Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
My best radio on limpopo fm ndi comrade ntanyiwa more fire 🔥 Mulibwanji Agalu mcp anthu akupha
Tiyamiketu AllAh kuti mwayenda bwino Brother Ntanyiwa .Chakwera angozikozelatu yekha
Allah ndiwabwino comrade akusungani ndimoyo
Mulungu ndiwachifundo akusungani ndi moyo pa 2025 wooooo
Mr ntanyiwa inuyo ndi one tikumakupephererani Kt mulungu azinkhara Nanu munthawi zose ameen ❤
Mumaitha mr mtanyiwa mumatiimir more fire
Ulemuwanu boss ❤
Za Skeffa sizodabwitsa Grace ananenadi
Timasuleni ife
Comrade ntanyiwa siku ntcheu kokhako ku zomba so tikunena pano Ana akubwezeda pa chikamveka primary school pamatawale 3000 mwana aliyense atokotele asithe atiojeza ku zomba kuno.
Nkhani ya Grace Chinga ija ndiulosi panopa zikuchitikadi Koma akumaona Ngati Ife sitikuziwa ntanyi tangosewelani oudio ya Grace ija anthu ayimvele okha
Alemekezeke yehova tinali ndi khawa heavy
Kumachinganso pa nselema ayitanitsa 1000mk mwana aliyese ndipo zikupelekedwabe
Big up comrade mtanyiwa
Akamuna bambo
atanyiwa nanga bwanji osaika ma # anu apapa kt tikwanitse kukutumizilani kamene tilinakoo ife
𝕌𝕞𝕒𝕜𝕨𝕒𝕟𝕒 𝕟,𝕟𝕥𝕒𝕟𝕪𝕚𝕨𝕒❤
My best radio on limpopo fm ndi comrade ntanyiwa more fire 🔥
Mulibwanji Agalu mcp anthu akupha