BRIAN BANDA KUCHEZA NDI NAMALOMBA NDI CHIHANA KU KOMVESHONI YA CHIPANI CHA AFORD PA 13 SEPT

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 ноя 2024

Комментарии • 81

  • @DerlinNyirenda
    @DerlinNyirenda Месяц назад

    Hard working people in Malawi have bought vehicles and moto cycles this year than ever in the history of Malawi

  • @ChimwemweKaonga-k5i
    @ChimwemweKaonga-k5i Месяц назад

    Malawi tiyeni tidzuke. Osatengera wakwathu wakwathu, tiyeni tiyengere fundo, that's my point

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Месяц назад +1

    Inde tonse ndife amalawi kugwirara ntchito limodzi ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️

  • @allanstanley8533
    @allanstanley8533 Месяц назад

    amakwana

  • @SandikondaIsaac
    @SandikondaIsaac Месяц назад

    We need nsima ndindalama mnthumba

  • @RicePaul
    @RicePaul Месяц назад +2

    Brian Banda well done

  • @SandikondaIsaac
    @SandikondaIsaac Месяц назад

    Gwirizano uwu uphulitsa 80 plus

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Месяц назад +3

    Andale si athu omavutika awa akawinamo basi akaiwala zimene akunenazo chimene chikufunika UTM ilowe boma osatiso DPP ayi

  • @DumisaniMhango-e4i
    @DumisaniMhango-e4i Месяц назад

    A mcp sakuiziwa north

  • @Cammie921
    @Cammie921 Месяц назад

    Brian Banda , don’t interrupt the lady she was talking before you , be professional!!!

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 Месяц назад +1

    ❤❤

  • @Okalekale
    @Okalekale Месяц назад

    Zipani zonse zomwe zinatuluka m'boma m'malo mogwilira ntchito a Malawi ndi za mbava,anthu adyera,akufuna kukaba okha pogwilitsa ntchito imfa ya Chilima.Mpata okuba analibe.Ndale za umbuli,Malawi sadzatukukanso.

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns Месяц назад +10

    I have nothing but to love ku zipani izi; DPP, UDF, AFORD, UTM & LEF❤ I hope if you will come together and have a strong round table discussion zikhoza kupindulira aMalawi from Chitipa to Nsanje

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Месяц назад

    Ngwilidzano ndiye ndiofunikira kwambiri cholinga mfitizi zisale zokha ndipo azayaluka osati maswera ai

  • @WilliamGama-w8m
    @WilliamGama-w8m Месяц назад +3

    Bola zipani za kumabanjazo kusiyana ndi chipani Cha mtumduchi

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Месяц назад +6

    Mugwirizane za mphamvu nose azipani zotsutsa, tikufuna chikangawa achoke 2025

  • @bandachawanangwa6437
    @bandachawanangwa6437 Месяц назад

    Uthenga wanga kwa atsogoleri azipani nonse. Siyani ndale ndi kulimbikitsa chitukuko. Mumatiuza kuti ndale sitidya nanga mumachitiranjibndale? Mudziwe kuti si zonse zomwe amachita azungu nzoyenera ku Malawi. Dziko lino kunena moona mtima silikusoweka zipani zomwe zimangolimbikitsa kugawikana kwathu. Ufulu kuti tikhale nawo siusoweka anthufe kugawikana mmagulu wokanganakangana omwe amangolimbikitsa tsankho, katangale, mikangano, kukondera , kuononga ndalama zimene zikanathandiza kutukula fziko lino. Tangoganizani ndalama zomwe mwaononga mmaconvention mwanu zikanathandiza chitukuko.
    Ine ndikuganiza kuti mukanatisiya aMalawi tikhale mmene mmene tilili ogwirizsna ndipo inu ofuna utsogoleri muzimasuka kubwera kwa ife kumatambasula mfundo zanu momwe mukuchitiramu kuti ife tikhale ndi ufulu wosankha mumodzi wa inu kuti atitsogolere. Koma mumvetse ichi kuti kutigawana mukuchitaku sindidemocracy. Pansi pamitima yanu mukudziwa kuti mukungosewera ndale.
    Kutsimikizira zomwe ndikunenazi, mumatiuza kuti pali inu andale ndi omenyera ufulu. Zinthu ziwirizi mumazipatula bwino bwino. Omenyera ufulu akamasiya mbali yake mumanenanso bwanji osangoyamba ndale. Malawi pazinthu ziwirizi akuna ufulu osati ndale limene kuMalawi kuno lawonetsa kuti ndi bodza, tsankho, kusasunga mapangano, kukondera, kugawana zigawo ndi mitundu. Mukamalimbikira zipanizi mMalawi simudzakhala mtendere. Ngati pano mukufuna mgwirizano wazipani bwanji osangothetsa zipanizo ndikungotiuza mfundo zanu kuti ife tisankhe chimodzimodzi ku constituency, ndi ku ma ward? Tanthauzo la democracy ndiulamuliro wa anthu ambiri ndi ufulu osankha ndi kuyankhula maganizo ake Munthu ndipo izi sizikusoweka chipani!

