This is not interviewing but kukambilana anthu a side imodzi ,,coz chimene ndimadziwa ine akamati interview.. interviewer amafusa mafuso not taking a side And we are following ❤ Just wait en see 😂
Akulu zimenezo ndizammafilimu. Inu ndi ine kutipatsa parachute kuti eni duphani tikafika pansi ndikuvulala modetsa nkhawa kapena kufa kumene as if we didn’t use a parachute. Vice president and his close protection team are not paratroopers trained to jump out of an airplane with or without a parachute.
Iyi inali podcast to puch DPP agenda osati interview. Mtolankhani akuchita kufunsa mafuso kuli nkhani ikomele DPP and pena akumayika ka opinion kake kokometsela chipani. 😃It is ok zipani zimakhala ndi ma podcast.
My comrade sure man you r the best politician we love you may our lord bless you with long life health life protection n guidance more faya my bro sureman
Za a mtali manja, zisiyeni, kodi munthu waku mec alipo amene bambo or mai ake sadachitepo ndale. Umbuli mukuchitau, kodi iweyo suleman mwana wako sakuyenera kutenga any position m'boma la DPP simply because you were there before. Ndi umbili ukuchititsani izi, bwanji last time DPP IG sanali a northern person for example.
Zamabodza izo Suleman, sete zako, have you forgotten munagula ma tractor ku India and you declared them zachabe chabe kenako munagulitsana nokha nokha a DPP, pano matractor mulinawo m'makomo, munagula pa auction ma 50 pin per tractor, lero mukunya mwano oterewo, anthu oipa inu?
Sukunama iwedi ndimpulusi wathu ndawonela mwanawanga snamphuzila papole ndintolakhani koma zakq 5 akusaka chito osayipeza pano mozikakamoza analowa chito ya police zosezi chikangawa i love you big boss sulemani
DPP nayo analindizofooka zake and some of the challenges we're currently facing ......akungopitilra kuchokera ku ulamuliro wa Dpp. MCP ndiye ikungotimaliza basi.Mcp and Dpp nonse ndiamodzi.
NTSB imangofufuza za ndege zomwe zinapangidwa ku USA koma zopangidwa ku Germany ali ndi bungwe lawolawo lotchedwa Bundesamt für Verkehrswesen (BAV), which is responsible for investigating transportation accidents in Germany.
Bomali Lili ndi mavuto oti likonze koma bomali silikadakwanitsa kuchita control shock yomwe malemu Chilima adachita go through, when the plane was out of control. Akulu akulu tisamalankhule za maganizo chabe, it doesn't matter how young and energetic we are, akulu akulu ngozi ya ndege simasewera, chinthu chija chimathamanga, imagine accident ya galimoto pa top speed ya convoy ya president, how much possible damage. Ndiye ndegetu imathamanga speed yoposa 400 to 600 km/ h, imagine At 400, and fall down from air,
I just luv the program but am finding some difficulties with person wearing a shirt.Am failing to call him a journalist because he is lacking journalism skills, otherwise he can do better. Talking about Sameer,he is a man of integrity and I do respect him alot. Viva Malawi 🔥🔥
Ndine ntchewa koma ngoz za kuchikangawa Aliyese sakusangalala nayo mpaka panopa. Ndine wakulilongwe koma ndikuopa mulungu tabwelesan black box anthu akukhulupililan koma apart from that aaaaq M.C.P wakupha
@EdwardPatel-f1g iweyo nde upanga chani chifukwa ifeyo ndi dairy ku ganyu kupanga mchele awawaso akupanga mchele wawo chifukwa chake akukamba za anthu ena kkkkk
Suleman ndiwe dolo serious,,, ndiye wat big boys ili kt 😂😂😂 I like you
Uyuyu timusalile kudya akhale VP adzachigwira bwino chipanichi who's agreed with me
Only GOD knows what is happening MULUNGU wazatheka bwanji apitilize kukutetezani ndikukudalisani Mr Suleman 🥳🥳🥳🥳🥳🥳
Koma ineyo kukamba zoona athu amene akumasapota mcp ali ngati mbuli kwaine 😂😂😂
Sukunama aise.. kuona munthu wankulu ukumangonvela chisoni.. kut koma nzelu zilimo.?
