    Zoona atulepasi wavutisa kwakwana Mr chikangawa

  • @MagretBanda-z4e
    @MagretBanda-z4e Месяц назад

    Gogogogo

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад

    ❤❤❤

  • @JosephMangawa
    @JosephMangawa 2 месяца назад

    More fire tidziwe zoona

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 месяца назад

    CDEDI ndi a mr. Namiwa powerful speech and it's true, Chakwera wawononga chuma cha dziko lathu, achoke chabe.

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 2 месяца назад +1

    Ndizonad mcp yatikwana ife anthu kuvutika chochi ndye umva mbudzi ina ya mcp ikuti Chakwera woyee ugalu bs

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi Месяц назад

    Mr namiwa inuyo mulungu adzikudalitsan mu nthawi dzonse mumatiyimilila kumalawiko

  • @CharlesNtasa
    @CharlesNtasa Месяц назад

    Gogogogooooo

  • @NuneAxmed
    @NuneAxmed Месяц назад

    Ndizomwe tikufuna atule pasi udindo basi amalawi very is no way demostration

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 2 месяца назад +2

    Choka iwe ndi nyawu wakoyo

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa 2 месяца назад

    Zoonad athletic udindo kut tibwelele kwathu kumalawi osati kujoni kuno tukhalila kukondwa ayi km ndimmene zillion kumalawi

  • @KennedyKanyama-ce8lb
    @KennedyKanyama-ce8lb 2 месяца назад

    Ukuku ndie kuyankhula kwabwinotu kimuwuza muthu chilungamo uyuyu zamukaniks sikudambwetu ku state house. Choka pamenepo muthu opanda mzeru iwe. Ulibe usogoleri iwe ok.

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 2 месяца назад

    Chakwera sakudziwa kt kukwera kwazithu pafupi pafupi kumabweretsa mavuto gati ndaramayo ndiyopanda mpavu

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes Месяц назад

    Chakwera achoke nazikonda koma zingatheke

  • @dalitsochibisa2986
    @dalitsochibisa2986 Месяц назад

    Can u advise the solutions

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 2 месяца назад

    Boma loyendesedwa ndi mbava komanso zigawenge

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 Месяц назад

    Alepheradi

  • @AdamYas-ec9oc
    @AdamYas-ec9oc 2 месяца назад

    Inde atule udindo basi chimene anena acidedi ndi zoona chakwera kwa kuba kumangana kuphana

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 месяца назад

    🥳💪🔥

  • @NuneAxmed
    @NuneAxmed Месяц назад

    A cidedi ndinu anthu oganiza bwino

  • @ZephMbeleswa
    @ZephMbeleswa 2 месяца назад

    Aaaaa wawa ati ndichani zaziiiii zopanda mtchele 😂😂😂😂

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 2 месяца назад

    Chisilu cha munthu chimenechi ......munthu opusa osaganizila za anthu omwe anamusiya pampando .....anthu wafuna posachedwapa ......the worst president since democracy came

  • @AustinMayere
    @AustinMayere 2 месяца назад

    Atule pansi''akawona ngat malawi ndi lilongwe state house yokga ndi makovoi akewo galu ameneyu.

  • @JAMESJOMOJACOBMHONE
    @JAMESJOMOJACOBMHONE 2 месяца назад

    Ine pheeee kumastqnd😢

  • @HusseinMofatt
    @HusseinMofatt 2 месяца назад +1

    Zoonadi guys a MCP yafika pa manyi

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 2 месяца назад

    Congtatulation CDEDI your strategy is so constuctive but one thing:There is need to accost HE not through representatives or media.

  • @anicakandiado
    @anicakandiado Месяц назад

    Atule pansi basi atikwana

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 месяца назад

    Tsono mukakhala president ndinu???? Mumangoyakhula koma simukuthandidzapo chilitchotse,,,kodi inuyo ngati Malawian mukuthandidzapo chiyani kunzika za Malawi

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke Месяц назад

    MBAMBANDE osaopa

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x 2 месяца назад

    Watuled udindo

  • @ZephMbeleswa
    @ZephMbeleswa 2 месяца назад +1

    Mbuzi yamunthu iyi😂😂😂😂😂😂

  • @KadomekaMaureen
    @KadomekaMaureen 2 месяца назад

    100%

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 2 месяца назад

    Sakumva chakwela kodi makolo ake alipo?moti gonthiyu sakuona? alephela atuluke basi komaso zitsiru zakutsogolozo zmangoti nyo pitani kumakakwela njinga uku anthu akufa ndi njala mankhwala kusowa waononga achoke basi

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад

    Atule pasi basi

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 2 месяца назад

    Chakwera and his Mcp alephereratu mu zaka 4 zimenezi chitsanzo omwe anapuma ntchito mboma kuyambira 2022, 2023 mpaka 2024 uno palibe walandira graduity yake ena akumwalira ndi umphawi shame on you

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi 2 месяца назад

    Zoona zake ndi zimenezo kuti muonetsetse amene akuti mafuta akwele ndi athu oti awapatsa tindalama Koma chakuti adziwe kandalama komwe akupatsanikoni Katha ife tidzavutikilaso limodzi

  • @MuhaShaibu
    @MuhaShaibu 2 месяца назад

    Anayambila muja

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 2 месяца назад

    Atule pansi

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 месяца назад

    Tsono akathula pasi udindo,,zithu zitsika???

    • @isaaczuze
      @isaaczuze 2 месяца назад +1

      Chisilu china chikuti Kodi chakwera akatula pansi udindo zinthu zisika......umbuli weniweni ukufuna apitilizebe kuonongo .....kumalawi kuli kuli mbuzi za anthu osati masewela .....chisilu chakochi tikufuna chichoke pabwele anthu oziwa kuyendesa Boma ....president sangakhale kugawa ndalama sikutha maplan kumeneko .......chakwera wakoyo waononga ukufuna apitilize kuonononga mbuzi iwe .....mapazi Ali mbuu ngakhale phaka ulibe .....umbuli

  • @CharlesNdalama-v5b
    @CharlesNdalama-v5b 2 месяца назад

    ase iwe mwini WA channel umandisangalasa voice yako🤣🤣🤣🤣

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 месяца назад

    Ndimaganiza kut ndi mitundu yina koma mbola zenizeni za alomwe tikuziwa kut muli pa chintchito nonse ngat mwatopa chokani Malawi muno zipitani kwanu ku mozambique

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr Месяц назад

    ❤❤