  • @DanielNamate
    @DanielNamate Месяц назад

    DPP singazabwerereso m,boma kwawo ku atha. Nayoso ARFOD mkachipani ka mthumba palibe chamzeru

  • @SandikondaIsaac
    @SandikondaIsaac Месяц назад

    Yeremia munthu mmodzi wachilungamo

  • @charleskhomolina2385
    @charleskhomolina2385 Месяц назад +3

    ndazikonda kwabas

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga Месяц назад +8

    Zosangalasa 💪💪💪🇲🇼

  • @AngelaMphinji
    @AngelaMphinji Месяц назад +3

    Dpp. Aford. UDF. Alliance yamphanvu!!!! Boma. 2025!!!!!

  • @DicksonLester-q7r
    @DicksonLester-q7r Месяц назад

    Mbambande namalomba

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Месяц назад

    Munakakhala ena anthu inu munakati ndi mmene zilimu tipange zoti UTM itsogore enanu mubwele mbuyo kuti Nkhani ya Infa ya chilima izafufuzodwe bwino anthu azamangodwe basi

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wx Месяц назад +7

    Zipani zonse zosusa timakukondani pangani chothekera achoke awawa malawi chikangawa party

  • @SurprisedDarts-di6fs
    @SurprisedDarts-di6fs Месяц назад +1

    APM vote

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 Месяц назад +1

    AMAFUNA CHILUNGAMO TIMAWANYADILA ANTHU AMENEWA

  • @JamesKapito-c9v
    @JamesKapito-c9v Месяц назад +2

    Moto kuti buuu wina alira

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Месяц назад +2

    Koma kugotuluka mcp 2025. Zozabweleso boma ndye iiwale

    • @SaidSamuden
      @SaidSamuden Месяц назад

      Ndipo zoona kungotuluka nmoba zathapo basi

  • @mphatsofost
    @mphatsofost Месяц назад

    Zinazi zakuntundu

  • @InnocentNkhonyo-rs9lq
    @InnocentNkhonyo-rs9lq Месяц назад +1

    Please communicate for the betterment of your people you are presenting

  • @Yona-w1y
    @Yona-w1y Месяц назад +6

    Zilibwino chikangawa achokebasi

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q Месяц назад +4

    Ndipo times eeeeish

  • @YusufuYunusuSavielMakey
    @YusufuYunusuSavielMakey Месяц назад +1

    Zabwino zonse

  • @JamesBanda-r3u
    @JamesBanda-r3u Месяц назад

    Good relationship bonivoyage

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Месяц назад

    ❤ bola osadza sakha m'ntundu polamula ngati momwe zikuwonekeramu 🙏🙏🙏🙏🙏

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba Месяц назад

    AFORD MP 1, next year 0

    • @Innocent-q3m
      @Innocent-q3m Месяц назад

      Afford has two MP(Chihana & Mzimba East MP)

  • @VincentLudovikombewe
    @VincentLudovikombewe Месяц назад

    Koma guys mumatha kkkkk

  • @wassiematula-fp9hq
    @wassiematula-fp9hq Месяц назад

    Koma ngakhale mumapempha simulandira, chifukwa mumapempha ndi zolinga zoyipa. Mumapempha kuti muzigwiritse ntchito pa zokusangalatsani nokha.
    Yakobo 4:3

  • @ElifalaThole
    @ElifalaThole Месяц назад

    Tiwaonela kumapeto kwake😮

  • @MiracleDamiano
    @MiracleDamiano Месяц назад

    Zonyaditsa zedi pitilizan mgwirizano wanu ndthu mpaka uyu kamuenda njirayi achoke