@@Franklifo2217xokonda kusiyana
I like this guy ali ndi utsogoleri uyu 💪💪💪 ndithu
Uyu or u president akhoza kulamula ndi mutu
This is not interviewing but kukambilana anthu a side imodzi ,,coz chimene ndimadziwa ine akamati interview.. interviewer amafusa mafuso not taking a side
And we are following ❤
Just wait en see 😂
Tazaimileni upresident bwana❤❤❤❤❤😢😢😢😢😢😢😢
Mtolankhani do not explain amaganizo ako. You are the interviewer. 😂😂😂😂
Ndege yasilikali imakhala ndi parachute. Anyamula bwanji vice president opanda zozitetezera mundegemo
Akulu zimenezo ndizammafilimu. Inu ndi ine kutipatsa parachute kuti eni duphani tikafika pansi ndikuvulala modetsa nkhawa kapena kufa kumene as if we didn’t use a parachute. Vice president and his close protection team are not paratroopers trained to jump out of an airplane with or without a parachute.
@joshuaagabu3032 4.5m high ndege ingaphanyike chonchi
@@henryphiri6100 Ndizotheka musiyawale pali component ya speed, ku korea ndege yayaka itafika kale pansi chifukwa cha speed inalephela kuyima msanga inakamenya chikupa ndikuphulika. Pali zinthu zambiri za technical zimene anthu ngati ineyo tikuwona kuti inali ngozi yachilungamo koma poti anafa ndi munthu wamkulu wa ndale zokambakamba sizimalephela. Ngati panali chiwembu zimenezo ineyo ndilibe umboni oti ndidziloza anthu chala zimenzo timusiyile Mulungu.
@joshuaagabu3032 magazi anapita kuti, nanga bwanji panalibe mafuta pogwera ndegepo. Mkulu dikirani mudzaziona. Inu kunalibe 1983
@@henryphiri6100 Ndichifukwa pamapeto a comment yanga ndinati ngati panali chiwembu mulungu adzatiwonetsa tonse nthawiyo ikadzafika.
Iyi inali podcast to puch DPP agenda osati interview. Mtolankhani akuchita kufunsa mafuso kuli nkhani ikomele DPP and pena akumayika ka opinion kake kokometsela chipani. 😃It is ok zipani zimakhala ndi ma podcast.
Iwe umati
My comrade sure man you r the best politician we love you may our lord bless you with long life health life protection n guidance more faya my bro sureman
Uyu ndi katundu ndipo kulimba mtima kwake kumandi limbitsa mtima kwambiri long live fada
Brother suleman you deserve to be a leader
Dpp my vote mcp out soon
Mr suleman ndikuziwa kt Apure azasila in udindo ,hope ya amalawi ili pain
Za a mtali manja, zisiyeni, kodi munthu waku mec alipo amene bambo or mai ake sadachitepo ndale. Umbuli mukuchitau, kodi iweyo suleman mwana wako sakuyenera kutenga any position m'boma la DPP simply because you were there before. Ndi umbili ukuchititsani izi, bwanji last time DPP IG sanali a northern person for example.
How would you feel Suleman, if someone addressed the president as "you"
Suleman we love you so much musasiye osawopa akuchepa mcp abwelele kudabwe
Zamabodza izo Suleman, sete zako, have you forgotten munagula ma tractor ku India and you declared them zachabe chabe kenako munagulitsana nokha nokha a DPP, pano matractor mulinawo m'makomo, munagula pa auction ma 50 pin per tractor, lero mukunya mwano oterewo, anthu oipa inu?
Zikunika president wa experience well educated and wa integrity with good strategies.
Suleman number one ❤
Let Kabambe team up ndi Sulemani
People with vision like you are highly wanted to run this nation
wamalapu Lapu bwino, ulemu wanu my uncle Suleman..
