Michael Usi Amung'alula Pankhani Yopemphapempha

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 окт 2024

Комментарии • 48

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 2 месяца назад

    Thank you for your speech my brother God bless you.

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад +1

    Usi ndi Chakwera ndiomwe adapha Chilima akufuna maudindo

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад

    Anapita kumakawapusisa anthu aku Mangochi galu amwneyu Usi nawonso amangochi kumangoombera mmanja zopusa zomwe amakamba Manganya

  • @joicemumba3608
    @joicemumba3608 2 месяца назад

    Amen

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 2 месяца назад

    Eish koma ku malawi mmm ayi zikomo, mizimu ikukwiya tsiku ndi tsiku yomwe idathera ku Chikangawa ndipo tikunva zinthu 😭😭😭

  • @DaudMbumba
    @DaudMbumba 2 месяца назад

    Ndizimene ntikafuna zimennez, ziko limkayenda bwinobwino koma ayi ndithu for this time ⌚ let us leave this in hands 👐 of god

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo 2 месяца назад

    Kamunthu aka kachabechabe kwabasi

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie 2 месяца назад

    Thanks u make me happy

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 2 месяца назад

    Koma zoona ngongole kuti mbweeeee

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад +1

    paja awa anazungulilapo mutu et ndichifukwa chake

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад

    Manganya akuzitenga ngati zikoli oyamba kukhala vice president ndi iyeyu kunali anzako sankapanga nyasizi

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад

    Michael Usi ndi mbuzi yamunthu galu

  • @HanifiYaumu
    @HanifiYaumu 2 месяца назад

    Ndikachitsilu ndiye mwati

  • @alidaniel-l7j
    @alidaniel-l7j 2 месяца назад

    😢

  • @RajabShahida
    @RajabShahida 2 месяца назад

    Kumeneko ndiye kuyankhula ndasangalala nanu dzikomo bwana

  • @JamesKhengemussa-t1d
    @JamesKhengemussa-t1d 2 месяца назад

    Khadzu khadzu pa Malawi,anthu daily ali ndi mkwiyo.

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 2 месяца назад

    Mizimu ya Anthu 9 ivuta kwambili.

  • @AdamYas-ec9oc
    @AdamYas-ec9oc 2 месяца назад

    Yu usi ndi chisilu

  • @QochiweNkhoma
    @QochiweNkhoma 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂 ng'alula

  • @Zamwano
    @Zamwano 2 месяца назад

    Uyutu akuyankhula kumayenda muma hospital mankhwala kulibe km kumaona ma doctors kuti akubwera mocedwa kkkkk km ziliko odi gonee ine

  • @SammyWaGonga
    @SammyWaGonga 2 месяца назад

    Kodi akuyankhurayi ndi ndani?

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 2 месяца назад

    Chakwela mbuzi yamuthu

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 2 месяца назад

    Mulungu akudalitseni abwana

  • @peterchiutsi
    @peterchiutsi 2 месяца назад

    Mmmmh guys mukuchedwa kkkkkkkkk Okudya zake alibe mulandu Mukulimbana ndi Micheal Usi bwanji za nsanje basi kkkkkkkkkk amalawi please lets change kaganizidwe kathu guys izizi sizizatithandiza

  • @kasupeowenpaul
    @kasupeowenpaul 2 месяца назад

    Exactly this truth and pain

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 2 месяца назад

    Good 👍

  • @michealchaomba9761
    @michealchaomba9761 2 месяца назад

    Ndiye kuti anamupha chilima kamba kakuti samatha kupha eti😊😂😂

  • @LekelenFab
    @LekelenFab 2 месяца назад

    😂😂😂😂

  • @nadiahPhiri
    @nadiahPhiri 2 месяца назад +2

    Kkkkkk km ndaseka

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani 2 месяца назад

    Munthu wankulu kulankhula chichewa chenicheni komanso ...chilungamo chenicheni mokwiya

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 месяца назад

    Zoona zipatala mulibe kathu one mwana wanga anadwala usiku kupita kuchipatala angoti mukamungulire panado is it normal citizens? Usi wasusuka ugwera mu sapha,

  • @DaudZuze-z1y
    @DaudZuze-z1y 2 месяца назад

    Ing'alume iwee😂😂

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 2 месяца назад

    Nguluwe yamutbu uyu

  • @HastingsShaba
    @HastingsShaba 2 месяца назад

    Goog sir

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl 2 месяца назад

    Zoonadiitu aise bomali zafikaponunkhadi

  • @ZecaFranqueMarioMario
    @ZecaFranqueMarioMario 2 месяца назад

    Koma malawi wayaka moto kuti buuuuuiuiiiii

  • @RobertMazula
    @RobertMazula 2 месяца назад

    Koma ukukhosomoratu wayezetsa..malawians voted for tonse not mcp..munchira 2025 Mcp boom!

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 месяца назад

    Kachitsiludi aka 😂😂😂😂😂😂

  • @HelmetMphambano
    @HelmetMphambano 2 месяца назад

    Ulira zenizeni iwe kapendiwe boma ndi machine

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 месяца назад

    Ndipo comander uyu ndi nyasi

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 месяца назад

    Ikhadzule basi kkkkk

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 месяца назад

    But Kaliyati can lead people? I don't think so

  • @ShadreckAustin
    @ShadreckAustin 2 месяца назад

    Chikangawa

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo 2 месяца назад

    Zopusa kobasi

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 2 месяца назад

    🤣🤣🤣🤣🤣

  • @aubreytiyess
    @aubreytiyess 2 месяца назад

    🤣🤣🤣

  • @LazarusMpinganjira
    @LazarusMpinganjira 2 месяца назад

    Zakuvuta 😂😂😂😂