COMRADE NTANYIWA MCP IKUFUNA IKWANILITSE CHIPONGWE CHOTELE KU DPP POMANGA ANTHU AWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 янв 2025

Комментарии • 61

  • @MussahJenala
    @MussahJenala День назад +5

    Allah protect sameer suleiman

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali День назад +3

    The best Radio ever

  • @HarryMakwale
    @HarryMakwale День назад +3

    Number one mr ntanyiwa ❤❤❤❤

  • @MathewsMakalan-l6v
    @MathewsMakalan-l6v 16 часов назад

    Big up Mr Tanyiwa mumatiimilia mulungu azikupasani moyo wautali azikutetezelani

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 День назад +4

    Mcp simudzalamuliranso anthu oyipa inu

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe День назад +1

    MR NTANYIWA ZIKOMO KWAMBIRI..MUSAMUSIYE CHONCHO CHAKWERAYU KOZ AZOLOWERA..MUZINGOMUTSATILA KUMASUNZUMIRA NKUMAULUTSA KWA ANTHU ZONSE ZOIPA ZIMENE ZIKUCHITA .CHAKWERA NDI CHIFWAMBA AMAIPITSA ANZAKE

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День назад +1

    Wina alira Ntanyiwa ...chaka chake ndi chino.....mcp iwona ...nyekhwe....😂😂😂😂😂😂😂

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День назад

    History is the best teacher.....

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika День назад

    It's the laughing for me...Ntanyiwa more fire 😂😂 atopatu akungomang moti yachipani akuopa chani..apa let's demonstrate to their houses.chimwendo,zikhale n jezebel let rise malawi let's rise...

  • @BlessingsGama-j3r
    @BlessingsGama-j3r День назад

    Kodi Mulungu wanga muweruza bwanji apapa 🎼 Mungoti pheee muoneeeeee .... Mungoti pheee muoneeeeee

  • @AlexChikoti-l9s
    @AlexChikoti-l9s День назад

    Kkkkkkkk my ntanyiwa ndaseka ukukhala Ngati ukumuyimmbila chikangawa Koma ndaseka😂😂😂uyu sawina chisilu chakupha saulos.

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    zafikapa,aboma,asapuse,a,dpp,alipakalikiliki,kupanga,zinthu,zoipitsa,boma,cholinga,anthu,asalikonde,

  • @DicksonDavie-p6b
    @DicksonDavie-p6b День назад

    Big up Mr

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe День назад

    KODI A MCP WO AKUFUNA KUMALIZA ANTHU ONSE A DPP KUWAMANGA ..MCP TU IKUOPA ZISANKHO KUTI ILIZA ZISANKHO

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День назад

    Dpp my vote

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 День назад

    Boma Latha Ili kuwayendetsa ulee basi kuyenda wapasi kuphulitsa utsi okhetsa misozi basi ndiye amawayitaniranji anthu.

  • @MariaDandazaraJSDmoio2024e
    @MariaDandazaraJSDmoio2024e День назад

    Mutetezeni suluimani koma mulungu amuteteza pa nyengo imeneyi mulungu akuona akatuluka itai CHOTI anthu amenewa akumapeleka uthenga wakumanga anzawo

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День назад

    Apm my Vote

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 19 часов назад

    Agalu okupha ayaluka sitikuwafuna kumene adzipita komwe anachokela ng'ona zamuchikangawa tatopa nanu

  • @IsaacKwenda
    @IsaacKwenda 15 часов назад

    Mr ntanyiwa wuremuwanu

  • @ChipiLiro-o5v
    @ChipiLiro-o5v День назад

    Kungositha bomali mcp isazapezekeso chipani chimenechi chizathesedwe chipani chausilu ichi

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx День назад

    Mulungu wathu sakulora sizithekatu kwawo kwa tha ndipo amalawi tichitepo kathu akuti tola achakwera

  • @LeahSimbeye-m3b
    @LeahSimbeye-m3b День назад

    Eya Mzichula date la siku limene mukupanga program komaso mwayiwala kunena nthawi

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    olokukhaleanthu,km,bola,tadziwa,kt,zikuvuta,chifukwa,cha,dpp,,kuba,

  • @LeahSimbeye-m3b
    @LeahSimbeye-m3b День назад

    I love you Mtanyiwa

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    kuchuluka,kwa,anthu,kupolisi,tilibenako,ntchito,,km,chilungo,chidziwike,anaba,kapena,,,,,ayi

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    mcp,singalongeze,chifukwa,choti,agwila,mbava,inuyo,mu,kudziwa,m,mene,zidalili,,,,,,,,,masu,apitawa,anthu,,amatukwanila,boma,zasuga,lelo,chimene,chimasowetsa,suga,,,,,,achipeza,mt,zalakwika,ku,,,wamanga,tikufuna,amalawi,,,adziwe,amene,amaipitsa,boma

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    mcp,ngat mbili,yaipa,mwaipitsa,ndinu,a,dpp,mumaba,ndalama,kumakampani,,zinthu,zikama sowa,,a,dpp,nkumasekelela,,kumati,boma,silikuyendetsa,bwino,dziko,lelo,tadziwa,amene,mukunyazitsa,boma,

  • @KondwaniGulonyonyo
    @KondwaniGulonyonyo День назад

    Kunkuyu ndichimwendo amaliza chipani chathu Cha mcp choncho akuyenela kuyankha atilakwila

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    zimene,akupanga,a,dpp,ndichimodzmodzi,,iwowo,kunyela,mnyumba,omwewo,nkuma,namizila,wina,,kumachita,anyela,,ndiwomwewo,wina,mbili,,yake,nkumaipa,,km,dpp,eeeeeeee

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc Час назад

    Akunama

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb День назад +5

    Achepa kwambiri.. ife Saver ya smartmatic yawoyo tikuyidziwa password 🔑... Munyaaa
    Dpp bomaa!!!!!