Ur strong leader mr Suleman
Interviewer wake wamolare😂😂😂 Odi ndizingoonera
Big up mr❤❤❤❤❤
Sukunama iwedi ndimpulusi wathu ndawonela mwanawanga snamphuzila papole ndintolakhani koma zakq 5 akusaka chito osayipeza pano mozikakamoza analowa chito ya police zosezi chikangawa i love you big boss sulemani
Sulemani sindidamuone koma amandiatsa chikoka sir i love you
Ndikamuwona Samia Suleman ndimawona ngati ndawona SKC chilima!! I don't know why!! Muthu olimba ntima kwambili!!
Ndipo zoona
Big up sir
This is Bishop Owen M.Tembo, let me encourage you, the Bible says do not afraid God is with you, justice is justice.
Dpp will come back into power
man of courage Sammeer
Sulemani mukunena chilungamo, momuopa mulungu koma mulungu apange zoteka kuti bomali lichoke chilungamo chioneke
Mighty DPP my Vote
Good boy big man 💪💪❤
MCP musamasewele ndi katundu waboma pangolini musiye sameer Suleman simungamake pa iyeyu.
May Allah bless u Mr suleiman ❤❤
Mr sulemani pliz dzusaninso anzanu ku parliament mukhaleko kagulu anthu olimba mtima ngati Inu pliz mwina nkuliphula dzikoli pa moto
I like this boss
Kunkuyu peleka black box
Following keep it up
sulemani big up osatopa osafoka🔥🔥🔥
Bwana sulemani chonde maganizo abwino musazasinthe
Bwana bigup inu mumakwana
DPP nayo analindizofooka zake and some of the challenges we're currently facing ......akungopitilra kuchokera ku ulamuliro wa Dpp. MCP ndiye ikungotimaliza basi.Mcp and Dpp nonse ndiamodzi.
NTSB imangofufuza za ndege zomwe zinapangidwa ku USA koma zopangidwa ku Germany ali ndi bungwe lawolawo lotchedwa Bundesamt für Verkehrswesen (BAV), which is responsible for investigating transportation accidents in Germany.
Koma mcp ambuye please kumene kuliko please please please ife akapolo anu simungaawatenge agaru amenewa
Suleman tizikupemphererani mufike mu September mulungu akudalitseni
Am not a journalist koma i think the interviewer needs not to take sides. Let him ask questions oyankhayo aziyankha not being directive
Ndipo live
❤❤❤❤❤you are blessed sir
Zoona ine pay slip yanga yochititsa manyazi😂😂😂 mdulidwe too much. Koma nthawi ya APM ndinalibe ngongore ine😢😢
A MCP akudana ndi makaladi , amiya anali nkaladi chilima komaso akuluwa awawa akufuna atsale okuda ngati makarawa
Mwazi onela Nokia mupange chothekela mutengenso Boma kuti muzawamange anthu amenewa
Mcp ikuyenenayo singafane nd DPP wava awa ationesa zosaona chikangawa party iweyo ngt ukufuna mcp uziikonda
❤❤
Anakwilira pa malopo inquiry ilimkati bwanji komatu MCP guyz Chaka chino chilungamo tichipeza ndithuuuuhh
❤❤❤Sureman
Big brain
Suleiman stop saying you can die for Malawians...this is an insult
Under APM the headlines were the same. Mr. Suleman corruption was just as bad, tizi pewa bwanji?
Ambuye mutetezeni Suleiman
Suleman tsogolo lako likuonekera ,si iwe Nankhumwa ai .iwe udxathandixa anthu Dxiko la Malawi tikudxiwa.
Komanso 4.5m high ndege kuphwanyika chonchija. Atenga nzeru zaku Zimbabwe. Nthawi yachisankho zinali choncho ku Zimbabwe. Amagwiritsa ntchito a intelligence kuti adziopseza anthu.
