KAPENA AMFUMUWA ATUMIDWA? NANGA BWANJI AKUCHITA KULANKHULA NGATI ALI NDI UMBONI ONSE? KU MCP - DOWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 27 сен 2024
  • KAPENA AMFUMUWA ATUMIDWA? NANGA BWANJI AKUCHITA KULANKHULA NGATI ALI NDI UMBONI ONSE? KU MCP - DOWA
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Комментарии • 39

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 5 часов назад +2

    Koma a chewa ndi mbuzi ndipo saziwa kanthu

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 5 часов назад +1

    Anangozindikila atatenga boma asakudziwa chilichose palibe chazeru akuchita 2025 out of boma anthu okupha inu

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 5 часов назад +1

    Kodi malo ndi okhawo ochititsa msonkhano. Kunonso ku Zomba kwa William ndi ku Chikwawa akuwafuna adzachititse msonkhano. Dowa yokha simungawine nayo.

  • @AfricaGxokwe
    @AfricaGxokwe 5 часов назад +1

    Galu wakoyo or utatani sangawineso ameneyo chi kangawayo mbuzi yamundu ndiposo ukamuuze Kuti chikangawa mboloyake yosadulayo

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 5 часов назад +1

    Kodi Dowa ndi kwa nyau kuja?Amfumu chitukuko chanji chomwe mukuyamikira kenakonso kakamba mavuto osaneneka?

  • @amosmuluwane4182
    @amosmuluwane4182 5 часов назад +1

    Ndiye kusagwila mutu Kwa afumu ndikumeneku akuti boma liwapase chakudya njala yawavuta tikamati boma la MCP ndilolephela tikunena zanjalayi silikuchitapo kanthu inetu ndimati kudowa mukukhuta

  • @chrisluke3555
    @chrisluke3555 5 часов назад +1

    Afumu kuyamikira konseko anthu awonso akuvutika ndi njara?kopandaso chipatara chaboma aaaa

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 5 часов назад +1

    Agalu awa azasinthe kaye tambala wokudayo nthawi imeneyo amayika tambala wokuda anali ndithandauzo akadali mtulo kkkk

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 5 часов назад +1

    Amangonva kuti anagwetsa ndege aja ndiati lelo awaona ndithudi ndamenewo

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x 5 часов назад +1

    Kusayenda inu kuli miseu ndi kuti kupatula lilongwe

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 5 часов назад +1

    Ndende is waiting for you, take care

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 5 часов назад +1

    Vote Dpp

  • @YasinSabili-dj9xe
    @YasinSabili-dj9xe 5 часов назад +1

    Vote dpp

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 4 часа назад

    Kamfumu kopusa anthu njala ikukuphani mudandaulanso njala bwanji popeza chakwera deliver fotsek

  • @LawrenceDickens-jk3zx
    @LawrenceDickens-jk3zx Час назад

    Amfumu 😂😂😂koma iweeee!!!!!!😘chikangawa yomweyo😅😅😅😅

  • @ShaffieKaisi-r5v
    @ShaffieKaisi-r5v 4 часа назад

    Mulilongwe misewu zigamba zokha zokha akukonzad misewu osanamizana😂

  • @GABRIELNGWENA
    @GABRIELNGWENA 5 часов назад +1

    Inu mwaiwala malubino mumapha aja a DPP

    • @GoodsonGeleta
      @GoodsonGeleta 3 часа назад

      Man nkhani yamalubino inkapha ndi mcp kufuna kuyipitsa dpp. Ngt inali dilu yaphindu kupha alubino ngakhale anthu aliku opposition akanakhalabe akupha

  • @LytonMabedi
    @LytonMabedi 2 часа назад

    Ngat kuli chitukuko bwanji akupempha zinthu? Mfumu yoima mutu

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 3 часа назад

    Being mfumu simukuyenera kupereka direction kwa anthu chifukwa ndinu mfumu.

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 5 часов назад

    Amalawi zinthu ngati zakwera tivimereze basi zakwera nafe tipemphe malipiro akwere and amabusiness muziika konko basi

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 5 часов назад

    Ndiye ukunenera chani zanjala?si kusagwira mutuko ndikumeneko.kumtumbo kwanu inu amfumu.

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 5 часов назад

    Ntchito zimene akugwira zopha anthu.

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 5 часов назад

    Ntchito zimene akugwira zopha anthu.

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 5 часов назад

    Very shameful! Mfumu into active politics

  • @RoseMsonkhoMalele
    @RoseMsonkhoMalele 3 часа назад

    Boma lake liti, anthu a mcp mitu yao sigwila

  • @Manganiphiri-ul1pq
    @Manganiphiri-ul1pq 5 часов назад

    Mafumu opanda fundo ngati awa kumangowadula mutu

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 4 часа назад

    More fire afumu machende anu😂

  • @MariaNyamwera
    @MariaNyamwera 5 часов назад

    Ma bodza okhaokha zauchitsiru

  • @AfricaGxokwe
    @AfricaGxokwe 5 часов назад

    Galu iwe choka apa mfumu iwe

  • @Malekano-k3x
    @Malekano-k3x 4 часа назад

    Machende ako mfumu iwe

  • @FelixScot
    @FelixScot 3 часа назад

    Afumu opanda fundo ndi awo

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 5 часов назад

    Mzankutu ukuyankhula zazii

  • @TimothyNkhutembaChirwa
    @TimothyNkhutembaChirwa 5 часов назад

    Ndinu zisilu A mcp

  • @JoasLevison
    @JoasLevison 3 часа назад

    Zosautsa kwabasi

  • @JhadahLeafs
    @JhadahLeafs 4 часа назад

    Anamapwala

  • @MillicaBanda
    @MillicaBanda 5 часов назад

    Zaziiii

  • @JoelNseu
    @JoelNseu 5 часов назад +1

    Kodi Mesa uyu mmati Dan lu akuti boma la chitukuko ,
    Chikangawa basi

  • @PreciousDzonzie
    @PreciousDzonzie 5 часов назад +1

    Boma ndilomweli❤❤❤❤❤