    • @chrisebanda5917
      @chrisebanda5917 День назад +1

      Mr. Ntanyiwa , if DPP Wins in 2025 16th September Elections, I hope you will come pa open. Bravo to you.

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya День назад

      ​@@chrisebanda5917azaopaso chani?😂😂😂😂

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya День назад

      Viva Comrade Mtanyiwa❤❤❤mwayambanso ya nama drama Wikino ya call kwa Apule??koma ndaseka😂😂😂😂

  • @JeffreyKambwemba-zs7wy
    @JeffreyKambwemba-zs7wy День назад

    COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM ❤❤❤❤

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    komano,anthu,amene,akudana,ndikumangidwa,kwa,anthuwa,,tiziti,akuwanamizila,,zakubazo,kapena,kapena,angofuna,kubisana,kt,aziipitsa,boma,

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    adagwetsa,kanpani,yasalima,suga,,ndi,a,dpp,km,a,dpp,omweo,amatukwa,boma,kt,achakwela,sadziwa,kuyendeysa,dziko,a,dpp,nkumasekelela,,kumati,ndiye,bwino,zinthi,zizisowa,kuipitsa,mbili,yachakwela,km,ife,tikufuna,chilungamo,chioneke,kt,anaba,kapena,,,,,,sanabe

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    akulu,akulu,tiyeni,,tiyankhepo,muja,anasoweela,suga,,anthu,nkumati,chakwela,akusowetsa,suga,kulikoti,a,dpp,akaba,zindalama,zambilimblli,,anthu,nkumanyoza,chakwela,ndizoona,

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel День назад

    Sizitheka..Kuli chi chinatindi cha anthu Ku Blantyre police..anthu agona konko

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    sanalakwe,kuwamanga,abweze,ndalamazo

  • @ChikondiSosola
    @ChikondiSosola День назад +1

    Awa azilongezadi

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    apa,ambili,sitimadziwa,kuti,akuononga,dzikoli,ndi,a,dpp,akaba,amazungulila,kubwela,pawailesi ,kulengeza,kt,suga,,,,wasowa,kumachita,iwowo,ndi,amene,akaononga,kanpan,,,,ndiyeno,tikufuna,tidziwe,kt,,,,mbili,yo,nyazitsa,chakwela,,inali yazoona,kapena,amamunamizila,apapa,tifuna,tidziwe,

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    zafikapa,ngati,addi,anapanganawo,awamange, chifukwa,mbili,yakusowa,kwasuga,idafika,ponyasa,

  • @CharlesMongola-jw7sk
    @CharlesMongola-jw7sk День назад

    Chakwera sangawine,or kuika mulu wamanyi a nkhumba kuti upikisane ndi Chakwera,manyiwo awina popanda kukaika

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    kd,apapa,amene,anachititsa,kt suga,azisowa,pakati,pa,anthu,akubawa,ndi,achakwela,nthawi,,imeneija,anali,olakwa,nindani,

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p День назад

    Chakwera ungofa bwanji

  • @BORNFACESIMBOTA
    @BORNFACESIMBOTA День назад +1

    Boma lamanyi

  • @natashamathala8715
    @natashamathala8715 День назад

    Ya SDA wakambayo ndizokuti azibusa ambili anabwela ndi cholinga chofuna kudzasintha malamulo omwe akuyendeoa pano a SDA wo chifukwa azibusa awo anachokela mma church ama Sundays ndi cholinga chofuna kuphwetsa mpingowo lelo ndi izo wakamba ndipo nzoonadi abusa apano ngokudya mbewa ngumbi nkhumba ndi zonse zoletsedwa mmalamulo ampingo pano akupangabe.

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika День назад

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @SamboRuphan
    @SamboRuphan День назад

    Kungomanga adada muwona ,, munya manyi

  • @SamLee-j7p
    @SamLee-j7p День назад

    Koma iwe

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick День назад

    tinkadabwa,antanyiwa,akulimba,ntima,bwanji,ndamazi,akumupasa,nindani,zakuba,zomwezo,nkumatukwanilaso,boma,eeeeeeeee,,,km,dpp,,,,,,,yokha,amwene,ishi,

    • @AnniePetro
      @AnniePetro День назад

      Koma bambo muli pa ntchito makoment m,mene mwayambira kulemba

    • @neemahkapatamoyo9563
      @neemahkapatamoyo9563 День назад

      ​@@AnniePetrondipo abambo amenewo nthawi zonse amalenbatu zotukwana osati zibwana

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali День назад

    ❤❤❤

  • @AmosMtonga-m6n
    @AmosMtonga-m6n День назад

    😂😂😂😂😂😂

  • @SydneyMakuluni-uf5bh
    @SydneyMakuluni-uf5bh День назад

    Bodzatu ilo