😂😂😂 Chakwera Ndi Mnangagwa kale
I love this my brother Allah bless him ❤❤❤
DPP inalibe transparency, zinthu mumafufuta ndi tipex, tipex adakuyalutsani agalu inu
Chakwela ndi mbuli yophudzira yosaziwa mayendesedwe adziko
Pangolin wathu
Malawi is going back to the dark 🌑 days
Forward with Dpp
Tikamupatsa 5 years dzina tonse titha 😂😂😂 chikangawa achoke
Kumalawi kwadzala zitsilu zokhazokha pa ndale.mumangokhala ndi ma propaganda auchitsilu.inutu simudzalowaso m'boma.dpp idawononga dziko lelo mudati mukoza dziko ,zitsilu inu .😅
Bomali Lili ndi mavuto oti likonze koma bomali silikadakwanitsa kuchita control shock yomwe malemu Chilima adachita go through, when the plane was out of control. Akulu akulu tisamalankhule za maganizo chabe, it doesn't matter how young and energetic we are, akulu akulu ngozi ya ndege simasewera, chinthu chija chimathamanga, imagine accident ya galimoto pa top speed ya convoy ya president, how much possible damage. Ndiye ndegetu imathamanga speed yoposa 400 to 600 km/ h, imagine At 400, and fall down from air,
Suleman ulibe umunthu, alubino wasowa kotenga, nthawi imene ija alubino mumachita kusaka in various homes, nanga anjinga za moto mumaundila kwa biwi, ziwalo mumapita nazo kuti?
Pangolin umakwana samil
I just luv the program but am finding some difficulties with person wearing a shirt.Am failing to call him a journalist because he is lacking journalism skills, otherwise he can do better.
Talking about Sameer,he is a man of integrity and I do respect him alot. Viva Malawi 🔥🔥
Ndine ntchewa koma ngoz za kuchikangawa Aliyese sakusangalala nayo mpaka panopa. Ndine wakulilongwe koma ndikuopa mulungu tabwelesan black box anthu akukhulupililan koma apart from that aaaaq M.C.P wakupha
Nde kupanda nzeru kumeneko anyamatawa nde mesa akukunyeressni manyi thumba lachimanga pano 60 nde pamtumbo pamenepo
Suleiman ndi Chilima 2
Ee zafika pamenepa mpakana 😢
Suleman wants to seek punlic sympathy. Za ziiiiiii
Nice you are recognizing munthu amakhala mu shock muchitsanzo chanu chomwe, nanga munthu wakuti ndege ikugwa, angakhale ndishock yanji?
Aportuguese aku Mozambique othawa nkhondo panyelo pamanu, & peter mathanyula mboli yamake muiwale zodzaphaso ma albino mmalawi muno dzimachende dzanu
😂😂😂 ma phuzo amenewa bwanji malume
@ amalawi ndife anthu opusa kwambiri kumalola anthu awa othawa nkhondo ku Mozambique adzitiyambanitsa tidzimenyana ngati mmene kulili kwawo panopa
Suziwa chomene ukunena
@@HamuzahRoben pakamwa pozolowera kutukwana, sangathe kuyankhula mopanda kutukwana 😂🤣
@@EdwardPatel-f1g eeee muli kutukwana kuposa zimayitu🤣🤣
Akulu awawa ndi Dolo hv amaziwa zochita pathawi yake
My hon Mp
Tikufuna athu ngat inu
You are out hope Mr Soleman
Aaaaa Inu musakhale gt abwino apa inu kupha mwapha anthu agt zaxzzzzz alibino anja amaphedwa daire zopusa eti
Munkapha ndinu musanamepo why simunamangeko muthu after mutawina😢😅😂😂😂Bakha
Ana ake atiwo
Iweyo 😂
Mulungu akutetezan mwin kulenga ozaopa komaso palibe wamuyaya ukamafunila zako zaifa ndipamene amamuonjezela mansiku amoyo
Ka midiya aka chazeru palibe ofusa manyaka
Wopembeza mafuno wopembeza pitala not mulungu
Malawi athu ngati awa sachedwa kuphedwa
Sule iweeee
Walowa mumalo mwa chilima iwe basi
DPP wa m'boma chaka chake ndi chino akane akane alole alole
Awawa mzeru alibe malo mowawuza anthu zoti muzapange
Iyi si program ya kampeni,. Anu nde mukufuna akambe zomwe apange bwanji.. tazingogwirani maganyuwo
@EdwardPatel-f1g iweyo nde upanga chani chifukwa ifeyo ndi dairy ku ganyu kupanga mchele awawaso akupanga mchele wawo chifukwa chake akukamba za anthu ena kkkkk
mbambande
Eeeee guys mumakwana