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Месяц назад

    Umayamba kumkonda usanafunsire 😂😂😂😂😂😂

  • @ChikutaEmmanuel
    @ChikutaEmmanuel Месяц назад +1

    Maganizo anga ngakut achihana kuphatikiza amutharika aaaaa zomwe adapanga 2019 mene idanyozekera DPP rero mkumat akupanga ubare zikuonetseratu kut andare ose ngakuba amangofuna kutipusitsa

  • @floncejeche8647
    @floncejeche8647 Месяц назад

    Zawonesa kale kuti akondana awiliwo

  • @AugustineChimaliro-e5i
    @AugustineChimaliro-e5i Месяц назад

    Zabwino zotse

  • @JustinLipipa
    @JustinLipipa Месяц назад

    Aaaaa wakumpingo bac na alliance iyi mmmmmm

  • @MatolaAbdullah
    @MatolaAbdullah Месяц назад

    Namalomba😂

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h Месяц назад

    😂😂😂😂 mkadzi ndiokondedwa

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings Месяц назад +1

    All those companies are failer

  • @franciskapakasa36
    @franciskapakasa36 Месяц назад

    These are thieves, people who just want to get to rich themselves , and ma reporter inuyo mukulemerera momwemo ,God is watching you will fail no matter what.

  • @AmosShadreck
    @AmosShadreck Месяц назад

    Nthawi mkachisilu 😅 it was like this past 4 years.

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings Месяц назад +1

    Zipani za family zikukumana chipani Cha abambo chipani Cha akulu anga kkk😂😂😂 or those are not parties are companies their can not rule Malawi

    • @JustinLipipa
      @JustinLipipa Месяц назад

      If this work out mmmmmm wakukasiya Basi kukayamba ma overnight prayers 😂😂😂😂

  • @BlessingsMarley-l2x
    @BlessingsMarley-l2x Месяц назад

    Zonyadisa ndithu Dpp Vs Afford

  • @PETERBENSON-h8d
    @PETERBENSON-h8d Месяц назад

    Mumakwana a times

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick Месяц назад

    Apa C

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 Месяц назад

    Chikangawa apite wawononga dziko,ndalama wagwesa wagwesaso, chifukwa chogwesela ndalama sichikuziwika

    • @Okalekale
      @Okalekale Месяц назад

      Mbuli sudziwa m'mene limayendera boma,chifukwa cha anthu ngati inu Malawi siyidzapezanso munthu ngati Bingu or Kamuzu,m'mangnamizidwa ndi mbavazi,wake up!.
      Chikangawa Chikangawa chani?,iwe ukaonetaeysa pamene paja MCP inapha anthu aja?,okay ngati anawapha bwanji mukufunanso okhupha ena a DPP?.DPP,UDF ndi zipani zokuphatu inu simudziwa?,bola mutati mukufuna UTM

  • @AbrahamLLoyd-xb2xc
    @AbrahamLLoyd-xb2xc Месяц назад

    Wabwino zonse

  • @Aubreysekeyah
    @Aubreysekeyah Месяц назад

    Kod pdp bwanji sakuiitana kpn ilikuchikangawa

  • @LuciusScott-h7b
    @LuciusScott-h7b Месяц назад +1

    Zosangalasa Mr chinaha

  • @AndreaKadzola
    @AndreaKadzola Месяц назад +2

    Zipani zolephera izi

    • @MiracleDamiano
      @MiracleDamiano Месяц назад

      Mmutu mozaza manyimo galu iwe komas olephera nd chakwera wakoyo kupusa kwako 🚮🚮😏

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile Месяц назад

    Timasanje tatizipani zazii mpaka afford kupanga convetion for what ,angawine koma shaaa Malawi walero

  • @KumbukaniLloydChokotho
    @KumbukaniLloydChokotho Месяц назад

    The problem with Malawian politician they do things out out anger without thinking of the future mcp& utm inapanga alliance nothing worked so aford sikufuna kutenga phunziro akufuna kupanga alliance ndi Dpp kungofuna kuchotsa Mcp osati kufuna kupanga contribute to the growth of country's economy koma I can assure you this marriage will never work these are greedy parties

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  Месяц назад

      Definetely, I agree with you

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 Месяц назад

    Zikuchitat kubeba